Breaking: Malawi Opposition members arrested for treason: Ulemu Msungama detained, Kabwila still on the run

Advertisement
Ulemu Msungama
Ulemu Msungama
Msungama facing treason charges

One of the senior member of the opposition Malawi Congress Party, Ulemu Msungama, has been arrested and is currently detained at Kanengo Police Station.

Ulemu Msungama posted on his facebook earlier without clarifying  that he was at Area 30 Police station.

A source very close to Mr. Msungama confirmed Msungama’s arrest.

Msungama is reportedly facing sedition and treason charges over a WhatsApp thread in which people expressed dismay over President Peter Mutharika’s governance on the face of a the current economic crisis. It is claimed people on the thread included Jessie Kabwila, Ulemu Msungama and MCP’s legal adviser and parliamentarian, Peter Louis Chakhwantha. The whereabouts of the other two MCP members remain a mystery.

Msungama is however the first to be arrested following claims by a pro-government news publication that MCP was working with the US government to oust President Mutharika. The US ambassador, Virginia Palmer, downplayed the claims as false.

MCP deputy spokesperson Ezekiel Chin’goma also confirmed Msungama’s arrest, saying he has been charged with treason.

Before Msungama’s arrest, armed police officers stormed the residence belonging to Malawi Congress Party (MCP) spokesperson Jessie Kabwila.

Her mother, Valesha Kabwila, confirmed what she described as terrifying scenario. However, the MCP spokesperson who had asked President Mutharika to resign during a Public Affairs Committee stakeholders’ conference was not at the house.

Parliamentarian for Dedza East, Juliana Lunguzi, expressed dismay at the developments. She also confirmed that Msungma has been charged with treason.

The Malawi Police and government spokesperson were yet to comment on the arrests and charges against Msungama and the other two MCP parliamentarians.

Advertisement

346 Comments

 1. Mukuti South Africa mungayerekeze ndi Malawi? Popeza Johannesburg yokha ndi dziko lonse la Malawi osatinso pa chuma koma kukula chifukwa mu Johannesburg muli mizwanya ya khwidi zokwana twenty seven thousand muchiwerengero cha ma City a chuma mu Africa. Ndiye awa andile treason basi. Ndi malamulo a dziko.

 2. ndipemphe adviser wa ambuye amuthalika kuti adziwathandiza ambuyewa akalamba kwambiri sakudziwa chimene akuchita nanga si anakhalitsa kunja,chifukwa atidye nawo ndi amene akumusokoneza.pepani amalawi anzanga ambuyewa akalamba kwambiri,chaka china tidzasintha malamulo osamaika nkhalamba pa utsogoleli.ngati amene mumamuyandikilanu mutilangizileko chifukwa ku dpp kuli anyamata fresh asukulu yawo osati izi.

 3. ndipemphe adviser wa ambuye amuthalika kuti adziwathandiza ambuyewa akalamba kwambiri sakudziwa chimene akuchita nanga si anakhalitsa kunja,chifukwa atidye nawo ndi amene akumusokoneza.pepani amalawi anzanga ambuyewa akalamba kwambiri,chaka china tidzasintha malamulo osamaika nkhalamba pa utsogoleli.ngati amene mumamuyandikilanu mutilangizileko chifukwa ku dpp kuli anyamata fresh asukulu yawo osati izi.

 4. koma ku Malawi kwathu kuno aaash,,anthu sangangolowa mu utsogoleri asanamangidwepo ayi eeeh,,chiwanda chimenechi oooout!!! pa easy madolo zikatere kumalawi kuno ndekuti atlast utsogoleri ndiwanu mtsogolomu

 5. Onse osokoneza chitetezo amangidwe and pamno Boma ili buzy kuthetsa njala osati kumawasokoneza anthu pa nkhani zosaziwika bwinozi and jasse u are the next target watch out.

 6. Onse osokoneza amangidwe basi and iwe kabwila will be the next target ubwele wekha pano boma lili pa ntchito yaikulu yethesa njala ndiye anthu ena osakonda dziko lanthu azitiopseza ife koma mwalephera basi…………

 7. Kumangova freedom of speech kwathuko kulibe bwampini akufuna u dictator wamkulu wake malemu kukupemphani kuti mutule pasi boma lakukanikani si kuukila manyazi chabe kumayesa ngati amalawi ndi atulo tizipeka msonkho iwe ndikumagula toilet paper yamchigalimoto chako zausilu bola pamenepo ulira mwina ugwaso kamba ka stress

 8. Kumangova freedom of speech kwathuko kulibe bwampini akufuna u dictator wamkulu wake malemu kukupemphani kuti mutule pasi boma lakukanikani si kuukila manyazi chabe kumayesa ngati amalawi ndi atulo tizipeka msonkho iwe ndikumagula toilet paper yamchigalimoto chako zausilu bola pamenepo ulira mwina ugwaso kamba ka stress

 9. Kumangova freedom of speech kwathuko kulibe bwampini akufuna u dictator wamkulu wake malemu kukupemphani kuti mutule pasi boma lakukanikani si kuukila manyazi chabe kumayesa ngati amalawi ndi atulo tizipeka msonkho iwe ndikumagula toilet paper yamchigalimoto chako zausilu bola pamenepo ulira mwina ugwaso kamba ka stress

 10. Kumangova freedom of speech kwathuko kulibe bwampini akufuna u dictator wamkulu wake malemu kukupemphani kuti mutule pasi boma lakukanikani si kuukila manyazi chabe kumayesa ngati amalawi ndi atulo tizipeka msonkho iwe ndikumagula toilet paper yamchigalimoto chako zausilu bola pamenepo ulira mwina ugwaso kamba ka stress

 11. Kumangova freedom of speech kwathuko kulibe bwampini akufuna u dictator wamkulu wake malemu kukupemphani kuti mutule pasi boma lakukanikani si kuukila manyazi chabe kumayesa ngati amalawi ndi atulo tizipeka msonkho iwe ndikumagula toilet paper yamchigalimoto chako zausilu bola pamenepo ulira mwina ugwaso kamba ka stress

 12. Kumangova freedom of speech kwathuko kulibe bwampini akufuna u dictator wamkulu wake malemu kukupemphani kuti mutule pasi boma lakukanikani si kuukila manyazi chabe kumayesa ngati amalawi ndi atulo tizipeka msonkho iwe ndikumagula toilet paper yamchigalimoto chako zausilu bola pamenepo ulira mwina ugwaso kamba ka stress

 13. Stupid government, u dont want to be criticised? How many people are you going to arrest ? Arrest all malawians because they are not happy with your ruling.

 14. mesa tinavomeleza kuti tikhale ndizipani zambili kuti boma likapanga zabwelela azipani ena anenepo son ngati anena kuti boma silikuthandiza alakwisa asiyeni azipani anene mavuto akulakwikao its freedom to speech

 15. mesa tinavomeleza kuti tikhale ndizipani zambili kuti boma likapanga zabwelela azipani ena anenepo son ngati anena kuti boma silikuthandiza alakwisa asiyeni azipani anene mavuto akulakwikao its freedom to speech

 16. Busy Kufuna Kulanda Boma Instead 2 Work Wth The Gvrnmnt Due 2 The Current Situation, Wht Kind Of Politics Is Ths Shame,shame, Malawian Leaders

 17. Busy Kufuna Kulanda Boma Instead 2 Work Wth The Gvrnmnt Due 2 The Current Situation, Wht Kind Of Politics Is Ths Shame,shame, Malawian Leaders

 18. We can’t just do and say as it pleases us. This is Malawi not SA. Njatani onse ofuna kuyambisa chisokonezo. Ngati ali anthu anzeru osapereka mfundo zothandiza bwanji?

 19. S A SIMALAWI KUNO TIMACHITA ZA CHIMALAWI MPHAMVA AZITENGA KWAMAFUMA KOMANSO NJOKA YA MPHILI IMALUMA MODABWESA KWAMBIRI POYAMBA PAJA AKANANENA KUTI OCHITA MOPOSA NDIMANGA SIBWEZI AKUCHITA MOPUSAMU?

 20. anthu ambiri panopa akubvutika ndi njala,anthu ena ofunila anzao zabwino akuesesa kuthandiza anthu ndi kena kali konse ali nako,ndiye anthu ena mmalo moti athandize boma pa nkhani yanjalai,akuyambitsa nkhani zina zoti zingayambise chisokonezo kuonjezela mabvuto ena pa njala pompaja!!andale amenewatu ena ali ndi ma truck,boma likuti lili ndi chimang mma admark,bwanji osatenga ma truck anuo muthandize kunyamula chimanga kukapasa anthu mma admark,mmalo mwake mukufuna muyambitse chisokonezo ku malawi mu dzina la freedom of speech, mukufuna kuthandiza anthu kapena mpando wa president?kuno ndi kumalawi,timamanga aliyense oyambitsa chisokonezo.

 21. anthu ambiri panopa akubvutika ndi njala,anthu ena ofunila anzao zabwino akuesesa kuthandiza anthu ndi kena kali konse ali nako,ndiye anthu ena mmalo moti athandize boma pa nkhani yanjalai,akuyambitsa nkhani zina zoti zingayambise chisokonezo kuonjezela mabvuto ena pa njala pompaja!!andale amenewatu ena ali ndi ma truck,boma likuti lili ndi chimang mma admark,bwanji osatenga ma truck anuo muthandize kunyamula chimanga kukapasa anthu mma admark,mmalo mwake mukufuna muyambitse chisokonezo ku malawi mu dzina la freedom of speech, mukufuna kuthandiza anthu kapena mpando wa president?kuno ndi kumalawi,timamanga aliyense oyambitsa chisokonezo.

 22. Eh apolisi gwirani ntchito yanu ngat munthu walakwisa amangidwe bas dispit nd wa opposition. Makape amenewa akufuna ku user backdoor kut atenge boma, koma akunama!

 23. Ndale zakumalawi zachikale bwanji ndikuthira umboni Haroon SA Mkumene kulindale ine ndimkakanaka ndikuzivelela ndekha komaso kuwonela pa Tv Zuma akunyozedwa nda Opposition

 24. Kuno ku SA, malema saopa pofuna kulankhula in august house evn out ov august house koma samumanga. Nanga kukadakhala kumalawi malema sakadakhala lyf prison?

 25. bE reminded that gov’t.changes think what come of tomorrow ife any hi ndi maso Loma muzitenge being this just the beginning prepared to arrest more

 26. Mmm amalawi anzanga mmexa mmati ng,ombe yayikazi sikoka ngolo nanga bwanji pitala u ndimamuna akulephele kukoka ngolo ine ndili odandaula kwambiri kt boma lithane ndimavuto alinziko muno kma lukanika nde mukama manga anthu nde kt njala itha

 27. IF OUR CONSTITUTION CRIMINALISES TREASON, AND IF WHAT MSUNGAMA SAID IS TANTAMOUNT TO TREASON THEN NKHANI PALIBE APA. LET THE GUY PROVE HIS INNOCENCE.

 28. …….freedom have limits, and malawi have constitution, president under malawi laws have what we call presidential powers….disrespect is not freedom.they deserve treason charges, they want to get into power by back door taking advantage of drought, these kabwiraz will cause unrest to inocent poor nyasas, arrest them all accordingly..! if it fails then hire me i’ll kill them all by throwing them into croc river….

  1. Kutukwana zomwezi?hahahahah mesa mukuti freedom of speech?Nayenso wapanga express ma views ake,if you feel offended by his comment kuli bwino kungodutsa tha u savage kuusiya pa display

  2. Kutukwana zomwezi?hahahahah mesa mukuti freedom of speech?Nayenso wapanga express ma views ake,if you feel offended by his comment kuli bwino kungodutsa tha u savage kuusiya pa display

  3. what sort of unrest are you talking about no food going to bed hungry and you say what come down to the villages people are suffering find solutions to end this and not arrests brother simon

  4. what sort of unrest are you talking about no food going to bed hungry and you say what come down to the villages people are suffering find solutions to end this and not arrests brother simon

  5. what sort of unrest are you talking about no food going to bed hungry and you say what come down to the villages people are suffering find solutions to end this and not arrests brother simon

  6. what sort of unrest are you talking about no food going to bed hungry and you say what come down to the villages people are suffering find solutions to end this and not arrests brother simon

  7. what sort of unrest are you talking about no food going to bed hungry and you say what come down to the villages people are suffering find solutions to end this and not arrests brother simon

  8. what sort of unrest are you talking about no food going to bed hungry and you say what come down to the villages people are suffering find solutions to end this and not arrests brother simon

  9. thank you prisva and you magwira, some pple adaphunzira kudambwe not in class….we are not all happy @ all, we are all suffering and this hunger kills us all but we dnt want to spill blood in my free malawi

  10. thank you prisva and you magwira, some pple adaphunzira kudambwe not in class….we are not all happy @ all, we are all suffering and this hunger kills us all but we dnt want to spill blood in my free malawi

 29. what kind of democracy is this?ambuye aja ndi aja anaphetsa anthu osalakwa ku mpoto inunso mukufuna kuthana ndi aliyense amene akukudzudzulani mukufuna anthu azingowombera ndi zaukape zomwe .koma dziko salamula chifukwa mphamvu ai ambuye mwayenjeza.

 30. what kind of democracy is this?ambuye aja ndi aja anaphetsa anthu osalakwa ku mpoto inunso mukufuna kuthana ndi aliyense amene akukudzudzulani mukufuna anthu azingowombera ndi zaukape zomwe .koma dziko salamula chifukwa mphamvu ai ambuye mwayenjeza.

 31. Im feel sorry for other compidle pipo for their comment mukuona ngati Ku SA kuli ufulu Nyambose anthuwa akuona ngati Joni ayiyamba ndiwo asiye

 32. Kondi mumagansa kuti ndale samalemu begumutalika iyeyu agasiye kodi ifeyo akutitega gati andani awo tikalilasomwezi pakaliti kasimu jafali sasafulika malisimbhek

 33. kodi kumangako mumanga angati ?ndi ndale zaukape zongomangana any how amalawi democracy mukaidziwa liti? kodi nonse life yanu ndi yosadzudzulidwa ?what kind of people are u?

 34. kodi kumangako mumanga angati ?ndi ndale zaukape zongomangana any how amalawi democracy mukaidziwa liti? kodi nonse life yanu ndi yosadzudzulidwa ?what kind of people are u?

 35. Ndichifukwa malawi ali osauka npaka kale athu amaziwa kuti boma limaba chithandizo chochoka maiko akunja koma amalawi kuopa kuyakhula ndichifukwa boma lili lonse likalowa limaba koma zimenezo sintendele muthu akazuzula zingwe cholinga tiziopa mukuzunza wanthu osalakwa

 36. Amalawi Muli Ku Sa Macomment Anu Mumakhala Ngati Uko Kuli Ufulu Theres No Fredom There Why Mumaphedwa Ngati Nkhuku Talk Of Xenophobia Ndee Ufulu?Mzungu Kukunyamula Kumbuyo Kwa Galimoto Kutsogolo Atawika Galu Pa Seat Is That Fredom Osakamba Zimenezo Mwina Mwangofuna Kuti Tiziwe Kuti Muli Ku Sa Kkkk Check This Out

 37. Zinazi osamaziyamba dala . Mabungwe ndi maiko omwe amatithandiza akanva zoti mwayamba kumangana pazifukwa za ndale akuthandizaninso? Mukatero mudziti a Opposition akumakanyelera kuma donors? Bp inatu mukuiputai

 38. Joni ndi joni malawi ndi malawi, ikanakhala mcp itawaphatu amenewa mmene anafera acina, gadama, sangala, matenje ndi ena iiiiiiiiiiii tambalaaaa iiiiiiii watha anthu

 39. Mfumu ina ikugwiritsa mphamvu zake molakwika kwambiri.Koma vuto ndiloti siikudziwa.Kalenso Mfumu DAVIDE inali ndi zonse koma chinachitika ndichiyani;’kutenga mkazi yekhayo wa ULIYA pamapeto pake mkumumpha mwini mkazi .Zotsatira zake inu mukudziwa bwino lomwe.Tisaiwale kuti tonse Mulungu anatilenga mofanana ndipo ndife ofunika kwa iye.

 40. Dziko lathu la Malawi lili ngati momwe zinthu zafikira pano kuli ngati mayiko ena bwenzi Peter atatula pasi udindo koma omwe ali pamavutowo nde kuombera m’manja kuti boma lachita bwino kumanga anthu chifukwa cha Whatsaup group

 41. We will organize the demonstrations soon wina ndine please come and arrest me Peter and Dausi you are still very far with democracy remember Dausi we were together one time at State house and you were not some body now you are busy arresting opposition politians watch out we are coming with the revolution wait

 42. Zawakani kenako kuyaba kumaga a opposition where is freedom of speech .let us wait and see soon Malawi will be like Zimbabwe

 43. Zawakani kenako kuyaba kumaga a opposition where is freedom of speech .let us wait and see soon Malawi will be like Zimbabwe

 44. Autchene unyolowo bas…..d@ freedom ov xprension has got its limit…..sitikutengera zaku SA tunena consititution ya2 ya Mmalawi muno kuchtra ntudzu olamulila nd mlandu ivn pamaso pa Mulungu Romans 13

 45. Autchene unyolowo bas…..d@ freedom ov xprension has got its limit…..sitikutengera zaku SA tunena consititution ya2 ya Mmalawi muno kuchtra ntudzu olamulila nd mlandu ivn pamaso pa Mulungu Romans 13

 46. Autchene unyolowo bas…..d@ freedom ov xprension has got its limit…..sitikutengera zaku SA tunena consititution ya2 ya Mmalawi muno kuchtra ntudzu olamulila nd mlandu ivn pamaso pa Mulungu Romans 13

 47. Political persecution,,typical of malawi politics,,shame on dddiiiiphophiiiii,bt de reality shall still be on de ground,u cant silence de critics,shupiti

 48. Ndale za chikale izi! Ingovomerani kuti kuyendetsa dziko sichithu chapafupi talephera apa. Anthu tikugula madeya kwa Admarc, pangani concentrate mavuto aanthu osakhala izi. Dziko ndi anthu ake!

 49. Ndale za chikale izi! Ingovomerani kuti kuyendetsa dziko sichithu chapafupi talephera apa. Anthu tikugula madeya kwa Admarc, pangani concentrate mavuto aanthu osakhala izi. Dziko ndi anthu ake!

 50. Momwe Zuma wanyozedwera ndi Malema komaso Lekota mu Parliament last week kuno Zuma akumva osati mukuti bwa bwa bwazo nde kutakhala ku Malawi kaya zingatani

 51. Momwe Zuma wanyozedwera ndi Malema komaso Lekota mu Parliament last week kuno Zuma akumva osati mukuti bwa bwa bwazo nde kutakhala ku Malawi kaya zingatani

  1. Boma kuti liyende bwino pazipezeka anthu olitsutsa. Koma mavuto omwe tilinawo ku Malawi munthu akangopanga oppose boma akut akuwukira. what kind of treason r u talking about?

 52. Fortunately, one day he will write some nonses on those walls enveloping him l guess. Not forgetting arresting others as well. I hate the archaic recycling political culture pervading my mother land!

 53. Fortunately, one day he will write some nonses on those walls enveloping him l guess. Not forgetting arresting others as well. I hate the archaic recycling political culture pervading my mother land!

 54. Fortunately, one day he will write some nonses on those walls enveloping him l guess. Not forgetting arresting others as well. I hate the archaic recycling political culture pervading my mother land!

  1. Ndinu zixiru nonsenu I belv kusaphunzira kumene kukupangixani mukungo tukwana without knwng anyting KUPUSA!!!!!!! Tangopitan. Mukasewele ma deal achimanga ku ADMAC mawa muone kusintha “SHUPITI”.

 55. chiyambi chovomereza ndi chimenechi kamuzu ankateronso koma ana akummawa analitenga dzikoliis this democracy? ngati anthu amakukondani musamaope nkhamba kamwa dziko ndi la tonse what goes around comes around think twice before you act

 56. chiyambi chovomereza ndi chimenechi kamuzu ankateronso koma ana akummawa analitenga dzikoliis this democracy? ngati anthu amakukondani musamaope nkhamba kamwa dziko ndi la tonse what goes around comes around think twice before you act

 57. chiyambi chovomereza ndi chimenechi kamuzu ankateronso koma ana akummawa analitenga dzikoliis this democracy? ngati anthu amakukondani musamaope nkhamba kamwa dziko ndi la tonse what goes around comes around think twice before you act

 58. Koma mmene amanyozera Julias Malema kuno ku SA,zitakhala ndale zaku Malawi bwezi tikuti forever kundende. Ndale zomangana nzachikale so where is freedom of speech?

  1. Boma lake liti lomwe angalandelo?a President akungowopa chabe. Akanakhala a Malawi ofuna kulanda boma ndiye akanalanda nthawi yamalemu Bingu coz ndamene adali pampanipani wawukulu.

 59. Koma mmene amanyozera Julias Malema kuno ku SA,zitakhala ndale zaku Malawi bwezi tikuti forever kundende. Ndale zomangana nzachikale so where is freedom of speech?

  1. Boma lake liti lomwe angalandelo?a President akungowopa chabe. Akanakhala a Malawi ofuna kulanda boma ndiye akanalanda nthawi yamalemu Bingu coz ndamene adali pampanipani wawukulu.

 60. Koma mmene amanyozera Julias Malema kuno ku SA,zitakhala ndale zaku Malawi bwezi tikuti forever kundende. Ndale zomangana nzachikale so where is freedom of speech?

  1. Boma lake liti lomwe angalandelo?a President akungowopa chabe. Akanakhala a Malawi ofuna kulanda boma ndiye akanalanda nthawi yamalemu Bingu coz ndamene adali pampanipani wawukulu.

  2. D@ freedom ov exprension has got its limit amwene ukabyonda umakhala kut ukuphwanyanso ufulu wamun2 wina en yu suffer e consquences nde ndizo amanga dis iz MW nat SA

  3. D@ freedom ov exprension has got its limit amwene ukabyonda umakhala kut ukuphwanyanso ufulu wamun2 wina en yu suffer e consquences nde ndizo amanga dis iz MW nat SA

  4. D@ freedom ov exprension has got its limit amwene ukabyonda umakhala kut ukuphwanyanso ufulu wamun2 wina en yu suffer e consquences nde ndizo amanga dis iz MW nat SA

  5. Ndiye kumanga ndi solution yoti anthuwo angasiye kutsutsana ndi mtsogoleri? just imagine time of late Bingu anthu ankamangidwa but amapitilizabe kunyoza mpaka pomwe anamwalilira. Ndiye asaganize kuwamanga ndiye chida chothesera kunyozedwa kwawo but it will be increasing

  6. Ndiye kumanga ndi solution yoti anthuwo angasiye kutsutsana ndi mtsogoleri? just imagine time of late Bingu anthu ankamangidwa but amapitilizabe kunyoza mpaka pomwe anamwalilira. Ndiye asaganize kuwamanga ndiye chida chothesera kunyozedwa kwawo but it will be increasing

  7. Ndiye kumanga ndi solution yoti anthuwo angasiye kutsutsana ndi mtsogoleri? just imagine time of late Bingu anthu ankamangidwa but amapitilizabe kunyoza mpaka pomwe anamwalilira. Ndiye asaganize kuwamanga ndiye chida chothesera kunyozedwa kwawo but it will be increasing

  8. Kodi freedom of expression imatathauza kutukwana kapena kunyozamunthu? M’mesa imatanthauza kuyankhula zakukhosi mosaopa komanso mosanyozawina?

  9. #Adam,differenciate btween treason case and freedom of expression den u wll come up with a conclusion.osamangothandiza amfumu kuledzera

  10. Kutukwana Its Been Predudess Even Mwana Pakhomo Amamenyedwa Akatukwana How Much More Kutukwana Presedent Uko Ku Sa Kulibe Ulemu Thats Why Amakuphani Ngati Nkhuku Inu Amalawi And Then Nkumayamikila Kuno Kuli Ufulu Iyambeso Mwina Xenophobia?Iwe Usamaletu

  11. Oro atatukwana sindikuonapo vuto kapena kuti wina akudwala kapena ali mwakayakaya chifukwa choti wanyozedwa or watukwanidwa. Mmidzimo timatukwanizana or kunyozana koma sitimangitsana. Koma wamatsayagwidi uyu wasowa chochita ndithu.

  12. @ Chifundo don’t mock urself,link ndasegula ndipo zomwe wamagwidwira ndizokhuza ufulu wake wolankhula. Treason singabwere without expressing chinachake. Apresdent akungo opa chaba but nobody can oust him paudindo

  13. Iwe Nyambose,tazingovutitsana ndi Pitala wakoyo. Ife tikungomvera pa news mmene akukuvutitsirani bwanamkubwa wakoyo. Anthu wopanda chitukuko ngani inu,munthu kupeza njira yothesera mavuto panyasaland mukut akuwukira boma. Mudzafa ngati nkhuku zachitopa

  14. A Malawi anazolowera kuponderezedwa,wina akalimba mtima kulankhula akuti kuwukira,koma azingosekelera ndizachibwana zomwe. Tidzakhala tikulira mpaka liti?

  15. Ufulu wanji womwe akumu phwanyila but people must suffer in the country. Anthu omwewa ndi amene anamuyika pawu president.he is wrong he is wrong no matter he is state of the nation.ulemu timamupasa kale more than else.

  16. southafrica yake iti malema mudamvapo akuti akufuna kulanda boma mwa upandu.kusouthafrica sadamange prince oka wakunigeria chifukwa chofuna kulanda ndiko lakwao through phone calls?pano siuyo aku saver 25 yrs komweko.maphonewa kumasamala nawo ngakhale iwo amadziwa kuti ndi mlandu thats why mukukambilana kwawo atchulamo treason.

  17. A President akungowopa chabe,palibe amene angalande boma ku Malawi. Kungot political issues sometime we can not understand,nthawi yomwe idali yoyenelera kulanda boma ndi nthawi ya first Bingu coz it was only time yomwe amalawi anali ovuta kwambiri. Ngat zidalepheleka 4 that time I don’t think kut panopa pangalandidwe boma

  18. Iwe Fynes nthawi yomwe Zuma amakakamizidwa kut apange resign udindo unamva kut winawake wamangidwa ndi treason. Coz boma limadziwa kut imeneyo ndimbali imodzi yakudandawula kwa anthu. Ndiye look on what happening dziko lathu chikumanile a PAC how many pple arrested?

 61. Malawi opposition will never help us instead of working with the government in this darkest hour to help us the starving citizens they are busy ploting a coup, if you work with Mutharika hand in hand it will help in some way to reduce these problems, wake up please do civilised politics put the interest of average Malawians at heart

 62. Malawi opposition will never help us instead of working with the government in this darkest hour to help us the starving citizens they are busy ploting a coup, if you work with Mutharika hand in hand it will help in some way to reduce these problems, wake up please do civilised politics put the interest of average Malawians at heart

 63. Malawi opposition will never help us instead of working with the government in this darkest hour to help us the starving citizens they are busy ploting a coup, if you work with Mutharika hand in hand it will help in some way to reduce these problems, wake up please do civilised politics put the interest of average Malawians at heart

 64. Kumpando,,,,stdya ndale pliz!ananetu agogo aja,,,”muzavutka”makan.pano justce inatha but ikulamulano nd dolla.komano tlowele kuti amalawi kwathu komwe kawawa iiih koma eeee

 65. Kumpando,,,,stdya ndale pliz!ananetu agogo aja,,,”muzavutka”makan.pano justce inatha but ikulamulano nd dolla.komano tlowele kuti amalawi kwathu komwe kawawa iiih koma eeee

 66. Kumpando,,,,stdya ndale pliz!ananetu agogo aja,,,”muzavutka”makan.pano justce inatha but ikulamulano nd dolla.komano tlowele kuti amalawi kwathu komwe kawawa iiih koma eeee

 67. Nanu a MCP malo moti muzipeleka fundo zoti tingapange bwanji kuti tithane ndi mavutowa muli buzy kulimbana ndi DPP. Nde anthu aika bwanji chikhulupiliro mwainu kuti muzasintha zinthu mukazalowa m’boma.Tikufuna fundo zothandiza osati kumalimbana ndi zinthu zaziii

 68. Nanu a MCP malo moti muzipeleka fundo zoti tingapange bwanji kuti tithane ndi mavutowa muli buzy kulimbana ndi DPP. Nde anthu aika bwanji chikhulupiliro mwainu kuti muzasintha zinthu mukazalowa m’boma.Tikufuna fundo zothandiza osati kumalimbana ndi zinthu zaziii

 69. Nanu a MCP malo moti muzipeleka fundo zoti tingapange bwanji kuti tithane ndi mavutowa muli buzy kulimbana ndi DPP. Nde anthu aika bwanji chikhulupiliro mwainu kuti muzasintha zinthu mukazalowa m’boma.Tikufuna fundo zothandiza osati kumalimbana ndi zinthu zaziii

 70. Kkkkk koma kumeneko Jessy mwano onse kutha nde mwati anali pawhatsap wagona kutiko? Focus on malawians who are starving with hunger than this fuck politics

 71. Kkkkk koma kumeneko Jessy mwano onse kutha nde mwati anali pawhatsap wagona kutiko? Focus on malawians who are starving with hunger than this fuck politics

 72. Kkkkk koma kumeneko Jessy mwano onse kutha nde mwati anali pawhatsap wagona kutiko? Focus on malawians who are starving with hunger than this fuck politics

 73. Kkkkk koma kumeneko Jessy mwano onse kutha nde mwati anali pawhatsap wagona kutiko? Focus on malawians who are starving with hunger than this fuck politics

 74. Mmalo moti muzimanga mbava zokuba makobili a boma muli busy kumanga anthu ndicholinga tizikhala ndi mantha, za ziiii!! Mxiiii

 75. Mmalo moti muzimanga mbava zokuba makobili a boma muli busy kumanga anthu ndicholinga tizikhala ndi mantha, za ziiii!! Mxiiii

 76. Mmalo moti muzimanga mbava zokuba makobili a boma muli busy kumanga anthu ndicholinga tizikhala ndi mantha, za ziiii!! Mxiiii

 77. Mmalo moti muzimanga mbava zokuba makobili a boma muli busy kumanga anthu ndicholinga tizikhala ndi mantha, za ziiii!! Mxiiii

Comments are closed.