Official: Sulumba seal Bullets deal

Advertisement
Muhammad Sulumba
Muhammad Sulumba
Sulumba: Now a Bullets player.

Former Blantyre United forward who was on loan at Mighty Wanderers Muhamad Sulumba has joined rivals Big Bullets.

Sulumba signed a pre contract with the peoples team a week ago but his move was put on hold following Wanderers’s resilient to allow him join a rival team. However, the forward has officially signed for Bullets on Wednesday.

Malawi24 has established that Nomads’ trustee Rashid Gaffar did everything in his power to stop the giant striker from joining Bullets but the player made it clear that his hear was at Bullets.

The forward had entered into the last six months of his contract with Blantyre United which allowed him to open negotiations elsewhere, and in turn signed a pre-contract with the league champions.

Bullets are also in talks with Civo Service United for the services of defensive duo of John Lanjesi and Emmanuel Zoya and according to information at hand, the two parties are set to hold final discussions over the weekend.

Advertisement

216 Comments

 1. A Sam munasula ndani anakathera ku Bullets maboza basi musamapange mosenphanitsa ngati mulibe coment zililani mukugona ok.

 2. While neba was busy kutokota bullets were busy underground making sure sulumbas deal is finalised.But in case neba sukuwona patali..Chitakuphetu in the next season is goalkeeping. Am sure you are prepared Kuvala zigoli zochuluka! Mind you we are prepared to turn sulumba into another hit man! Pans ice timamenus 12.player no 12 is the red army .

 3. While neba was busy kutokota bullets were busy underground making sure sulumbas deal is finalised.But in case neba sukuwona patali..Chitakuphetu in the next season is goalkeeping. Am sure you are prepared Kuvala zigoli zochuluka! Mind you we are prepared to turn sulumba into another hit man! Pans ice timamenus 12.player no 12 is the red army .

 4. Hahahahahahahahahahaha neba kulira ndi mtima…monse muja mumamusungiIanji ngati salima player wa bwino enanu munkachita kulemba heee sulumba akundimvesa kukoma za ziiii musanyoze coz mwabetsa…welcome to the world of football brother man…….neba ufiila maso suunati NBB for life

 5. Hahahahahahahahahahaha neba kulira ndi mtima…monse muja mumamusungiIanji ngati salima player wa bwino enanu munkachita kulemba heee sulumba akundimvesa kukoma za ziiii musanyoze coz mwabetsa…welcome to the world of football brother man…….neba ufiila maso suunati NBB for life

 6. Iwe Thoxy ndiwe kape. Sulumba anali wa BT UTD mwina sukudziwa. Wapenga kapenatu. Chimutu.

 7. I Knew It Would Come To That,,,,welcome Sulumba To NBB,,,the Only Team That Won The Super League Title In 2004 Without Losing Any Game,,,,NBB Has Won The Superleague Title 13 Times As Compared To Any other Team In Malawi…U Have Really Joined The Football Power House In Malawi…Congrats For Adding Salt On A Fresh Wound,,,,nyerere Zikulilira Iwe

 8. Zilibwino padakapanda NOMA bwezi Bullets kulibe,chifukwa ndiyokhayo imawapezera ma player mbambande omwe amapangisa kuti team yawo iziwike pa Malawi Pano komaso kuti isatuluke mu league.

  1. Mpira ndayamba kuwusata Dzana.Inu munayamba Zaka ziti?. Ndalama yomwe mwamugulila Agawana iye ndi AGENT WAKE ;NAKOMA.

 9. Komatu mukumunyozayo anali topgoal scorer kwanuko,ayipe lero….welcum Muha

 10. Inu amalawi 24 musatinyase nalo boza lanu mwanva?mwalemba kale zonyoza nbb apa mukutulusa za sulumba angakusekerereni ndani?calinga tinene kuti mwalemba za nzeru? Simukuti nbb ili pamavuto azacuma sono maplayer oo tizikawapasa cani?cosaniiii zanu za sulumbazo

 11. Wamuthawa jabulan linje, kunena mosabisa sulumba mpila mulibe iwe uende bho ndipo ukafike bho tizikumana mkat mwandime, ine noma ndi 4life isanebwele iweyo sulumbawe timamva kukoma ndikale pita ukazione uzatiuza ife ndinganga pambuyo pa nyelele,

 12. Wamuthawa jabulan linje, kunena mosabisa sulumba mpila mulibe iwe uende bho ndipo ukafike bho tizikumana mkat mwandime, ine noma ndi 4life isanebwele iweyo sulumbawe timamva kukoma ndikale pita ukazione uzatiuza ife ndinganga pambuyo pa nyelele,

 13. Inu mwasowa chochita eti watinyasa silumba musalembeso za galu wanuyo sathaso mpira kaya wakupatsani ndalama kapena.

 14. Inu mwasowa chochita eti watinyasa silumba musalembeso za galu wanuyo sathaso mpira kaya wakupatsani ndalama kapena.

 15. kod inu mugot sulumba he z not a good player as u thot tamenya nawo pa thawira ground kumachinjiri and he was easy to mark ndie pano mukumupopa ….to tel u the fact dollo nd sparrow sowoya uja osat makaka aplayer mukucemererayu eish

 16. kod inu mugot sulumba he z not a good player as u thot tamenya nawo pa thawira ground kumachinjiri and he was easy to mark ndie pano mukumupopa ….to tel u the fact dollo nd sparrow sowoya uja osat makaka aplayer mukucemererayu eish

 17. Mungovutikatu abullets zasulumba wanuyo Noma tinathana naye kale ndipo tilibe naye ntchito kodi Sulumbayo ndimlendo muYerusalemu muno musatisekese mwamva ndi chani chooneka wapanga Ku Noma kuti timudandaule sorry maule akanakhala Linje koma waphonya yekhayekha aaaaaa nkhawa njeeeee we have very very good squad than Sulumba wanuyo

 18. Mungovutikatu abullets zasulumba wanuyo Noma tinathana naye kale ndipo tilibe naye ntchito kodi Sulumbayo ndimlendo muYerusalemu muno musatisekese mwamva ndi chani chooneka wapanga Ku Noma kuti timudandaule sorry maule akanakhala Linje koma waphonya yekhayekha aaaaaa nkhawa njeeeee we have very very good squad than Sulumba wanuyo

 19. kkkkkkkkkk..ayamba kumunyoza eti.his style of play imafunika midfield yachango podyesera mipila ngati ya bullets.no doubt akakhala player wabwino ku bullets.zophonyazo mzakomweko akuchokelako

 20. kkkkkkkkkk..ayamba kumunyoza eti.his style of play imafunika midfield yachango podyesera mipila ngati ya bullets.no doubt akakhala player wabwino ku bullets.zophonyazo mzakomweko akuchokelako

 21. Pali Mau “akuti Fupa Lokakamiza Limanwanya Mphika” Ndiye Musiyeni Player Kt Asankhe yekha komwe akufuna kupita, osamutchingira ai. mapeto ake ndizija amasewera osakondwa. aliyense ali ndi ufulu wochita chomwe akufuna.

 22. Pali Mau “akuti Fupa Lokakamiza Limanwanya Mphika” Ndiye Musiyeni Player Kt Asankhe yekha komwe akufuna kupita, osamutchingira ai. mapeto ake ndizija amasewera osakondwa. aliyense ali ndi ufulu wochita chomwe akufuna.

 23. Neba njenjenje kuli kunjenjemera welcome bro #sulumba eko vala jersey iyi*Red&white siunati neba uchiminanso season yake ndiymeney

 24. Neba njenjenje kuli kunjenjemera welcome bro #sulumba eko vala jersey iyi*Red&white siunati neba uchiminanso season yake ndiymeney

 25. ndie kuti ma social & electronic media mwasowa nkhani zomauza anthu eti?tikhalira kumva za sulumba ma player ena kulibe?kambani zoti anthu atolepo zothandiza.

  1. palibe kuphulika man,kodi soul brother ali ndi zigoli zingati?nanga sulumba ali ndi zigoli zinga?pamenepa stiliker ndi uti?ndie bwino azikakhala pa bench ku bullets…ndikuziwa ka jah ukudyako ukazimisira uyamba kuganiza bho ngati anthu ife..!kkkk

  2. koma mlungu amadziwa popeleka zinthu anadziwa kuti kodi ku bullets sponser amane angawathandize ndi uti?ogulisa fodya thus why fisher yo akusuta pamene wakhalapo koma siyekha ena tiwaona posachedwapa akubwera poyera..kkkkk noma yomweyo kuti wa wa wa wa.

  3. Ndinadziwa Kut Mbuz Zikutsusa Apa Ndi Za Noma Kkkkk Pepan Zakuvutan Azikamenya Kwathu Tamulandila Paja Ife Sitibentchulitsana Mwasasuka Neba Zavuta Takugailankon Ndalama Za Kunyasa Muguleko N’chinayo Kufera Kuela Asu Sadakwanebe Kukupusitsani Neba Zakuvuta Wachita Njengunje N B B Woyeeeeeeeeeeee!

  4. Aaaaaah,tilaweko za fodya ayi Paja sulumba ndi player wa blantyre unite si wa noma ndimafuna tikoze pamenepo wamva mbuli iwe?kwa ife anali pa loan tinali tisanapeleke dollar timafuna tione ngati azipanga perform bwino..sori neba paja ku noma kuli ma lawyer

 26. ndie kuti ma social & electronic media mwasowa nkhani zomauza anthu eti?tikhalira kumva za sulumba ma player ena kulibe?kambani zoti anthu atolepo zothandiza.

  1. palibe kuphulika man,kodi soul brother ali ndi zigoli zingati?nanga sulumba ali ndi zigoli zinga?pamenepa stiliker ndi uti?ndie bwino azikakhala pa bench ku bullets…ndikuziwa ka jah ukudyako ukazimisira uyamba kuganiza bho ngati anthu ife..!kkkk

  2. koma mlungu amadziwa popeleka zinthu anadziwa kuti kodi ku bullets sponser amane angawathandize ndi uti?ogulisa fodya thus why fisher yo akusuta pamene wakhalapo koma siyekha ena tiwaona posachedwapa akubwera poyera..kkkkk noma yomweyo kuti wa wa wa wa.

  3. Ndinadziwa Kut Mbuz Zikutsusa Apa Ndi Za Noma Kkkkk Pepan Zakuvutan Azikamenya Kwathu Tamulandila Paja Ife Sitibentchulitsana Mwasasuka Neba Zavuta Takugailankon Ndalama Za Kunyasa Muguleko N’chinayo Kufera Kuela Asu Sadakwanebe Kukupusitsani Neba Zakuvuta Wachita Njengunje N B B Woyeeeeeeeeeeee!

  4. Aaaaaah,tilaweko za fodya ayi Paja sulumba ndi player wa blantyre unite si wa noma ndimafuna tikoze pamenepo wamva mbuli iwe?kwa ife anali pa loan tinali tisanapeleke dollar timafuna tione ngati azipanga perform bwino..sori neba paja ku noma kuli ma lawyer

Comments are closed.