Gaffar dangles K1m carrot to each Wanderers player

Advertisement
Rashid Gaffar

Mighty Wanderers trustee Rashid Gaffar has promised to give each of the club’s players a bonus of K1 million if the team wins this year’s Super League.

Speaking during Wanderers’ executive committee elections on Saturday morning, the business tycoon, who is also a Member for Parliament from Blantyre, said time has come for the team to win the championship and participate in Africa’s continental showpiece next year.

Rashid Gaffar
On the splash : Gaffar

“I would love to see the team travelling to Egypt, Ivory Coast, Nigeria, South Africa and many more African countries to play in the CAF Champions League.

“This will only be made possible if these players win this year’s championship and let me assure them that I  will reward them K1 million each if they win the Super League,” said Gaffar.

He also added that Nomads executive will ask sponsors Be Forward from Japan to provide loans for players’ vehicles.

The billionaire was also quick to promise the players that once they win the league, they will spend a month in Japan for off-season break.

The Nomads have had an 11 year Super League drought but are optimistic of grabbing the title this year following the arrival of some new players at the club in the on-going transfer market.

Advertisement

356 Comments

 1. Bullets camp u may also do th sem thng by promcng yo pleyas a paket of cigaret 4 each pleya if only they mek it a treble as a motivation factor kkkkkkk

 2. Bullets camp u may also do th sem thng by promcng yo pleyas a paket of cigaret 4 each pleya if only they mek it a treble as a motivation factor kkkkkkk

 3. Koma anthu muli ndi vuto munthu akufuna kukweza mpira koma inu zolankhula bweee auzeni zinkhwaya za team yanu zipange zanu bwanji

 4. Mwakhala mukunena kuti Bullets singakhale nd sponsor….lero?can u remind me? Nyasa cha?
  lero mwasintha tune muli sponsorship yathu(noma)
  nd yama dollars?
  sponsorship ya bullets yasintha machitidwe azinthu a noma opusa mwayamba zaumbuli

  chomwe mumafuna? bullets tizikhala osauka mpaka kalekale
  anthu osatha Mpira inu ngati tamakutengerani zikho tilibe Olo 1 tambala ndiye lero? muka promisane 1 million?
  ma player wo signing on fee yawo nd Bwanji ku noma?

 5. mwayiwala kuti Muma faita relegation season
  yomweyi apa
  and gaffar promise anakanena kuti position 4 maybe.no 1 will doubt wanderers of finishing pa no4 but 1 ayi Ndizofunika anamandwa izo

 6. Ngat kuli mbuli dzapila ndi anoma chifukwa chaka chilichose league ikamayamba amabwebweta dzambiri km mapeto ake dzimakhara zopanda sogoroso

 7. gaez noma mpatali tiona thise sezn ngati mutapange zopusa zanuzo. Tangoganizan k1 m kwapuleya aliyense mukuonangati nchibwana aaaaaa nyerere npatali zilikoliko kaya

 8. osati league yokha olo akatenga cup china chilichonse yet inu Bibi mukuti akagure chimanga akapanse anthu kudera kwao ur combinin 2 different things, no wonder mumagulitsa ma memory card anyimbo kale

 9. Ine monga nzika ya Malawi ndine wokondwa pa nkhaniyi koma sikuti kwambiri, monga Sapota wa NYASA BULLETS,ndili ndichikhulupiliro kuti nkwabwino league yanthu ikhale yopaambana ngati m’mene zikuchitikila ku EPL,ma Team ang’ono akukong’otha akulu akulu mosayang’ana nkhope so yah competition is wat we want apatseni mwina nkuthamanga. Komano ndili ndi vuto limodzi kwa#GAFFAR,kuti ganizo mwaganizali kunakakhala kuti mwaganizila ntundu wanu wa Malawi panthawi ngati ino ya Mavuto kukanakhala kotani? Or mutati mutenge K5,000,000.00 for example mugule matumba achimanga and mukagawe dera liri lonse mungafuniko kumabanja ovutikako half thumba per Family and ndi anthu ochuluka bwanji pa ndalama ndanenayo? Komanso Chimwemwe cha anthu aja chitha kubweretsa Mtendere kwainu kuchokera kwa Yehova,popeza mwachitira anthu ake Chabwino. Pomaliza ndalama nzanu awo anali maganizo anthu chabe,koma mutatero zinthu zittha kusitha kwa ena ndithu

 10. Makape enanu kuTeam kwanu kulibeko Trustee wandalama kuti apange promise? Heee? Nde mitu mfwee mfwee apa ngati nkhani zathu zikukuhuzani bwanji.

 11. Nchifukwa chake mpila siuzatukuka. Ndalamazo thandizilani team kuti ichite bwino osati kupeleka kwa ma individual players chonsecho mukudziwa kuti wanderers siingatenge league.

 12. Yamzako ikauka yamikira ,that’s why pachingerezi pali mau otiDream come true unyambita mapazi anyerere this year ukhaula,oooooooooooh icho chosasambacho

 13. Gaffar mwana wake amuthamangtsa ku xool chfkw chosowa fees ndye makape anoma nkumadalira malotowo? thats kudzkwata nchala, munuwuze gaffar adzapalire mtedza kuno.

 14. Maloto a chumba!!! Kodi noma ndithu mpakana kutenga leaque? Musayilakwire noma level imeneyi sinafike.Sulumba awalandayo ndi amene adzawapweteke moyipa.

 15. Ndalamadxo moti muthandizile ovutika mukupasa wodziwika kale poti Amati chuma chimapita kwa achuma osauka kumasaukabe akafuna thandidzo kuwakumbitsa zutsime ndimitseu nsambi kwabasi

 16. chokani abullets mafuna chani pa page yathuyi?? muli ndiyanu page munaona ife timalowerera?? ochititsa manyazi ndinu chatha chikho cha standard bank osatengako mwanyaaaah manoma 4 ril

 17. chokani abullets mafuna chani pa page yathuyi?? muli ndiyanu page munaona ife timalowerera?? ochititsa manyazi ndinu chatha chikho cha standard bank osatengako mwanyaaaah manoma 4 ril

 18. Kkkkkkkk,akulonjeza chifukwa akudziwa kuti is IMPOSSIBLE,kkkkk ndichipongwetu ichiiiii mukatengela kumanda,moti simukunjenjemela ndi NBB?

 19. Kkkkkkkk kuwalonjeza zindalama zonsezo coz mukudziwa kut sangakwanitse eti? Tangoyerekedzani kulonjedza BULLETS muone

 20. Kkkkkkkk kuwalonjeza zindalama zonsezo coz mukudziwa kut sangakwanitse eti? Tangoyerekedzani kulonjedza BULLETS muone

  1. Kkkkkkk ukufuna ma Refu amenyedwe chani?akangoluza azingoti ndi refu olo samasewera azikana kuli kuopa kumubwenzera Gaffar zake azawapase 2020 tikazawapasa zowayeneleza kuwinako

 21. Sitimatekeseka, kapena kung’ung’uzira cha m’phewamu. Tikamati B*4*ward *nkuzamalisira Wandalazi, timanena zimenezi. Ndili pa show tsopano, ena ationetse, professional player wao.

 22. Sitimatekeseka, kapena kung’ung’uzira cha m’phewamu. Tikamati B*4*ward *nkuzamalisira Wandalazi, timanena zimenezi. Ndili pa show tsopano, ena ationetse, professional player wao.

 23. fans vuto lanu ndi chani? inu mawlonjezapo kulira ndi umphawi. manoma kungowina super lengue tipita ku europe just for a walk manoma wooooooooye

 24. Nomads yomweyo all teams can not finish at position one.do u think nomads can not win?maganizo anthu openga inu,shame on u.nkhani iliapa ndiya nomads osati mahule inu

 25. bwana mkubwa wa zinda bt walamula team ya nbb kut itoletole za fodya zose chifukwa zikunyasitsa mzinda ndipo wat tikuyenela kusamala chifukwa kusuta kumaonga moyo

 26. A Gaffer ayionera patali kuti nzosatheka. panakhalira inu supporter wa noma mukalonjeze lero? Chumba cheni cheni komanso chokalamba kkkkkkkk

 27. Super League Inayamba 1985 Panopa Yatha Zaka 30 Koma Team Ina Yozitcha Kuti Ndiyayikulu Yangotenga Ka 5 Kokha, Pamene Anzawo Akulimbana Nawowo Atenga Ka 12 Koma Safuna Kuvomereza Kuti Anzawowo Ndiwakulu, Ufiti… Chani??? Ndipo Neba Ndisakunamize Uli Ndi Ntchito Yayikulu Kwabasi Kuti Uzapange Mbiri Ngati Imene Inapanga Bullets Ku Mbali Ya League.

  1. Timu ya noma ndiyoyamba pamene bullets inabwera pambuyo pa noma. Ngakhale bullets itatenga zikho zambiri kuposa noma, zoonna nzakuti noma ndiyaikulu basi. Go back to xool!

  2. Timu ya noma ndiyoyamba pamene bullets inabwera pambuyo pa noma. Ngakhale bullets itatenga zikho zambiri kuposa noma, zoonna nzakuti noma ndiyaikulu basi. Go back to xool!

  3. Team Kuyamba Kale Its Not An Achievement Bra! Nkhani Ili Yapa Ndiyakuchita Bwino Kwa Team Not Zanuzo, Kodi Chonyaditsa Ndi Chani Kukhala Oyamba Kubadwa Koma Opanda Kalikose Ndikunkhala Omaliza Kubadwa Koma Ozidalira Pawekha?? Kuona Fisi Sikubadwa Kale Koma Kuyenda Usiku

  4. Team Kuyamba Kale Its Not An Achievement Bra! Nkhani Ili Yapa Ndiyakuchita Bwino Kwa Team Not Zanuzo, Kodi Chonyaditsa Ndi Chani Kukhala Oyamba Kubadwa Koma Opanda Kalikose Ndikunkhala Omaliza Kubadwa Koma Ozidalira Pawekha?? Kuona Fisi Sikubadwa Kale Koma Kuyenda Usiku

 28. yakuwawani 1meter komaso ka relax ka ku Japan koma neba sanje sudzathekaso. Inu u hav promised to receive K40 pin after winning kagame whilst us eash kundivetsa tseketseke bluez

 29. Umphawi ndiomwe ukukucitixani agalu inu.mukatenge fodya mudzikagulixa otherwise akuxiyani kukuthandizan. Kusuta kumaononga moyo

 30. Ngat ku team kwanuko kwaculuka anthu ovutika pliz muxaexexo anzanu kut ndiovutika. Noma 4 sure!! KUSUTA KUMAONONGA MOYO kkkkkkkkkk

 31. Eya neba tamakatu tikuve paja ndiwe wamatama ndiye wako ndani wabwela poyela ndi chilimbikitso muli phindulanji mundudu neba ndikuwona mmene anduduwa akutengela ukupanga matukutuku kwambili

 32. Kungoti Ambiri Abullets Ndi Aziwanda Amadzidzimuka Ndi Zochepa Ife Eni Ake Tili Chete!!!! Koma Iwowa Kuma Bwebweta Adakupepetulani Sing’anga Mapeto Ake Muyamba Kuukilana Wene Mokha Ife Tingo Tsata Fundo Zomwe Zikukhazikitsidwa Maso Patsogolo Muzingo Lira Chwi!!!!,chwi!!!!!,chwi!!!!,ngati Makoswe Oti Agwidwa Ndi Mphaka.

 33. Bullets ikutenga League mpaka 2020 osafuna asiye, Team imawina League kawiri opanda oyithandiza, ndiye tilekelanjiso kupitliza titapeza ndalama???? BB team ku Malawi the Peoples Team

 34. This is the news to wanderers fc not nyasa big bullets,mind u mumakonda kulowerera zakuchipinda chaeniake bwanji pangani zanu za 2010 Nizo.

 35. Muzivulara pa pitch mukusewela mwa hard kufuna one mitre ife mwachifatse tikufuna kutolera ma filiyi poinsi MAULE IMANDIMVETSA KUKOMA INEQUALITY

 36. The champions pple deserves the champion team team WE dont count out th promises all we always do s to combine th winning system THUMBS UP MAULE NOPULOBULOMO

 37. Gaffar ndi mbuli yotheratu munthu ungamulonjeze patient kuti ndizakupatsa ndalama zambiri ngati mphatso ukazachira mmalo momupatsiratu kuti apite zipatala zikuluzikulu,bodza lamkunkhuniza ndalamazo akanakagula maplayer ku egypt,ghana,ivorycoast,nigeria,igeria even europe kut ipose team iriyonse mmalawi/mu africa afta o walephera kumulipira Chipuwa

 38. mita anyamata amakanika kulipira rent ku chilomoni uku, nkumalonjeza ndalama zonsezo ziliko season ino ndithu.

 39. Kkkkkkkkkkkk koma team yanga ya #Bullets yafika pa u #BokhoHaram ma team onse akuiopa #bullets,, but let m tel u dat #Bullets z here to stay and were forever #CHAMPIONS!!!!!!!!!!!

  1. Hahahahahahahahahahaha sory man but its fact beliv that,,this season tikuphwanyani inu a noma ndi mafupa omwe,matumbo,.#watchOUT

 40. kkkkkkkkkkkkk ngati mpaka pano ayaya sadalandile zawo ndiye league yake it mudzatenge inuyo.muyambe mwapatsa ayaya ndiye mudzilankhula mzamutu zanuzo.plz NOTE team imene ili ma champion pano ikayamba kutenga league,imatenga mpaka mzaka 7 motsogoza ndiye pano kuli zina 5 zosayamba.ba lotani maloto achumbawo kaya.

 41. That means mapuleyawo alibe umwini and they don’t love the team. Ife kumaule timatenga mosatana popanda kulonjeza mapuleya because mapuleyawo ndimaule enieni and amaikonda team. Eg Fisher and Chiku.

 42. tiyeni league iyambikepo muwone ngati mutachite zomwe mukulemba panonodzi,team yochitisa manyadzi ngati iyo sponser kuma khala nayo koma palibe chisitha aaaa.bullets for real.

  1. Titenga titenga 1mita nyimbo yapakamwa ya Neba moti Gaffer waitchulira dala mita akuziwa kuti Nebah ndiwaturo sangatenge kkkkkk

 43. Anyamata nkhani yabwino imeneyi.My team wanderers i cant support enawo ma salvage andeu nthawi zonse.1m mpatali work hard.Bravo Gaffar.

 44. Nthawi zonse chilimbikiso chimapita kwa olephera, ine pheee pambuyo pa MAULE tasala ndi zaka 5 tikutengabe league wina alira chweeeee

 45. kodi a noma inu super league muna wina liti? kkkkkk 12 year ago ndye lero basi atrustees anuwo angokhuta ndudu kuyamba kubwebweta apa.tazibwetani ife tikumwa wamkaka evryday

 46. Imwe anyamata amvingambwe mitu yanu sigwira mkumangoyankha nkhani zomwe simukunziziwa munthu walonjeza bas mwatsusa tigule praye mwasusa eee timu yanu ndi yanthu afuntha mzikhala ndimanyanzi poika comment.

 47. Mpira patsogolo ndrama pa mbuyo nde #maule amenewo. We are the champions fo eva, Manoma mulibenso mwai mwachepa mwamva? Makape!!!!

 48. Iye kudyela khwani nde kuti wauzidwa kuchipatala ndi doctor kuti adye amene akulonjezayo zache zinayela ndipo amanena ekha kuti ali ndi makobili oti atha kutelekela m’golo wanyemba ndikuphya osatitu khuni ayi koma kusongezelela ndalama nkukazingaso tomato anyezi zonse nkuphya ndalama zina nkusala nde iwe wa bb kaya ulimi wafodya wakukwana peza lina thandizo

 49. a bullets ndinu ochititsa manyazi kwambiri mukulowerera za ku noma bwanji akuti noma ikatenga league this season kaya itenga kaya sitenga ikhalabe noma. Ndiye sizomanena kuti siingatenge league inu mudatenganu ndinu angel inuyo mwangochuluka sanje osamakangosuta fodya kunyasa bwanji!! Chitani manyazi

 50. inutu abulets mitu yanu simagwila ntchito kuyambila kale ndiye ndindudu zabwelazo aaaaaaaaaaa kumento sopapano anzanu kunjoya m nkosayamba tawonani eeeeeeee zikungobwela zokha ndipo musanayambe trening mutolele ma pisi afodya ooooonse akunyasisa town

  1. iwe ukuona ngati olonjezayo ndi opanda nzeru jst to giv a million kwacha to a player bcoz of winning de trophy ?…..Naye waona kale kuti or zitavuta bwanji simungatengeso League dat is why he has xuzen to promise dat masacar sum of money to test the fools mentality to kipon trying to move the mountains……hahahahhahaa……muisovenge……Nyasa kuti buuuuuuu…!.!!

 51. U must start now by giving them good salaries and allowances.U can’t wait up untill the end of the season,that is not helping,u must start now bro #Rashid.

 52. kusaukaku ndiufitidi eti, ,,, mukuyankhula zambiri ngati mutazapange ndunu bwa, ,,,, Kazigulisani nduduzo makape inu isiyeni noma hlo.. Gaffah for noma and noma for life

  1. Ndie akuti after training Player aliyense will be given packet ya fodya ngati achitira ku bakery muja; ama wa patsa bread poweluka. Koma Neighbour!!

  2. Emmanuel sananame ai kuona ndi momwe team ikuchitira i swear bfr God frst game mwaluza kale nde muzifuse kut rafiki wanuyo azadusa pa lanjesi

  3. Munthu akunena zopereka K1m kwa player aliyense coz he’s capable to do so, nanga ma vendor angatiyimirire ndani poti takumana akuba tokhatokha? Tiye tidikire tione ngati sponsorship ya nduduyi tithe zaka ziwiri tili nayobe

  4. 3-0 yake imeneija ndi ana a Mzuni ndiye uzilota Gaffar atakupasa 1mita iweyo iweyo iweyo Nebah?kkkkk akuziwa kuti Noma singaphule kanthuuuuuuuuuuu bola yophatikizana ija itha mwina kuyeselako ndiye mwina muphatikizane ndi Mzuni yomweijatu kkkkkk

  5. Bullets team yosauka u play for money makape inu…. he can not bid 1M for you coz akudziwa kuti u will bet ur hearts, probably you’do anything to win the league either through threats, which is always part of yourgame or worst enough get into diabolics! MANOMA WOYEEEE!! #BeForward_AlwaysGoForward

 53. Taona nanga mpaka akuti akupatsa 1mita/player cholinga utengeko league bwanji osanena cup?akudziwa kuti league ndi za ana amuna.

 54. Neba matrusteee ako akadanena izi bwenzi mukuti #Mapesitina tamayamikirani anzanu . Trustee wathu ndi iyeyu and timamunyadira inu tulusani wanu trusteee timuuone and zomwe akadanena kuti ndiwaunza masponsor kuti apatse maplayer athu ndudu kuti akayamba business

  1. Sizikugwirizana,,iye nd boma?? Ndizampira izi axe he z not responsible for those pipo dying of hunger,question bingu for that zili apa ndi za football

  2. Bruvo hx malawian same like u.is hz responsibility kutengapo mbali cz hz one of millioners him self.take a look wat he did bushiri ds past months. Dnt jst point finger mr president.evn ma company mabungwe njala ikuwakhuzabe cz chothandiza anthu 20/30 instead of help 14,000000 people wake up budy

  3. Bruvo hx malawian same like u.is hz responsibility kutengapo mbali cz hz one of millioners him self.take a look wat he did bushiri ds past months. Dnt jst point finger mr president.evn ma company mabungwe njala ikuwakhuzabe cz chothandiza anthu 20/30 instead of help 14,000000 people wake up budy

 55. 1Million X 35=35million KwachaNgati Amakondadi Mpira Taperekanso Promise Imeneyo Ku BB uwone ngati next season siudyera nkhwani?mr.r gaffar thinking imponsibilities.

  1. Why to bullets Cecilia NyaZimba Magawa, This is for wanderes familly to motivate the children in the family. Those are our tycoons we have to be proud

 56. Koma atolankhani enanu kusazitsata eeeeesh. Gaffa said team ikatenga chikho iyeyo aziikapo 1000 000 yamuthumba mwake kuti ma player agawane. Komabe ine ndikuona kuti akudziwa kuti noma siingatenge chikho this season .

  1. Maloto achumba awa….m’malo molipilira ma player anuwo nyumba busy ndikumalonjeza zosatheka bwanji? kaya ife bola moyo tidzaone ngati mukutengadi chinkho cha SUPER cho.kkkkkkkkkkk

Comments are closed.