Love your country, Malawians urged

Advertisement
masauko-medi
masauko-medi
Medi: Lets be patriotic.

The Department of Immigration has urged people living near the country’s borders to love Malawi and be patriotic by reporting illegal immigrants to authorities.

Chief Immigration Officer Masauko Medi made the remarks amid increasing reports of illegal immigrants entering the country.

He said lack of patriotism by the citizens is fuelling the illegal entrance of immigrants into the country. Medi added that the proliferation of the illegal immigrants in the country could be a thing of the past if the local communities were reporting to the department.

The Immigration chief also expressed concern with some Malawians who receive bribes from the immigrants.

Medi then revealed that inadequate resources are among the factors hindering the work of the immigration department.    He said the department has 700 officers across the country.

He however assured Malawians that his department will start campaigns to bring awareness on the issue.

 

Advertisement

137 Comments

 1. Vuto boma la Malawi mukukana kuwapangila anthu ma National Registration Cards which can make it easy to I identify and differentiate Malawian citizens from illegal migrants..
  I know the problem is not Department of Immigration or National Registration Council but policy makers…
  Wakeup!!!
  Dziko lopanda ma NRC???
  Wina akayamba nkhani ya NRC Akuti ndale.. Akufuna tibwelele mu nthawi ya MCP. Masiku anonso??

 2. Angawagwire bwanji poti maburundi akhala ngati kholo la iwowo apolice, mesa akudyela momo kkkk apolicewatu ndiochenjela anaphuziladieeee!!!

 3. Ife a Malawi ku Joni kuno tilipo mwina kuposa omwe ali kumeneko ndiye mwati tipange chani ziphuphu basi inuyonso makolo anu anachokera ku Zaire muyambe ndinu ulendo,Foreigner wamkulu ndi GAY mwavomeredzayo basi chase away gay first kkkkkk

 4. Ife a Malawi ku Joni kuno tilipo mwina kuposa omwe ali kumeneko ndiye mwati tipange chani ziphuphu basi inuyonso makolo anu anachokera ku Zaire muyambe ndinu ulendo,Foreigner wamkulu ndi GAY mwavomeredzayo basi chase away gay first kkkkkk

 5. Ukufuna udzilandira zamahara? Pita uzikawasaka wekha, ukutiphimba kumaso ngati sunalowemo mma shop mwawo bwanji mkulu wa immigration tyming chanii?

 6. Guys tell me something,where were our elders when our boundaries were demarcated because sometimes I don’t understand how our borders were demarcated, when driving along these areas you automatically sense fraud

 7. We people brought the boundaries but for sure God the Creator dont know that there is Malawi, ayi ati Zimbabwe, SA achina Britain. God did just create the Earth so dont mess up we are all immigrants, if you are a Yao, Tumbuka, Ngoni etcs go deep with your history we all came frm far away & ended up here in Malawi dziko lomwe pansipake pali chimoto anthu tikungovutika ndi malawi a moto umenewu. Never play with Fire…

 8. Most of the officers sir at ur office are very corrupt,kumene ndimakhala ine am sorrounded by Nigerians and Zimbabweans some of these pipo are using our passport not fake but original and printed their at our immigration offices but atrue citizen is struggling to get one,This world is very unfair where the poor can’t be recognised

 9. Mr speaker sir go to zim to Zambia SA you see Malawians what are you saying africa is for africans all of them

 10. Tatuluxani vacancy mulembe ma officers ena apa. Inu ma burundi ali mbwee mu nchesi and kawale oxamapita kumakafunxa if ey ma paperz bwa? Tima barber shop tomwe ma officerz anuwo amakametexa ndi ama bulundi even tima groceries tomwe mumakagula sugar tama bulundi

 11. Stupid. We will not. U the Immigration Officers, are on payroll from Nigerians, Congolese, Burundis, Tanzanians, Lebanese n many more. You are very very stupid.

 12. Zikomo potipasa phanvu, ine ndikuuzeni muyende chochi mukafika mu town ya limbe mbali yomwe kunali police yakale jupter, mbali yoseija ku ma shop a ma Burudi , china, Indias and swahiri please go and check those peaple en arrest them

 13. That’s stupid coz his doing well from the money of ppl getting passports and visas chewing it a lot and telling su to love our country.yes we do but if there is nothing we can do in our country then we move to others

 14. Mungolankhula mmaso muli gwaaa even manyazi mulibe anthu akagwile ntcito ndi inu pamene inu simukuthandiza anthu musolvr even nditawaona nditha kuwasia

 15. There can never be an illegal immigrant of African decency in any of African countries. Africa is for all Africans. Viva African Unity….One love..

 16. U are telling us to love our country yet u r on e 4 front issuing malawian passport to these foreigners who don’t even know how to say muli bwanji

 17. U are telling us to love our country yet u r on e 4 front issuing malawian passport to these foreigners who don’t even know how to say muli bwanji

 18. Tidziziwa bwanji kuti uyu ndi legal kapena illegal immigrant? tidzayamba kulimbana ndi munthu oti ali ndi mapepala;

 19. Tidziziwa bwanji kuti uyu ndi legal kapena illegal immigrant? tidzayamba kulimbana ndi munthu oti ali ndi mapepala;

 20. Whatever this officer is saying, it’s complete bullshit. Because themselves are the owners of corruption. They can’t give passports to the owners by time is issued unless that particular person pay them again. All in all I can only say fuck u Mr officer.

 21. Basi anthu moti akasake chakudya cham’manyumba mwawo azikhara busy kuyang’ana zaanthu ngati amenewo, iwe uli chete mu office ukatha mwezi kulandira, ine ndili kuno ku jonzi man koma anthu akuno samakatipereka ku police koma boma yokha imagwira ntchito yake yotifusa passport or id, ine sindingapange zimenezo kumupeza ndingachite kumuuza make a plan,

 22. Basi anthu moti akasake chakudya cham’manyumba mwawo azikhara busy kuyang’ana zaanthu ngati amenewo, iwe uli chete mu office ukatha mwezi kulandira, ine ndili kuno ku jonzi man koma anthu akuno samakatipereka ku police koma boma yokha imagwira ntchito yake yotifusa passport or id, ine sindingapange zimenezo kumupeza ndingachite kumuuza make a plan,

 23. Do your duty you are paid for here in South Africa its the responsibility of home affairs to curb illegal immigrants not the citizens to report illegals ayi pezani njira ina katangale wayambira kumtundako nayenso last man kumudzi akufuna naye adyerere dziko lake. Sent a thief to catch a thief, atabwali sametana amaopa kumetana mipala.

 24. Chief what about your people in South Africa? let them stay we all africans let’s learn how to love other people for welcomed them.

 25. Point of order!!! Mr speaker sir,u must b very stupid!.Burundi nationals r about 2 inherit Malawi and hv already occupied half of t yet u r there eating the monies. Mr Speaker sir u must specify the Nationalist which u r against with.Or shud we say a Chief criminal z speaking 2 non criminals?

 26. Es malawi is poor country anzanuo adadziwa kuti apolisi amaenda ndi futi inu muenda ndindodo thats why tanzania akufuna kukulandani nyanja malawi iz too lazy security kenako akulandani sanjika poor governers

 27. This stupid government just employ thieves if they can’t help also I can’t help them, biggest criminals are police

 28. ife tizikugwilirani ntchito inu kumalandira ma salary.And most of the foreigners have Malawi passports.where do they get them?Jst shut up your mouth mr chief officer!!

 29. Ife anyamata akuno tinkayesesa kuthandizana nanu kumbuyoku koma mapeto ake timayika moyo wathu pachiopsezo ndi Amalawi anzathu omwe amathandizila kulowesa ma foreigners amenewa.Panopa timawaona koma palibe chimene tikupanga.Mutakhala serious vuto palibe titha kuyambilaso.

 30. Illegal immigrant chonsecho akulamulirayonso ndie immigrant number one. uchotsa bwanji chitsotso chilimwa wina apo chako chili chothoo. tayambani mwalowa kaye mma office a bomamu tione ngat simugwiramo wina immigrant mmenemo. ngat ukukanika wawuwisi nanga kulii bwanji wowuma. afuseni abwanawo first.

 31. masauko made ngati iweyo silufuna ntchito tayisiye, ukuganiza ngati ife tingakugwilile ntchito yoyang’ana anthu olowa tilandila nawe fuck uuuuuu!

 32. nosense!!!we are all Africans.the boundaries were made by Europeans but we are all one and will all leave this earth one day.

 33. Kaya zanu zimenezo ndi ntchito yanu ___mwina muzikaima mmalire mwadziko penapaliponse kuti muzigwila nokha_____ ngati zimawakanika awa adziko LA South Africa anthu oti adalambula nseu waukulu bwino kuzungulila mmalire la dziko lawo ndikuikanso fensi wire ngati aluteteza nyama mu_game nkumapanganso frequent patrolling koma at a zosaphula kanthu anthu nkumalowa ndipawaya pompo.______ ndiye dziko lathuli ngakhale pa border sipokungana ngati maboda ena anthu akhoza kudutsa nkumalowa opanda chilolezo.____tatieni tilmbane ndi zina mutikwana chifukwa musatitseke mmaso chilungamo tikuchidziwa kuti inu ndiye eniake amadilu amenewa pano mwina mwaona kuti mbali yanuyo kuli quite kkkkkkk akuyenda zamthengo tsopano wena apezeko dollar

 34. How Can One Love His or Her Country When there is Hunger?
  How Can One Love His or Her Country where they allow Somo ndi Gomola?. Akazi Okha Okha Ndi Amunanso Okha Okha?. What Is Happening my Beloved Neighbour Malawi?

 35. Ngati ndi chamba kamweni madzi tose tili amodzi cholinga mkalandilepo basi, yaa zoputsa mwalemela chifukwa cha ziphuphu inu kapumeni adzanu akufuna pamenepo.

 36. I think government has been clueless all the years, why u do not make new system of ID’s then it would be easier than to sniff them like security dogs, mwagwira mwachangu than report to cops bcoz the cops also are full of corruption, they will do nothing only chasing up for money.

 37. I’m your father your Lord, GOD & I created earth & heaven.I created you in my image ,now I send you to go and live on earth wherever possible & I created everything on it for you to enjoy BUT do not forget to remember Me, Your GOD by praying.

 38. malawi is a borderless country everyone can enter anyhow no citizenship id no registration responsible officers are busy respecting every foreighner for exchange of money foolish.

 39. How many malawians living outside the country ?leave them if they found thier living there ,malawi have failed us you dnt need our support too

 40. maBurundi ambirimbiri ali mtawunimu atinamize kuti sakuwawona zakuba basi a polisi enieniwo akumapezeka nthaei zina ali pamashop amaBurundi omwewo sono ma illegal immigrantswo nde ati? sitingawadziwe ngati ma Burundiwa ali ma legal immigrants instance pa Mangochi mwina ¾ ya mashop ndi maBurundi eni nthaka business osayrnda kamba kogawana macustomer, Blantyre Bangwe Mvula okhaokha maBurundi sizobisanso ayi amakhalira kulankhula zilankhulo zawo zija ankabweramo amati akudzachita business? kapena apolisiwo sadziwa kuti anthuwo ndi maforeighner a immigrationwo mwina nawonso sakhala serious or else amadya nawo. no excuse no apology chilungamo pamwamba pa chinzake.

  1. Akanize anthu obwera chifukwa chani? Ndi a malawi angati ali kunja kwa malawi komanso amalawi samatha kupanga business. For example amwenye akhala ali muziko mwathumo muulamuliro wa Kamuzu mpaka pano palibe amene anatengelako business ngati imeneyo. Ma china omwewa ayamba posachedwapa akulemela amalawi akuona ndi maso. Ndiye muziti ma foreigner chani? Mabulundi mukunenawo ndi ponse ponse or ku zambia, Botswana, Zimbabwe,mu Johanesburg ndiye ambiri mbiri. Or atakusiilani shop’yo munalizamo zonse mmalawi ndi business zili kutali kwambiri , koma MABODZA basi ndi BAWO.

  2. Akanize anthu obwera chifukwa chani? Ndi a malawi angati ali kunja kwa malawi komanso amalawi samatha kupanga business. For example amwenye akhala ali muziko mwathumo muulamuliro wa Kamuzu mpaka pano palibe amene anatengelako business ngati imeneyo. Ma china omwewa ayamba posachedwapa akulemela amalawi akuona ndi maso. Ndiye muziti ma foreigner chani? Mabulundi mukunenawo ndi ponse ponse or ku zambia, Botswana, Zimbabwe,mu Johanesburg ndiye ambiri mbiri. Or atakusiilani shop’yo munalizamo zonse mmalawi ndi business zili kutali kwambiri , koma MABODZA basi ndi BAWO.

 41. Kupusa ,akukanika kukonda mtundu wa amalawi,kut azipanga biznesss momasuka ,mmidzi mwao,ma burundi ali thooo mmidzimu kugulitsa mafuta oyeza,ndi nyemba kupha bizness za amalawi inu a immigration ,mumakhala kut,zitsilu zidude inu eti shatap zanu

 42. Ndiye Ife okhala Ku maiko a eniake nafenso tikupititsa matenda maiko aeniake? There’s a illegal immigrants every country because they are seeking a better living.

 43. illegal immagrants are ones who help to increase malawi population and they are ones who make progression in businesses and externalize our forex leave this country struggle with poverty so when you people live near malawi’s borders see a strange person try to cross borde without travelling documents report immediately to the police. do not allow them because most of illegal immigrants flee from their countries with strange diseases that have not medicine so when you recieve them and allaw them to stay in this country you put this country at risk of diseases which ultimately leads to high cases of death rate hence increase in orphanhood.

 44. Hahaha tortoise like stone. Corruption ili ndi inu a immigration kukamba zimenezi?Zoona kuti mfiti. Ndiyimene imabangula kwambiri pa maliro kufuna kuputsitsa anamfedwa eti?

 45. You mean that you dont know that your officers are behind all this?corruption is on the rise in this counrt these people will take this country from us believe me

 46. Mfiti za anthu izi,,,sitimakuopani, koma timalemekeza ntchito yanu ndi uniform yaboma. Ukandiyambe sunamvale uniform ukayisovaso. Munthu anyamula katundu ku joweni mumafuna atakhala wanu! Mxiim.

 47. what about those who already sneaked in and are doing businesses freely hav they got valid documents what about overstays? All this is the duty of Immigration Department. In Mozambique just close to Blantyre Tete you cant walk 50meters without being asked of an ID or passport everycorner of city of Tete you are questioned!

 48. Apolisi apa mwanza nawonso amawonjeza kutibela amakhala bize kutchaja katundu ngt munthu ukugulanxo kena tikamabwela kumalawko chonde muzitikondako mchitidwe umatilipilisa katundu uthe

Comments are closed.