Kabanza owners battling teargas and riot police in Mzuzu

Advertisement
Kabanza

KabanzaThere is pandemonium in Mzuzu as Kabanza owners have closed the road leading to Mzuzu Airport.

Reports say the police wanted to stop the Kabanza owners from operating within the city and this led to the tense situation.

According to our sources, there is a heavy police presence in the area and the cops are using teargas to scatter the angry crowd.

However, Malawi24 understands that the Kabanza owners popularly known as Sacramentos in Mzuzu are successfully battling the riot police officers and teargas.

“The police officers have been overpowered and they are being beaten by the Sacramento owners,” said source. “There is chaos in Mzuzu.” said our source.

According to reports, Police wanted to stop the Kabanza owners from trading within the city and this led to the tense situation.

*This breaking news story is being updated, please visit this page again as more details will be published shortly. If you want to receive all the breaking and latest Malawi news alerts via email, subscribe in the comment box below

Advertisement

85 Comments

 1. bt 2b honest kumbali zonse et….maguyz akabanza simumayenda bwino town atleast kumayendako kumakwalalako

 2. Koma mmene chuma chavutilamu mungamuletse munthu kupanga business ufiti chiyani. Ndiye muona kuti azitani. Nonse akabadza mupite kwa mayor ndi mabanja anu azikakupatsa zakudya ndi rent. Mbuzi za a tsogoleri

 3. Njinga mwalanda nanga muwapatsa zochita?. mwina ayambe kuba??? anthu osowa chikondi. anthuwa kabazayu sakupangila kukondwa koma kusowa ntchito ku malawi. ena mwa iwo kusukulu anapita alinazo zoyeneleza #mapepala# koma ntchito kusowa

 4. Amene muli ndikuthekela zilalatani ine ndingova chisoni ndikaona osauka akuzuzika anapeza chochi lelo mwalanda yambani kuba basi nanga atani

 5. Vinjinga vakapalasa nde ndinaviwonadi vankhaninkhani kuthandidza wanthu m’Mzuzu.

 6. Wanthuwo atubacha nawo ndi nthowa yakusaniliya ndalama alekeni, mbava zifwasa,apolice akulimbana ndi anthu akutulusa thukuta kupeza chakudya.think twice.

 7. ndiye ngati boma likuletsa kabadza akufuna kuti anthu adziba? maiko ambiri akugwilitsabe njinga ngati trasport, palibe choletsera kabaza chifunika ango khadzikitsa malamulo okhodza kabaza

 8. Every one have a right todo busines otherwise maybe the police must clarify the policies to follow but not to stop kabaza its acheap and quick transport especialy in our locations

 9. You can not scrape kabaza transport outright. This is a cheap form of transport even to the low, middle and sometimes the upper working class apart from the general travelling public. What the authorities should do is to regulate this form of transportation. There are developed economies like India, Kenya where I have been to and other countries where the bicycle is still being used as a most dependable form of transport. You see kabaza has in a way alleviated the massive unemployment in our country and there are unspeakable benefits accruing to most Malawian house holds from this enterprise. I think there’s nothing illegal to engage oneself in this business but perhaps government has to come in to regularise same by introducing road tax for example, wearing of helmets, bicycle inspection exercises, passenger and goods carrying capacity regulations etc etc but let this trade flourish

  1. ndimafunisisa nditasusana nawe komano nditafunsa nzeru pa za mitengo yathu ya ya transort muno malawi ndapezadi kt kabanza is the cheapest transport ever in malawi.wat usually happens is that its like we hire the bicycle kutitengera ku malo aku mtima kwathu.i agree with u interms of cost.

 10. njala imeneyi azitani kuti apeze ndalama sitingatukuke kumozambic ali mbwee kumakhalapo ndi umunthu muli ngati inu kuvutika choncho

 11. Akabaza mufapo zazii!! wina ali ndi mfuti iwe, akugenda apolice ndi miyala chabwino aliyese agwirise Ntchito chida chake!

 12. Achita bwino kulanda mu town njinga kuchuluka kupotsa galimoto zimangotiwonetsa ngat kut malawi ndiwotsalira we’re living in a modern world full of competition kapalasa tinadutsa pano tilipa motor bike as a*last means of transp. Mu city . Osat njira balala mu city ngat njingazo zikupangidwa kumzuzu ana amangosiya xool pa njira bcz of kabanza. Ndepoti amalawi mnazolowera kutsutsa zilizo gvt can implement. #kabanza mu city must fall. Azikapangira muma district otherwise zimangotiwonetsa umbuli ngati kt tonse ndife mbuli

  1. Iwe,kunoko ma motor bike alipo koma anthu samakwela coz ali vry expensive.jxt imagine, kukwela kabaza 4rm twn 2 zolozolo ndi K200 moto bike ndi K1000.ndi m’mene ndalama yavutiramu ndindani angakwele?olo iweyo ukungowona kuvuta apa sungakwele ku umila kuli ndiwe

  2. U dont knw what you are saying madala… Pple are feeding their families thru this business and furthermore kupelekera fees mafana kuma sxuls. The govt shud legalise this business coz it is reducing unemployment levels in the country

  3. it takes time someone to understand i know @Paul , Ulemu and Mira the world is changing dont waste tme thinking malaw will use kabanza for whole generation .am telling u only malaw uses that disgusting method in the cities plz work up believe me

  4. look mmene mukutchenera mumakwanitsa ma make up ,kumatchisa zobvala and what soever why? development .malaw 20yrs ago kunalibe kuminula pano bwa ndani akufuna kutsalira nobody *changes*@maggy. Where there is no kabaza pple still survive let mzuzu compete with other cities the very same way mumapangira lero style iyi yatsitsi mawa iyo time out for kabanza#mzuzu kabanza must fall osati nyansizo azikanyamulira zokolora kuminda

 13. akabaza amachoka kumudzi nkumazayendesa zinjinga mtown nkumazapangisa ngozi….mpaka 700 accidents zanjinga,komanso amakonda kudutsa malire amene anawapasa……this time the police was right and deserve Gratitude

 14. ok asiya kulimbana ndi ma Vendor pano ziri kwa akabhaza et kkkkkkkkk koma a Malawi tidzacya liti kukhomererana ndi zolimba zitsulo

 15. apolice akupanga chocho mwezi wanjalawu wavuta patawuni akufuna podyela o$awa$ekelera vindele azolowera kudya thukuta la athu zi$elekwete

 16. Izitu nzodetsa nkhawa ku dziko izi. A kabaza amenewa mukaakhomelela nkuwasiitsa biznes yawoyi, wat else are they going to be doing apart from umbava?? Kenako muzidandaulanso kuti apolisi athu ali ndi zipangizo zochepa, chitetezo chachepa. Zoziyamba dala izi. Bola la zitsiru ngati ili sinnalione

  1. kale amapanga chani its only malawi having such bloodfuckin busness mu city kma dziko langa inu ladzadza ndi ..kaya ndingati chani kaya hmm kapalasa mu city kuposa galimoto*shame

 17. Pali kanamacende kena kake dzinalake mbayani,ndi amene wapangitsa zonsezi amati akalanda njinga amakalipilitsa MK6,200 ndipo amacita izi atavala civilian ndiye pakumakhala povuta kudziwa pakati pa a police ndi mbava,komaso ngati apolice kunoko ali ndi njinga akumaba za akabaza zomwezo kumatumizira abale awo.

 18. A police akupanga nkhaza kwambiri kwa akabanza that’s why, ,,

 19. akabanza nawonso ndi business yawo,apolice yawa mitu yawo siigwila bwino ntchito.akuganiza ngat ndalama anzawo akazipezela kut? munthu abe walakwisa,apange business mukumulondalonda,mukufuna atani? tangoziwani zanu zomadyela anthu amagalimotowa basi………iiiiiih koma alonda athu omwe timawatcha apolisiwa,ndiokanika,sazathekanso!

 20. kkkkkkk koma Atumbuka aaaa Simudzathekaso mpaka munayambisa xenophobia ndi boma kkkkkk mwayambano kutha matha et

  1. Mind u akabaza ambili kuno ku mzuzu ndi a chewa anzanga oti makolo awo ali kuma estate ku rumphi & iwowo akudana ndizolima thus y anangoyamba business ya kabaza

 21. Komanso timakonda kabaza chifukwa amakakutula mpaka pakhomo komwe ukupitako poti ma minibus ambiri amathera mtown koma kabaza amakafika kulikonse

 22. Mbava za a Police. Mzanu uja amene anakhazikitsa gulu la dzigawenga ku Mangochiyu bwanji simunatsire Teargas? Shupiti zanu aPolice. Akabazawo mukawasiyitsa ntchito yawoyo muziwadyetsa ndi inuyo?

Comments are closed.