‘My wife can pay me K350,000’ – Kanyenda

Advertisement
Essau Kanyenda

The veteran Polokwane City forward was heavily linked with a move to either Big Bullets or Silver Strikers but he has completely trashed the rumours saying he is able to make the K350,000 offered to him.

Speaking to a local newspaper, Esau Kanyenda, said he has no plans to play for any local side once his time at the South African club is over.

Essau Kanyenda
Kanyenda: Has slammed Malawi teams.

He also added that he has been offered a job at the club once he hangs up his boots.

“There is a possibility that when I retire, I will get a job (at Polokwane), so why should I blow the chance? I have also heard news that I am demanding K350 000 per month. Even if I retire now, I can be earning that money while just sitting idle and taking my kids to school. My wife can pay me that,” Kanyenda was quoted by one of the local dailies.

Unconfirmed reports pin him Malawi’s richest player having plied his trade in Europe and South Africa since leaving Dwangwa United   some time back.

He started his professional career at Jomo Cosmos before playing for a Russian Club.

Kanyenda is the only player from Malawi to have played   in the UEFA Champions League.

However, both Bullets and Silver have denied that they had an interest in the veteran forward.

Advertisement

612 Comments

 1. Tingokumbutsako ways,kanyenda amagulira team ya Dwangwa utd ma boot 30,walipilira anthu 15 school from secondary to college alindi team ya mpira yothedwa kanyenda fc.Malawi kunyoza palibe zingatipindulire ayi.ine ndimaganiza kuti tisangalara atapeza ntchito ya mpira ku joni konk.chifukwa maduka and mabedi akumayitana ma player aku malawi kupita ku joni eg Chiukepo.malawi ndife a nsanje mpake sitimakonda.Ronaldo cr7 sanapite ku xul but he’s rich.

 2. Just fucken leave him he thinks like is the star while is not but I must remember where is coming from kuno Ku south Africa sikwawo anthu a kunowa sawona kuti ndiwe ndani or kuti who he iye ndim’ Nyasa basi.Kodi nafe timawutha koma sitinakonde coz timadya tsabora tili mafana ndiye tinangoima kusewera mphira ndiye asamayese ngati tonse ife ndimakape eti I said again folk u Kanyenda

 3. Zawonetseratu Kt Munthu Akamakalamba Zeru Komaso Zolankhula Zimakhala Zosalongosoka, Zoonadi Akazi Ake Amamupatsa Mazuna Ndy Nanga Kuma Team Kuli Akaz Kt Akamupatseso Mazuna Ndizoona Kt Only His Wife Ndy Angamuganyulire

 4. Zawonetseratu Kt Munthu Akamakalamba Zeru Komaso Zolankhula Zimakhala Zosalongosoka, Zoonadi Akazi Ake Amamupatsa Mazuna Ndy Nanga Kuma Team Kuli Akaz Kt Akamupatseso Mazuna Ndizoona Kt Only His Wife Ndy Angamuganyulire

 5. Of course Bullets and Silver were too ambitious but there is a better way of turning down the offer than this. Granted he has money and his wife can pay him (for doing what?), but he should have responded professionally. We have seen great players who appreciate the fact that a certain club is interested in their service though they are unable to join the club.

 6. Of course Bullets and Silver were too ambitious but there is a better way of turning down the offer than this. Granted he has money and his wife can pay him (for doing what?), but he should have responded professionally. We have seen great players who appreciate the fact that a certain club is interested in their service though they are unable to join the club.

 7. I think this guy Esau Kanyenda is a very disciplined athlete., hence his financial success. This also has a positive impact on his career. If we had this crop of prayers! Continue working hard Esau. I like this prayer bracket of Kanyenda, Mtawali, Maduka, Kamwendo, Mponda. If Malawi had more footballers of the Kanyenda character, bwenzi pano tili mu top 50 ya Cocacola Fifa ranking.

 8. Koma ndiye wamwanolatu,nafenso osewera wa ku south ayi koma local.Komanso omwe amafuna iweyo ndiye asowa maplayer mpaka azigogo.

 9. Nkazi wakoyo ali ndichani mazoba ngati inu…kutheba mmamenyanso maclub ofoira…mukadafika pa a china Roony,Messi nde mukadanyera mbaletu..mangogwanso ngroud zoba..

 10. Nkazi wakoyo ali ndichani mazoba ngati inu…kutheba mmamenyanso maclub ofoira…mukadafika pa a china Roony,Messi nde mukadanyera mbaletu..mangogwanso ngroud zoba..

 11. Kkkkkkkk Liyadah Slyv Chippie John Tembo Danny Tiya Palichina Enita Bonongwe Guember Jeno Giroud Mayamiko Kalimacheuka Christopher Mbacheche Matengo

 12. What I learnt in life they say,u don’t have to burn the bridges that take u to the other side,in case u will need to go back,Mr kanyenda could just say,”I want an improved package “not saying my wife bla bla bla,like it or not Mr kanyenda in chewa we say,kukada zimabwelela kukhomo,be warned

 13. Kulira kwa retired soldier,then play for the love of soccer not money,actually no club can take you with your performance

 14. Kkkkk,I would like to urge Mr E Kanyenda to eradicate producing such words to the people of Malawi,coz initially he must recall his old days.He derived away from Dwangwa foot ball club,hw much did he earn from this club?This is a time to him to say thanx to his former clubs.We had too much players like Mtawale,Maduka,Mabedi,but these pple did not say such words to the pple of Malawi.

 15. mmmm pamsasa saipitsa,,, before his wife where were he?

 16. Esau ali ndi ufulu kupanga zimene akufuna. Mukufuna mumupangile zomwe iye asakufuna. Musiyeni apange zakumtima wake.

 17. Always i used to say mbuli izi ngakhale ra primary zilibe when aging comes mumabvetsanso chisoni!! So osamatumbwa as if you have PHD. Kapila kakekati? Mind you akadzakuyinga udzatifuna

 18. A kanyenda mwalemera liti kuti muyambe matuktuku amenewa,,,,remember u ascended to that level coz of the same cheap league,let him not behave like a snake that shows innocence when young and it grows it bite even the one who tamed it,,,secondly,leave your wife out of this,, we don’t have appeatite to about her existence,,,, let him God gave him talent to help others,if he doesn’t need those peanuts why not play and donate the orphan children. We hear people with a lot money donate,, but don’t see kanyendas name

 19. Guys, Esau Kanyenda Panopa Ali Pena Pake, Mukufuna Abwele Kuno Just To Use Him Pa Ka Ndalama Kanu Kochepa, Ayi Musiyeni Azipanga Zake, Funani Ma Player Muma Primary School Muwapeza.

 20. Bulutu Iwe. Mesa Unasulidwa Ndi Ma Club Aku Malawi Kuno? Nkazi Wako Akumachindidwa Heavy, Kupanda Zimenezo Bwenz Uli Ndi Ndalama Iwe? Unatha Iwe. Mpira Sukutha Pano, Mbuzi

 21. Bulutu Iwe. Mesa Unasulidwa Ndi Ma Club Aku Malawi Kuno? Nkazi Wako Akumachindidwa Heavy, Kupanda Zimenezo Bwenz Uli Ndi Ndalama Iwe? Unatha Iwe. Mpira Sukutha Pano, Mbuzi

 22. Amalawi ndichifukwa chani sitimvetsetsa zinthu? Munthuyu he’s not stuck in the past, akuyankhula chimene ali lero & akunena zoona, Mulungu ananchotsa pamene mupadziwa inupo anamuyika pena..! Asau sakunyoza! Kungozolowela kudana ndi chilungamo basi

 23. Mmesa asanavaye kunjako ankasewera DWANGWA UNITED ndye pot yabwelera mulig yaikulu.Akasewera imeneyo(dwangwa).koma nkhalamba imenei mpaka itidwalitse mutu?ikagwele

 24. Mmesa asanavaye kunjako ankasewera DWANGWA UNITED ndye pot yabwelera mulig yaikulu.Akasewera imeneyo(dwangwa).koma nkhalamba imenei mpaka itidwalitse mutu?ikagwele

 25. Foolish Kanyenda!! Mpira umaphunzira ku Dwangwa United ndie utichani? Sanakuphunzitse ndi Hule wako ukumuchemelerao wamva? What a fool player!!!!!!!!!!!!!

 26. Foolish Kanyenda!! Mpira umaphunzira ku Dwangwa United ndie utichani? Sanakuphunzitse ndi Hule wako ukumuchemelerao wamva? What a fool player!!!!!!!!!!!!!

 27. Iwe kochokela kulibe ntchito iweumachokela kuti that,s bleu shit u dont know how to open your fucken mouth. Let him talk whatever he want

 28. Iwe kochokela kulibe ntchito iweumachokela kuti that,s bleu shit u dont know how to open your fucken mouth. Let him talk whatever he want

 29. Anthu simufuna kumva zoona.I feel Kanyenda is expressing his mind. From the comments, its clear many do not have am idea as to how much do our clubs offer to the players.
  What he is saying maybe 100% true.

  If he could deny playing for the country…..I would not complain, but I would regret and cry

 30. Anthu simufuna kumva zoona.I feel Kanyenda is expressing his mind. From the comments, its clear many do not have am idea as to how much do our clubs offer to the players.
  What he is saying maybe 100% true.

  If he could deny playing for the country…..I would not complain, but I would regret and cry

 31. Kanyenda anatha uyu,,ngati mumamusata akalowa mumpira amangogwaigwa ndiye asati nyo apa,,moti ogulao angosowa zotenga ,,#asatinyase_galuameneyi

 32. Kanyenda anatha uyu,,ngati mumamusata akalowa mumpira amangogwaigwa ndiye asati nyo apa,,moti ogulao angosowa zotenga ,,#asatinyase_galuameneyi

 33. Because you are there so you can’t play in a league of your home land? Kkkkk glory to be God

 34. If is very true that Kanyenda has said this, Then its very shameful, I may ask him to say withdraw the statement, and apologize to the nation. Sangafananize Malawi teams and his wife ,pipo out there have rich women.

 35. Essau ndakufira heAvy .if u think akudzipopa take a look of our local playerz m,mene akuonekera ,kunvetsa chisoni guyz kikiki limatchuka ndi dzina okudya money ali phe

 36. Essau ndakufira heAvy .if u think akudzipopa take a look of our local playerz m,mene akuonekera ,kunvetsa chisoni guyz kikiki limatchuka ndi dzina okudya money ali phe

 37. Essau ndakufira heAvy .if u think akudzipopa take a look of our local playerz m,mene akuonekera ,kunvetsa chisoni guyz kikiki limatchuka ndi dzina okudya money ali phe

 38. Essau ndakufira heAvy .if u think akudzipopa take a look of our local playerz m,mene akuonekera ,kunvetsa chisoni guyz kikiki limatchuka ndi dzina okudya money ali phe

 39. Essau ndakufira heAvy .if u think akudzipopa take a look of our local playerz m,mene akuonekera ,kunvetsa chisoni guyz kikiki limatchuka ndi dzina okudya money ali phe

 40. Essau ndakufira heAvy .if u think akudzipopa take a look of our local playerz m,mene akuonekera ,kunvetsa chisoni guyz kikiki limatchuka ndi dzina okudya money ali phe

 41. Vuto laife anthu ndilimenelo mpakana kumanyoza choncho kwanu mr esau lemekezani kwanu angakhale mukhumbe kwa america koma malawi ndiwanu tsono ngati inu mukutelo kulibwanji akunja(malawi its our home like it or not we belong there what we should do is to respect ourself then others will do the same )

 42. Vuto laife anthu ndilimenelo mpakana kumanyoza choncho kwanu mr esau lemekezani kwanu angakhale mukhumbe kwa america koma malawi ndiwanu tsono ngati inu mukutelo kulibwanji akunja(malawi its our home like it or not we belong there what we should do is to respect ourself then others will do the same )

 43. Vuto laife anthu ndilimenelo mpakana kumanyoza choncho kwanu mr esau lemekezani kwanu angakhale mukhumbe kwa america koma malawi ndiwanu tsono ngati inu mukutelo kulibwanji akunja(malawi its our home like it or not we belong there what we should do is to respect ourself then others will do the same )

 44. Vuto laife anthu ndilimenelo mpakana kumanyoza choncho kwanu mr esau lemekezani kwanu angakhale mukhumbe kwa america koma malawi ndiwanu tsono ngati inu mukutelo kulibwanji akunja(malawi its our home like it or not we belong there what we should do is to respect ourself then others will do the same )

 45. Vuto laife anthu ndilimenelo mpakana kumanyoza choncho kwanu mr esau lemekezani kwanu angakhale mukhumbe kwa america koma malawi ndiwanu tsono ngati inu mukutelo kulibwanji akunja(malawi its our home like it or not we belong there what we should do is to respect ourself then others will do the same )

 46. Vuto laife anthu ndilimenelo mpakana kumanyoza choncho kwanu mr esau lemekezani kwanu angakhale mukhumbe kwa america koma malawi ndiwanu tsono ngati inu mukutelo kulibwanji akunja(malawi its our home like it or not we belong there what we should do is to respect ourself then others will do the same )

 47. the comment “my wife can pay me 350g” doesn’t make sense and i would rather call it stupid. that z if this is true

 48. Looking at the comments ,it clear most Malawians are absurd what Esau is saying has more sense than ur comments,Is looking at his future beyond football so why should he come to Malawi and become a beggar ine ndilibe polobulemu with what Esau has said.

 49. Guys just pay attention not to insult he is talking wat he can not do and he bears witness on wat he has seen just like that

 50. Kkkkkkkkkkk guys munthu walakwa chani ndimayesa akufotokoza zoona zaumo akusangalalira ngati akufunidwa mpatseni zomwe zingampangitse kusintha maganizo osati kutukwana so chi Malawi chimenecho

 51. Ndipo ndiwe galu ukanakhala star bwenzi uli ku real,man u,arsenal,man city.Timatimu take tomweti tapajoniti umakanika kusewera team ya mupremier monga Orlando,Chiefs koma iwe usandiseketse

 52. Kuyankhula kwa munthu kwa munthu oti adapitako ku xul, sataro,and asonyeza ndi mbuli yo phuzira.tikamati kanyenda szikutanthauza kuti ndi waku jozi, iyeyu,kunyadira polokwane city.team yaku midzi mu RSA?

 53. Wayankhula bwino kumalawi koma kuponderezana. Taonan muli nd ma prayer abwino achina chiukepo, kangunje, fodya, koma palibe chimene mukuwacitila, munthu kumalandira 30 thousand malaw kwacha pe month atan nayo.

 54. Wayankhula bwino kumalawi koma kuponderezana. Taonan muli nd ma prayer abwino achina chiukepo, kangunje, fodya, koma palibe chimene mukuwacitila, munthu kumalandira 30 thousand malaw kwacha pe month atan nayo. Kumaganiza walankhula bwino pamenepa i am on his side

 55. mawa tizava kuti kanyenda wakana kuti sanayankhulepo zimenezi.ndi anthu osandifunira zabwino akunena zimenezi.koma aguluku nyinda inu simuzava ndimaboza.

 56. Palibe amene angamangogwira ntchito wthout benefit ngt Kanyenda akutero basi akuyenera kunyadira ntchito yake,only his wyf can afford it.

 57. east west your home z best, kwa eni kulibe nkuwe, time will come u will go 4 the same money, ziwani kuti kuno ndikumudzi kwanu thawi izakwana mzawapeza mateam amene mkuwanyozawa, think b4 u put things out of ur mouth plz.

 58. Kod inu,akhale player wamphavu akasewere team ya mpulukwane city,si bola azizipopa achina Gaba ndi Ng’ambi,osati kape ngati iwe funk u.Why always ukudana ndi komwe wachokera?

 59. KKKKKKKKKKKKKKK Man kanyenda muli bho kwambiri ma Club aku Malawi ndiosauka kwambiri kupatulapo B4ward MANO nde ukasewele ku Nyasa Bullets azikulipira 35000.00MK zimenezi zingatukule player? osalola zopusa man ndakunyadila

 60. kd inu a malawi24 anakuuzan ndan esau akufuna kt career yake izathele ku malawi kuno? nanga zomwe wanenaz zikuonesa kt mumatnamiza ndi nkhani zanuzo bwanj ngat simungakwanise kuwauza amalawi choonad mungosiya? zikuoneka ngat mwatopa sopano

 61. kd inu a malawi24 anakuuzan ndan esau akufuna kt career yake izathele ku malawi kuno? nanga zomwe wanenaz zikuonesa kt mumatnamiza ndi nkhani zanuzo bwanj ngat simungakwanise kuwauza amalawi choonad mungosiya? zikuoneka ngat mwatopa sopano

 62. Kkkkkkk zivere muntolo Neba. Even if u win a league for 10 consectives u can’t afford to pay him. Boss u r right its high time now in Malawi that pple mst stop thinking that prayers they play soccer bcz they luv to play. These pple they need money to support their families.

 63. Kkkkkkk zivere muntolo Neba. Even if u win a league for 10 consectives u can’t afford to pay him. Boss u r right its high time now in Malawi that pple mst stop thinking that prayers they play soccer bcz they luv to play. These pple they need money to support their families.

 64. Vuto la munthu, akaona kt zikuyenda amaiwala komwe wachokera. Wayamba matama apa. Shame on u, remember your background first otherwise God can punish u for your words.

 65. Vuto la munthu, akaona kt zikuyenda amaiwala komwe wachokera. Wayamba matama apa. Shame on u, remember your background first otherwise God can punish u for your words.

 66. Anthu mukuwona ngati tikumunyozanu sitikumunyoza tikufuna timuphunzitse aziyakhula bwino ndi kwao ku malawi adzatipeza imagine ma player amzake akumayiko ena kumva mmene wayakhulira iyeyu samuseka kuti wanyoza kwao ndindani player munamva kuti wanyoza dziko lakwao as kanyenda done? Plz kanyenda try to edit your speech when u want to talk a malawi watikwiyitsa samatero ayi pomaliza mkazi wanu amakuchitani nkhaza amalora muzikaswewera mpira kumavulala iye ali ndi dola?osamangokupatsani bwanji plz dont do it again tawonani amtawali anali komko pano ndi a coach coz sananyozeko and tinasangalala naye amalawi inu zomwe mwapangazi ndi mmene akubwelera ma comment inu mukasiya kusewera mukuganiza ndani mmalawi adzakukondeni? Think

 67. Malawi is not South Africa. After all, there’s no one anamuuza kuti adzasewele BB kapena Silver Strikers.

  Koma kulankhula kwa ndithe ndithe, Nanthambwe anadzitengela.

 68. He is stupid after all he does not play impressive football.If he was playing for Downs,Pirates or Chiefs i would give him a round of applause but Polokwane just making me laugh hahahahahaha

 69. I don’t know if indeed this remarks are coming from him kanyenda if so iam deeply disapointed with him when you reach that age in your career going to play home is not about money any way it is his choice we can only say so much no need to cruxify him football is a short career him wnt to make money while he can

 70. footbal is a carear its not educathon. it goes with performance. when you are failing to back-up your performance then you end to the extent that no any local club needs you. so, kanyenda should close his mouth

 71. footbal is a carear its not educathon. it goes with performance. when you are failing to back-up your performance then you end to the extent that no any local club needs you. so, kanyenda should close his mouth

 72. Kwinaku ndiye kunyadwa mwamva iweyo kutani ? ndalama kwambiri. Ukutchula mkazi wako bwanji kukongola kwambiri pali chani pamenepo ndalama zake ziti si jon ndi yomwe yakupangitsa iwe ndimadana ndi zachamba ine

 73. Kwinaku ndiye kunyadwa mwamva iweyo kutani ? ndalama kwambiri. Ukutchula mkazi wako bwanji kukongola kwambiri pali chani pamenepo ndalama zake ziti si jon ndi yomwe yakupangitsa iwe ndimadana ndi zachamba ine

 74. Kwanu Nkwanu Amwene Mthengo Mudalaka Njoka Kod Achina Mtawali Kina Sanali Odziwa Mpira Ndie Inu Mukuyankhula Mokhuta Coz Mwameza Ka Ndiii Musaiwale Kut Chouluka Chingauluke Bwanji? Koma Chidzatera Mutipeza Mutakalamba Or Maclab Mukuwanenawo Osakufunani Nkomwe Or Even Kut Mwina Mukakhale Borera Ili Ndi Dziko Watch Ur Mouth When Speaking Mr Kanyenda Shame On You

 75. Kwanu Nkwanu Amwene Mthengo Mudalaka Njoka Kod Achina Mtawali Kina Sanali Odziwa Mpira Ndie Inu Mukuyankhula Mokhuta Coz Mwameza Ka Ndiii Musaiwale Kut Chouluka Chingauluke Bwanji? Koma Chidzatera Mutipeza Mutakalamba Or Maclab Mukuwanenawo Osakufunani Nkomwe Or Even Kut Mwina Mukakhale Borera Ili Ndi Dziko Watch Ur Mouth When Speaking Mr Kanyenda Shame On You

 76. Esau kanyenda simtumbuka and esau samapanga matama amalawi mitima yanu ndiyotani nzanu walakwa chan mukhalila yomweyo mzanu akuphaka lyf patheba olo akakhala kuti akuchokela pa bench anakuza kuti samalandila mpilatu ndintchito umbuzi basi mmafuna azizalandila 100:000 kwacha pamwezi anthu openga

 77. Esau kanyenda simtumbuka and esau samapanga matama amalawi mitima yanu ndiyotani nzanu walakwa chan mukhalila yomweyo mzanu akuphaka lyf patheba olo akakhala kuti akuchokela pa bench anakuza kuti samalandila mpilatu ndintchito umbuzi basi mmafuna azizalandila 100:000 kwacha pamwezi anthu openga

 78. Koma Kanyenda yu akanangoka mwaulemu osati mpakana kuyankhula those kind of words…he is a Malawian then he cannot speak that to his fellow Malawians…adzawafuna amalawi2.

 79. Koma Kanyenda yu akanangoka mwaulemu osati mpakana kuyankhula those kind of words…he is a Malawian then he cannot speak that to his fellow Malawians…adzawafuna amalawi2.

 80. Why can ublame him if he is not interested ,john maduka never played for alocal club after plying his trade at bloemfontein celtics he is now working at axlub in rsa leave kanyenda alone he served malawi alot and he is respected person in mwan soccer

 81. Why can ublame him if he is not interested ,john maduka never played for alocal club after plying his trade at bloemfontein celtics he is now working at axlub in rsa leave kanyenda alone he served malawi alot and he is respected person in mwan soccer

 82. Hahaha i would say thd same if this was me. In short this is to tell the football association that recruit energetic boys and turn them into homeless people on tour. No food no shelter no allowance. And you still want him to praise you? Those saying he is not giving back to the community well remember he is a veteran he has played for local but ended up being used as well. Those saying its not good to play for money well go and do this charity game then. For him this is a job he has a family to look after so yes money is important. Even international players all they play for is money coz it’s their career their job

 83. Hahaha i would say thd same if this was me. In short this is to tell the football association that recruit energetic boys and turn them into homeless people on tour. No food no shelter no allowance. And you still want him to praise you? Those saying he is not giving back to the community well remember he is a veteran he has played for local but ended up being used as well. Those saying its not good to play for money well go and do this charity game then. For him this is a job he has a family to look after so yes money is important. Even international players all they play for is money coz it’s their career their job

 84. Oooooo I thought football is a carier but dn I m shocked to know that to dis dude its a business aeeeee pasavute mr kanyenda go to ur wife nd b driving ur kids to school!aaaaaaaaa malawi has gud players who play in honour of their country nt for being rich

 85. Oooooo I thought football is a carier but dn I m shocked to know that to dis dude its a business aeeeee pasavute mr kanyenda go to ur wife nd b driving ur kids to school!aaaaaaaaa malawi has gud players who play in honour of their country nt for being rich

 86. Mpira wake uti omwe amamenya kanyendai chilichose chili ndi thawi kukusowa ndikuvomeleza zoti anatha kale wangosala zina lokha bax, azikupasa ndalama yoseo Madara ngat iwe kapena azimenya ekha ground lonse. Alipo okutha kuposa inu koma sakulira zambili.

 87. Mpira wake uti omwe amamenya kanyendai chilichose chili ndi thawi kukusowa ndikuvomeleza zoti anatha kale wangosala zina lokha bax, azikupasa ndalama yoseo Madara ngat iwe kapena azimenya ekha ground lonse. Alipo okutha kuposa inu koma sakulira zambili.

 88. With such behaviour malawi will never grow up on football,I thought players like him he must sacrifice to the nation to improve football.what will hapen when one day will want to stand as FAM president or as Sulom president

 89. With such behaviour malawi will never grow up on football,I thought players like him he must sacrifice to the nation to improve football.what will hapen when one day will want to stand as FAM president or as Sulom president

  1. I think those who claim to know something would usually make a change when they are called to help on international match. But is this the case with our so called professional players?

  2. I think those who claim to know something would usually make a change when they are called to help on international match. But is this the case with our so called professional players?

 90. I have no right to judge .only God who brought his one and only begotten son Jesus Christ to die for us can judge.Ndani amene anganene kuti sanachimwepo ayimike manja .alemekezeke mulungu wamwamba mwamba.

 91. Look your fellow good players, Yaya,Messi,CR,Hazard,Rooney,,,they are playing for Aumphawi,Amasiye,Ovutika of their countries.Ukanakhala kuti ndiwe Dolo,ukanathandiza club yako Dwangwa united koma Ee ndiwe zo,o,baaa, Dolo la

 92. He is talking shit all the players go back home just to give back the community ,he is just selfish ,he played everywhere but he is still poor if he can act so selfish,we saw big names players the likes of shoes ,Benni Macarthy ,Mc fish ,kamwendo who made their trade in overseas but still came bck ,they never played for money, Here in south Africa he is still playing the small team that even spend more days in the bench yet he can still talk nonsense, anyway for me inever been his fun and idnt see him as aworld class player

 93. Zoona big kanyenda mpila wakkumalawi bola mulimi amakhala ndalama nanga 10000 upanga nao chani bolaso kukhala gaden boy pajoni amakupasa abavu 180000

 94. there is no need to play again here, our local players are not insured

 95. Sometimes it’s good to accept..It’s his right to speak on his talent and those are facts he shared with the reporters…Why are malawians bitter?he’s the only player that made it to UEFA..be proud he put this country on the map and other young players can be discovered

 96. Kkkkkk wayenela kudzimva coz akusungunula Rand but akuyenela kudziwa komwe wachokela.Awa ndi magulu a ana amene amakana makolo awo akamayenda ndi ndodo.

 97. koma guys kumkonda mkazi paka kulowa ndi mutu omwe eee stop your fucking shit akazi amliyenda angakulipire chonchi iweyo iwe ndani wanyera mbale yodyeramo iweyo

 98. i dont even blame him this z alwz how ageing pipo tok….amava ngat 3 500 paja nkhalambazi musaiwale zikatsala pang’ono kumwalira makutu amagothatu

 99. PANYO PAKE NDE OSAKHALA KUMAMENYA KONKO BWA? Galu we don’t need u kuno mbuzi. Kp playn for ur wife azikulipila zat money

 100. Maniwa sanayankhule bho penapake….kmaso penapake ma club akumalawi kuno care imabvuta ndithu…more money shld be invested in football…zimakhala zosevtsa chisoni kuwaona ma player odziwika bwino akungotuwa midzimu ena kumangodzifela….akapeza mwayi anthuwa safuna kubwelaso after akamakumbuka zipsinjo ayaya

 101. Just follow what peter mponda is doing. Gud development to the country. But you NGANGANGA kusewela mpira koma mmadziwa kuti you exceeded the xpiry date.

 102. Timakupatsa ulemu koma zokha walakhulazi ayindithu,pajon pano mukuferanso pa betch full time komaansi kakalabu kamene mukuzipoperako kakutulukaso mu psl kakubwelera ku division and polokwane city singafanane ndi wanderers kapena bb.mkazi wako ndindani kuti akakulipire ndalama imeneyo kapena ndihule umamu user.musamathe mawu kupolokwane mukulandire R7500 dolo gaba muhango inuyo ayi man munali kalero

 103. Nde chamba chimenecho palibe team kumalawi imene ikukufuna, iweyo watha chifukw chikha kut ukumenyabe bwino sibwez ukubwerera, team yakeso polokwane mkumati ndine professional? Kagwere uko

 104. Kuyamikila kwa amalawi ndikunyoza koma iwo alive ndi buti yomwe musiyene Essau akhale Essau ndani sakuziwa kuti ndikatakwe mbuzi za athu kukhalira kunyoza.

 105. Kuyamikila kwa amalawi ndikunyoza koma iwo alive ndi buti yomwe musiyene Essau akhale Essau ndani sakuziwa kuti ndikatakwe mbuzi za athu kukhalira kunyoza.

 106. Olo osazabweraso kuno tlibe nawe deal shupit kuda ngat wafukulidwa padothi

 107. Kanyenda wayiwala komwe wachoka eti team yomwe mumamenya ku SA team yoti kunoko ndi Epac chifukwa singafanane SS OR BB N NOMA unatha iwe timakana kuti uzikhara chifukwa chake even Flames imakusiya

 108. Kunyoza pomwe wachokela,kamwendo bwanji?inu mwapambana chani osamatumbwA choncho,mwachokela pati kuti akazi anu apeze yokulipilaniyo?

 109. Mr ngatidi zili zoona kt mwayankhula choncho,simunapange bwino moyo umatembenuka nokha ndikukhumudwanso.

 110. You are fucked up Kanyenda and Iwas shocked with the roumer that Bullets want to employ you,I guess its just waste of money for aretired player like you! At Bullets we got young talented players that they are managing to give us Champions leaugue and plays better than you. You have failed at Polokwane city and always you were on the bench that means you are fucked up, so if any club in Malawi is interested with you even if they can afford K80,000 every month its much better for you! So dont be foolish in complaining like that or telling the nation about your wife pliz be humble like Asamoa, Yaya, Messi and Ronaldo.

 111. Umphawi wake umenewo mungamukwanise????.ngat mukukanika inu kulandira mokwanira,,komanso amakuchedweseran ,,,,nanga kuli bwanj iyeyo

 112. Tamandani Wazayo Phillip Nsaliwa also played in the Champions League with AEK Athens so maybe not entirely accurate to say Kanyenda is the only Malawian player yo have done that.

  1. I know where you are coming from that’s why I said it’s not entirely accurate but I think it’s fair to say he is still Malawian.

  2. I get your point. The story says: “Kanyenda is the only player from Malawi to have ever played in the Champions League…” Quite wrong indeed. Nsaliwa, though Canadian, is also from Malawi. Kudos!

 113. Nde osangokhala pansi bwanji nkazi wakoyo azikulipira ulere? Kudzimva sugar loteleko yet wachokera ku ma club ukuwanyozawo…anthu osafuna kutukuka dziko lanu inu…too much pride

 114. I doubt if someone like Mr E. kanyenda can speak like that, but if it is really true then he is supposed to apologise because malawian teams are the ones who lifted him up to the 350,000 he is claiming today, were the ones who managed to pay him nicely while holding the ladders to the 350,000 he is mentioning now, atleast if u could say 350,000 USD

 115. Atumbuka ndi choncho. Boasting too much. Tinakuzolowerani

 116. I dont blame him for what he has said, he has spoken his mind more over zikuoneka kuti sanapemphe kuti akufuna kusewera ku Malawi ma team athu phuma kobasi, mpaka kuneneratu salary munthu asanaonetse chidwi? Kuyamba kunkanganira asanapemphe? Wakana wachita bwino kafuneni ma player mmidzimu kokabudula or kosanthe mukawapeza. Leave this man alot, he has served malawi nation kwakana. More over welfare ya ma player omwe anapuma sioneka bwino. Amadzifera no care. Khala konko Esau dzipanga ma business ndikutukula banja lako a Malawi adzangoku user nkukutaya awa, alibe khalidwe.

 117. @kanyenda mpira wake utiwo umene mumamenya inu mufuna muzilandira Nawo 1million? usandikwiyitse chiyambileninso kumenya national team sunakwaitse kuchinya zigoli 20

 118. Anthu awa ndi aboza,ndinu nomwe mumati Esau akubwera azakhale coach ku Dwangwa united,inu nomwe mumati akupita ku bullets kapena ku silver and lero mukulankhulanso izi.Ai ndithu ndkwiya nanu tsopano chifukwa mukuchulutsa maboza

 119. Kanyenda ukuyankhula kwambili kuno ndiku Mw palibe team yomwe ingakupatse ndalama zopotsa Mk500.000 ngati simukufuna kuzamenya mpira kuno bwerani muzizangokhala osati kumatha mau apa

 120. Mtima wa umphawi unawalowa awa. Chili chonse awelengele ndalama mpaka change cha ndiwo chomwe amawabela akazi awo. Mxiiiii after all munathanso

 121. ndi kape ameneyo munthu alwz pa betch bas fwefwefwefwe anzanu anachoka kwa azungu nkumazasewera ku mayiko akwawo not tht they want money no but bcz they love their country n dnt dare to at evn one point to play for alocal club

 122. Anthu ananu mumangonyoza koma 350 ndiyochepa abulets munyanya player aliyense akangobwera mumat wanu kanyenda nd dolo o ndili ine osalola munthu uzikhala nd clas osamangot uzicheeper

 123. BEANCH ikumupha pa ntheba kkkkkkkkkkkkk bwanji osangoti ndantha i cant play anymore,ana ku MALAWI akupha chikopa more than you after all no club wants you here ma player abwino tili nawo kale………

  1. He cant fit in any other team in RSA as he is now,nthawi yake inantha and u said he is rich,wat do u mean? kuli ma player olemera kunjaku koma sanayambe alankhulapo nyasi ngati izi,e.g #RIVALDO,anabwera kudzamenya kuno ku africa osati pofuna ndalama koma kuukonda mpilawo,now he is playing in a local team in his mother land so who is #kanyenda? wapangapo chani choti anthu nkuchilodza? ndi league yanji anatengapo yolodzeka? shame on him.

 124. Mnnnn mukanakhala adolo bwenzi muli ku maiko akunja omwewo man;vomerani kuti munatha basi.wachikulire pano ndi #GABA mudzimpatsa ulemu

  1. Bwanji osakutenga matm akutheba siwa theba iwe unganyoze dzko lako iwe walemela ndDwangwa iwe yaku mw mmesa upte ukamenye mu swasea cty ndekuli ma dolo nt wthdrw ur sttment

 125. Cheap talk, just reject the offer than to down play your country like that.Remember that you got your break thru while playing in Malawi not in your ‘Wife’.Have some respect please i berg!!

 126. Olo ku polekwane city umakhalira panja Jomo sono anakuwuza kulibe malo ku cosmos. Osangoyamba kumenya dedza bwanji kuti mwina ndi kubwerera mwakale osati za ndalamazo

 127. Lero wayamba kunyoza komwe wachokera…..ngakhale azigogo kalero amakutembelera ukachita mwano oterewu. #foolishman

 128. Ukanat umamenya kaizer chiefs kapena pirates nkanat ndiwe dolo koma polokwane hahahaha chimoz moz bangwe madrid

 129. Akanyenda mumalandira zingat ku DWASCO inu?ndipo mkazi ukunenayo banja lot m’makhalira kukangana tsiku ndi tsiku angakupatse ndakama?

 130. Munthuyu sakunama palibe club imene ingakwanise kumulipila kumalawi .player wakumalawi akulandila less than hundred thousand kwacha.. Imene ili r2500 . Ndindani player wakuno ku south africa angalandile ndalama imeneyo . Pamene kuno player akuyambila pa r20,000 imenene ili million kumalawiko

 131. Kanyenda Anakakhala Kuti Ndi Dolo Bwenzi Ku Nation Team Asakumusiya Bwenzi Game Ili Yonse Akumenye!! Akhale Ndi Umanyaka Wakewo.. Akhale Dolo Osawina Barllon’di Oh Award?! Mthakwa!!!!

 132. Sinkhani yomunyoza poyankha yimeneyi ayi, tivomeleze palibe club yingamupasedi ndalamayo, ngati boma likukanika kulipila anthu ma leave grant ukuganiza club yingatenge ndalama zonsezo?

 133. What happened to the word ”GIVING BACK TO THE COMMUNITY?…this guy needs to grow,We supported him from young age but look at him today?Bola tizingochemelera china Ronaldo ndi Messi omwewa basi.

  1. Which grass?East or west home is best.They must come home and establish businesses and employ people.Hw long will he be in forein countries?Eish man.

 134. Malawian players get up and fed up in s.a and still tolking shit u aint even on standard bull shit

 135. Aaa,Esau ukayamba nawe kutokota motelo ulemu wako utha kwaife mtundu wako ukhala ngat munthu wandale oti anayamba bwino kumaliza ndkuipa

 136. That’s the problem with u guys…u do everything for money..Benni Mac Carthy,who is good in everything than Essau joined pirates who were not even paying 10% of the money he was getting in Europe …learn to do it for the love of the game,it’s not about money always

 137. Hahaha koma nde pompous tu. Ma local teams nonse #muisovenge

 138. Kaya uli ndi ndalama ndizako ndi ana ako pano nkhani ndiyofuna kudziwa dzimene uchite koma matama thooo ndindalama zakadzi ako tituma anthu akamubele tisaname.

  1. Iwe unayamba wagwilapo k50.000 yako-yako yopandamo chenje chawina? mpila amapindulisanji ma bubu ngati amenewa kkkkkkkkkkkkkk koma iwe!!!samala pakamwa pakopo wamva, Truck driver ndi ntchito zamabig mphwanga

  2. Iwe unayamba wagwilapo k50.000 yako-yako yopandamo chenje chawina? mpila amapindulisanji ma bubu ngati amenewa kkkkkkkkkkkkkk koma iwe!!!samala pakamwa pakopo wamva, Truck driver ndi ntchito zamabig mphwanga

 139. Man @kanyenda .musathe mawu kwanu ndi kwanu mnthengo munalaka njoka ndalama ukuyichepetsayo kwa anzako ndiyambiri ndiye ngati sungakwanitse timangokana osati mkazi wako akhonza kumakulipira thats nonsence

 140. U can play just for the love of the game not for money, Ben Macthy made alot of money over seas back he come back home and play for Orlando Pailates even John shoes did the at at Kaizer Chiefs.

 141. Kulakhula mopusa uku,, osangolakhula mwaulemu kuti sukufuna bwanji than kumanyoza azibale ako,, lakhula manyi akowo uzatipeza kwanu ndi kwanu

 142. zopanda umbon bcz mu2 woganiza bwno sangatuluse mau amenewo…… wachokera kt iyeyooo ?
  it miz akupanga compare ma team aku mw nd mkaz wake hahahahaha………..

 143. Mr Kanyenda akanangokhala pansi ngati nthawi yawo yakwana kapena angodikila Polokwane City yo iwapatse ntchito.

 144. Unatha iwe zachamba basi…..ukamati palibe local club ku Malawi ingakwanise kukulipira mpirawo unauphunzira kuti mmesa ndiku Ma local club komweko?…….ukuona ngati ife tinga kudandaule eti?….You mast think twice b4 you say!

  1. KANYENDA IS STUPID,Chikhala dolo akanabwera azizamenya ulere or kulanda wat ever angamupatsecho ngati kunthokoza pa support imene ngati dziko takhala tikumupatsa.tell him kuti kuli achina #chiukepo kuno ndi ana ena omwe #golo siliwaonera kukondwa………….akagweeere uko ameneyo #WANDIKWIITSA_KWAMBIRI

  2. nkhani siyoti anasewerapo kapena ayi chilungamo ndi choti kanyenda doesnt have love for his local clubs they are playes that so love they local clubs and give back to their communities that will rather accept peanuts to show love for the locals club eg carlos tevez went back to his boy hood club boca juniors from juventus while juventus wantded him to extend his stay,to be honest GREED is the thing that is driving kanyenda the wrong way

  3. Ine ndi mapanga za Information Comminication Technology palibe chifukwa choti ndikafune kusewera mpira koabe ukamufunse Ccta wako ngati nthawi yomwe ndimkamusewera ija sindimkamukwanisa….this is going to: Cliford mponda nd james jenyana Phiri..??????

  4. zimenenso amamenya ku plokwane city zo kkkkkk bolanso Vambuena wa ku france uja amantha kapena nditi mwanyama akuuthanso kkkkk

  5. Ndikuti anatha kalekale…..panopa sakumvekeranso ku Polokwane amangomuika pa sub…Bola Gaba atamatero zikhonza kukhala zomveka…..⚽⚽⚽⚽⚽

  6. Komanso kuno akusewela ka team kochepa kwambili, kapena kamalilpira achina R5000″ he is talking sh**t he isn’t a profic as well.

  7. Komanso kuno akusewela ka team kochepa kwambili, kapena kamalilpira achina R5000″ he is talking sh**t he isn’t a profic as well.

  8. Malabwanya enieni a player man ….machine ndi awa osati kanyenda wanoyo ..matama basi…Walemba zili pachithunzi chi nangandiine⚽⚽⚽⚽⚽

  9. Aaa Man Tinene Zoona Kanyendayu Ngati Sakufuna Kusewela Ku Malawi Akhale Tilibe Naye Ntchito Munthu Wachokela Mu Dwangwa Utd Aziti Palibe Local Ingamukwanitse Mbuzi Imeneyi Eti Chisiyeni Fotseki

  10. Kodi inuyo mukadakhala Kanyenda mukanabwera ku Malawi kumazalandira ma peanuts ndi Kwacha yathuyi ikungogwa tsiku ndi tsiku? Put yourself in His shoes first before imposing what you think should have been his decision.

  11. Kodi inuyo mukadakhala Kanyenda mukanabwera ku Malawi kumazalandira ma peanuts ndi Kwacha yathuyi ikungogwa tsiku ndi tsiku? Put yourself in His shoes first before imposing what you think should have been his decision.

  12. Sopano umati tikadapita kuti poti kwathu ndikonkuno….anthu sanapitepo ku UK ndikubwerako kumazakhala kuno kwathu……bwanji akamwalira kunja kwawoko amawatumiza kuno kwathu osawayika komweko, siku sonyeza kuti za kwathu kuno ndizopambana kuposa zakunjazo..ngakhale ndi manda omwe pamodzi ndi ma loca clubs….iwe ukuona bwanji?

  13. Sopano umati tikadapita kuti poti kwathu ndikonkuno….anthu sanapitepo ku UK ndikubwerako kumazakhala kuno kwathu……bwanji akamwalira kunja kwawoko amawatumiza kuno kwathu osawayika komweko, siku sonyeza kuti za kwathu kuno ndizopambana kuposa zakunjazo..ngakhale ndi manda omwe pamodzi ndi ma loca clubs….iwe ukuona bwanji?

  14. He doesn’t have to, stay where your bread is buttered Kanyenda. Just like everyone else is looking for greener pastures these days so too can sportspeople.

  15. sorry my dear nomatter what bread is buttered there but what we need is to show that we are apriciating for being malawians and we are aproud for our own indigineous things…..and how many people were dead beacause of eating Mandasi opaka mapeyala instead of buttered bread don’t you grown up of eating chinangwa and mbatata????….????

  16. You think who are you ….to say fonso labwino…..Iwenso ukundifunsa zo sewera ku ma local clubs ..iweunasewerapo ku ma interational clubs ko…hahaha???

  17. Am still reading and Cheking all replys just wait you will get what you deserve to due to the way you have reply….inside Billys Comment….very soon I will start giving you hampers….koma awiri amene anachita reply moyambilira ziwaonekera okhapamapeto azonse …..???

Comments are closed.