Chakwera apologizes to Malawians for MCP’s atrocities

Advertisement
Lazarus Chakwera

Opposition Malawi Congress Party (MCP) president Lazarus Chakwera has apologized to Malawians for the hardships they faced during the era of the party’s founder Kamuzu Banda.

Speaking during the burial ceremony of one of Malawi’s founders, Rose Chibambo, Chakwera apologised to those who were forced to leave the country.

Among the exiled sons and daughters of Malawi was Chibambo who fled to Zambia after being taken as a traitor to the state and threat to national security.

Chibambo and others had opposed Kamuzu Banda’s decision to charge for health services and to move slowly in Africanisation of the civil service. This was coupled with a general feeling that Banda was becoming increasingly autocratic, leading to the 1964 Cabinet Crisis.

Lazarus Chakwera
Lazarus Chakwera;Made the apology.

Chibambo and her family faced constant harassment from MCP loyalists until they fled to Zambia in 1965 where they faced the challenge of starting a new life.

When her husband Edwin Chibambo died, former Zambian President Kenneth Kaunda offered a plane to carry his remains to Malawi but Rose Chibambo insisted on burying her husband in Zambia for fear of facing humiliation in her motherland.

Late Chibambo returned to Malawi in 1994 after the country adopted multiparty system.

Former President Bingu wa Mutharika honoured Chibambo by naming a street in Mzuzu City after her and having her face on the country’s K200 banknote.

She died in the early hours of Tuesday, 12 January, 2016 aged 87.

Advertisement

246 Comments

 1. Anazunza a Malawi for 30 years (1964-1994). Muyenela kupepesanso for 30 years ( 1994 – 2024). Pamenepo mpamene a Malawi azakhululuka. Koma chifukwa choti mmukazimvabe u MCP kapena udhuli. Tipanga assume munayamba kupepesa 2004 after mutaluzanso zisankho. So from 2004 kupepesa for 30 years kuzatha 2034. Pamenepo muzawina inu a MCP. Bola zizikulu nthawi imeneyoooooh zisazakhale ndi nkwiyo wozizunzila makolo awo. Full stop

 2. Anthu Amene Mukupanga Comment, Mulibe Mzimu Okhululuka. Ngati Mukakanika Kutero, Mulungu Angakukhukilen Mangawa Anu? Zoti Adzalamulira Ndan Kaya Mcp Sidzalamuliranso, Izo Ndi Zina Koma Nkhan Apa Nd Kukhululuka. Osamangopsa Mtima Zili Zonse. Tiyen Tiende Limodz Posatengela Ndale Kutukula Dziko Lathu. Ndizakhala Osangalala Kuona Wa Mcp, Dpp, Pp Kaya Udf Kukhala Pamodzi Ngat Amalawi Kugwirana Manja Kutukula Dziko Lathu. Zakale Zatha Taona Zakhala Za Mtsogolo.

 3. most of, all things we use today anali great kamuzu schools roads hosptalz…oipa ndaawa akuleepera chitukukowa koma bizy kuba..tembo ndamene anali gangster

 4. Mtendere ulikuti pano,oredy pple r running away frm ths countrys hardships and u call that mtendere?pple are forced to do domestic work in RSA and they are subject to alot of painiful circumstances that dont occur here,,yet we ve what u call a pieciful country,,it was better those days,,there was food, money with value

 5. Kunalibe mavuto nthawi imene ija. Amavutika ndi amene amalimbana ndi boma. Lero olo ukhale mu blangete mavuto kuchita kukufunthukula. We used to walk long distances usiku opanda kuopa munthu, today we fear kuyenda masana sana. Those were the good days before the vocabulary of corruption came in.

 6. thanks to chakwera it takes a very strong man to say sorry my grandfather was a victim of mcp on his part i say thank you some we regard you as weak

 7. Kodi mumakhala ngati ndi ku Malawi kokha kuno kunali ulamuliro wankhaza bwanji zaka zambuyomo??? many countries suffered the same thing apaa zaChamba basi Viva Chakwera Viva MCP Kuchaso pompano !!!!!!!!!!!!!!!!

 8. Don’t involve Kamuzu on your silly mistakes so that we can vote for you even that time the use of cards had a reason and when lllovo wants to raise the price of sugar per kg Kamuzu used to visit the Company for a talk now see the price of sugar,does anyone bother to visit the lllovo sugar company to ask why? Its its hard to understand that even the so called MPs they are their just to fulfill their family needs,they don’t care about other families,God isnt sleeping will punish everyone of you according just wait and we are watching you muli otanagnidwa ndi chitukuko madera a anzanu koma dera lanu anthu akuvutika nkhani ya madzi,magetsi ngakhale fertilizer yemweyu kuti munthu apeze thumba limodzi kodi achinyamata omwe anakuvoteraniwo mukuganiza kuti sakuona kumbukira nthawi ija pamene sumumagona kufuna kuti muwine lero mwawina mwaiwala chitsime chomwe mumamwerapo madzimudanagure zinthu zonsezo samalani ili ndi dziko mmawa muzalira.

 9. Don’t involve Kamuzu on your silly mistakes so that we can vote for you even that time the use of cards had a reason and when lllovo wants to raise the price of sugar per kg Kamuzu used to visit the Company for a talk now see the price of sugar,does anyone bother to visit the lllovo sugar company to ask why? Its its hard to understand that even the so called MPs they are their just to fulfill their family needs,they don’t care about other families,God isnt sleeping will punish everyone of you according just wait and we are watching you muli otanagnidwa ndi chitukuko madera a anzanu koma dera lanu anthu akuvutika nkhani ya madzi,magetsi ngakhale fertilizer yemweyu kuti munthu apeze thumba limodzi kodi achinyamata omwe anakuvoteraniwo mukuganiza kuti sakuona kumbukira nthawi ija pamene sumumagona kufuna kuti muwine lero mwawina mwaiwala chitsime chomwe mumamwerapo madzimudanagure zinthu zonsezo samalani ili ndi dziko mmawa muzalira.

 10. Olo mupepese ku ntundu wa amalawi lero mmbuyo monsemu mudali kuti kuyambila mchaka cha 1994 ena mwa ife tidataya mabanja athu katundu wathu angakhale malo amene lero nkumati nyong’onyong’o za utsilu abusa achakwera komanso ndi ime poyera pano munthu kusiya nseu nkumayenda mthengo nkupenga zoti tidzamangidwe nyakula mmmm ife iai kaya inu anzathu apakati koma kuangochi tidaona mbonaona ndi agalu amenewa zankutu

 11. Olo mupepese ku ntundu wa amalawi lero mmbuyo monsemu mudali kuti kuyambila mchaka cha 1994 ena mwa ife tidataya mabanja athu katundu wathu angakhale malo amene lero nkumati nyong’onyong’o za utsilu abusa achakwera komanso ndi ime poyera pano munthu kusiya nseu nkumayenda mthengo nkupenga zoti tidzamangidwe nyakula mmmm ife iai kaya inu anzathu apakati koma kuangochi tidaona mbonaona ndi agalu amenewa zankutu

 12. Tikaonetsetsa mavuto mdziko muno akuchuluka kwambiri paulamuliro wa Dpp,udf ndi Pp anthu amasangala koma peter ndiye uve weniweni bolaso Bingu.

 13. Thats troo man ndipo chipani chimenechi kuti chidzawine ayanjane ndi anthu achigawo cha pakati ndi kumwela osati ku mpoto kokha.

 14. Ndakhala ndikudikira apology imeneyi for a long time. Anyway, kukhululuka ndakhululuka koma mabala ndiwo akupweteka. Tisaweluzane, oweluza ndi mwini wake Namalenga, amen.

 15. PALIBE ZOTI CHAKWERA APEPESE NGATI ANAPEPESA NZERU ZAKE NDI ZOCHEPA.KAMUZU ,TEMBO SANAPEPESE.ALIYENSE ANAKUMANA NDIZOKHOMA

 16. muwasiyire a Tembo ndi anzawo ena kupepesaku osati inu bwana chifukwa mwina mu nthawi imeneyo maganizo oti mudzakhala a Pulesidenti a Mcp mulibe

 17. Apology has been accepted and he also need to be told that Malawians will never again be taken for granted by allowing Mcp to rule us again.The venom that was left by Kamuzu Banda is still ruling the MCP PARTY.

 18. Ngakhale unyengerere anthu mwa mtundu wanji kaya ndi kampeni,Bakili ananena kale kuti olo wina atandithira doom mkamwa sindingavotere mcp.a Chakwera opposition yakuyanjani basi

 19. ATCHEYA ANAYANKHULA MAWU N I QUOTE Anthu openga mwapanga bwanj?john tembo z a big crook,crook,munthu oti mmanja mwake muli magaz angakhale president,anatenga agadama kupita nawo kumwanza kuthambani kukawapha,anatenga msomali kumukhoma gadama pamutu ndipo gadama analila uku atafinya kolona wake a tembo mukundiphelanj?nde munthu ameneyo angakhale president?mwafasa kunamiza a malawi mwat kwacha,kwacha,kwacha tingavotele tambala wakuda ife?chipani cha mcp sichizalamula malawi NEVA,big crook,kkkkCHAKWERA UKUTAYA NTHAW KUPEPEXA ZICHAN

  1. Don’t be misled here CHAKWERA is not Tembo or Kamuzu. MCP 2019 BOMA

 20. kkkkk.. apology my foot….. Its too late…. No more turning back.. kumanda sabwerera.. U guys in mcp idont see any one in your camp rulling this country.. NEVER! my God is alive and he wont let it happen!… we are moving with time…. we hv 3years and 3months, and 16 days before campaigns closes in 2019 election but no rally has been held inthe south by this mcp ruler and what we hear is about Dowa, ntchisi, mchinji, Lilongwe, Rumphi and u expect to win avote inthe south which is ur determiner inthe next election. Idont think u can!…. Once more u should come to the south and apologise to the people who dont dream of voting for mcp… because u treated us as ur dogs. Long live democracy,

  1. r u a prophet u self? in Malawi anyone can be a leader because it doesn’t need 50 + to win. you can win even if you have 20% of voters. dont rule out anyone.

 21. Which apology ngati a2 ena nafa ndie apology alandila ndani kod mmmm chakwera watchout this country sila a2 openga ndie aaaa ungakhale olephera samala

 22. Akanayamba ndi a Tembo kupepesa zaka zambuyomu ndi Chakwamba. This apology is not a reflection of the MCP ‘s attitude on their past conduct. They are not serious. They should not have done it so late.

 23. Aaaaah Kamuzu was a great man n i dnt think amalakwisa zinthu ndi iye chonde musamunamizire. A Tembo ndi anzawo ndi amena amakonza ziwembu ndi mavutowo but chitukuko chinaliko osakhala ndale za pano zomangotukwanizana kuiwala kuti mawu a mlungu akutinji. MCP inaipa pomuthamangisa Chakwamba so that munaipanga kukhala ya nthundu umozi, ometa okhaokha so that all others are inferior. So i dont think izawina n l pray kuti isazawine even ena atamabera mavoti koma mosazawine coz a malawi ambiri nd osameta thus muzazunza anthu *abusa*.

  1. Eeeeeh kubera ndi chikhalidwe even Bingu anamubera Chakwamba in 2004 n tembo anamubera chakwamba ku ma primaries ndikumupitisa kukhoti in 1999.

  2. Anyway l m not Peter fun either. Presidents of my time are Kamuzu n Bingu bas omwe anali ndi insight n amaziwa direction ya malawi. 2014 there was noboday of good reasoning nkukhala president maybe just our professor John Chisi kkkkkk

  3. Imran samala ndinkhani zandalezi, ukakhala nazo ndimbali kwambiri udzakhumudwapo. ambiri tsopano azindikira kuti ndale ndi uchitsiru basi. ndipo anthu amene amakhaLa nazo serious kwambiri amangokhumudwapo atagwiritsidwa fuwa lamoto pamapeto pake

  4. Kkkk yap siine wandale coz ndimaziwa kuti mu ndale maka za ku malawi zilibe phindu. Koma emphasis yanga ndi yoti kamuzu asamanamiziridwe kuti anaipisa zinthu coz ndi iye ekhayo ndi malemu bingu amene anatukula malawi and amene anali asogoleri abwino enawa angotaya nthawi.

  5. Ndiyamike #Anthu nonse amene mwapanga #Reply pa #Mau omwe #Mtsogoleri_wa_Chipani Chotsutsa wa MCP Lazarous Chakwera maka #Iran Pius, Khin Jumbe, Pieter Cisale, komanso Joyce Gomonda thank kuti mu conversation yanu munalibe/mulibe Mau a Mnyozo kapena Kukwanana. Apa mwaonetsa Umunthu wanu wabwino, so let me say thank u all, thats what we want our Malawi to be and with people who r cool when acting.

 24. zosamveka zimenezo kuti tikhuluke mcp abwenze kaye gadama,matenje,sangala,chiwanga ,twaibu ndi anthu mathousands osaona aja omwe ananamidzidwa kuti kamuzu wawakhonzera party akukawatayira mung’ona onsewa akhale ali ndimoyo apo bi sitingamve kupepesako ati bwenzeretso ndalama zomwe timadulira makadi mwina koma kupanda apo zimangolowa mkutulukira uko

 25. MCP chipani chakhaza ichi chimakhoma misomali pamitu pawathu ichi kupanda maliro akanapepesera kuti? I cant waste my time kutsatira tambala wokalamba wakuda.za ziiiiii

 26. Mukazathesa chipani cha mcp anthu azaiwala khaza zomwe zimachitika kamuzu anali muthu wabwino koma omuzungulira monga……. Ena ndiomwe ayambisa tizipani tamanjawa kkkkkk mavuto kuthawa kulima eti

 27. Kuno sikudzatheka chomwe mukuyankhula simukudziwa kodi anthu onsewa sanali a mcp achoka kumeneko apita ku udf achokanso apita ku dpp achoka apita ku pp achokanso apitanso ku dpp tiyeni tidzingolumana pano nde zikuwonetseratu kuti masiku omaliza aliyense ndi kokera kwako ma kampanimu mabwana kutafuna ndalama ngati ma juniors satha kutafuna ndalamazo hahahahahahahahaha Mulungu angoweruza dzikoli

 28. Udzapepetse kumtundu wa a Malawi akadzamwalira a tembo apology imeneyo izakhala 100% recieved osati pamayiwa. Tikadakumbukira zambiri

 29. Kupepesa ndichinthu cha mtengo wapatali. Ena amene analipo analephera kutero poziunjikila mkwiyo wa Mulungu pamutu pawo. Pitilizani kuzichepesa posayang’anila udindo muli nawo Mulungu azakukwezani. Kunyozedwa sikuzachoka chifukwa ndizo ntchito za mdima uno. Maso pa mtanda wa Yesu amene amagawira moyo. Pokhala apereka moyo sangalephere madalitso chitetezo ndi zonse.

 30. Malawians will never forget whatever a little mcp done in country, dont cheat us we forward now

 31. Kodi kamuzu mukunenayo he was the best President ever and whatever he did had a purpose look at what is happening,if you want pipo to vote for you then stop all the past histories just do your campaign.

 32. Kodi kamuzu mukunenayo he was the best President ever and whatever he did had a purpose look at what is happening,if you want pipo to vote for you then stop all the past histories just do your campaign.

  1. Best of the best # Bingu only 7yrs hw many zitukuko zolodzeka anapanga anasintha Malawi within short time against 30yrs of Kamuzu

  2. best of the best was bingu 8years zitukuko mbwee! Osati 31years popanda cholongosoka bizemkumangochedwa mkudzuza anthu mkumawalanda ziweto zawo mmalo mopanga chitukuko zichulukirenji zaka koma zopanda phindu shame

 33. Zandale ndilibe nazo ntchito ine wanga nduyang’ana za kumwamba ndudodikira tsiku lobwera Yesu basi,bachedwani ndi ufumu wamdziko lapansi

 34. Zandale ndilibe nazo ntchito ine wanga nduyang’ana za kumwamba ndudodikira tsiku lobwera Yesu basi,bachedwani ndi ufumu wamdziko lapansi

 35. Kumaganiza Ngati Anthu Ochoka Nthupi Mwa Munthu Kodi Munthu Akapepesa Sindiye Kuti Wadziwa Kulakwa Kwake Nde Ngati Enanu Musakumvetsa Osangokhala Chete Bwaaaa Kungobadwa Anthu Osokoneza Basi Ndakunyadirani A Chakwera Apa Mwaonetsa Kugonja Anguluwa Asiyeni Sadzatheka Kwawo Nkunyoza Basi

 36. Kumaganiza Ngati Anthu Ochoka Nthupi Mwa Munthu Kodi Munthu Akapepesa Sindiye Kuti Wadziwa Kulakwa Kwake Nde Ngati Enanu Musakumvetsa Osangokhala Chete Bwaaaa Kungobadwa Anthu Osokoneza Basi Ndakunyadirani A Chakwera Apa Mwaonetsa Kugonja Anguluwa Asiyeni Sadzatheka Kwawo Nkunyoza Basi

 37. Kukuchedwa kucha;pomwe pafika dzikopa zusowekera mtsogoleri yemwe aliko ndi mbiri yoopa Mulungu kuti kapena alanditse dzikoli ku chionongeko chomwe adachiona #SODOMU+GOMOLA

 38. Kukuchedwa kucha;pomwe pafika dzikopa zusowekera mtsogoleri yemwe aliko ndi mbiri yoopa Mulungu kuti kapena alanditse dzikoli ku chionongeko chomwe adachiona #SODOMU+GOMOLA

 39. Dziko laMalawi lili pachilala chifukwa choti mngulu wachitchona monga Peter sangakhale president pokhapokha ngati anthu akulamulildwawo ndi Angitawu.

  1. Njala inayamba kalekale mapresident apitawa onse adutsamo even amene ukufunayo azadutsamo ndipo anthu azaliranso even mu bible inalembedwa. Mind u president sagwetsa mvula

 40. Dziko laMalawi lili pachilala chifukwa choti mngulu wachitchona monga Peter sangakhale president pokhapokha ngati anthu akulamulildwawo ndi Angitawu.

  1. Njala inayamba kalekale mapresident apitawa onse adutsamo even amene ukufunayo azadutsamo ndipo anthu azaliranso even mu bible inalembedwa. Mind u president sagwetsa mvula

  2. good admn ipotse pa subsidy. Dpp inabwenzeretsa ma admarc amene anatheratu during udf era, Bingu left stocks of maize in all grannaries bt joice used all as a campaign tool uyu wangoyamba zomunena mbwee forgeting root cause

 41. Tidakhuluka kale ndichifukwa timakhala nanu limodzi mwantendere pakana kukulorani kuyankhula pamaliro a munthu woti munamuzunza komabe mabala adakatiwawa thats why mtundu wa a Malawi motsogozedwa ndi Mulungu siiukuvoteraninso kuti mulowe m ‘boma komanso a Chakwera ichi chinayenera kukhala choyamba kulankhura mutangotenga udindo wa baba Ntembo ku MCP

 42. Tidakhuluka kale ndichifukwa timakhala nanu limodzi mwantendere pakana kukulorani kuyankhula pamaliro a munthu woti munamuzunza komabe mabala adakatiwawa thats why mtundu wa a Malawi motsogozedwa ndi Mulungu siiukuvoteraninso kuti mulowe m ‘boma komanso a Chakwera ichi chinayenera kukhala choyamba kulankhura mutangotenga udindo wa baba Ntembo ku MCP

 43. Alika Investments offer skills training in Construction/Mining/Lifting Machinery Operator, welding, Electrical, Plumbing and Carpentry.
  We offer free acomodation and breakfast for trainee from far.
  Our certificate and operators license recogonised and accredited
  We enroll New trainee on daily basis just come when your ready with: I’D, passport or permit, 1 passport size photo, training fees of courses you want to train.
  More info call/sms/watsup +27733219261 for more info.
  http://www.alika.co.za
  E-mail [email protected]
  Facebook Page: Alika Training Academy
  Share the info with your friend who maight be intrested. Like our face book page and share on your timeline.
  CATALOG with price list attached.

 44. kumalawi sindamaona atsongoleri amasophenya muona amcp akadzalowa boma adzasiya mavuto aanthu kuyamba kungula mangalimoto achipani eish malawi lachitatu mupite kuwenera mukaone mene anthu akukwelera mabus kupita ku jonz

 45. i thot ulemu wa 200 kwacha note anapeleka ndi joyce banda? okay chabwino ine i was not there when all that chakwela is apologizng about hapened,but i can feel the pain that those who where there that time felt..kodi M.C.P founder kapena oyambitsa ana kamuzu kapena anachipeza chipani iye anangoyitanidwa? tandiwunikileni bwino pamenepa!!

 46. Who is suppose to apologise btwn chakwera and john tembo? Achakwera simunalakwe but tembo ndiyemwe akudziwa zonse he is de one to apologise not u

 47. Chakwela was not in politics then and his apology will only remind Malawians how cruel MCP was at that time.Let him forget about the past and forge ahead.At the moment his hands are clean .

 48. kungochoka ku ubusa wati ndkalamulire dzko basi,simudzawinaso inu en mulungu sanakondwele nazo zosiya ku2mikira iyeyo ndkuka2mikira dzko

 49. Nyc dat u hv offered an apology bt wea hv u bn all de years u hv bn given dat MCP presidency????dat wud hv bn ur 1st priority Mr Reverand bt anyway apology accepted though it wont change anything

 50. Kupepesa chifukwa cha maliro kkkk, khoma iwe nde chitsiru chenicheni Kumaliro nde malo opepesela kkkkkkk.Manja okotombala nkati kobwe.

 51. Mulungu ndiye thandizo la wina aliyense. Andale mumakhala anthu okhulupilika musanalowe m’boma mukalowa m’boma matitenga ngati ndife ng’ombe za pangolo mumafuna kuti tizikulambira ngati ndinu Mulungu. Kuyambira lero mudziwe kuti Mulungu wakwiya ndi nkhanza, katanga, kupha koma zoipa zonse zomwe mumatichitira anthu osauka ife. Mukapanda kulapa muzingovutika choncho kusowa mtendere wa mumtima chifukwa cha ndale zanu zankhanzazi

 52. Being apologetic heals nothing while time healed the wounds and bruises developed off the atrocities.I wasn’t born then,but I hear my people suffered big time and it would have seemingly made sense if the oppressors themselves apologised rather than someone who took no part in that shit.

 53. let us forgive and avoid fixing our development ideas on past events.Let’s forge ahead and develop this country as one people.

  1. inali ntchito yachina jzu.kkk amwenewo jabulosi weniweni pano amakumbukira akumva chisoni lucky ur born free kma ife tnadutsamo mmm terrible

  2. Kkkkkk agogo ake amapanga mathanyula, mcp imadana ndizimenezo,anachita bwino kuwapha,mathanyula zipangani panopa ndi mtsogoleri wanuyu opanda mano mkamwayu

  3. even ine mano ndilibe ena chilema chichita kudza take#note .Anazandimenya ndi chibonga pamutu ndimafuna kt ndimuwone bwino bwino kamuzu ndili mwana myp pano mkutukwana pres. Wopanda mano democracy

  4. clement you mustt be very stupid, zikugwilizana ndi umathanyula izi kapena mathanyula ndiweo?? Kupusa eti kuzolowela ukapolo wakwanu kumaubwelesa pa air kuti kupphedwa ndikumenyedwa its no big deal, mbuzi yamunthu ndi usavage wakowo, kusamphunzila you dont know your rights. I didnt see that stupid comment earier, za uchisilu. Galu wandikwiyisa kwambili mwana wappatchili iwe

  1. Which future are you talking about people? There is no more future, the world is coming to an end now. Cant you see these so called Homosexual?

  2. dont tell me God now shares His secret with you….world coming to an end?????? are u sure about that? u mean we wont get to the next voting term the world will be gone?

  3. Mr #Brian the bible has stated: when you see Natural disasters, wars, mtundu ndi mtundu kuukirana, anthu kukonda ndalama. Just know the son of man is about to come. And ku Sodom zitafika pa Homosexual Mulungu sanachedwe kuononga dziko.

  4. A Thomas Tgro Mkandawire musazilimbise mtima, u Gay ku Malawi kunalibe, aneneri abodza osanduka njoka kunalibe zimenezo. Kaya tikuonani pitirizani kunamizana. Nthawi imene Mcp ikanalowa m’boma ndi pamene kunali a Tembo koma osati pano Mulungu sanalole.

  5. A Thomas Tgro Mkandawire musazilimbise mtima, u Gay ku Malawi kunalibe, aneneri abodza osanduka njoka kunalibe zimenezo. Kaya tikuonani pitirizani kunamizana. Nthawi imene Mcp ikanalowa m’boma ndi pamene kunali a Tembo koma osati pano Mulungu sanalole.

  6. mavuto alerowa ndie bolaso ulamuliro wa kamuzu omwe uja.anthu angolowa m’boma kukadzilemeletsa osati kuthandiza anthu za ziii.

  7. mavuto alerowa ndie bolaso ulamuliro wa kamuzu omwe uja.anthu angolowa m’boma kukadzilemeletsa osati kuthandiza anthu za ziii.

  8. Ben Chidzungu ndanena kale kuti dziko likupita kumapeto, palibe chikondi, ngozi zachilengedwe, maukwati aMathanyula, nkhondo, ma cash gate/umbava ndi zina. ‘Mukaziona izi dziwani kuti Yesu wayandikira.’ It’s too much now whyyy? Answer yourself.

  9. Ben Chidzungu ndanena kale kuti dziko likupita kumapeto, palibe chikondi, ngozi zachilengedwe, maukwati aMathanyula, nkhondo, ma cash gate/umbava ndi zina. ‘Mukaziona izi dziwani kuti Yesu wayandikira.’ It’s too much now whyyy? Answer yourself.

  10. Ku Malawi chipani chikalamulira nkugwa basi sichibweleranso. MCP, UDF nthaei yake idapita kale foward ever. Chakwera ngati ukudzawina chipani chake chisakhale chimenechi ayambe chanyuwani kaya mwina history isintha apapa koma with Kabwira MCP singalongosoke mpaka kuwina.

  11. Ku Malawi chipani chikalamulira nkugwa basi sichibweleranso. MCP, UDF nthaei yake idapita kale foward ever. Chakwera ngati ukudzawina chipani chake chisakhale chimenechi ayambe chanyuwani kaya mwina history isintha apapa koma with Kabwira MCP singalongosoke mpaka kuwina.

  12. ena mukuti mavuto omwe adalipo nthawi ya mcp bola kulekana ndipano chifukwa choti mudali ana simudawawone mumangomva. chifukwa cha card ya umembala anthu sankaloledwa kupita ngakhale kukalandira thandizo kuchipatala zotsatira zake amamwalira, ena kuphedwa physically pazifukwa za ndale monga a gadama, matenje, chiwanga, ena adathawa muno kukakhala mmayiko ena ulendo wa Kamlepo Kalua, mabishop kuzunzidwa kunyozedwa chifukwa chachilungamo, akamati ku arial kunali kumalo kozunzilidwa anthu pazifukwa zing’onozing’ono monga bambo ngati wakaniza mkazi wake kupita kunsonkhano wa Kamuzu kapena sanagulire mkazi wake nsalu yachipani cha mcp, anthu osauka omwe sangakwanitse kudula msokho amagona mmanda kapena mphanga zosiyanasiyana maka kuno ku chigawo chakumwera makolo athu anaona zoda mutu ndi chipani chimenechi moti sindikukhulupilira kuti angawononge voti yawo kuvotera MCP. ngati tinali ana takula kumene chonde tisamacomente zakale tisiyire omwe akuzidziwa.

  13. ena mukuti mavuto omwe adalipo nthawi ya mcp bola kulekana ndipano chifukwa choti mudali ana simudawawone mumangomva. chifukwa cha card ya umembala anthu sankaloledwa kupita ngakhale kukalandira thandizo kuchipatala zotsatira zake amamwalira, ena kuphedwa physically pazifukwa za ndale monga a gadama, matenje, chiwanga, ena adathawa muno kukakhala mmayiko ena ulendo wa Kamlepo Kalua, mabishop kuzunzidwa kunyozedwa chifukwa chachilungamo, akamati ku arial kunali kumalo kozunzilidwa anthu pazifukwa zing’onozing’ono monga bambo ngati wakaniza mkazi wake kupita kunsonkhano wa Kamuzu kapena sanagulire mkazi wake nsalu yachipani cha mcp, anthu osauka omwe sangakwanitse kudula msokho amagona mmanda kapena mphanga zosiyanasiyana maka kuno ku chigawo chakumwera makolo athu anaona zoda mutu ndi chipani chimenechi moti sindikukhulupilira kuti angawononge voti yawo kuvotera MCP. ngati tinali ana takula kumene chonde tisamacomente zakale tisiyire omwe akuzidziwa.

  14. Mr #chikuni Ine Ndikugwirizana Nanu Chifukwa Lero Tikungot Mavuto Mavuto Kma Nnnaaa Za Nthaw Ya Kamuzu Sizoyelekeza Ndipano Ndizibwana Zoti Zibambo Wamkulu Kumavala Xool Unform Ya Mwana Wake Kuli Kuopa Msonko Sakuziwa Zoti Nzimai Akangokhala Ndi Mimba Afunika Adule Khad Yamwana Osabadwayo Mtenndere Kunalibe

  15. mtendere sinsima yokha ayi amene amakuwakuwa apa ndi nkhani za mcp munthawiyo munali ana mavuto amakumana ndi azibambo anu kwa munthu wodzindikira sangatenge voti yake mkuvotera mcp ndipo amalawi sadzakhululukira chipani cha mcp never ndipo akamati pepani akukhala ngati akutionjedzeranso mkwiyo kuchipani chimenechi.pepani sapolesa chilonda koma kuwonjedzeretsa mkwiyo musamatiyese akongolesi

 54. kodi ndiye muzipepesa kangati…Gwanda chakwamba ,John Tembo,anapepesa kale….ndekuti mumadziwa kale kuti chinachake ndithu chikusowekera kuti MCP idzalowenso m’boma……kupepesa kwakukulu ndi kuthetsa chipani chanucho baxi choncho a Malawi adzaiwala

  1. ndikamaona ma comment achonchi ndipamene ndimadziwa kuti Mmalawi akakwiya ndi basop, anali kuti all thz years mesa ankakana kuti iwo sanali ankhanza…anthu ena they live miserable life because anawaphera abambo awo or abale ndipo mabala awo akanali osapola

 55. WELL SAID YOU MUST ALSO APOLOGISES TO THE FAMILY OF ARON GADAMA,DICK MATENJE,TWAIBU SANGALA AND DAVID CHIWANGA WHICH WERE KILLED BY KAMUZU DURING HIS RULE.THEIR FAMILIES ARE WAITING FOR APLOGISES ALSO.

Comments are closed.