Ailing Mutharika’s K65 million toilet stirs trouble


Mutharika buys presidential motorhome
Mutharika buys presidential motorhome
A model of Mutharika’s K65 million toilet

President Peter Mutharika’s extravagance once again has not gone unnoticed.

After revelations by newly crowned PP third Vice President Kamlepo Kalua that the Malawi government had spent K150 million to buy a van for the state President, state house came clarifying that the figure was below that.

However, if the state house thought that the clarification would go down well with Malawians, Malawi24 can reveal that the plan has backfired. Malawians are taking to social media to condemn the extravagance.

” This latest shenanigan from President Peter Mutharika is a clear testimony to the fact that we do not need ageing, ailing old men as presidents in Malawi,” posted on Facebook Allan Ntata who is a renowned critic of the regime.

Ntata apparently went ahead to allege that Mutharika’s needing of a toilet was a clear sign that the Malawi leader was not enjoying good health owing to his old age.

Meanwhile others have faulted Mutharika for prioritising his personal comfort while the country battles poor services for service users.

State house justified its extravagance on the grounds that Mutharika was not using the helicopter on domestic travel.

Inside the presidential motorhome
Inside the presidential motorhome
The presidential motorhome has a bed for the ageing president
The presidential motorhome has a bed for the ageing president

394 thoughts on “Ailing Mutharika’s K65 million toilet stirs trouble

 1. Pena pake osamatinamiza 65million toilet yake yakuti? Ili ndi mateyala Kodi? Ndiyagolide kodi? Zachamba eti

 2. Malawi 24 ndiyaboza not worth to trust my friends .Ananama kuti prophet wasanduka njoka zilizaboza.Even if is true do you think akanapanda kugula ndalamazo zikanatifika ife?Za ziiiii leave Peter alone nthawi yanu ikazafika nanu muzagula chimbuzi chanu

 3. The office of the president is worth it. It was embarrassing kuona the late president kulowa mmunda wa tea ku Makoka,Thondwe, Zomba atazingidwa ndi a chitetezo uku akukodza. Sizaulemu. Moreover ma sphincter muscles lose the elasticity with age,mumafuna azipana mkodzo kapena bibi president?

 4. Malawi tsekulamaso.palibe chachilendo apa.ndani safuna kukhala wodyelela?its a must,this is a highest office.president akangogula galimoto mwapeza nkhani,m’mwenye akagula galimoto yodula mumvekele its oky.why malawi?mufuna president aziyendela Pickup,azidya ku chiimilile,toilet yokumba,aziyenda ndi Gututu inu kumtima mbee.tiyeni tikambe zomanga dziko.

 5. Guys Ulemu ndi ofunika ,Timafuna munthu Ophunzila lero ndi uyu ,ndiye mukumunenanso mmalo mokuti muzingophunzilapo zambiri.Amalawinso Tulo!

 6. mmmmmh poyamba amapita kutchile mmene zi2u zuvutilamu nkumango pangila zosadziwika that’s nosence ngati pali chi2u chopanda zelu ndikugula chi2u chot ulinachokale chnacho chizitan?

 7. Stupid what kind of country is this pple are dying bcaz of hanger with disease, un emplyment and ur there waisting money for matuzi. shame on uuuu

 8. kkkk..President wathu ndi dLu,akumakhuta ndipoyenda pomwe…maPatients anaiwala njira yakutoilet nanga akanyera chani poti sakudya kathu..mine r eyes..

 9. Apa Ndie Mphawine Ndili Bwino Chifukwa Kwathu Akakumba Toilet Palibe Amadziwa Koma Kungokhala President Eeeee Guyz Ndi Mavuto Chilichonse Chomwe Akufuna Kupanga Chiulutsidwe Basi Ma Boardguard Mkat Aaaa Bola Mphawine Ndimaenda Mtima Uli Ziiii Uku Ndikukanda Maluz kkkkk

 10. Kkkkk Mr president!kubiba mpaka kugula toilet ya 65million?amalawi akuvutika ndi zimisokho mukuwadula paliponse pachomwe akugula or kulandila inu nkumaseweletsa ndlama mopusa chonchi?shame on u!

 11. Kkkkk tchto zamanja anu zija zikukuchtirani umboni a bwana busy kumagula matoilet guyz kkkkk evin tanzania or zambia zanga khale busy kumagula toilet yoyenda nayo ndiye kut abwana akumanyelanyela pafupipafupi eti kamwazi atu ameneyu mwina akumadya bwino ife kungo tisiya pa dzuwa basi kuno chimanga tilibe vuto lanu ndichiyani bwana ngat tidakulakwilani po voter chonde mutikhulukire talazi

 12. a John Dube ndi Mr usuf umbuli ndikosayenda ndukumene kwakukulilana inu mukuona kuti nzachilendo zimenezo taendani maiko anzanu muone. zimene mukukambazo zimapezeka pamalilo ndipo kuchita kupanga hayala ndalama zoposa k65 million kapena azungu akamadutsa kumalawiko nkumapita kumulanje sumumaona akukoka ngolo mbiyo mwake inu mumaona ngati ndichani imeneija imakhala nyumba yogona kuphatikizapo toillet komanso fridge nkati momwemwe ndie inu mukuona ngati ndichani 65million samalani pofuna kulankula kuopa kusakedwa ndumbuli wanuo

 13. #Arthur bwino nazo azanu akusanduka nazo njoka zimenezo muzingoyakhula zithu mukuyakhulazo koma musanyoze mthundu wa athu pakhaniyi ayao apanga chani kuti muzanyoza??????????????

 14. Kkkkkkkkkkk my motherland Malawi I cry for you because manipulation is every God’s day. Do you think they really need to save you from poverty? No!! am afraid you will never reach anywhere my motherland. Ohhhhhhh!!

 15. mukamamva kut za mziiiiii ndi izi……. Umphawi wanu amalawi……… kod mumulonda mpaka lit???? that thoyaz iz government property not 4 munthalika family. akanyeranyeramo azaisiya inuso mukazakhala president muzanyeramonso.. pot akunyeramo ndiwina basi???? mukusakasaka amabungwe kut akutolen et???????? kumazimverako chison…… umphaw wanu….. kuzolowera kunyera kutchire ndi mmwadzi……… ayao achabechabe inu………

 16. mukamamva kut za mziiiiii ndi izi……. Umphawi wanu amalawi……… kod mumulonda mpaka lit???? tha thoyaz iz government property not 4 munthalika family. akaneranyeramo azaisiya inuso mukazakhala president muzanyeramonso.. pot akunyeramo ndiwina basi???? mukusakasaka amabungwe kut akutolen et???????? kumazimverako chison…… umphaw wan….. kuzolowera kunyera kutchire ndi mmwadzi……… ayao achabechabe inu………

 17. Mutu kumamawu gwiritsa ntchito moyenera pamene Kamuzu anali pa mpando ndikukumbukira kuti sugar akakwera amapita ndikukapempha kampaniyo kuti itsitse sugar ppokumva zovuta za kampaniyo ndipo amapereka ndalama zomwe kampaniyo ikufuna ndicholinga choti anthu asavutike,panopa petrol ndi zinthu zina zinakwera kwambiri sugar ndiye akupangidwa komweko kumalawi kodi ndi anthu angati omwe akukwanitsa kugura ija imatchedwa kuti bread basket pa moyo wawo Wa siku ndi siku .

 18. Akufuna adzinyela muma bucket nkumakataya kuchigwa,mulibe mmanyazi omwe mukuona ngat bibi wa bwana ali ngati wanuyo?awatu sama biba chisawawa ngat inuyo!jb anapeleka 50milion game ya bb ndi noma jst 90mins what more is 65milion for an equipment to be used for quite a period?zachamba.

 19. Ndichifukwa chake amati voting lanu ndilofunika choncho mukapita kokavota kavoteni mwanzeru pakuti blanket kapena mafuta ophikira aja amakunamizani nawo aja ndizopanda phindu sizingafanane ndi kufunika kwa voting lanu chifukwa voting ndi tsogolo lanu A Malawi dzukani kwacha tsopano .

 20. Kd family imeneyi imabwera ndi mavuto osiyana siyana bwanji ? Wina wagula toilet yoyenda nayo , wina amakonzera mpaipi , bola wapaipi inali yontchipa , km awa ndeeee .

 21. Kodi iyeyi sangamanyeleletu asananyamuke mpaka k65 million iyeyu wayamba kutsegulamimba kapena aaaaaaa otsatilawo kumaombrla mmanja kkkkk

 22. kodi munabadwa bwanji anthu inu? nsanje sikupindulilani mpaka mudzafa let de president enjoy his fruits,wait for ur tym tidzaone ngati mudzagule galimoto la chibudzi momwemo koma ya K40,000 poti ndinu a low budget.

 23. amalawi munangozolowela kutsutsazizose imeneyond nkhan chifukwandnu otsutsa ndye zilizose kumangotsutsa msiyen munthu ndnthawiyake anjoye kkkkkkkk!!!!*kk.

 24. Zinazi ukanva ngati maloto 65 million yonseyo toilet kkkk Osamangonyera m’jumbo bwanji ndalamayo nkuthandizira anthu akuvutika ndi mavuto osiyanasiyanawa

 25. Beautiful congratulations to our president that is what I call class it shouldn’t only happen in the west we can also do it here

 26. Dzuka malawi zuka lija nd kale unayamba kugona, guyz amene ali nd nymbo imeneyi ya Kalawe nd Ennoh andtumzre link yake olo ili ya rmx

 27. Pple ur just saying peter this peter that… Don’t we have a cabinet where Pple discuss issues? If that thing has been purchased that means it was discussed en accepted… It shouldn’t be peter peter coz ts nt personal… Ask the whole body

 28. I can imagine a cleaner from Thyolo placed in this pupuh motor with the responsibility of changing the pupuh and pee bags.

 29. Thats what he wanted, pompous life style while poor malawians are starving in jails and hospitals due to lack of food, even others are dying coz lack of medicen what a shame of this president…..!!

 30. 65 million yachulu ndi mabuto ali ku Malawi. Mzipatala mankwala kulibe odwala sakulandira zakudya ndizithu zoti pa ulamuliwo wambuyomu sizinachitikepo. Asogoleli mukanaganiza kaye. Amalawife tikulira dziko lathu lomwe likuwawa pano.

 31. Why pple r angry for that mobile toilet?how can u feel kumva kuti a president aimisa convoy alowa ntchire kukazuthandiza,every president got that in every country if u don’t know.

  1. zopusa basi wanena kut asakhale ndi mobile toilent ndani?sikumaona mmene anthu ako akukhalira mzikomo mkumagula zamanyado.nanga pano mmene amalawi tikulilira pano.

 32. I think its Malawi government buying for the office of the president not for Peter Muntharika. When he leaves the office, the mobile toilet will still be used by the next president. MK150million nkachaniso as far as government expenditures are concerned. A Malawi kukokomeza basi.

  1. If it is a nasty thing why is it expensive? Apapa bola mcp idzawine your presidenti adzagwiritsanso ntchito bola asadzakhalenso namba thu.

  2. Olo undinyoze, nothing changes. Government doesnt take mare views to run its business. It needs sober minded people to understnd its policies the way they work. Ukutukwana ine, I am not Finance Minister after all, nkhwidzi zimenezo, munya nkulira mmalo momangogwira ntchito zanu or business. #Nkandawire

  3. koma tikati tifunsane kut kodi dziko likuyetsedwa bwino,,pansi pa ntima yathu tikudziwa ndikuwona kuti sizili bwino…ena amene mukukweza dpp abale anu penapake amagona ma admac dairy…

  4. Anywhere in the world people are crying. Globally economy silibwino. It takes individu effort to get out of these problems, but waiting for goverment or social service for survival, its the worst human behavior on earth. #bwana Kalimowa

 33. Complete nosense. Kodi presidentiyo amachita kuyenda nacho manja chimuzi cahkecho? Nanga nduna zimamulondola ngati ngumbizo nazo adzigulira ma toilet awo? Iyeo presidentiyo sangamakachite chimbuzi kunyumba kwake, mesa kuli dzimbuzi zambitinso. And if he is not well enough just because he too is human why cant he work from his residence? Must he be out all the time? For what? Can he send his deputy preseident? Or nduna imene. Ngwazi ampanga bwanji? Is this not going to cut on expenditure. Dzachimbuzizo ndiye zosalongosoka in my view

 34. Hahahaha! Seriously,this is not an accumulation of experience.You spending the day outdoors,but watch the sun where it goes down.Better to respect to other planets.Others are homeless,others are dropped away from xool for financial problems while you are busy venture with toilet.Maybe mwayamba kutsegula m’mimba?

 35. kkkkkk kkkkkk kkkkkk koma Malawi walelo. zipindula chani kumtundu wa Malawi? mesa inu aboma munkakwela pa chulu nkumalalika mwati nyumba yamalamulo yalakwisa kugulila galimoto Dr chakwela? nde inu 65 mita mwati ya mtsogoleli kkkkkkkkk, nde mudzitha kuvomeleza zina zinachitika osamangolalika zili zonse, koma nkhani ndiakuti zipindula chani ku mtundu wamlawi? tinene kuti magalimoto amene amakwelawo sanali abwino? Vuto ma President apamalawi kudzikundikila, tikunena pano njala kumuzi anthu kumuzi akugona nayo, mzipatala mankhwala akusowa ena nkumaononga ndalama ngati zimenezi, kuno kulibe kuganizila anthu osauka ndiovutika kulibe. tingodikila Mulungu pakuti ndiye oweluza olungama.

 36. So u wanted #1citizen 2use de bush wen travelling.B wise mumati nature call ikafika zipita kuti?palibe vuto APA ngakhale anakakhala kuti its Kamulepo n power could have done de same

 37. Guys, palibe chanzelu pamenepa chomwe akupanga mkulu uyu, osango funsa anzake njira zomwe ankagwilisa ntchito, alipampando pomwe ali iyepo.

 38. Guys, palibe chanzelu pamenepa chomwe akupanga mkulu uyu, osango funsa anzake njira zomwe ankagwilisa ntchito, alipampando pomwe ali iyepo.

 39. This vehicle will be part of Presidential convoy which not only President Mutharika will be using but all future Presidents of Malawi.Let start respecting our President.

 40. The reporter has misled us just because he hasn’t explained well to us what this TOILET is all about. The second problem is that Malawi doesn’t have respect on her leaders. The third problem is that many that are commenting here are biased. When approaching issues of national interest we should bring in constructive arguments and alternatives than insulting our leaders.

 41. Mungoona kupanga criticise,muzaziona mukazakhala presdent…

 42. BECAME A GREAT MEMBER OF ILLUMINATI SUCCESS CLUB FOR
  WEALTH, FAME, RICHES AND POWER CALL +2347065758576 PLEASE
  MAKE UP YOUR MIND BEFORE YOU CALL BECAUSE ONCE YOU ARE
  IN
  THERE IS NO GOING BACK ONCE YOU ARE SUCCESSFULLY INITIATED
  JOIN THE ILLUMINATI SUCCESS CLUB FOR WEALTH, FAME AND
  RICHES,
  HAVE YOU MADE UP YOUR MIND TO BE A MEMBER OF THE GREAT
  ILLUMINATI SUCCESS CLUB, THEN IF YOU ARE READY TO BE A
  MEMBER
  CALL IMMEDIATELY, BUT BE AWARE THAT THIS ILLUMINATI
  SUCCESS
  CLUB DON’T WANT YOU TO JOKE WITH ANY OF THERE RULE AND
  REGULATION AND ALSO NOTICE THAT YOUR MONEY IS NOT NEEDED
  AT
  THE TEMPLE? CONTACT US TODAY BY CALLING US 2347065758576.
  Are you a business man, politician, artist, worker, Pastor student and
  want to become rich, wealthy powerful and famous to make your
  wishes come true in life. You can achieve your dreams by being a
  member of the ILLUMINATI SUCCESS CLUB.
  WHO CAN JOIN THE ILLUMINATI SUCCESS CLUB…
  i believe you have heard different stories about our members all over
  the world.this is to tell you that everyone is welcome. all that matters
  to us is for you to MAKE UP YOUR MIND BEFORE YOU CALL ,don’t let
  anyone talk put you down,just
  believe in yourself..and we shall live in you,
  you shall be reborn and see life in new dimension
  TERMS AND CONDITION
  * You must be able to keep the secret to your self
  * You must have strong belief of Success
  * All men and women are welcome to join this Temple of
  Only Success, Respect and Super-Rich
  * share no secrete with anyone,not even your wife or mother,
  because we are watching..don’t look for what you can’t see. 07065758576

 43. U always take Malawians 4granted.That’s nothing to me n can u show us what the life president was using……opusa iwe Ntata cos even lero abambo ako aka atakhala mpando omwewo adzapanganso zomwezo……Kamlepo…udzingotokota koma palibe angakunyengelere ngati Muluzi uja……viava APM!!!!

 44. NDIYE NDIKUMATI BOMA LILIBE NDALAMA AKUFUNA AID YAKWA MADONOR PAMENE MUKUSEWERETSA NDALAMA CHONCHI ANTHU OKULA MOVUTIKA AKAPEZA NDALAMA AMAVUTA NAZO NDIYE NDI IZI

 45. K65 What??? Million? Toilet?? Bt Chimanga Now Cost K4,000 Per Tin(20L) Bt Many Pipo R On The Posting Waiting List! No Job, Etc. Kaya!

 46. Point of clarification Malawi24;not all Malawians condemn this but Malawians who do not vote for Dpp. Kma a malawi mumatha kutsutsa ee chilichonse munthu apange ichi ayii. Kma wa opp. section 65 no1 budget no2 nkumawombera manja wosanenapo zanjala

 47. Kkkk akuvuta ndi asenawa anazolowela yawo ya m’madzi ija ndiye akuona ngati Bigman naye angamapange zimenezo aiwala kuti ndizabomaso czakunyumba kwake longa mbuya kkkkkk

 48. It is presidential!!!! Kodi jb sanazisiye???? Koma umbuli winau…. Even chakwera akadzakhala kuti sanampolamile mkuwina naye adzanyela monwemo…. “Presidential”

 49. a malawi chwelengero chathu ndi chochepa…bwanj osangotigaila aliyense 1 mita mita budget ithere pompo.,…mukutizunguza mitu achna pinya munthalinyanu..,,.,

 50. matama oxewa kan naexo amavna nawo guleyu ? nde zkuxonyeza kt naexo ndmatenda, ife tkapta ku chlendo imatha or wk kma osafa kma iyeyu ndekt nd 20 mins iryosetu kkkkk……azake aja bwanj ? 2016 loading……

 51. Kkkkkkk koma amalawi mumafuna azibusha mu thengo munthu wamkulu yo??? Kapena aziyenda ndi gututu ku boot ya njale yake kuti aoneke kuti wasaver dollar??

 52. That’s good than kunyela kutchile. Akufuna chidyelano cha manyi chithe osadanda He is our President and he deserves more than that

 53. Acording to me there’s nothing wrong with this Development being our President He deserve it even more than that and in other Nations the issue can never even make headlines.The problem in Malawi is that even the so called Graduate they are Premitive. shame on us

 54. iwe akapitako abwana ndizikatola zomwe azikagwetsazo chifukwa 65mita ee munthu wake sangatulutse zoipa kuja ndalamasosa

 55. A malawi ndichani? mwayamba kusewelesatu ndalama bwanji osakathandizila ana amasiye coz that money can change somebodys life chonde Mr munthalika muziyamba mwafunsa kaye public before musanapange zithu mwapanga zobowatu.

 56. Kodi mukufuna azikanyera Ku tchire akamaenda?if Toyota land cruiser cost over 45 million NDE mukuonda ngati chimbuzi choenda nacho chingakhale bwanji?mind u its nt only toilet there, there is also a clinic , dining ndi malo ogona mmenemo!

  1. at a time we are in, its not fair kumawononga ndalama zambiri on a single person when all over us are suffering. him too should felt the same pain we are feeling by making sacrifices.

  2. Lkkk a prisca inu mungafane ndi presdent?
   Vomelexan kut ndife osauka n w r diffr from presdent inu ndi ine titha kunyela pa tchile pomwe presdent sizingatheke

  3. AAAAA iwe@ balakasi wangokubhowa koma zoona zake ndizoti president ayenera kugulilidwa zoyenela pa ulendo sikuti azatenga pochoka pa mpando ayi

  4. The car z meant to be on the convoy, funsani ngati ma president ena analipowo sankagwiritsa ntchito. Amalawi sometymz tamaganizani mwa umunthu. Do u think dat car saves as a toilet only ? Think before commenting not for the sake of just commenting. Nsanje ndi kaduka bax

  5. Call us whatever but understand our argument guys,,we’re nt writing in the sake of commenting, if that so called toilet mobile was there before,then let him use the old one,as for now we don’tve enough funds for that,,he’s already highly respects,,

  6. mayb tyming? but bwampini does wateva he feels should be done! that’s the waste ever presd. imposed on us!
   he wants to sell off Kamuzu Central Hospital? after he n other zealots bought Malawi Savings Bank, y can’t he sell off MBC, it’s just a waste of government financial resources

  7. Koma kuMalwi mumabowa, utake president as who? He s aperson lyk anybody,Mulungu simumamuopa mumaopamunthu mukukanika kulepheretsa za magay zomwe GOD can b plsed with koma bzy kukonza ponyelera bwampini

  8. “Clinic dining n’ malo ogona” kkkk ichi nde ndi chitopa basi kuopa kukomokera panjira… Kaya ife tikungodandaura zokweza school fees zija pano school ndi ya atsikana okhaokha poti ndiwo ali ndi ma donors owaninkha scholarship…

  9. Common sense is not always common. All these days where was he use to answer nature call? Citelis palibas in capitalism society. Who gets what and why? Mind you! Dont just clap hands any how. Confrict of interest brings change. Let’s maintain our standards as Malawians.

  10. pot president amanyera manyi a sausage nde akhonza kugula chimbudzicho,,, kunya ndi kokoma,, koma chimodzi ndi ichi :asaike ma label nkanyumba kameneka paja mkuluyu kukonda ma label too much

  11. Paja kwathu kuno u president ndimalo oti munthu aremererepo, mumuuze ngaki ku America anali iyeko anachoka waumphawi,asatipatse umamphawi kuno,,mubale wako bingu tinkamdandaura chonchi mpakana mmanda,dandauru pamunthu wosauka limampha, # pitirizani!

  12. Big up Emmanuel Maulana! very pleased to know that there z people who can think ! osamangoti chilichonse boma lingapange kumangolira kuti ndife amphawi kodi ndiye umphawi wanuwo mumafuna Peter nso akhale mphawi chifukwa inu ndi amphawi?In life there must be ‘haves’ and ‘have nots’ ! Tidzalira ndi umphawi mpaka liti?Amalawi ambiri ulesi kufuna ma miracle nchifukwa chake dziko lathu likusaukirabe chifukwa ladzala ndi alesi ndiye paja ulesi umadzetsa nsanje komanso nkhanza! tiyeni tiyambepo kupeza kulimbika ntchito osamangoyang’ana ku boma

 57. Koma tsono toilet mpaka 65million zoona zimenezo akulu inu mmene njala ilili dziko lino ndalama imeneyo mukanati mupereke ku Admarc kuti atsitseko chimanga sizikanathandiza?

 58. Chonsechi chongobibamo president? Koma ndiye mpaka K65m ya Bibi ya munthu!! Bibi gate imeneyi. kkkkkkkkkkkkkk

 59. That is what I voted for. Shame on myself. I love you party just because of the late president. Mukutizunza kwathunthu.

  If I remember very well, weren’t you riding public minibuses and buying ‘bonya’ during campaign? What was the meaning…

  You will get frustrated.

 60. Kkkkkk moti ma tchire onsewa osangoimitsa nkukhotera kaye pambali bwanji? Nkhani yake yomweyi yozithandizayi mpaka ma million? Chabwino

 61. Malawi uzachangamuka liti?kodi mukamalankhula mmaziwa chomwe mukutanthauza?koma zoona mungamakhale busy kunyoza mtsogoleri wanu?udindo wa msogoleri wadziko mzosiyanatu ndi wanu osegula kumandawo ndipo akuyenela kupasidwa ulemu ndipo toilet yo ndiyofunikadi as we go muzaona ubweno wake for sure mudakali mtulo

 62. Thou no proof,this was necessary but not @ a time wen pipo can’t even afford to buy atin of maize,leaders,we atimes understand you but go down see how we are suffering.

 63. Mukanakhala president inuyo mukanatani a Malawi24 ndi nonse mukuchita ma comment opanda tsogolonu? Shame on you phunzirani kukhala ndi ulemu.

 64. There is some news that you can publish for the nation to know and learn something than telling us stories which are stupid by nature and can profit nothing to us so if you have nothing worth to tell us u better shut up and turn your computer songs or play some games,what is the matter with the government buying amobile toilet?are you going to have ajumbo bang in your hands and follow him during his rallies so when nature cal you will be giving him and keep it after use?its amatter of our poweress kwacha but president is supposed to have those previledges,shame to you guys and in some countries it too expensive so watch out

 65. this is stupitdent you pitala leave us alone ndiiwe wa cashgate ya chimasomaso bola anzako aja ankaba mwa mchibisila Koma iweyo aaaaahhhh shit Malawi

 66. aaaaah, 65 million is alot of money for just a toilet. that money could have been used to buy new equipments in the escom to reduce the blackouts and not increasing the tarrifs as what has been done. azipitiratu ku toilet ya ku kamuzu palace asanapite misonkhano yakeyo. its time for Peter to start priotising things that could beneffit the 17 million in this country. imagine he has cloacked one and a half year in office and nothing tangible we can say proudly we have achieved as a nation yet we are the poorest nation in the whole world but have abundant resources.

  1. Hahahahahaahahaha koma umphawi nthawizina sizinthu. Kudandaula ndi ka toileti zoona. Izi zidalipo kuyambila nthawi yakamuzu, Bakili, JB, komanso uyu akuenela kukhalanacho. Sizachilendo izi

  2. Its the issue in the sence that we are suffering in this country,why not use the previous ones & use that money for something,crying for my beloved country,we gave it to a total stranger ;(

 67. Izi Ndye Zopusa, Atadzibibira Iwowo Angadandaule Ndan?Ndalama Zonsezo Zofunika Atagulako Ma Ambulance Kt Mwina Tizikachita Kufera Kuchipatala Kamba kosowa Mankhwala Bt Nt Transport.

 68. Amalawi taphweka kaya ndi kupusa kaya ndichani, mpaka kugula toilet,kusonyeza kuti Kamuzu yake anatenga pochoka,Bakili anatenganso yake ,ami nawo yawo anatenganso nanga malemu munawakwilira limodzi ndi toilet?yaaah tiona zinthu

 69. kkkkkkkkk koma ndi ada bwampini tiona zosawona ndithu kakakaka mpaka mobile toilet? koma ngati boma ndalama zachuluka bwanji tithandizire anthu ovutika ndi njala ummmmm no nw its too much inu inu!!! anthu tikuvutika ndi njala kunja kuno koma a president ndi boma lanu mkuzunza anthu koma

  1. Pa convoy ya president aliyense pamakhala motor home yomwe amagwiritsa ntchito ngati toilet, dressing room komanso kudya zakudya. Si Peter yekha wayamba izi.

  2. tsopano thoyazi yakareyi anati yatha? kungoti munthu wanuyu saganiza bho man munthu uzipanga chinthu pa nthawi yoyenera.

 70. kodi mabuleki anatha mwa mkuluyu??kepena ndi mimba mwa mpwelele,kapenaso kt mwa mpedzedze kapena kt iiiiiiiiiiiiiiii iwe uli pa mpando WA u president we undiyankhulitsa kuipa

 71. The toilet vehicle we had was bought with bakili muluzi in middle 90s, whether u like or not Bakili,Bingu&BJ use the same old toilet,until devastated. So its among President requirements. Need to be bought

 72. For me i think the idea of a good toilet and resting area is good .after all munthu uja needs care. his old .maybe price koma its worth it.

 73. nanunso a Malawi24 khalani ndi ulemu!! Galimoto imeneyi moti ntchito yake ndi toilet basi? Whatever you haters may say this whatever you call it is a vital part of a presidential convoy! Nanga mumati president azikaphela mbuzi patchile pali ulemu??????????

 74. Enanu zukusangalatsani eti,a bingu wamutharika sadafike apa may his soul rest in peace,mudatisiyira mavuto okhaokha

 75. axaaaaaa! Uwutu ndu fiti!!! Mmene dziko lili pamavuto basi wina kukazigulira chi2 65………………..! This is an autocracy in a demacracy of the… Realistic pple!!

 76. Its sad development for someone to post this. Why can’t you respect the office of presidency? Yes I understand you have your own fundamental rights and freedoms for posting this but then,what is your motive or so what?

 77. abale abale abale eeeeeeeehh kodi munthu ameneyo bwanji vuto lake ntchiyani? Ndalama zomsezo zachani iyeyo ngotani sangagwilitse ntchito chimbudzi chokumba nkumati ndalama kulibe akuwonongela kugula chimbudzi chomyelamo manyi malo moti apangile zinthu zoti anthu zapindulile zaziiiiiiiiiii basi zopanda ndi nchele womwe apa

  1. Idalipo gamotoyo koma njachikalekale komene odaonapo mdipiti wopulezidentiwo, nuja pomawoneka chigalimoto chonga nyumba chija tele

 78. Akutsegula Mmimba? If Timayenda Mzuzu To Blantyre osatenga toilet, ndiye kumayenda ndi toilet pali ponse? Ulendo uno tiphunzira zambiri.

  1. kodi mkuluyu amakonda zotunyatunya? shaaa mazila oboyilatu amenewo amapangitsa zosomasoma. agogo anga a Naphiri anandilangizako kuti paulendo wautali kumafunika kusomeratu!

 79. MW24. .fact that you don’t like Peter ..koma he deserv respect please khani yoyendesa ziko ndiyonyela are just synonymous please respect is needed

 80. MW24. .fact that you don’t like Peter ..koma he deserv respect please khani yoyendesa ziko ndiyonyela are just synonymous please respect is needed

  1. Even if it belongs to Malawi, the question is, is it a priority? How many cartons of malaria drug and painkillers could that amount buy. The truth is, APM has no passion for poor Malawians…

  1. Even if it belongs to Malawi, the question is, is it a priority? How many cartons of malaria drug and painkillers could that amount buy. The truth is, APM has no passion for poor Malawians…

 81. Mmmmm koma nde bozatu..K65 billion ??.mesa dollar yogula Jet imeneyo ikukwanila..please osati panga drag kumiseche

 82. Mmmmm koma nde bozatu..K65 billion ??.mesa dollar yogula Jet imeneyo ikukwanila..please osati panga drag kumiseche

Comments are closed.