Malawi’s former ruling,Peoples Party (PP) has appointed Uladi Mussa as its acting Vice President, Malawi24 has learnt.
The appointment has been made by the party’s leader, Joyce Banda who remains outside Malawi.
It has come when the party has been under leadership woes as Banda has been accused of leading the party over the Internet.
A faction in the Northern region has been pushing the party’s leadership to rope in Khumbo Kachale to be the party’s interim president as Banda has been out of Malawi ever since she lost the polls in 2014.
Mussa has been vocal lately leading the party in parliament, despite calls by Christopher Mzomela Ngwira to have Kachale as the leader.
uladi musa tchito kutukwana asilamu amzake akagwere uko ameneyo•
Boma iloooooo
Kutukwana heavy mwina ziyenda poti ndiolimba mtima
Wokamba azikambaäa..ine nilibe pulobulemuu..ine nilibe polubulemuu its orkeeey
Kodi ?mmene adyera of maliro sabwerera fame
Mwini wake wachipani Joice Banda anathawa kale kumalawi ataluza akukhala ku south africa
eyetu malume Abel Tembo
Naye RICHARD wangoti zii sakanaimira mmalo mwa a darling?
Zoona change golo wakhaula mzomera ngwira amafuna kuikapo mtumbuka mzake wauponda basii mungoyambisa chanu atumbuka nonse mudzisapotana kt mwina ndikuvakofungo laupulezidenti km mukadikira zathuzi ndithudi mpaka yesu azabwera kulibe kulamula dzikolino…kuphuzira ndikwanu km kulibe kulamula mulindimwano ngat Livingstonia omwe amakangana malo ndi Nkhoma Synod pakasungu mpaka uyo ku Lilongwe zitsiru zaanthu.. azawo a BT synod ali pheee…
Koma kachipani aka… kotha mapulani ndithu. Kanthu akufuntha okhaokha
Maliro akatuluka m’nyumba sabwelera PP sungani chipani chapangozi .
paja change goal chipani chake anachigulitsa ku pp ndiye tidikirenso kuti mmene zatelemu pp aigulisa kuti.
Anything wrong agalu inu tisiyeleni chipani chathu ana opanda kwanu inu
chipani chathadi ichi…
We dont need president in Malawi. No profit fo dat. Mfana wapa Estate ku Nkhata Bay
end of pee pee!
Khumbo mwamuika pati poti naye wanyanya ok pp ndi dhill osati chipani ichi cha dpp
Kodi mesa vice president ndi Ralph jooma koma chipani ichi aaaaaa
khuruku wachabechabe Uladi mussah kodi nanga kachipani kake kaja bwanji anakathawa? atsogoleri adyera awa mbava
Kdi Panopa Presdent Ndi Ndani Kodi Mchipani Cha Pp?
Kkkkkk, sakudziwika
Kkkkkkkk Ok Chipani Chopanda Tsogolo
Kwabasi. Aliyense angoziyendera yekhayekha kkkkk
Kkkkkkk
Komabe chipani chimenechi sichidzalamulanso dzikoli. Azingopanga phada wawoyo koma palibenso kutenga boma m’Malawi muno
Great information
Umama ubalekile uzovuwa kuphera kwanyanga
Sono mukumasankhana maudindo koma Amayiwo ali invisible , ziyenda? Ziyenda bwanji osapangana?
Yanyamuka wakuphompho.
Akanasankha A Richard Banda Alowe Mmalo Mwa Darling Awo
kkkkkkkk usandisekese ukuwanenawotu ndi magulu Aachina MALEWEZI kkkkkkk Anawawona Atcheya Akawatuma ndinayiwala style,kupepela kwenikweni kkkkkkkkkkkk.
Kkk Osat Magulu A Chlembwe? Kk
Koma ka page aka check your story again mjomba.
Tiyeni nazoni ndalezi koma musachigawenso
Ok nkhani ya bwino tapulika
pp pa ground inatha yatsala mmabuku
If the party leader thinks she wont be in Malawi anytime soon it’s better to call for a convention to elect new president and other structures otherwise personal hand picking might bring confusion.
Ine ndamva zoti wasankhidwa kukhala interim president, osati vice president ngati mmene mukunenela enanu mtima news page tanuti
Kutha ngati makatani heeeee
Am not supportg any part in Malawi coz they dont think about voters@useless GVT
Kutha kwa ka chipani kaja kumeneku, ndiye poti a change goal naonso amangofera fungo tiziona
Umama ubalekile. …kkkkkk
koma. mupindula naye. uyu. kulalata. kwakeko. mAbolA. sondA. kuti. wAwAaAwAA.
Uladi musa woyeee
Now you will lose mpoto suport. Ic this coming in 2019
haha inu mumafuna mtumbuka mzanu zavutapo apaa…or muyakhala muonangat PP singawine….kumpotoko sikuzachochera puresidenti mudzingovutika ndimatukutuku
Hahahahahahahahahahahahahahahahahahahahh. #sam i feel sorry 4u, can you check my status please!
Okkyy thats why ua talking like this,,,, ua 4rm lilongwe & umakhala ku ntchisi. Nchifukwa chake…
achange goal nawo ndi chuma chamasiye chotha ngati curtain kkkkkkkk
mmmmm change goal munthu wadyera ngati ameneyi koma!!!!!!!!
ali bo kma azalowanso m’boma?
kkkk mukungoika mbala eti ndimunthu woti kumuika pa mpando wa wachiwili kwa igwe ameneu
Congrants mr change golo
Mkuluyu ndi mwini film
Anali ndi cholinga eti? Change goal in action