Nomads join race to sign Essau Kanyenda

Advertisement
Essau Kanyenda
Essau Kanyenda
Kanyenda: Big name in town.

Malawi’ 2015 Carlsberg Cup Champions, Mighty Wanderers, have joined arch-rivals Big Bullets in the race to sign South African outfit Polokwane City FC striker Esau Kanyenda.

Kanyenda whose contract with Polokwane expires at the end of season intends to come back to Malawi in order to end his active football career.

Kanyenda revealed that he has only one more year to play football before he retires.

An inside source from Nomads camp has disclosed to Malawi24 that the Lali Lubani outfit has plans to start discussions with the player for a possible move to the club.

“A striker who is over 34 years and will be able to give you 15 goals per season, he can’t be a bad signing, Kanyenda is among them,” said the source.

The former Jomo Cosmos forward is also among the players that 2015 Malawi Super League Champions, Big Bullets, want to bring in and he has already shown interest to join the club.

Advertisement

59 Comments

 1. NEBA PAJA NDICHONCHO,Akamva za BB amamva choti juuuuuu!Nanga vimaplayer vonse alinavovi mvantchito yanji apa akufuna kuphumitsa anzawo.BB NDI DHILU

  1. Abale, mumamva bwanji zamasewera zomwezi mpaka kumatukwana ndikumalalata mmalo mongopereka maganizo anu omwe muli nawo? Kunyumbako ndiye kumakhala zotani china chikangolakwikwa??

 2. Strike wokhala ndi 3goalz whole season pita ku chigambwe fc konko az wise pple wi choise wisely tikufuna ana owona goal mwakula bambo asileni ana

 3. Ntchito lekelani THE B 52 BOMA(Muhamald sulumba) Jabulani Linje, Staniel Sanudi, Kaliati, Thedi Sumani.Thedi Sumani ndiyemwe adapangitsa kuti Fisher ayambe kudya thabwa,nkhalamba kunoma ai.Uyoyo apite ku Bulletsi cifukwa imasunga makape ndinkhalamba osati noma yathu ai asiyeni ana acisodzela agwire nayo ntcito manoma bx.

 4. sinamvepo bullets ikupanga zosanzira noma imapanga zake .bullets inatenga kochi kananji noma nawonso ati kananji yemweyo.kunali gabadidho nawonso kukatenga kape wina akuti omegadidho bullets ikati itenge ana a fizd nawonso konko .saziwa chomwe amafuna lero ndi iz

 5. kanyenda timacheza naye pa ngwa tili mafana ngakhale iyeyo anali wamkulu koma kamba kosazikonda timacheza naye, iyeyo amakonda noma.

 6. ndi mphale ife a noma sitikumufuna apite ku nyasa fc komweko ndi timu yokha mmalawi muno ili miziam ya maplyer kunoma tikufuna ma new players not old players like him

 7. kodi ndimayesa kuti mumati ku BULLETS,kuli nkhalamba nanga esau mukumufunayo ndimnyamata?ESAU akubwera kuBB chifukwa ndikumene kuli k500 m,the richest team in malawi.

  1. kkkkkkk tikukozeni pang’ono ka comment kanu.osati chifukwa cha 5 Million Ayii!!kkkkkkkkk koma chowona chake ndi ichoo!! mwachitchula kale kkkkkkkk ku Noma kulibeko Ma Agement ake koma kwanuko,nkowona akubweladi kwanuko musakayike kkkkkkkk.

 8. Mutengeni mapuleya menemunayambila kutenga mapuleya muja palibe chomwe mwapangapo mukuthamangitsa mapu 12 ndiye mumawagulilanji kungoononga ndalama za B4 forwad basi popanda phindu zachamba basi muziona ambwelele inu

  1. kkkkkkk osadanda ndiwanu kwathu kulibeko ma Agement ake koma alikwanuko kkkkkkkk muchidule ndiwanu kwathu sitilola khalamba zingatiwonongele team kkkkkkkkk.

 9. Nde mwati #Noma nayonso ikunufuna? Ndikutha kuona akusayinira #nyerere ameneyo chifukwa ndi yokhayo yomwe kukapita player luso lake limawonjezereka osati timatimu tinati

  1. Ayaya ma player ake ati, Jimmy komanso Mr Epac ndi aja zao palibe. Kkkkkkkkkkkkkkkkk. Vomerezani kuti ndinu mphale basi. Paja chilungamo chimapweteka etiiiiiiiiiiiiiiiii.

Comments are closed.