Malawi Police are Africa’s most corrupt

Advertisement
Malawi Police

Malawi police officers are the most corrupt in Africa, according to a study conducted by Afrobarometer.

The research report which was released on Tuesday has singled out Malawi as having the most corrupt law enforcers on the continent.

In the report, the Pan-African research network revealed that the Malawian law enforcers have held to the record for the fourth year running now.

The report named ‘People and Corruption: Africa Survey 2016’ states that Malawi is one of the countries in which police officers receive bribes to “ignore crime”.

“You can pay off police officers to ignore any crime, however horrific and devastating it’s just a matter of price,” reads part of the report.

Ironically, in Malawi, the report says, two thirds of those that took part in the research believe that corruption has gone up for the year just ending because police officers take a role in it.

Malawi Police
Police officers in Malawi named the most corrupt in Africa.

The study reveals that 9% of the respondents in Malawi blamed government for being slow to fight corruption with 64% believing that it is the citizenry’s role to redress the situation.

Malawians involved also were part of the 35% of respondents on the continent who openly said they would not report corruption to necessary officials because they fear of landing themselves in trouble.

The survey, which was conducted in 36 countries from March 2014- September 2015, according to a published report by the African Independent, involved up to 43,143 respondents who all gave out their experiences and perceptions of corruption in their respective nations.

The survey had gone ahead to state the frequency of bribery cases in six key public services including schools, hospitals and police services as well as the quest by the people to end corruption.

In the report, Afrobarometer said: ‘’Public services are burdened by having to pay multiple bribes every year, rather than just once or twice.’’ The report therefore mentioned schools, police stations and hospitals as institutions where people pay bribes for the services they seek.

Recently, in a report that Malawi24 carried, our reporter Happy Arnold Soko found out that police officers receive up to MK120,000 to withhold a case before it is taken to court.

The story also revealed that police officers in the country are pocketing up to MK120,000 a month from suspects who are forced to pay for what is supposed to be free police bail.

When contacted by Malawi24 for a comment last week, National Police Spokesperson, Nicholas Gondwa, pointed out that police bail is free and no suspect is supposed to pay.

“No any police top authorities condone such behaviours, the Inspector General himself is against this. If police are demanding money from suspects to be given bail it’s very unfortunate and that’s total corruption,” said Gondwa.

Advertisement

580 Comments

 1. takaoneno kaye maiko a anzanu mmene amawasamalilira apolice ndipo ndiolemekezeka koma bwanji mmene amapangila katangale what more with the poorest police officers of malawi,a barometter anuwo ndi ofoila

 2. Lucky of discipline is the Genesis corruption shall never end is global financial crisis but here in Malawi our men and women who are interested in money than anything. What they luck is discipline put it in the police. Another thing is that people nowadays are joining for the sake of money not for the love of that particular job hence that they demand money

 3. Apolisi ena ndi apolisi othandiza koma ambiri eeeeee ndani sadziwa kubakwake? Vuto loti amangolembana pachibale pawo nanga wapolisi wagwidwayu pa nkhani ya Issa Njaudyu moti tichite kufunsanapo apa?

 4. Unless prominent figures of malawian gvt stop corruption and control pay rates…. Fi dem police & control th economic crisis th@ is affecting malawi as a nation, thus when you xpect these guyz to xcersize the discipline that they were taught @ th training……,

 5. Mmmh apolisi akumalawi ndi mbava zotha ntchito and ngati akundimva amve ndiagalu akuba,and im going to talk with zomba traffic police,inu ndiye agalu bola malawi ithe ndithu angobwera mulungu adzaweluze mwachulutsa kuba heavy thats why mvula ikuvuta kubwera kubako machimo achuluka mumawabela anthu osalakwa ovutika……..

 6. It’s Nigeria….stop tarnishing the image of our country…nanu zinazi osamangokhulupirira. ..nxaaaaa!! kumasangalala dziko lanu likunyozedwa….corrupt yes they are but number 1 ah no!

 7. Am agree,these are crooks more especially traffic police officers are very corrupt,they pretend as they know their work by going to the roads early as far as five oclock in the morning yet they have got a mission of harrasing travellers,you are very stupit,go to your work at eight oclock,once I caught you,you will be in trouble,I am a true citizen of Malawi,zotiberazo ife ayi,amene amagulaso mowa ndi ochepa,SITHANI PLZ!

 8. ndi tchito yakeyi akuyenera atero yopanda tsogolo azidyeratu ikatha tchito ndi pakhonde pa mwenye kulondera kkkkkk

 9. ndi tchito yakeyi akuyenera atero yopanda tsogolo azidyeratu ikatha tchito ndi pakhonde pa mwenye kulondera kkkkkk

 10. So what are the cause of such rise of corruption and what are the recomendations of such research. Where did they conduct such research in Malawi? Can they give atleast three practical examples. I find the research that is lacking authority and cridibility. When obtaining data, u never use one method. Is phone call only reliable means of finding out the truth about something?

 11. Tiyeni tipemphelele Malawi mavutowa asamachitike! Iweyo ukuopa kutchula akuluakulu anaba ma bilion aja? Kodi. ndalam zimene zija anaba ndi a police! Plz guyz dont do things kuti mumve kuti police iyankhula chani!

 12. Iiiiiiiiiiii muvutana nawo sindikuwabakira osakawo palipose dipatiment imeneyo ndimavuto okhaokha kuno ku sauth africa ngatiso uko kwathu basi munda ndikatangale wawoyo atani ngati katangale akumyamba ndima presdent.

 13. i have searched and found that Malawi is not among 20 most corrupt African country so how can Police be on no 1.for a country to be declared corrupt they look into all government departments. i doubt this rersearch it cant be no 1.

 14. Apolisi pali chani ma 50 kwacha omweo ndi amene mukuwanena nawo?? Tapitani Ku Immigration/ MRA mukaone mmene amapangira katangale mmmmmm koma kungoti vuto siiwe olembawe ai koma kusayenda ndi kusazindikira

 15. Achibale,zimenezo zimacitika pa maiko ambiri so a better way ku mafunika kuti govenment a malawi a pereka maripiro a bwino kwa athu ose ogwira nchito kwao.acoraption itha ose pa dziko lose.for exaple:zimafanana ndi ku gwira nchitu kwa muntu a sa ku phatsa maripiro a bwino,palipe zina madala mu amba kuba becouse of not getting enough.point yanga ndi yimeneyou thats why apolisi aku malawi angokhala a ku bela anthu ntawi yose chifukwa ndi kuti ama landila ndalama yochepa kwambiri.

 16. Yes it is absolutely right with your research, coz they are the most less paid in Africa with less equipment to do their job whilst their bosses are continuing Cash gate there by letting them down

 17. Pali apolice ena samafuna akumachita zachinyengo koma kamba ka situation yomwe amakhala zimawapanga kuti achite zachimyengo, si a police okha omwe amakumana ndi mavuto oti nkupanga zachimyengo aphunzitsinso amakumana ndimavuto ngati omwe amakumana ndi A police wo koma nanga Ana choko?
  Mpofunika boma lilemekeze anthu ogwila mboma zotsatila zake chinyengo chizachepa not kuti chizatha ayi koma sitizakhala ndi mbiri yonyatsa ya zinyemgoyi

 18. tingathane naye pokha pokha titakhala ndimalamulo okhazikika chifukwa mmalawi muno tangokhala ndi malamulo opanda kugwira ntchito mwachinsanzo wapolice akapezeka olakwa samapasidwa chilango khani zawo zimabwisidwa nde pazifukwaz ndipamene zikutivuta boma likuyenera kukweza malipiro awo komanso nyumba zokhala awapase zabwino ndinso akapezeka wapolice olakwa asamamuyikire kumbuyo nkhani zawo zizikhala za open ngat munthu aliyense

 19. nkhani yakatangale ikufunika kuti aliyense payekhapayekha ayambe wasiya katangale then tithana naye. kodi apolisiwo amapanga katangale okha? mesa amapanga ndi inunomwe.

 20. What people are saying bad things about our mother land they should visit neighboring countries and copier with our police.but to my view that is false about africa

 21. Not true Mocambique Police is a Law into themselves very corrupt not disciplined. In Tanzania they openly request for a soda you don’t give them you are in trouble.

 22. Guys if you could have visted Tanzania and see what Police does there mmmm then you coul have concluded which country is more corrupt

 23. Koma ndie ndizoonadi ku police ya ku malawi kuli katangale ochuluka ineyo olo mutati nditchule maina ya apolice amene adalandilapo ziphuphu kuchoka kwa ine atha kukhala ambiri, komabe ndiyamike iwowo pakuti akadapanda kutero bwezi ine ndili mundende, komaso pothandizika paine ena adaphwanyiridwa ufulu, ofunika kupeza njira yothetsera katangale.

 24. Mmmm thus not true, just go 2 Mozambique, many of our police officer r professional capable than in many countries, only very few i will say yes

 25. palibe chabwino apa, apolice akunenedwawo nde mbava zotheratu muthu akugwira day shift kma mazulo akupanga yake vakabu. Wapolice wanji olowa ndi certificate ya grade8

 26. bodza limenelo apolice athu amagwila bwino tchito yawo ndindani wapeza zopusazo ? Taona apolisi amaiko ena okuba machitsazo congo, akumocambigue amaopseza aku zimbabwe amalemba timilandu tosaveka bwino amene aja kwathu kumalawi amangodutsa apolice athu siakuba ngati alipo ndikagulu kochepa kodi malawi akumupezelela bwanji?

 27. Bodza leni leni. West & East Africa akanapitakoso APA zikuwonesa kuti sanapiteko amawopa Boko haram. Nanga Mozambique, RSA. Zim.kkkkkk zabodza zenizeni.

 28. mabvuto ali nd apolcewo zomveka kupanga chnyengo ndpo a polce nd aboma iwo akuwonera akuluakulu amboma kuyambra msogoler wa dzko mwatan inu mukusambra a polce? dzko lonse palbe pomwe katangale sachtka

 29. Not true ,go to Tanzania, Mozambique and zim.who asked you for favour when driving an authorised vehicles on the road of Malawi. You gave your self its you who are corrupt

 30. Amalawi azindikile kuti pamene chinachake chikuchitika ndiye kuti pali chomwe chikupangitsa. Osatola anthu mkamwa inu zoona zenizeni mukuzidziwa zilembani nthawi yanu.

 31. If our police officers r de most corrupt in Africa,i see no problem on dat coz if u can agree with me, corruption is worse where there is disatisfaction.look @ their salaries,its just a chicken feed.so how do u think de police officer can survive.we have 2 learn how we can deal with de causes of dat corruption rather than treating symptoms.

 32. I hope Afro Barometer go it ryt. Our Police department z dirty. But w are in a difficult period. Apart meagre salaries but mmm it z too much. Policemen hv lost their integrity. It z shameful n sad story for our nation.

 33. Muwaonjezere ndalama anthu amenewa osamangowanena kuti korapasono nthawi zonse kodi mbuzi mukumayimana udzu pomaimangilira kufupi ndi udzu kodi siyingadule nkukapeza mpumulo?

 34. Apolisi ndi anthu komanso akugwira ntchito kuti athandizile ma banja awo.tsono munthu akukupatsa ndalana uzikane? mukuganiza kuti mulungu angatsike yekha kuzakupasani ndalana.amene akupanga nsanjewo akaphudzile ntchito ya upolisiyo kuti aipeze answer.ine sindinganene kuti akusokoneza kapena sakusokoneza chifukwa ntchitoyo ine sindikuziwa

 35. Ngati president ali wa corruption….ndiye mumaona ngati a police atani…..akakudyerani kwanu???? Keep it up a police inunso ndi anthu mumafuna kunjoya

 36. Guyz zinazi kumaona apolisi kuno kwathu akukhalila kulimba, nyumba zosalongosoka,mwachitsanzo nyumba za ku Limbe Police,malipilo onyenyeka,allowance njema,jombo uniform ndi zomwezija zochoka nazo ku training,promotion mayazi, nde muganize munthu ali ndi mkazi ndi ana iye angatani? kudya pomwe aimangilila basi nde ena mukamafunsa kuti akupanga izi why nkhani yake ndi imeneyo.

 37. @Rex msuku there is no need to trust these fucken bustard so called afrobarometer chomwe akuziwa iwo ndikungonamiza athu basi.

 38. Inu mukunama katangale waapolice ali ponse ponse kumatinso bola kumalawi zilikobwino, muzienda nkumaona zomwe zikuchitika maiko ena, osamangoipitsa apolice athuwa

 39. That man hasn’t been to South Africa and Zimbabwe: In SA where I live you can get away with almost anything if you have money and you are not a celebrity; only celebrities get into shit coz media trails them; but if you just someone unknown and u caught with anything bad including murder; u can just pay your way out; In Malawi you can only get away with a few things

 40. Katangale alibe kuti ukumalandila ndalama zochepa kapena zochuluka kuntchito. kumangokhala kusakhutisidwa kwamtima. taganizani atsogoleri adziko koma nawoso ndi a Cash gate heavy. ndiye apolice akatangale aliposepose.

 41. For someone who has travelled far and wide in Africa and encountered police organisations, Im compelled to question the integrity of the researchers and the institution(Afrobarometer) itself. Should we trust u when u come up with research findings for some sensitive issues??? We won’t, especially when the painting is on the wall..

 42. Mukanena kuti a police akuno ku RSA amalimbana ndi obwera okhaokha ndiye mukulakwisa. Tatiyeni tione a metrol police zomwe amachita panseu amalandila ndalama mwachinyengo mopanda kuyang’ana kuti uyu ndiobwera kapena ayi. Komaso mbadwa zake zakunoko zikalakwilana umaona apolice akulowesapo kachinyengo ndithu chocho apolice alibe mbali kuti uyu ndiobwera kapena ayi.

 43. They r putn our flag on d world map coz they hv bin doin d ryt tingz n no one talkd abt it nw dat its d other way round u r busy advertisn them com-on men let dem b!

 44. Chinyengo chili paliponse man, kuti akuyikile magetsi a Escom ngati usawapatse kalikonse adzingokuyimba nyimbo koma magetsi osakuyikila, ngakhale ku immigration ndiye chisimu, ngati ulibe kapamwamba passport sutenga. Mukufuna munene chani apaa

 45. It is unfortunate! Let them be reformed. They will be able to realize the benefits of honesty, doing right, performing with excellence and respect for others.

 46. inu a Afrobarometer koma ku mozambique munapitako kukafufuza?,wat about SA,,?,,,,,ndinu zitsiru kwambiri,,simukudziwa chomwe mumafufuza ,kuyipezerela Malawi’yo kapena bwanji.

 47. Katangale sangathe,kodi antha bwanjiso pamene kuyambila President ndiwakatanga……..chimozimozi mwana, kholo lamwana kukhala losuta fodya mwanasa antha kukhala osutaso fodya!

 48. Katangale sadzatha mpakana ambuye Jesu adzatipeza,katangale wayambira kumtundako i mean bwana president oti ali ndi zonse zodziyeneleza pamoyo wawo,koma katangale thoo.

 49. Katangale sangathe until Jesus will come,even president amapangaso katangale,komatu amagona pabwino,kwangoti katangale ndikanthenda kopanda mtera.

 50. sakulakwitsa anthuwa amalandila money yochepakoma amagwira chitchito chotopetsa,akuti member of paliament dzindalama dzimbilimbili koma wa police kachenje basi ,aganize bwino

 51. best solution to end dis z by consulting junior police officers & ask dem de main cause?… in scientific xoolz of management we say its a junior hu suffers & know de problemz @ any work place.. eg: l see senior police officers living in big/beuatify govenment houses in areaz like 47, 49 & 3 in LL…. new naperi, nyambabwe, BCA hill & anglez go there in BT.. may suggetion z may be these juniors r not considered in termz of there welface..

 52. Nkhani Ndiyoti Timayamba Ndiifeyo Anthu Kumayenda Pansewu Ndi Galimoto Zamilandu Komanso Katundu Wamilandu Kudalira Katangale Yemweyo Kumachita Kusungilatu Ndalama Yoti Timpatse Wa Police Ndiye Muona Ngati Ndani Angakane Ndalama Tikuzionatu Ife Mmisewumu Ndiye Zowanamizira Apolicezo Ayi

 53. Zomvetsa chisoni izi chaka ndi chaka kukhala patsogolo ndinkhani zakatangale, kunenadi zoona apolice awonjeza kwambiri pankhani zakatangare , mwina vuto ndipalipilo awo ndiochepa kapena nyumbazao? Komano kupatulapo zimenezi nchitidwewu wangofikapo pachikhalidwe ndipo nkovuta kwambiri kuti asithe zakatangalezi , pakuyenera kukhara ndondomeko yoyenera pakudzudzura apolice’wa anayenera kumvetsetsa kuti dziko lathu ndilosauka, boma lilibe ndalama ,palipiro awo awakwanire monga akudziwira basi.

 54. Dem baddes criminals.. Malawi police officers are good for nothing,,they cant serve and protec without lickle penny..

 55. galu ndi galu basi sangasinthe ndiakubadi kwabas olo atagulilidwa jombo za bwino anthu odyela huwa awa asiyeni choncho azisokesa jombo choncho

 56. Is it the department of the Malawi Police Service only?..make researches in all gvt Departments and Statutory corporations like the MRA,IMMIGRATION, MEDIA-HOUSES,DEPT OF ROAD TRAFFIC,WATER BOARDS,ESCOM and others too numerous to mention they are NOT corrupt as such but am sure there could be huge traces of corruption than you anticipated!..this only symbolises the level of poverty of a country!..Corruption MOSTLY haunts minds that are mentally,physically and financially weak! A *Poverty Tree* that grows too big, bears fruits that have **Big marks of Corruption!**

 57. People you’re saying South Africa, Zimbabwe and Mozambique police are the most corrupt, its because you use the route to South Africa. If you were to walk to USA, you’ll say Zambia, Angola police are the most corrupt. If you ask foreigners especially Pakistanis and Indians who do deals with police at KIA,they will say Malawi police is the most corrupt.

 58. Apolice Akumalawi Nivakuba Kwambiri Amazitama Kt Ndalama Yapamwezi Sitiwerengera Ndiyatiyi Ndi Kachaso Pambalipa Kachibuku Koma Zakatangale Ndeyogura Za Badjet Man, Apanso Ma Road Trafic Police Eeeeeh Nde Machacha Pakatangale Amachita Kuima Kumbuyo Kwa Minibas Ngati Akuona Katundu Chonsecho Akufuna Ndalama Enuwake Amati Tilipo Atatu Nde Ugwese Ma Aluvera Atatu.Haaah Palibe Angathese Katangale Ku Malawi Poti Anajaera Kale Kamchitidweko.

 59. Ndi abodza kuno kwa africa paliponse apolice amachita katangale osati kumalawi kokha kuno. Inu a24 muwauze kuti akunama ayambileso. Kenako atiuze zotsatila

 60. Zabodza kuno apolice ndi ovutika samaba ai amagwila ntchito usana ndi usiku pogona alibe osapanga kafukufuku ameneyo bwanji

 61. Zankhutu Eti! Katangale Amayamba Akumipando Yosianasiana Mpakana Uyo Mumati Msogoleri Wadziko Nde Mukuti Munthu Wamba Angalore Kuvutika Njira Yachidure Ilipo Haaaah Mwazazindikira Mochedwa.

 62. Tawonani kuti mupange ziwonetsero zongoyenda chabetu simukupanga chirichose mukawona wapolice watenga gologodela wake kumaphaso mzika tawonani azathu aku SA Zenophobia munawona wa police akuwombera zika yadziko ? Ozindikira athuwa ndimakape basi kuno ku SA Timati matsotsi emenewa mbava zenizeni ine nde ndiyamba kugulitsa chamba palibe zomangana apa bwanji alubino akuphedwa ngati nkhuku guyz chamba ndi dilu kupa kwachaka ndilemelaka

 63. Boma lake liti? Ngati anthu amene akuyendetsa bomali ndi omwe ali patsogolo kugwiritsa ntchito apolisi munjira zosakhala bwino zambiri. Chimene chimapangitsa kwambiri ndi tindalama tochepa tomwe boma limawapansa anthuwa. Taonaninso nyumba zomwe amakhala anthuwa. Mukuganiza kuti iwowo safuna kuchita bwino pamoyo wawo? Nanga atukuka bwanji ngati salary siikwana olo badget ya masabata atatu a mmwezi? Aonjezereni ndalama anthuwa ndipo muona kusintha!

 64. Kodi mungoti malipiro ati ? Kuba sikuwona malipiro guyz tawonani pano alubino akuphedwa anthuwo akawagwira mkumawapatsa chigamulo chochepa kwambiri chifukwa choti alandira ndalama. Kodi umoyo wamunthu ukukhudzana bwanji ndi malipiro? Nanga poti loko kuti mwagwira wakuba mkupitanaye ku police mawa mukampeza akudya chap kumsika nde zikugwirizana ndi malipiro? Awa asiyeni abeni mgwanya ena zina zinali mbava kale chifukwa chachibale mkuwalemba job ndepano zimabela mu jezi

 65. Don’t jst say abungwe lina, titchulireni dzina la bungwe lomwe lapanga kafukufukulo kuti tidziwe kuti ndizoona zomwe mwalembazi. I do nt agree wth this statement, I respect Malawi police pa ntchito yomwe amagwira. Police yathu ya Malawi ilibe zipangizo zokwanira kugilira ntchito koma still amatha kupangapo kanthu pakachitika vuto. In world where ever u go there’s corruption koma chifkwa choti dziko lathu la Malawi ndilosauka amabugwe opanda maina omwe mukuwanena apawa amati Malawi ndi dziko la Malawi liri ndi police ya corruption. Iwowo potulutsa report limeneri apanganso zachinyengo posanena za maiko ena kuti kuli corrupted police, therefore them also they r corrupted

 66. Malawi padziko lonse lapanse malawi ipa nawo pa top ten losauka ndiye apolice amayetsa kudzipezera kangache kokadyetsa mabanja awo choncho boma ngati lingakweze malipiro apolice zitha kusintha apo biii azibabe

 67. Bodza limenero…kodi Cashgate ija anali apolice??ngati Boma silikusamala apolice vuto ndi bomalo,,iwowo akungopanga zoti nawo athandizike…Komanso mayiko ena simunawone kapena zomwe zikuchitika.Apolice osawanamizira,,Bwampini ndiye Mbava yayikulu akuzunzitsa anthu

  1. Aaaa Bon zoona nanga kumalawi mavuto amene yikubweretsa nbuziyi kale zinali choncho?Olo dziko lathu ndilosauka koma mpaka pomwe zafikapa??No its just too much

 68. Mwa a police wonse akatangale ndi a pa musewo,kaya mmati a traffic,ee ameneaja man amawonjeza,koma ndikukayika kuti boma silikuziwa aaa nanga mbomamo mukubedwaso koopsa nde angalese mnzake ndani? Tiyeni nazo mlungu akalanga yekha.akanangowachopo pa msewopo chifukwa akugawana half half ndi bomalo.

 69. Akunama. They probably haven’t been anywhere else in Africa. Try Tanzania, Mozambique, south Africa, Zimbabwe then we can talk about corrupt police. Fake reports

 70. Mukuti amarawiamopa aaa amenetikukamudaurirayo ndiyembava yeniyeni amakhara akuzikharidwerakatangare waoyo ndiyeukapita kuktdandaura kumangokhara kutaya thawi

 71. ndipo ngati kulidi wakuba mosachita manyazi ndiye ndiye wa police wa malawi amakubera koma choonadi akuchidziwa asatana tsiku lina mudzayankha mulandu

 72. Ndzonad ndmbava pakhomo pa chitseko chawo analemba kut belo ndyaulele koma mmmm sim,mene amakakamilila akut ya fanta ngat samalandla agalu amenewa.

 73. Mmmmm zinazi kumazionatu bwino inu ofufuzafufuna asaaa ndimmene amachitila apolice kuno ku south africa coraption za malawi yanuyo mukunamatu apapa’muyambeso kufufuza

 74. koma.msewu wa.49.lilongwe.aikidwa kudzalanda.ma.k500.ma.bus.driver.basi palibe.chomwe.akusecha.kungomwitana.driver.basi.akawapatsa k200 basi ma.loadblock ali mu 49.load ingochotsani plz.its nating

 75. Kuyipitsa Malawi always. president is corrupt, Nduna Corrupt, mulimi is corrupt. DC is corrupt mupita nazo kuti zimenezi. Talembani zotithandiza kuti tiphuzileko pilizi chonde

 76. kodi yunifomu imeneyi yikusiyana bwanji ndi malawi #army awa athakusokonezelana ntchito,malawi gvt should change the uniforms tiziwaziwa ife akumudzife kuti uyu ndiwa polisi uyu ndi wa army!

 77. Its not only malawi police,but Africa as a whole.This is because of the peanuts that they are earning out of their hard job!!, no wonder.

 78. Kumangoziona .com,olo atamangilidwa nyumba nde angasithe nchitidwe wa chinyengowu?anazolowela kupanga ziphuphu bas nde olo zitatan sangasiye ziphuphu,,,

 79. katangale sanganthe ndipo sazanda chifukwa apolice amalandira ndalama zochepa.ngankhalenso manyumba awo ndiomvensa chisoni.sungakayang.anire ku bank nyumba mwako mulibe ufa ayi .mbuzi imanya pomwe ayimangilira.

 80. Kodi si inu mumati jb awina, adawina? Lero ndiye tikukhulupilireni? Who finded your research. To hell with your research, you’re anti police mupite kumaiko inewa. Mwationerera aMalawife eti chifukwa cha cashgate kapena.

 81. Zoona man ine nthawi imene ndi mapangitsa passport yanga ndi dali pa line kuti ndilpile,adango bwera mzuku molo moti akhale pa line amvekere taima kaye sukuona kut abwera abwana,km ku malawi mumalemekeza obwera,ife mumati funa nthawi yovota basi.

 82. Inu Apolice iyo ndi tchito ngatipalinjila yodyela dyelani man koma osamapanga chipogwe azanu ngati apolice Aku Ethiopia Ai

 83. apolisi asiya bwanji kulandila zinyengo ngati akulandila salary yokwanira nkomwe apa!!!zinyengo azipanga basi ndipomwe nawonso amadyera!!

  1. Akulu akulu.apolice amalandila za nsinkhu wawo .tisamati amalandila zochepa ndani ndalama dzinamukeanapo?olo inuyo zikukukwanani. ngakhale alandile za mbiri chinyengo sa ngasiye chifukwa olo mmakampani mabwana omwewo ndi amene amapanga katangale. aliyense amapanga za sayizi yake.olo inunso mumapanga dzinja musiye .mukuwona ngati sikatangale? koma mwa udze akonde ziko lawo koma mukanena za ziphuphu. konse dziko lapansi. zikuchitika mwamva .olo ant coraption ali dziko lili lonse chifukwa cha ziphuphu.inuyo ndiye woyipa kuposa .apolice omwewo mutapedza mita.koma okhawo ochita chifunilo cha mulungu.sanga chite ziphuphu.yesu woyeee.

 84. Kunena zowona kafukufuku uyuyu salibwino ayi ndipo mukuwanamizapo athu apa.mukafuna zakatangale yemwe mukunenayo tabwelani muzawone kuno ku south africa muwone zomwe amapanga a police kunoko ndipo muchita kuziwaso kuti malawi yomwe mukuyinenayo ilikobwino ndithu.

  1. nde afike mu joz especially park station amakubera tindalama tonse kaya ukupita kumudzi uva uli ndi ova stay tinkhan tawo tosaveseseka

  2. komanso akafike mu msewu wa Jeep ndi Nagget akaone m’mene apolice akupangira katangale,kukugwira pano akutaya ndi R100 kenako amangozungulira kuseli ndikukugwiranso umvanso R100 bolanso kuno kuma sipano pajonz ay

  3. sakukambatu zamusewu zokubela ……malawi muthu okupha amatha kutuluka kupolice south africa katangale alipo ndiwowabela obwela munsewu ndemusianise ….ku jozz ainyawo sapangidwa katangale pamene kumalawi police amabela ainyathu musiyanise

 85. KKKKK . WA KAFUKUFUKU AMENEYU BWANJI SANENAPO ZA MALO AWA : AUCTION FLOORS , IMMIGRATION , MRA , KOPEREKA MA CONTRACT A BOMA . KOGURA FERT . WA MA KOPONI , ROAD THAFIKI , ETC ?

 86. Apolic akumalawi ndi makape vuto ena analembedwa ndi ma j c akumazunza mzika kumasamala obwera ndili kuno ku s africa koma eni amanjoya pomwe obwera ndimavuto ,so mbuzizo zisiye kuwabera amalaw fosek!

 87. Ngati Katangale akukula kwaakuluakulu aboma (chpani) ndie mungaembekezele cholungama kwa apolisi? akulu akulu akulu amboma nkhaniyao ndkatangale nawo apolisi amangoona ngati ndiumwai wapadela potengela nchto yomwe amaenela kuigwira.zkuenela kusntha kuyambila kwa akulu akulu amboma.

 88. Ngat amapasa ndalama zochepa nde akufuna atani? Aphuzitsi nso ayambe kupangisa rent ma classroom kut azipeza extra money ..anawo aziphuzirila kunja ..shupiti

 89. Koma ngati opanga kafukufukuwo apatsidwa Ndalama, bola akabweze, kaya ndi sing’anga ndekuti sadziwa koma ngati mmodzi mwa a prophet a amasiku anowa, ndekuti ulosi uwu ndionama ndithu.

 90. The issue is Malawi is the poorest country in Africa & Poorest Security officers in the region who can beg even k 50 in our borders and clear the road for the smugler and criminals to pass since their salary do not cover 14 days of 30 days.

 91. Apolice aku malawi ndi amatchasi amabera evn muthu osauka sawerenga ndipo akaona kuti muthuyo ndiozindikira amayamba kumumenya kukatsekera opanda mlandu mawa lake amati file yasowa mwachidule athuwa ndiopa tchito yao sakukwanitsa malipiro ochepawo alipoteropo.

 92. Better we have some institution to represent us in Africa on position one apart from our Malawi Queens.Next lets scoop position one in the world

 93. vuto ndiloti apolice a mayiko azanthu amalimbana kwambili nd anthu obwela e,g aku jon koma kuno kwanthu mayi mayi amatikakamila kwambili ife eni dziko ngat ulibe ndalama nde uli madzi ukagona mchitokosi basi koma wobwela makamaka azanthu woyela khungu awa eshiii or atalakwa amwene amangowasi chifukwa amawapasa ndalama chimenecho ndcho chinyengo akunenacho iwe ukuwa bakilawe sunaziwonepo

 94. Pakhale ndondomeko zabwino makamaka mmalo kapena pa station pamene wa police amapezekapo..OC akhale oopa mulungu kut adzionetsa chitsazo chabwino,anthu wambafe tiyambe kuyenda njira zasitileti pofuna chilungamo posagwiritsa wa police ngat chiopsezera azathu, Boma nalo likoze ndondomeko zabwino zowasangalatsira a police kut adzikhutitsudwa, koma sikuti katangaleyo angatheretu zingothandizira kt achepe pang’ono..

 95. Inu simukudziwa chifukwa chake apolice akwathu sitimawasamala imagine nyumba amagona apolice akumalawi sizabwino malipiri awo si abwino ngati mukufuna katangale athe yambani mwakoza zithu ngati zimenezo apolice nawoso ndi athu amafuna zabwino

  1. Keith kuteleku vuto ndi chisamaliro cha athuwa tisamangowona mbali imodzi imagine ife pano tili busy pa fb iwowa ena ali mmakomo mwa athu kuwalondera ena ma bank koma allowance yawo ndi yochepa kwambiri yambiri imapita kuboma tiyeni yipemphe boma liwaganizire boma lathu likukanika kupeleka chisamaliro chokwana wa police akapita ku workshop ndiye kuti ndi bwana emeneyo

  2. atate fisi ndi fisi sangasanduke mbuzi olo mutamuika nkhola ngakhale akukhala nyumba zabwino kumayendera magalimoto abwino chotani azapilizabe katangale timaziona ife atraffic akukhala nyumba ya boma ali ngalimo yabwino koma akupangabe katangale

  3. Kodi whynot south africa only mentioned malawi poti ife tikamawona za katangale kumbali ya a police ku john kwawonjeza abale anthu amagwidwa depot timanva iiii tangowapatsa apolice kenakake anditaya vuto la amalawi anthu akamanyoza dziko lathu timakhala pa for front kuma peleka ma comment oyipitsa dziko lathu tiyeni tipite kumayiko azathu zomwe timapanga ifezi kulibe ndizomwe zimapangitsa kuti mayiko azathu aziwoneka ngati sikuchitika katangale kumachitika bt they no hw to handle issues osati akatulutsa ma report basi ifeso kumawavomereza kwawoko ndiye kuli katangale kwambiri

  4. Komaso tisayiwale muthu sangakhale wa traffic asanakapange up grade maphunziro ake aku policeko zomwe zingampangitse kukhala ndi rank yabwino yomalandira salary yoti atha kugula galimoto and timayamba tokha amalawi kumayenda pamsewu ndimagalimoto amilandu kumakozekeratu kuti akandigwira ndingowantchula kenakake even wa traffic asanakugwire mumakhala mwasungila kale mmanja timawonatu ife musawade tonse ndife akatangale kuteleko tikayamba ife kusiya kumawapatsa ndalama asiye chifukwa katangale apolice amapanga ndi ife osati zinyama ai

  5. Eetu nyson tisiye ifeyo kuwapatsa nawoso asiya nanga owapatsa tikuchuluka ndiye asiya bwa tonse ndi akatangale si apolice okha

  6. Fundo ndiyomwe wakamba january and vuto amalawi timalimbana tokhatokha pamene pajohn they r after obwela.Its not chisamaliro koma kuti timawaopa apolisi pamene pajohn eni ake sawaopa apolisi.Zinyengo timayamba ndife amalawi kuti tipange zinthu mofulumila

  7. Maggie usamaikire kumbuyo mbava zoba powopsyeza ndi uniform.Dzowa kuti fulu amamunyerera yemwe wamunyamula.APOLISI AKU MALAWI NDI A KHWANGWALA ndipo I Do agree with the results

  8. Mmmmm madalitso sikuwayikira kumbuyo umvetsetse tonse ndife akatangale, katangale kuti achitike that means there are two parties chomcho mbali ina italimba mtima kuti sipeleka chiphuphu sangapangeso l can give u an example wachibale wanga anamangidwapo and for him to hv a belo apolice anati tikambilane l agreed to discuss with dem ndipo tinagwilizana kuti ndipeleke k5 pin ndinavomera bt ndinapepha lisiti kuti ndikhulupilire zoti ndalama ndikupeleka ikupita ku account ya boma and they failed to produce a lisit end result sindinalipile bt anapatsidwa bail free apa katangale sanatheke reason mbali ina inakana ndichifukwa ndikuti tonse ndife akatangale palibe wabwino chachikulu tidzipange blame amalawi sitidziwa malamulo tinakadziwa bwenzi tikumawawuza chilungamo izi sibwenzi zikuchitika, mada we are all to be blamed not only de police.

  9. Zex umvetsetse we are all to be blamed katangale is every where lets think about de cashgate scandle sikatangaleso ameneyu let us kook at all angles

 96. Malipilo awo ndi ochepa ndinkuwona ali akatangale. Koma nomber 1 pali apolice akuno ku R S A ndi a chinyengo bad.

 97. akuluakulu tisaikire kumbuyo apolicewa ndi mbava zimenezi amalanda moopseza sikut anthu kumakhala kufuna kwawo kma kuopsezedwa bas.

 98. Katangale sazatha,ndipo sazatha,mawu oti (KATANGALE)KAPENA (ZIPHUPHU )amene anapeleka mayinawa analakwisa m,malo mongoti (KUBA)mukuganiza mayinawa m,mesa anachokela ku boma komweko?Umbandawu ukuyambila mu office ya pulezident musatipusise ife si ana ayi asiyeni apolisi akuyambani chani,2 ,I CAN USE THIS ENGLISH,WITHOUT CORAPTION NO GOVERMENT CAN MOVE IN THIS WORLD OKY,CORAPTION IS THE TOOL KWA ANTHU ANDALE,PALIPONSE PALI KUBA,OTI ATHETSE IZI SIAPOLICE KAPENA BOMA KOMA INE ,A 24 NU,ALIYENSE ATENGEPO GAWO OKY?

 99. ur so stupid kodi wa police ndalama zimene amalandira ndizingati? kodi ndimayesa mumati amboma ayamba kulandira sarary?nanga ma change mukutipatsawa ndi sarary?

 100. Vuto Ndimalamuro Anthu Komaso China Nchoti Katangare Mmalawi Muno Amayambiri Kulikulo Nde Kafa Nsiyanji Ngati Ine I Cant Have A Chance To Stand With Them My Life Will Over.

 101. thy tirelessly & thy are most effective koma taonani ndalama zomwe amalandirazo? Mzochepa anthuwa zinthuzi amachitira kuwawidwa mtima let th govt pay them more

 102. vuto ndloti a police aku south africa amalimbana kwambili nd anthu obwela koma kuno kwanthu amamukakamila mwini dziko kusiyana ndwobwela mwachisazo tili nd ma china nd amwenye zimapezeka olakwa ndwobwelayo koma akangoti tiyeni nayo ku police uyu kunena mwini thaka kalekale amusekela muchitokosi mwina olakwaso siyeyo chifukwa amaziwa kut iwe ulibe choti angadyepo koma obwela amaziwa ili nd ndalama chimenecho ndcho timati chinyengo tikunena zapa jon amalimbana nafe amaziwa kuti ndife anthu obwela koma kuno kwanthu eshiiii unawonapo wa traffic akuyimisa galimoto ya mzungu ndkusecha ata koma zanthu eeeeee

 103. What number is Afrobarometer in terms of corrupt researchers ? The Malawi police could not bribe the researchers coz they are the poorest on the continent !

 104. iwe just get your passport and get it stamped pa calomue border and see wat happens…thats just stupid!!!taona corruption ifeee mwina you just see it from the tells…

 105. This is a true reflection of what is happening on the ground but the reasons seem to be valid as well. This could be because they r the most less paid in the continent too thou the south african police too may be the second to malawi police

 106. Ineyo zoonadi ndinali ku Dedza a traffic ose kumangolandila ndalama kwama driver a min bus ndipo ndizoona kumseu amapitila kukakolola osati kukagwila ntchito yawo

 107. Noway to rectrut mbava zimaba dzina la Police ;kumagula fetelezawotchipa kuno kwa Dzoole Admarc.komaso akamaba amangosithidwa ukagwila ntchito malo ena chifukwa nchiyani sheeeti .Akuba kuchuluka kuno SC DZOOLE

 108. Very very true! Inu amene mukukakamira kuti koma South africa nu, mwina ndikale mudachoka bwerani kaye mudzaone nokha ziri kuno.

 109. Very very true! Inu amene mukukakamira kuti koma South africa nu, mwina ndikale mudachoka bwerani kaye mudzaone nokha ziri kuno.

 110. its not true, if you want to see corrupt Police just go to South Africa and Mozambique. Zonama walemba za boza ameneyo.

 111. I agree. Ukachita ngozi pa msewu amakudyera wolakwawe plus wolakwiridwa. Ukaberedwa umadyeredwa za maunits,kuti ayambe kufufuza kapena mayendedwe kenako wakubayo akamugwira amadyeredwanso pomuuza kuti azipulumutse yekha.

 112. ANTHU MUSAFANIZIRE KU RSA. KU RSA AKATI MUPITA KUKHOTHI ZIMAKATHERA KUKHOTHI AKAGWIRA MUNTHU WAKUNJA NGATI ALIBE KALIKONSE MPAKA DEPORTEE. MW OLO UBE AMAKUUZAKUTI NGATI MULINDIKENAKAKE KUKHOTHI SIMUPITA THEIR IS DIFFERENCE.MW MLANDU ULIONSE ADYEPO

 113. And thats fact road block iliyonse ndrama mxiee galimoto la nzungu kapna wadziko lina samayakhura ata matha kma kpezera nzika eni thaka shut up zawo

 114. sm not very sure abt this its total lie com to south thats wen u will see yotal coruption and day ligut lobbery by the nen in unifoarm not in malawi u can even google on the internet its not a secret

 115. How did they conduct their study to come out with this unfounded claim? can they compare our poor and humble police officers with Mozambique, Tanzania, south Africa who are beyond corrupt. leave malawi alone ngati sakukupatsani business pitani kwina.

  1. it’s not low salary that is leading malawi to be the most corrupt country in Africa.It is moral decay of our leaders.Be reminded that a country is like a family.If parents are irresponsible,don’t expect anything good from the children.IF MALAWI IS TO CHANGE FOR THE GOOD,OUR LEADERS FROM THE PRESIDENT TO THE SMALLEST GOVT. AND NON GOVT INSTITUTIONS MUST BE
   DELIVERED AND WORSHIP GOD IN TRUTH AND SPIRIT.NTCHEU

   MKOMERA GAMA.

  2. it’s not low salary that is leading malawi to be the most corrupt country in Africa.It is moral decay of our leaders.Be reminded that a country is like a family.If parents are irresponsible,don’t expect anything good from the children.IF MALAWI IS TO CHANGE FOR THE GOOD,OUR LEADERS FROM THE PRESIDENT TO THE SMALLEST GOVT. AND NON GOVT INSTITUTIONS MUST BE
   DELIVERED AND WORSHIP GOD IN TRUTH AND SPIRIT.NTCHEU

   MKOMERA GAMA.

 116. Inu mukunena ku malawi kokha bwanji mubwere kuno ku south Africa mudzapeza kuti amalawi amene akumagwidwa deportee akumakhala kuti anagwidwa coz analibe ndalama yodzipulumutsira kuti awasiye

 117. Koma sangapose akuno Ku South Africa ndiodziwika ndipamalamulo osati aku Malawi only problem is high living of standards & poor equipment of their job + hunger esheeee adya chiyani

 118. i agree with the afrobarometer that malawi indeed have most corrupt law enforcers on continent and true its bcoz they are paid less. partly i blame ordinary malawians who are encouraging the practise by not biding to the laws of this country. imagine minibus drivers are packing four pipo on minibus chairs and when they reach traffic stations they just dish out money to the officers and then they are allowed to drive off. govt should increase the officers salaries and we also the citizens let us be patriotic to our country by abiding the laws of this country and the officers wont have a chance to do corruption.

 119. Akadye kuti ndi kasalary kochepaka.hey guys keep it up if they don’t increase malipilo,zinthu zikudula masikuano but remember God will judge you for sin you commit.Amen

 120. Mmmm mukunam inu sangapose aku RSA reasech yanuyo ndiyaboba yambiranson kkkkkkkkkkkkk koma inu openga et muzuyenda kaye mkumaona kut zinthu zikuyyenda bwanj mukungoplemba nkhan muli neng’a!!!!!! Pansi pakacere ndikumamwa akacaso

 121. Aflobarometer yawona only Malawi ~kodi pena bwanji osamayamikira zinthu zikamayenda bwino“Choose another country NOT Malawi Police”

 122. south Africa police are most corrupt not malawi just vist in park station in jubeg &every Saturday uwona chimbaula chaima pa commitional &delivers street nkhani ndiyokuti make plan !!!osamangoipisa mbili ya amalawi imeneyo si life

 123. Afrobarometer, your reseach is also corrupt. Did you made a physical study throughout africa and see what the police from other countries are offerring their services or you just at in Mw hotels and come up with your fake results. Plz, go out and do your job and comeup with true results

 124. Zaziii zopanda pake y not your nation mumasiya mavuto anu kulimbana ndi africa why cant u research on yo useless gay nor crimate change issues yet we knw u r the cause en brain child of all evil acts

 125. Very true, mainly bkoz are foolishly/unprofessionally over used by ruling party to suppress the opposition, without paying then their dues! Less care from the employer(govt) but much job!!!

 126. It is very possible even if they can say malawi civil service is # 1 in africa that is most corrupt …it is due to low salaries against high living standards

 127. Guys I think you have never been to Tanzania, Mocambique and Zimbabwe, Athu alibwinotu awa they just need a minor panel beating

 128. if u go to zimbabwe they rate as the worst, south africa rate theirs as the worst, nigeria mozambique the same, all african countries rate their police forces and governments as the worst

 129. Kkk…Afrobaromer could have Just rated the whole Malawi a corrupt nation,corruption is done by 2 ppo,in this case you drivers who offer bribes.

 130. Mmm bola kumalawi zimamvekako pang’ono kutengera ndindalama zimene amalandira koma apolisi akuba komanso achinyengo number 1 ndi a dziko la SOUTH AFRICA.

 131. Researches done by afrobarometer r always bogus,in 2014 they said JB ‘ll win da election wat was da true outcome of da election,experience is a good teacher.

Comments are closed.