Breaking: Walter wins as Mijiga, Yabwanya withdraw at eleventh hour

Advertisement
Walter Nyamilandu
Walter Nyamilandu
Nyamilandu: Has won.

Dust is refusing to settle at the 2015 Football Association of Malawi (FAM) Elective Annual General Meeting (EAGM) currently underway at Nkopola lodge following the decision by presidential candidates Willy Yabwanya and Wilkins Mijiga to withdraw from the race at the eleventh hour before Walter Nyamilandu has won for the fourth time.

Speaking in separate exclusive interview with Malawi24 a few minutes ago , the two confirmed the development saying they cannot be part and parcel of illegal proceedings.

“Yes we have withdrawn from the polls. The appeals committee ordered the electoral committee to postpone the polls following the floating of Article 22 but these people have vacated the injunction and they are now conducting the polls.”

“We won’t be part of this illegal proceeding. Too much irregularities yet the electoral committee has defied orders from the appeals committee,” said Yabwanya.

On his part, Mijiga said it was not on to go ahead with the polls yet the whole process is illegal.

“We are surprised with the electoral committee’s decision to go ahead with the polls yet the whole process is illegal. Why are they undermining the orders from the appeals committee? We won’t be part of it,” explained Mijiga.

The stand off between the two parties refused to die in the early hour of yesterday when Mijiga, Tiya Somba Banda and Yabwanya obtained a court injunction against the electoral committee’s decision to carry on with the polls.

FAM legal team vacated the injunction on Saturday afternoon, giving the Fa’s electoral committe all the mandate to go on with the polls.

However, five of the eight Super League of Malawi (Sulom) delegates were absent from the polls.

As it is, the incumbent FAM president Walter Nyamilandu will go unopposed.

THE OTHER SIDE.

Nyamilandu has since won the poll with a whopping 27 votes against, 7 for Mijiga, 2 for Yabwanya

MORE REACTIONS TO FOLLOW.

Advertisement

659 Comments

 1. Zili bwno pot kufuna kwake kwachitika kma athufe sizinatisangalase apitilize kudya ndalamazo mene angathele palibe omulesa

 2. guys ngat nyamilandu wdwina,ndekut iyeyo akuko akutha kukwelana nd mkazi wake mokondwa.So ifeyo monga aMW okwiya tingot tikawonanso nsete zomwezija,answer yake nd DEMO bas.

 3. SIKULAKWITSA CHIYAMBI NDICHOBVUTA ZACHITABWINO ENA NDIKUMAFUSAFUTSO MKUMATI CHIFUKWA CHIYA MAYANKHO NDIAPAFUPI KWAMUNTHU WANZELU

 4. SIKULAKWITSA CHIYAMBI NDICHOBVUTA ZACHITABWINO ENA NDIKUMAFUSAFUTSO MKUMATI CHIFUKWA CHIYA MAYANKHO NDIAPAFUPI KWAMUNTHU WANZELU

 5. Zimenezi munakatifusa zisakho zisanachitike olo tinene maganizo athu tipindula chani anyamilandu tingowawuza kuti alimbikitse mpira ma district

 6. Wina akakhuta cheula kumanyoza BBndiye kuti cheulacho anaikamo chamba. with or without BB ndi Deal. Iwe neba uzingotsitsa ma points ngati wa night

 7. Mwa ma candidates aja anayenera kuwina ndi iyeyu chifukwa anali ndi mfundo kusiyana ndi enawo. Amangolimbikira ndalama za FIFA kuonetseratu kuti amapitirako ndalamazo. Awa aszaimenso iyaaaaaaaaa

 8. Chitetezo kwa anthu ndi ndalama zomwe za pa gate. Aonetsetsenso kuti asamakhale ndi mbali . Tikufunanso apemphe boma limange stadium yamakono ku Bt.

 9. Kodi kuti Nyamilanduyi awine ndi a noma apangisa?Paja a BB ambili ndi mbuli paja.Olo tiyankhule zambiri palibe chingasinthe,zachitika zachitika basi.

 10. There is no where to run, and we should not expecting something new, ngakhale dziko likulamulidwa ndi mbava, we are still moving with reverse gear

 11. Uganga 2 Malawi 0.Nyamulandu is a fool,a learned savage,those who hv voted him to win are most stupid.,they dont want malawi to succeed in football.The 12yrs nyamulandu has been a president of FAM,we have seen no development in malawi football,why should he cling to power and why vote him to power ? It is here we see nyamulandu and his voters being fools.I see nyamulandu being greedy here.Akupezamo cholowa on the expense of malawi football.What he has said in his manifesto is laughable.12yrs on the helm he has nothing and says he says this and that now ,Stupid,foolish.nosense,manyi, Shame on you !!

 12. 1.He must reduce corruptions even favouritsm. 2.He need to show transparency and accountability in all planes. 2.He need to heal the views or suggestions of other people.

 13. 1.He must reduce corruptions even favouritsm. 2.He need to show transparency and accountability in all planes. 2.He need to heal the views or suggestions of other people.

 14. 1.He must reduce corruptions even favouritsm. 2.He need to show transparency and accountability in all planes. 2.He need to heal the views or suggestions of other people.

 15. 1.He must reduce corruptions even favouritsm. 2.He need to show transparency and accountability in all planes. 2.He need to heal the views or suggestions of other people.

 16. mpira siudzapitamso patsogolo ku malawi zimafunika kumalandilana kumayesa mzeruzina posatengela kuti munthu wina ndi wa ndalama.

 17. Amijiga ndi ayabwanya munaziwa liti kuti pali za chinyengo , munangokhala chete osayankhula kapena kukadandaula ku khoti . Mukupita kukhoti nthawi itatha komanso osasatila chigamulo chakhoti,ndie kuti inu muli pamwamba pa malamulo mziko muno. Enawatu anali mantha chabe ,mwawapusisa anthu , munali ndisapoti yambili kuposa wata ,mukanamvela za khoti mukanawina koma ,wata wangotola pomwe iye analibe sapoti yochuluka .

 18. maganizo ndi ongoyamikila anthu amene amazitsata kuti asankha munthu amene amamukhulupilila kuti amatha zikamalakwika olakwitsa c wota koma amene amusankha coz mwai osintha unalipo kwa ife tingoti go deaper wota nthawi ndi yomweyi kumachitilatu

 19. Nyamilandu again???we malawians easily forget jst bcoz we go 4 popularity why votin dis man into power even his manfesto wz very poor compared 2 others MALAWI WIL NEVER PROSPER

 20. Ife a mpandadzina palibe vhomwe chingamveke olo titalankhula tiri mbulanda.
  Osankgawo asankha mogwirizana ndi m’mene iwo amadyera koma dziwani kuti mpira wa miyendo umene mumati feetball sudzapita patsogolo muno m’Nyasaland.
  Kaya zawo izo.

 21. Ife a mpandadzina palibe vhomwe chingamveke olo titalankhula tiri mbulanda.
  Osankgawo asankha mogwirizana ndi m’mene iwo amadyera koma dziwani kuti mpira wa miyendo umene mumati feetball sudzapita patsogolo muno m’Nyasaland.
  Kaya zawo izo.

 22. Kodi Inu Mugobwebweta Chani? National Team 2010 Sinapite Ku Afcon Inali Nthawi Yandani? And Ngati Vuto Ndi Walter Nyamilanduo Bwanji Mumachotsa Ma Coach? Ok Pampandopo Pabwera Mijingao Mukuwona Ngati Sangabe Ndalamazo Palibe Wabwino,kma Choti Mudziwe Walter Adzasia Enkha.Walter Ndilu And Amene Sukufuna Ndinu A Bullets Pamene Munthu Wakupezerani Wokuthandiza Team Yanu Tamusiyani Walter Alamulile 4yrs Ina

 23. Kodi Inu Mugobwebweta Chani? National Team 2010 Sinapite Ku Afcon Inali Nthawi Yandani? And Ngati Vuto Ndi Walter Nyamilanduo Bwanji Mumachotsa Ma Coach? Ok Pampandopo Pabwera Mijingao Mukuwona Ngati Sangabe Ndalamazo Palibe Wabwino,kma Choti Mudziwe Walter Adzasia Enkha.Walter Ndilu And Amene Sukufuna Ndinu A Bullets Pamene Munthu Wakupezerani Wokuthandiza Team Yanu Tamusiyani Walter Alamulile 4yrs Ina

 24. One step forward and two steps backwards, there will be a change but to the negative side, 8yrs running the association but losing every much and yet we have chosen to face the same blow, let’s change otherwise…!!!

 25. Amalawi tichenjele pazithu ngati zimenezi azingotigwilisa ntchito tisamaiwale chonde abale sidzulodzuloli amalawi tapusisidwa ufulu watu ulibe ntchito

 26. If all soccer lovers were given chance to vote, Walter could have been voted out…The electoral system of voting is corrupted no wonder he won

 27. If all soccer lovers were given chance to vote, Walter could have been voted out…The electoral system of voting is corrupted no wonder he won

  1. just same as u can miserably lose if u contest in any muzik competition! why did u give us Yabwanya? mpaka yabwanya?? olo dadada wadoda amene uja? give us real ppo! not folly embeciles from the northern part of mw! pliiiiz

  2. Wabanya and mijiga were the worst Chris Mainje but I believe Walter carried the day because of these affiliates okonda kudya maskono…

   Some reputable guys who could have ousted Walter has failed Malawian soccer by not competiting with him and let those 2 do the election, otherwise if it were like a national wide vote people cud have voted him out kikikiki

 28. sinanga amasakha amadya nawo wosaganizira komwe kukupita mpira ku mw. Zayenda chinyengo kumene koma likubwera tsiku muzanyaluka agalu inu, zitsiru mukatero muzikwatilira mahule ndalama zakubazo. Mphaka inu aids ikudunsani pati wosafa nayo.

 29. sinanga amasakha amadya nawo wosaganizira komwe kukupita mpira ku mw. Zayenda chinyengo kumene koma likubwera tsiku muzanyaluka agalu inu, zitsiru mukatero muzikwatilira mahule ndalama zakubazo. Mphaka inu aids ikudunsani pati wosafa nayo.

 30. Palibe zifukwa zomva maganizo thu apa. Gwira ntchito yanu ife tizingomva zotsatira basi. Anthu anena maganizo awo mbuyomu komano palibe ganizo ilo munaigwiritsapo ntchito, nonse akuba okhaokha.

 31. Dzibani ndinthawi yanu iyi. Flames imatichitisa manyazi ndiponso macompany ndi ambiri omwe angamathandize masewera koma amasowa nzeru zanu kuwapanga convice. Ntchito kuika mmatumba mwanu basi.

 32. Kusankhaso Nyamulando ndi Zamanyi ,zautsiru.Tandiuzani ndi chitukuku chanji cha mpira chimene Walter wapangira malawi ? Zokomera yekha ndi banja lake.Posankha mtsogoleri ndikuti akugwira ntchito yabwino.Nanga Walter wagwira ntchito yanji yotukula mpira ku malawi,National ma zero nthawi zonse,Stupid.

 33. a malawi tiribe tsogoro ra masewelo nyamirandu zoti ndimbava simadziwa ndani pakuti tasankha kuberedwa nyamirandu pitiriza umbava wako

 34. Kunena mosapsatira ngati simukutitapa mkamwa ndichakuti kusankhidwanso kwa anyamilandu sizidanisangalatse chifukwa munthu akakhala pampando amajaira kmanso amakhala kuti wapeza njira zozama zobera ndiye kusankhidwa kwawo kachikena satukura mpira kma kumangoba basi bwanji panthawi yomwe analinso mkulu wa FAM timu yathu ya flames imango gazidwa? ndiye akamati audzatukula mpira kwaine ndati kwaine ndibodza lamkunkhuniza.

 35. he shud regard all teams equall.not bcoz he once played for Noma and it shud have upperhand,no.we r watching.

 36. Guys. wat du u want here?? Walter has been elected by other ppo, and y mukumtukwana as if wazisankha yenka?? he was elected by big ppo who hold degrees than us. we shall never prosper wen we jelasi other ppo. lets unite and together we will develop wat u call it football devlpment. Dont keep on kunyoza coz it wont bring any change bt it will give us bad pics. Simuziwa ma plan a Chauta. iam supporting a comment by someone kt ena aja sanasewerepo mpira kumalawi. Congratulations Walter Nyamilandu. We love u !!!!!

 37. kma malamulo akanasintha kt macoach onse amene mateam alimu s.leage azivota nao osat timagulu tina tot sitikukhuzidwa ndimpila wamiyendo chinyengo bas!!

 38. Or titati ctikumufuna wat can be a change,,tingovomeleza bt don’t expect any change in as far as football z concerned,,#Dzuka_malawi.

 39. walter achoke since him start 2 be a leader mpila unalowa pansi malawi so he shud gv chance kwazake kt ayendesekoso mpila u u said kut anakatenga chileso bt y stl continue kt an2 avote ?? Izi ndizokanika ngat tukanika nazo panozi chilungano muchiziwa bt mukuluphera kwamasula atsogoleri akubao en nw ua asking ife kt maganizo anu ngotani mufuna tinene kt chan amalawi masukani maso khalani ngat muli mu democrancy osamaopa wina ali kutsogolo kwanu kt azilakwisa inu kumangoonerela bas ??

 40. Pempho ku FAM kt akonzenso ndondomeko yakavotedwe # ikuchepa ya ovotawo.Tiwavomereza kma moumirizidwa kmano ankhonza kutolera mitmayathu yoswekay pokwaniritsa zomwe amalonjeza.

 41. zomwezi mpaka 4th term? Osasintha constitutiön bwanji? Akapusa azaona zija waona sepp blatter zomafuna kufera paudindozi. Zaka 12 zinakwana,had it bin alindi cöncrete plans n’ vision atakwanilisa kaleka.

 42. same oid story blah blah blah he is bin there 3terms aiready bt nothin changes kodi kulibe ena angayendese fam mucita kukhala ngati ndi ufumu bwanji?

 43. Palibe cha tsopano chomwe osankhidwayu angachite..Kupatura kukondweretsa amene anamusankha..Apa tavomereza kut mpira wa miyendo uthe,itsale netball, nanga mkuti tiona zina uuuu ndakaika,ma afiliyetsi awononga mpira kumalawi..Bola asatisokonezere ma club athu adzingopanga zaku Fam kwaoko…ga

 44. mpira unatha ku malawi kuno,vuto ndi loti pali anthu ambili oziwika bwino ku nkhani ya masewero ampira bwanji sanatengepo mbali kuti apikisane ndi nyamilandu?pano wawinatso ndiye tinsanve wina akulira kuti pakuti sipakuyenda bwino,zozifuna tokha amalawi zimenezi.

 45. Ngati wawina ndiyekuti samalakwisa ,apitilize pomwe adasiyira.Anakatenga chiletsowo ndikuwona ngati zampira samazitsata coz kulibe khoti limagamula mulandu wampira.Zikanatero bwenzi ref ngoleka ali ku maula,Bwana nyamilandu tikufuna under 12,14,17,20,&23.ngati ku South Afrika&zambia basi mwatitha.or bb itakhala yopanda sponser ilibe ntchito.

  1. Anali wosatilidwa ndi bullets suppoters,Ndipo adatumidwa kukatenga chiletso ndi andale omwe ali mu bb.ndani adawonapo zampira zikulowa mu khoti?Mmesa amafuna atsogolere mpira ndiye malamuro sakuwaziwa atsogolera bwaa??Team Imodziyokha nalawi muno idalowapo ndale ndipo ndiyandale nyasa bb.Ngati ndikunama undiuze chmamacho?

  2. Anali wosatilidwa ndi bullets suppoters,Ndipo adatumidwa kukatenga chiletso ndi andale omwe ali mu bb.ndani adawonapo zampira zikulowa mu khoti?Mmesa amafuna atsogolere mpira ndiye malamuro sakuwaziwa atsogolera bwaa??Team Imodziyokha nalawi muno idalowapo ndale ndipo ndiyandale nyasa bb.Ngati ndikunama undiuze chmamacho?

 46. kwa onse okondamasewero wa akuyenerabe kupitriza kukanganirana kusapota ma team a kunja maka national team bora enafe bb imatimwetsakobe wakhathkhath

 47. Guys Tsanamizanepo Zot Ayi Frames Izwina,sizngatheke Kut Nyamilandu Azpita Ku Stadium Frames Ikakhala Nd Game Naye Ndkulowa Mu Ground Ndkumamenya Mpira Ndcholinga Chot Awine,ndzotheka?

 48. Mpira ku Malawi suzasintha ngati anthu omwe akuyendetsa mpira akhalebe omweo. Chikufunika ndikusintha maudindo!! Anthu omwe zakhala zikuwavuta kuchokera mthawi yomwe anaikidwa pampando mpaka pano, lero akuikidwanso, mkumati zinthu zingasithe??? Zinthuzi zikufunika kumapatsanako mpata kuti ena amene akuoneka nditsogolo lampira komanso tsogolo losintha zinthu apatsidweko mwayi kuti enawo avomereze kuti zawavuta. A Malawi tizakhala otsalira mpaka kalekale chifukwa chamoyo omwe tilinawo ophangira komanso osafuna kuvomereza chomwe chatikanika. Tilinso ndiumoyo ofuna kulemera pachinthu chofuna kuthandiza anthu mdziko muno. Enafe sitingayankhule zambiri chifukwa OVOTA sitikhala ife ayi, nde pachimene chasankhidwa kale sitingachisokoneze kapena kuchiphwasula chifukwa povota sipakhala anthu wamba ngati ife ayi koma ama udindo awo. Nde tingopempha kwainu mmakhala ndimphamvu zovota pachisankho chomwe chidzachitikecho mukuyenera kudzatsata zomwe a Malawi ambiri akufuna komanso osadzatengera zoti ndindani wanu kapena waudindo otani. Chomaliza, chomwe chinalembedwa kuti chidzaululika ndithudi tisakaike chidzatelo ndithu, nde kwaanthu amene ali ndi maudindo mu FAM ambiri akudziwana maline awo nde tikupempheni kuti zinthu zisanafike povuta pomati apolice adzikufufuzani zomwe munatenga ku FAM ngat BLUTTER ku FIFA mkofunika ku siiratu zomwe mukupanga then mkuyamba kusintha zinthu ku bungwe la FAM kenako mpira ku Malawi udzayamba kuyenda bwino. Ilo linali pempho langa kwainu amaudindo ku FAM. Zikomo kwambiri.

 49. Ndine ikhutira ndimomwe zaendera zisakho. Nyamilandu apamba kamba kakusowa anthu omwe amatsata zamasewero omwe sadapikisane nawo pa mpandau. Limbikitsani masewero anyamirandu pomwe mwaupezaso mpandou

 50. an election is a process and not an event…there were many flaws in the process leading up to the actual day of the voting. this, in my opinion, undermines the credibility of the outcome of the elections. it is such a shame for Malawi football. back to Mr. Nyamilandu, after 12 years at the helm of FAM u still not convinced you have given it your best??? you still need another term? and people believe we can get a different outcome if the input is the same??? anyways, kumeneko nde ku nyasaland

 51. Ndiyambe ndikupepetsa kwa onse oikoma Malawi national team pamodzi ndi ma player anthu….zinthu zaipa basi..Timafuna atayendesa anthu Ena bungwe la mupila ya miyendo..tiyeni tilikonde dziko lathuli kuposa Ndalama za mu ma gate ….

 52. Munthuyu Ndikape Angokakamira Zinthu Sakuntha Wawusiru Angozisiya Anzake Ayesepo Chamba Basi Munthu Wopanda Masomphenya Pa Udindo Angoziwa Kukwatitsa Basi Chamba Eti

 53. Let those who voted inform the Malawians why they chose Nyamilandu for de third term,yet flames is always aloosing team.

 54. INE LANGA NDI FUNSO BASI, KODI A MALAWI AZERU KULIBE, WA ZERU NDIYEYO BASI? ABALE!!!!!!!!!! TIDZINGOLIRA MPAKA LITI?

 55. kungot omwe amavotawo nzeru ndiponso amadziwana kwambiri ndi walter…….. dey cnt thnk kut nyamilundu ddnt brng any change in da past three years but akumukakamira…..walter anakana kudzayimira ngat president,why did they force him??? basi chilichonse corruption basi….. a MALAWI sitizatheka abale

 56. awonetsetse kuti ndalama za m’magate zisasiye kubedwa, ground lomwe linatsala ku BT la chichili litsekedwenso, ma team aziti akaluza sponsorship adzitha, Ziphuphu zisathe kwa oyendetsa masewero a mpira wa miyendo ndi Flames ipitilize kuluza monga ima chitila muja. poti ndi nthawi yo kolora.

 57. Ngakhale tinene palibe chingasithe. Takhala tikunena kuti tikufuna Flames idziwina, maudindo asithe ku fam and more. Palibe ngakhale ganizo limozi limagwirisidwa ntchito. Apange kufuna kwawo nthawi idzakwana adzayaluka. Kulira kwathu Mulungu akumva. Dyera too muc, awina atukule mabuzinesi awo ndi ndalama zammagate uku mapuleya akuvutika.

  1. Zithandiza chani olo tinene? atolankhani samanena kut lets do this ,,,, kut mpila wathu usithe, koma chimasitha ndi chani? akufuna kuba kutukula banja la kwao osat mpila ku mw , chikhala saabamo sakadagulila ma affliests

  2. i dont belong to any of the chosen one or those who contested but my opinion is that lets be constractive guys, we will not yield anything in castigating people, the thing is what should be done to emplove our team! as an individual ask yourself what have you contributed to the team? its not a one man job, sometimes its even us people we go to the stadiums kuti tikavenche.

 58. God will surprise you this time around that things will work for the betterment of our FAM. If you know he has been failing pray to God that this time around he should not, and I believe that is the spirit of patriotism we want in our not just kumunena olephera koma osamupemherera kuti asinthe. He may fail to deliver due limited resources at his exposure, come out and provide for him to deliver.Galimoto imaphweka amayendetsa ena but when give chance muzachita zomwezo even worse than him, Let love lead

 59. The problem is that those who took part in the presidential candidate were not familiar with football rules that’s why they have hung themselves. Walter congrats you have won bas

 60. Nyamilandu or ma player wo kuluza luza mpila, sivuto lawo anthuwa koma kobadwila. Ku Malawiko vuto ndi dziko. Ngati zimaba nduna ndi ma president, nyamilandu ndindani payekha. More over nyamilandu himself is not a FAM. What r those people who surounded nyamilandu do? Nothing! And r the ones who pushing this to happen.

 61. Tili ndi vuto lalikulu hvy a MALAWIFE or kumaona ndimaso anthu kuti zinthu sizikusintha ,,sitimatutumuka ndipomwe tikuzionjezeranso.
  Ndiliti flames idapanga mbiri even mu afcon? Ife ndifedi anthu ogona sitizadzukanso mpaka kufera kuturo komko.
  Kumangopitiliza kuvotera zinthu zoti sizikubweretsa zinthu zamakono koma kuononga zidalipo kalezo.
  *Shame*

 62. Nde even f we cn say situmufuna wl t change anytng?avotaso,jst brng achange 2 dic world so cald soccer ma player asamachite kutuwa abale.walfare yama player musithe chönde chonde.tiveko kut player wa malawi wagula mdenge lol.

 63. I was 100% No!! to vote for Walter.but what has happened has confused me alot.I can only take it as God at work.Northeners may be denied a chance to rule this country but surely they seem to be good administrators.So we have ernest and now walter again.These school loving jews of malawi have a very big influence in this country.Lets just accept it.God has seen no need of a change.Hope he is going to correct where he didnt do well.

 64. Kumalawi masewera sadzatukuka. Ndichani chasintha ma term 3 a Yamirandu pankhani za masewera- ndiumbava okhaokha basi. Pempho : amalawi tikapitiliza kuika pa udindo mbava, dzikoli lidzinka lisaukirabe.

 65. Maganizo Athu Ndi Oti Lero Tidyera Nkhuku Ndi Mpunga Za Nyamilanduzo Ndi Zanu Zisandikhudze Ine Ndidzadya Nawo Ndalama Zakezo Ine Kkkkk

 66. KENDO.mumuwuze nyamilanduyo kuti mpando sakakamira chosatila chake ndi…………..and no one happy about zachitikazi something happen to nyamilandu chifukwa dziko ndilosiyirana musiyeni ameneyo wakakamira poison

 67. Ngati wawina nyamilandu zakhala bwino ndiyekuti akuyendetsa boo enawo akagwere uko nyamilandu ntchito yabwino wina afune asafune nyamilandu wawina basi

 68. Kodi ife tinalakwa chani kuti tidzingodandawura tikakhara ndi game ya national team.kodi ife ndi Zambia timasiyana chani? Idzitiposa Tanzania zowoona? Zosezi amapangitsa ndi water nyamilandu coz muwone ndalama zomwe amalandira ma prayer wanthu.nde muwone zomwe amalandira anzathu Ku Zambia,Ku Tanzania.muwona zifukwa zomwe sitichitira bwino.sikuti ndalama tilibe koma zimapita muma nthumba mwa wanthu ena.

  1. pilirani yakhula ngati ndiwe ozindikila, ntchito yakoyo ungagwire bwino ngati malipiro asakunkhutira nawo? iyoso ndi ntchto amwene mwatani kodi.

  2. Pilirani Mphande boma limaumira pampira komaso ma Academy abwera pompano nkana even Ziese coach odziwa ananena kuti olonflames itakochedwa ndi Fergusson singawine ma reasources boma limaumiraBy the way allocation ya fam ndizingati paja mubudget? Blame politicians not Walter umbuli uthe.

 69. Ndikakhala ine ndinasiya kalekale kusapota flames coz of him and kuwina kwa iye kusonyeza kuti ndiwonjezelanso dzaka dzina ndisakusapota timu ya flames

 70. Ife ndiwodandawura coz mpira wathu ukupitilira kulowa pasi.sikudana naye mkuluyu koma zowona zake water palibe wachitapo koma kupititsa pasi masewero a mpira.ma panado akanamwedwa coz Malawi national team zoti idzawina ndikutisangalatsa.tiyiware mpaka zaka 4 zikubwelazo.

 71. Palibe anabela apa, koma kuti ovotawo ndi bambo H20 Nyamiladu ndigulu limodzi lambava. Amaziwa kuti akanangoti anasankha new blood,zambiri zikanaululika. Palibe zotukuka mpira apa

 72. Aaaah! Ine sznandsangalatse, Palibe nzeru kusamkhidwa kwa a Nyamilandu. Masewelo sapta patsogolo. Zimafunika tikanasintha utsogoleri umenewu.

 73. Ndimaganiza kuti ndibwino munthu akakhala pampando nthawi yake ikatha asaimenso kachikena apatse anzake mpata chifukwa amazolowera samva zanzake.

 74. Sepher Blater wakumalawi 4th time?tiyeni tivomereze basi poti udindo ulionse amasankha ndi mulungu.Congrats Mr Nyamilandu!!! mauleeeeeee woyeeeeee

 75. h has bn in the offce for 12years bt palibe chaphndu nda chiona ine wapangapo.afuna atiuze kti z th only guy mmalawi mmuno.the fact z w dnt want hm n akadafuna chilungamo itatengedwa court injunction iwo apanga vacate akadasankha anthu ena 36 to vote . sadawine pachilungamo

  1. Big Walengan Modekha Azanu Mwawacitsa Manyaz Manyaz,coment Kumadekha Nayo Mukamawelenga,cabwino,pot Olila Samamugwira Kamwa,dekhan

 76. Vuto silawo kulowa kwapila pasi koma kusava mwpuleyawo ndi apulezediti ngati satengapo mbali zikufunika ndindalama zokwanila ndi nthawi

 77. vuto ndiloti anthu amene amavotawo ndiamene amadya naye limozi ndalama zaFAM nde it was hard kwaenawo kuti awine.zikanakhala ngati momwe amapangra zisankho zama Mp bwezi sanawineso.Ithink ths should be discussed otherwise,tizingopitilira ndimunthu m’mozi.Nyamilandu sangasinthe zithu anali kuti 11years inayo?pano ndipamene waziwa kuti amalakwisa?”fisi ndifisi olo atasintha tchire sazadya kholowa”thats why atamva zainjuction amanjenjemera.Ine i agree zisankho sizinayende bwinodi and am not happy to see Nyamilandu in FAM presidency office

 78. Maganizo anga siziribwino tinakaona utsogoreri wina paulamuliro wake sindnaone chosintha tikumamenyabe mipira yachikarekare

 79. Dyera basi 12yrs in office apangachani? Kungofuna kuwononga basi, munthu wanji osafuna kuvomereza? Ndikwabwino tidzivota dziko lonse osati ovota ake adzingokhara able ake okhawokhawo. Inunso a media you are the contributing factor sumumabwera ndikunena chilungamo pazomwe zikuchitika pa ground. Mpira amasewera mu office? Watopetsa Nyamirandu wanuyo.

 80. Dere z alot of wayz of toping a siting leader evn prezdents of cantriez hav bin topled Walter adzachoka tsiku ndilimodzi pakhalekhale njira idzapezeka adzachoka akunva kuwawa komanso mochitisa manyazi

 81. Ine being a genuine citizen ov this democratic nation am not happy at all ndipo ndizauchtsiru zimene zachtikaz..,ameneu amasokoneza ma sponsershp kumapanga divate,bt dis tym around timudula machende ameney football siyakwawo ay

  1. Walephera kusintha all these years ndiye asinthe lero? Leadership ikasintha zinthu zimasinthaso musayembekezere kusintha kulikose. Ndalama za mmagate zidakabedwa ma stadium adakatsekedwabe above all flames idakaluzabe

 82. pamenepa zangowonetsara kuti ngati tinali ndi mtima ositha zithu timanyika nsima m’madzi timangofuna kuwonetsetsa kuti iwowaso akamapanga zoputsa adzidziwa kuti paliso anthu ena udindowu amawufuna nde chofunika ndi kungotorerarana basi to have great vision as we are One aways

 83. kodi nchifukwa ninji anthu amakakamila maudindo ampira? sipa district or massa or pa region or ku fifa kumene. noone is best on his own. how do u discredit thoz that hav not bn there? he has bn choosen by thoz who also want to cring to there positions.if courts can stop governments, why not futbal?

 84. Mpira sungapite patsogolo ngati palibe ndalama zokwanira. Tikuyenera kusintha machitidwe athu azinthu but all in all congulaturations mr Walter olirawo asiyeni samugwira pakamwa

 85. Malawi has a very different taste when it comes to football, we declare Malawi ‘NO FOOTBALL ZONE.’ I just feel Walter has nothing new to offer, If we are to reach new heights we better do something new we have never done in the past. Old broom knows all corners of the house hence he knows where and how to corrupt these people to win, unfortunately as usual the the old broom will not sweep the floor clean… Iam afraid we are still half way deep in our own shit and our sense of smeling become used to the filthy hence the Nilibe problem mood is activated,

 86. Chavuta apa ndi history. Walter anafunitsitsa kwambiri kuti anthu azidzanena kuti president wa FAM m’mene Bingu Int. Stadium inkamangidwa ndi kusegulidwa mchaka cha 2016 anali iyeyo, basitu. Now he has two big stories to tell: 1 >took flames to Afcon. 2 >opened Bingu stadium in the capital city.

 87. Fake election same recycled FAM officials, another fours years of the dark ages in fooball development; Walter Nyamiland said if he wins this staged election all Super League games will be pegged at k2,500; Who will pay such an amount? Are we in England? Or is it a new football cashgate bonanza; Who will pay? May be the government paying for suporters: If Fans were failing to pay K500: The same dude who failed our football is back in town- Mayo ine mpira ku Malawi;

 88. Fake election same recycled FAM officials, another fours years of the dark ages in fooball development; Walter Nyamiland said if he wins this staged election all Super League games will be pegged at k2,500; Who will pay such an amount? Are we in England? Or is it a new football cashgate bonanza; Who will pay? May be the government paying for suporters: If Fans were failing to pay K500: The same dude who failed our football is back in town- Mayo ine mpira ku Malawi;

 89. Choyamba ndikuti nonse amene mukunyadila kuti munthu wodzikondayu wawina ndinunso ozikonda ndipo ambili mwainu ndi anoma mukungoyang’ana zabwino zomwe amakubweleselani ku club kwanu basi kodi mpira pamalawi pano upita pasogolo choncho

 90. Nyamilandu ma bodygurds ndiye muyenda nawo zaka 4? muziwalipira ndalama zanu kapena za fam?m’neneri okonda chuma ozikonda yekha opembeza munthu Joshua

 91. Losers in the just ended FAM election,let’s join hands & support the newly elected president for the betterment of our football in Mw,or else go to court as it is ur custom but otherwise Walter has won!

 92. madise ndiye amayendesa chisankhochi? judge chikopa says no to the votes ,nyerenda go ahead ,who was right madise should quit not fit for his post

 93. Kaya Nyamilandu Kaya Ndani I Dont Care,,, Chomwe Ine Ndikudziwa Ambuye Alinane Cholinga, Khalani A President Pansi Pano Munjoyeretu, Mudyeretu Ndalama Za Anthu Avutika Ikudza Tsiku Muzalakalaka Kufa Chifikwa Cha Ululu Koma Imfa Sidzakugwerani

 94. “If I can stand again as President in 2016 I can still win, am not old enough to step down but I would rather do so to paveway for new ideas that can propel USA forward” Obama addressing the AU summit in Addis Ababa a paraphrased quote. But Malawians drum up support for life presidents even if they can spot some shortcomings from them. Indeed this paranoia will not bail us from what we have been crying for decades below the line. Lets develop our mindset.

 95. Izi zidzingobweretsa zipolowe mabwalo ampira koma dot. expect flames to perform .Koma kufa kulipo and judgement day after.

 96. “Malawi Dzuka”
  I Honestly Condemn The Whole Process Of Those Elections, If Walter Was Truly Honest He Could’ve Probably Bear With Those Other Candidates But he Downslide Them Delibaletly So That He Could Cheat As He Did..
  Munthu Wamtaliyu Tatopa Naye..Shupit!!

 97. Anthu akumalawi angondithesa nzeru,amaona kuti zinthu sizikusitha basi kakaka yemweyo,sizinandisangase, ati 12yrs mukulima mungakolore 3yrs? At HARVESTIN TIME mmm tiyenazoni anga ndimaso poti mpira kulibe kumalawi

 98. its still a fallacious to me that he has won hence he was the one having choices of who to take as an affliate for voting, a soccer politically connected, and possibly sicrete affliate funder,hw can ths person fail? fairness in malawi is just a mouthtalk ,kuononga dziko chifukwa cha mpunga weniweniwu thats malawi.

 99. hahahahaha…olo mulire magazi Walter ndi Walter basi….mwayesetsa kumunamizra za illovogate….mmmmmh mwagwa nayo!!!

 100. Amalawi timava nkhwangwa ili mmutu mpira walowa pasi tikufuna utheretu tsopano sitifuna kusitha zinthu Nya wavoteredwa ndi anthu ochepa ofuna nthito ku illovo,musamadabwe kumakwera team yobwera zifukwa zina ndi zimenez

 101. ayabwanya ndi amijiga ndi ana kwa walter.wakulira ku illovo pano ndi bwana komweko,nde mukudziwa wamenya mpira pano ndi FAM presdent.zammagazi zofunika achina jomo osat anthu wamba!

 102. Ndiwe citsiru walter, tinatopa nawe ife ndipo ndiwe munthu olephela machende ako ukuwona ngati fam ndiyakwanu eti? Zimawu ngati bembelezi andi ndiwe citsisu cha munthu umandinyatsa ngati manyi amunthu wa njala kagwele uko

 103. mr president nyamilandu khulurikirani onse amene okutukwanani onse atonkhani yoza mumayakhulidwe mungoti ambuye khulurikilani adani anga onse samaziwa chimene amandiyoza.

 104. why z d@ only walter has nt said whether or not its an illegal? Mmmmmh malawi the flames we’l neva learn indeed! No fair play here Itink!

  1. amainje mwakomenta ngati munthu wanzeru2 koma ayi ndithu chitselekwete chamunthu. The wise men once said; “Only fools Rush in”! Moti wangokomenta usanamvepo kalikonse apa. Sam say A WISE SON BRINGS JOY TO HIS FATHER WHILE AFOOLISH SON BRINGS SHAME TO HIS MOTHER,So z CHRIS aka mutu wamamina MINJE

 105. oyoza onse coyamba mayazi agwere munthu amene ukuyaza amakhala apongozi ako munthu uyo ukumuyoza akhala mtsogoleri wako mako ndi mako ngakhale atyoke mwendo ndimako basi oluza vomerezani kuluza chacikulu moyo2o2o ndi pafupi.

 106. Asafuna akakolope nyanja. Mwalila lila apa misozi iuma sopano walter ndi Dhilu enanu timangokumvelani akazafuna azasiya yekha ndithu

 107. Kodi Mijigo Nd Yabwayabwa kaya mukut ndni mayinawo, anasewera kut mpira wake, Walter wasewera wandrers, tikudziwa tonse. Talowapo mu word cup qualifierz, Africa cup tachitapo bwino under Walter emweyu, waipa chan? next term adzaimaso, wina afune kaya asafune. Nyerere woye !!!! Oooooodi ukooooo Walter aduse

 108. kodi man amenewa alibe zina zochita…?? ine ndie andikwana n’nsaname, chitengeleni mpando palibe cha nzelu Flames inapanga… i think ali ndi Minyama

 109. Thats y malawi amasalidwa izi always khalamba ku paliament enaso awa ku fam ko ndiufumu kapnaso uyu ndikamuzu wamuyaya patsaniko anzanu dyera ayi

 110. palibe amasiya ekha mpando onona pa malawi, tieni tione kuti zitifikitsa pati. we could v tried new blood. poti zili choncho tie nazoni.

  1. Tayamba iweyo ukatopa utiuza,zachamba eti malo moti uzikapanga zokapanga chitukuko chako uko basi wagundika pa nsewu

  2. Kkkkkk eee tayiwala tikumbutse iweyo? Chitsiru ukamati kuyenda pamsewu ndiye chani? Misala chani? Iwe mutu wako ugwira? Dennis phiri tachiuza ichi kkkkkk

 111. Mpira suzapita pasogolo mdziko lathu lino kumangomukakamira munthu wadyera ngati ameneyu zaka zonsezi walephera kutukula masewera ampira wa m’miyendo lero mukumuvoteranso. Kodi mukutiona ngati ife anthu oputsa nonse amene mwavota mupanda nzerunu muzafa imfa yowawa.

 112. Walter Win Jst Bcz Ov Poor Votng Not Bcz Ov Good Leadership Y Y Y Malawi Alwayz Forcing Thngz Yet Dey Hve Failed Already & Thats Y Malawi Wil B Poor In Everything. Zuka Malawi Iwe Zuka Lija Ndikale Unayamba Kugona.

 113. CONGRATS Walter,mulungu akalemba walemba,ku Court zomwezi! LONG LIVE FREEDOM OF SPEECH, LONG LIVE MALAWI’S YOUNG DEMOCRACY….kkkk…eeee…koma yah….mpaka kupeza ma distinction zomwezi…kkkk

  1. catholic university ukuphunzilako kaphikidwe ka mbwanda eti? olo mpikisanowo unaliponso apa? yabwanya? nde zichani? ma vote 2? winayo waononga ma million za ziiii ma vote 7 ? pusa!! Walter ndi number one!! haters go to hell

 114. At times things happening in Malawi sound CRAZY ,someone will like to know 4 th.term for the benefit of WHOM ?.is it for the benefit of football in Malawi ?.

  1. paul mbolo yoondayo, dumb embecile motherfucker!! keep crying folly bitch! if u cant fight us, join us, wipe ur stinking asshole

 115. If Walter is a real leader and a good fan of soccer…he would not have contested these elections. We gave him much time to transform soccer in Malawi but to our dismay he has failed. But if the peaple have put him into the driving seat again…then let it be…..but with the new government that is coming..we hope for the best from FA…without any interference. Good luck Walter Nyamilandu..

 116. #higgamkandawire #lifulitete #kimkamau #luciousbanda #tithamandiza #georgekapachika ndi ena omwe ndakuiwalani manyazi akupoleni mwagwa nayo mahater #walter adzachita kusiya yekha tiachina yabwanya tanuto mutiuze tikayambirenso1

  1. kikkkkkkkk thanx chicco eeh anthu awawa asse eishhh amachita kukhala ngati kuti walter anaadyerapo chinachake achita manyazi heavy

  2. vuto lake amaona ngati kukhala ndi mau aakulu ndikumanya zingini nevaaa walter ndidzamugwetsa ndekha kikkkkkkkk mafana adakali panowa saangamuthe nanga president akakhale yabwanya? Kikkkkkkkk

  3. #fundo n #ncruzado yabwanya amakanika kulongosola manifesto yake yomwe kumangodziluma poyankhula olo nkanakhala ineyo affiliate sindikanavotera matapwasi ngati amenewo

  4. #chiko amaona ngati anthu nde anjenjemele chifukwa wina ndiwaku canada? Za zii walter adzachoka yekha akadzafuna osati nditiachina mijiga tanuto

 117. Mpaka liti Malawi? Lets learn to change 4 the better and welfare of ur players@aaaaa inu mwayiwala pompano Daglas Chirambo ankasowa thandizo ngati Fam kulibe? Nanga Navigeter Mzikambani uja? Akuluwa azaphunzila liti kutumikira bwino pomwe amapezera mchere

  1. nanga finye iwe siunawathandize bwanji? iwe uziganiza zokhoza msce usanafike nku secondary komwe? ukafunse club yao big bullets not FAM

 118. apange concentrate ntchito yake Ku illovo mizimbe ikubedwa kwambiri Ku nchalo he should tighten security

  1. Pakati pa iwe ndi ine walemba zopusa ndani? Ine ndanena kuti ndi security guard? Idiot read before u comment

  2. TD, ndiiwe mbuli, ukunyoza utsogoleri lero? unyoza mpaka 4 yrs? nde za umbulizo! inu munakhulupilira yabwanya?? kkkkkk!!! funny!! its football affairs! not za ku chikangawa ukko kukaya ayi! ndi dadada yemwe anadodapo amene aja? za finye basi … haters always come last, they always lose… and that applies to u mr big tummy, remember to mentain 6 packs, osati chibukhu , mang’ ina mmimba thooo!! u r sllow…

  1. The officials of the affliates like southern region football league, referees’ association, netball, basketball, northern and central leagues etc are those that vote.

Comments are closed.