Health NGO stands firm against Bullets multi-million sponsorship

Advertisement
Nyasa Manufacturers and FAM officials with Bullets signing the deal

Drug Fight Malawi, a local Non-Governmental Organisation (NGO), has petitioned the Football Association of Malawi (FAM) to stop Nyasa Manufacturing Company from sponsoring Malawi’s football heavy weights Big Bullets.

Nyasa Manufacturers and FAM officials with Bullets signing the deal
K0.5 billion Bullets sponsorship under fire. (FILE)

Speaking during a press briefing in Lilongwe, Chief Executive Officer (CEO) for the NGO, Nelson Zakeyu, said the deal is likely to engage more youths in smoking habit.

“We are humbly requesting FAM to seek greener pastures for our local teams somewhere else but not with Nyasa Manufacturing Company.”

“Their agreement with Big Bullets will likely increase smoking habit in our youths so we don’t want that to happen. We are asking Bullets to terminate this contract,” said Zakeyu.

But in their response, Bullets through their vice general secretary Kelvin Moyo said their agreement with Nyasa will continue.

“We have been in the wilderness for the past 11 years so we won’t allow anybody to jeopardize this deal. We consulted FIFA through FAM and we were given a go ahead to sign the deal so we are not bowing out,” he said.

Bullets landed a five year deal worth K0.5 billion (K100 million per year) with the tobacco manufacturer.

The two parties will officially launch the partnership next week.

Advertisement

114 Comments

 1. Proudly Lubani fan..koma naa apapa apa tiwonepo bwino. Kodi wina nkuyamba kukoka fodyayo kamba ka Nyasayu ngati? Che Zakeyu mwatani kodi? Zimenezo ndisamvenso, Nyasa, tasainani kontalayo musamvere wafodya wamfupiyu

 2. Ine siwa Bullets kma iyi yokha nde mukunama nayo inu ama NGO isiyeni timu inyambiteko ndalamazo apo bii pelekani ndinu sponsorship yo #NDAKWIYA_NANU

 3. The NGOs are using wrong arguments. NGOs must tell government to ban the tobacco firms or even farming of tobacco.
  In this case, NGOs have nothing to say FIFA already approved this contract

 4. anayamba za anti Tiwo.. kenako anaphetsa anthu ku nzuzu.. kenako anatiphera chitsulo cha njanji.. pano ali ku bullets.. akulora ulimi wafodya ndi kusuta koma kuthandiza anthu ayi… ma NGO akufunika kufufuzidwa

 5. kusamala mano sikusuka ndi nswachi kokha amwene,,BECAREFUL!!

 6. Ma NGO a ku Malawi kufuna kutchuka ndi zopanda nzeru ngati zimenezi. Kodi fodya akusutidwayu timasutira kumpira? Pofunikanso amene akupikitsana pa zisankho za FAM ayankhulepo kuti tidziwe chidwi chawo pa nkhaniyi

 7. nde azitipanga sponsor iwowo a health ngos…..sizotikhomelera apa…..kod a carsberg amapanga bwanj sponsor cup….dont ey promote beer? isnt beer hazardous to our health? osamangoona zinthuzi mbali imodzi…en f in any case akanangonugula ndia boma kut abhane fodya wina aliyense ogulitsa kusiyana ndkuletsa sponsorshp koma fodya adzigulitsudwabe…….viva ma pale

 8. Thats nonsense at all , u already know that flames is sponsored by carlsberg , so why not taking action on that ? If u r only against Bullets , watch out plz !

 9. Zandiwawa kwambiri, komabe mudziwe kuti nyasa malamulo amenewa amawadziwa.koma iwo amafuna kupanga malonda ndipo zawayenderadi anthu agula fodya mwakathithi . Komatu iwo sangapereke 100,million pa chaka ku timu !!!!! Alibe ndalama!!!!!!!! Ndiye tiganize mozama muona kuti nyasa ndiye tambwaliiii!!!!! Chifukwa amadziwa koma bussnes, thank you the stupid Nyasa for the business lie you brought to our financialy struggling team,

 10. Bullets walakwa chiyani? Munthawi ya Muluzi anaikonda team yi nkumayithandiza. Koma zonena zinali zambirimbirinso. Chabwino Muluzi anasiyakuthandiza team. Kuchoka apo Bullets yakhala ikuzunzika kamba kosowa ndalama kwazaka zambiri, lero yachitanso mwayi anthu ake nomwenu munkalankhula zopusa pano ndinu amene mukuyetsa kopondereza team. Ngati chauta wapereka mwayi ku Bullets, simungasinthe chomwe wapereka.

 11. neba ndiwausilu hvy, wapanga dala kudutsira kwa zakeyu wakeyo, sakudziwa kut angomuphetsa amenuyu.

 12. Zakeyo tamufufuza amakhala ku Lilongwe ku falls ndipo tithana naye

 13. Azakeyu, mwatumidwa or… Embassy Trophy,Chibukhu, BAT 555, Limbe leaf Wanda laziii, Castle, Heniekken,Khazibek.. Lero inu mwadzuka chipwenene mpaka kukhutu, manthongo phwii mmaso, mwasankha kuyamba “Jealous” dzina lodyela.. “NGO” . mutasowa poyambira koma mwati Bullets? Anthu onse akulima ndi kusuta fodya m’dziko munowa akutero chifukwa Nyasa ikuchita sponsor Bullets? Mwa mavuto onse dziko la pansi likukumana nawo inu manthu wake ndi Nyasa pochita sponsor Bullets basi? Azakeyu chonde musatichimwitsepo apa, ife a banja la Bullets tikukukanani!

 14. ndizona kuti aFifa analetsadi koma ndiye funso mkumati nanga bwanji companyyi yakhala ikuthandiza team ya Nyasa ndiye lero ndikumati ayi chifukwa choti Big Bullets? komanso sibwino kumati ndi a Wandereres ndiamene akuchititsa. chilichonse WANDERERES tiyeni titukule mpira chonde BB tiyeni muzikura

 15. Amabungwe inu!!!! musamaime pamtunda mkumat mukuchita chilungamo pofunira zabwino umoyo wa anthu,bwanji osakhala buzy kumapanga kafukufuku wa mankhwala a TB??? Ngat mukuona ngat akunyemerani K500M ndye mwalemba mu water..

 16. Nsanje inayi ndiyopha mwana wako yemwe team yakhala ikuvutika simumathandiza mumasangalala. lero ena aitola zonena zambili .amene zikumunyasa aziphe kapena asamuke kuMalawi.Osuta ndi osuta basi munthu sangayambe kusuta chifukwa chokonda team

 17. Zakeyu or whatever you call yourself and your sponsors for your foolish NGO
  do not think that Malawians are stupid?How can you terminate a lucrative sponsorship to a team which is already doing well locally on an unfounded grounds of tobacco? Are you so daft to know that Malawi economny is still dependent on tobacco? To hell with your foolish sponsors ngati akupatsa dollar ukabweze pompano.

 18. Nonsense kusowa chochita mkumafuna kukhomelera team yomwe ife timaikonda ……mbolezanu nonse amene mukumazicha ma NGOs…fuken people. ..mbuzi za wanthu inu ndindani dziko la Malawi ndinu ngati mwasowa chochita osayamba uvender bwanji mkumagulisa mabilinganya

 19. Ngati Akufuna Zimenezo Ayambe Aletsa Company Yofula Mowa Kuchita Sponsor Masewero Ampila Chifukwa Anthu Akumwa Akumalezera Ena Kumachititsa Ngozi Mmisewu Koma Sakukambapo Kanthu Nanga Bullets Yakulakwirani Chiyani?

 20. Where is its hqs? Who registered this NGO.?? Who is it representing.??Who is funding this rubbish NGO?? Who is its board chair???? Pple r now busy planning to plant the same tobacco why cant it go in the fields and stop the plantation

 21. Zakeyu kufuna kutchuka baxi koma wachosha wolakwika

 22. Alcohol is dangerous to one`s health….nde ngati akufuna zoti sponsorship ichoke,ayambe Heneiken away from sponsoring Champions League….and why do Carlsberg make alot of noise ndi Liverpool pano as their secondary sponsors…

 23. pasavute stop nyansa and take bullets other wise mukangopanga zachamba mutimva kuwawa Mauleeee!!!!……..woyee

 24. Mbuli za xull. Ngat ukufuna kut ana asamasute ulese malawi yense kut asamalime fodya tione ngat ka udindo kakoko sakapeleka kwa wina mawa. Sungalekese ndowa kuchucha madzi potungilamo ena mbuli iwe! Timaimata . Ndiyen mawa uliuze boma kut liuze anthu ake aleke kulima fodya. Enanu mumasangalala kutukwanidwa i think.

 25. Kodi makamaka Bullets inakulakwirani chani agalu inu? Mwati mupezere podya ndalama nkabungwe kanuko eti?

 26. Kusadziwa ndikufa komwe palibe cholakwika apa . Kamupani yopanga dundu boma linabvomereza chifukwa chakusowa ogula fodya wa alimi . Bata Bullets yabvutika nthawi yayitali . Kuletsa kuthandidza Timu sikungapange anthu kusiya kutsuta. A Malawi kumudziko chenjerani ndi Mabungwe ena. Akubweza ndalama zaotsuta . Apatse inu mudye nokha ?

 27. Malawi sidzatheke jelasi Wanderers inali Limbe Leaf wa Danzi akuchita Sponsor a Limbe Leaf opanga fodya anthu sankanena izi

 28. Tim ya bibi ili ndi tsoka. Ikufunika mapemphero. Kutukwana ndi kunyoza mabungwewa sikungathandize ayi. Kumbukirani paja mudanyoza bakili muluzi zinthu sizimakuyenderani

 29. They must oppose Carlsberg sponsorship and hence cancel the cup before ordering the reverse of the nyasa sponsorship. Amalawi, what’s wrong with this brilliant deal.

 30. iwe ngati umatamba ndibwino uzikapangira achibale ako okhaokha kumuzi kwanu ife zopusa zakozo tisaveso ngati akutuma akupwetekesa ase samala ukapanda kuzitenga bwino upeza nazo mavuto

 31. Boma lilipakalikilik kuphunzi alimi kasamalidwe ka fodya why can’t stand agaist the government kuti lisiye kulima fodya? plz i beg of u don’t ensult mapale anasintha osayambitsa ziwawa mziko muno azakeyo pangani zanu leave nyasa and bb alone chonde.

 32. wy not stoping farmers to grow tobacco and stops the goverment to support the growing of tobacco?wy AUCTION HOLDING is runin every? TCC,TAMA etc wy not stopn them ndeno mwasowa chochita uko mwat mulimbane ndi banja lamapalestina.tiyen nazon ife nde tinamva kale kuwawa2

 33. Ndidzitsilu pano mabungwewo amati chiwelewele ndichoipa kupezekanso kuti akumagawa makondom kodi pamenepa amalimbikitsa chigololo kapena amafuna kulesa chigololo?

 34. Am not a BB fun but this is stupidity at its best,where were you when bullets had no sponsor,if u promise to sponsor them its fine,NYASA TOBACCO your welcom.

 35. Kodi zikhuzana bwanji mpira ndi fodya kodi Chamba chikusutidwachi amapanga nda Nyasa nanga ma Drug tikumenyawa amapanga ndi a Nyasa omwewo ngati winawe zakupweteka ku bwera kwa Nyasa ku Bullets ukanango nena osati zomwe mukunenazo Chikhala ndalama zogulira nduduzo zimachoka mthumba mwatu or tinene kuti. kusayenda ndiye kukupangitsani koma ngati sizitheka chomwe mudziwe choti nonse mukulimbana ndi Nyasa siinu amalawi n usamukenso ku malawiko kupusa wina apita ali chiimire

 36. Ngati NGO ilindi fund ipereke 500M ku Bullets. Mwana ukamamulanda chinthu umapatsa china aziseweretsa. Anthu sitingayambe kusuta cauz our team is getn funds 4rm Tobacco company!!!!!

 37. bungwe limeneli ndilitinso kod? athu amamwa ndiikusutawa akupangapo chan tavutka 11years ndye akut chan ngat mukufuna kutchuka muvulalatu pangan zanu

 38. Why all this time Zakeyu, do u know how much pollution is caused by vehicles? if it is another what wud u say? fotsek.

 39. Ine ndi wa nyerere kma ndkambe nawo zimenez:choyambirila kwa NGO imeneyö ndngot machende anu,mukufuna kutchuka chyan?wakutuman ndan?A carlsberg nawo mesa nd ma sponsor a flames + al nd cup yao?mukufuna kunena kt chyan kwenkwen?Mboli zanu kwa masiku atatu mwamva!Bullets family osaerekez mkomwe kulola matoga amenewa.

 40. ine a Malawi mmandivesa chisoni kwambiri mu2 akamavutika inu ndiye yaaa kusangalala lero bullets yapeza owagulira soup mwayamba milandu. mwaziwa lero kuti fodya ndiwoipa coz akufuna kumathandiza team? ndichifukwa chiani simmalesa carsbeç cup mowawo ndiye wabwino? mwandikwiisa kooopsa a2 oipa inu. tinene kuti inu amene mukulesa izi simusuta fodyayo? bwanji osasiya kusuta kenako muziti asathandize team?

 41. Carlsberg sponsors the flames, BAT sponsored some cups, Castle Lager sponsors COSAFA, Wonga (a gambling Company) sponsors Newcastle, Heineken sponsors UEFA Champions, Limbe Leaf Tobacco Company Sponsored Wanderers. BAT recently run Pallmall National Pool tournament in Malawi. In all these sponsorships, I have never heard that the youth are indulging into immoral behavior because of a particular sponsorship. Now what are you talking about? Usawi chi?? Mukamva ufiti ndi umenewo.

 42. Chamba akuvomeleza a boma chi!!! Ma farm onse amalima fodyawa? kodi akutumani kapenatu? koma ndiye mulimbe nazotu? ndalama za bungwe mukusowa nazo kopita kapena? anuamata akusutawa ndudu amagulisa ndi BB mbuyo? muuzane kuti Ukuti apitilizabe!!!! Kusuta anthu sazasiya its a habit. Kufuna ndalama zochuluka kumeneko achinyama kumwalira ndi mowawa bwanji flames ikuthandizidwa ndi company yopanga mowa? mesa nako kuli anyamata. Fodya fodya chani?

 43. Debatable issue. Komatu ku BB ambili amasuta ndiye sakuonapo vuto koma umphawi wathuwu utionongera dziko. Ukasowa banja kwa nthawi umangotenga ngakhale okutha mano nkamwa,wachamba,wamowa, okuba komanso umatha kulowesa mbava mmudzi. Kkkkkkkkkkkk nebayoooooooooo .pafupi ndi pompokkkkk

 44. Palibe nkhani apa a FIFA anavomereza enawa azingofwenthera polira ndi nsanje komanso kufuna kutchuka koma sizisintha kanthu bullets pano ndi ma level ena Mulungu akati ee palibe angati ayi viva bb mumva kuwawa zenizi

 45. Carsburg Cup , Mighty Limbe leaf . Pamene ankapanga sponsor a limbe leaf Munali kuti ? Kodi Carsburg munayiuza kuti isiye kupanga sponsor chikho chawo ?

 46. Heineken is a beer, alcoholic but are the sponsors of BPL, Let the cigarette company to support in football, the Drug fights are stupid people, there stupidity is on: why allowing cigarette company to come in Malawi, is the CEO of the company say that when they sign with BB they will give free Tobacco to supporters????? Let BB be BB.

 47. If this NGO can sponsor the team with equivalent of the same ,then who are we to say no but what l know Malawi is a Country of full of jelous people

 48. Do’nt try to stop this nyasa to help bullets where were you all these 11years.

 49. A useless healthy NGO they want that money diverted to them the deal has been already sealed too late for tears try other things eepa porah!

 50. ZAKEYU, Ngati ukufuna kufa Chidule pitiliza zimene ukupangazi, tikukudziwa kumene umakhalatu. Uvutitsa banja lako ndithu

 51. bullets yakhala zaka zingati yopanda sponsor ikuvutika.now yapeza sponsor mukuti chani ana anjoka inu eti.bwanji inuyo mumaleka kuyithandiza nthawi yonseyi.pano sponsor yapezeka mukuti mfweeeemfweeee.chikho cha embasy chija mumkaleka kuchithesaso bwanji.

 52. Where were these Vampires and beasts During embassy trophy era???? Nanga carsberg cup samailetsa???? Leave our neighbour alone #nyerereYOPANDAjelasi

 53. Ma N G O Nthawi Yonsei Munali Kut Kod Simudziwa Kut Kumalawi Anthu Amasuta Fodya? Mwasowa Zochita Et Munyamuka2 M N G O Akuba Inu!

 54. Thats aproblem of malawian jelasi 2much chifkwa zikoli lili lotsalira; mukganiza mukatero athu asiya kusutako wayambitsayo go 2hell ziko laonongeka kale ili ngat mwana wa 16yrs akgona ndikhalamba

 55. Wapeza potchukira galu iwe. usakuletsa malonda Ku Kanengo ndiku Limbe leaf? Noma ikupweteketsa.

  1. Ukuwona ndiwe kuti palibe cholakwika sinanga thandizolo limabwera kwa iweyo koma pa malamulo a mpira ndizoletsedwa kuti no any tobacco companies sponsering football in the world.

Comments are closed.