Act in two weeks or we will meet in the streets – students warn Mutharika


Malawi public protests

Malawi University students that stormed Parliament today have threatened that they will take to the streets after two weeks if government does not adhere to their demands.

Malawi public protests
Students to Mutharika: “We will meet in the streets!”

In a dramatic presentation of their complaints to Parliament, the students challenged that there is a need for the current allocation to the National Council for Higher Education (NCHE) to be doubled so that the students can access loans for their education.

The students are demanding that government increases the loan allocation from K1.5 billion to K3 billion arguing that the current allocation is too little to cater for the student population.

“We have information that out of 3,000 students from the Polytechnic who applied for the loan, only 96 students have been given the loan,” said a student from the Polytechnic Davies Jiva after submitting the petition.

The students have challenged that if their demands are not adhered to then they will take to the streets and stir trouble.

Recently, students protested in South Africa in the popularised Fees must fall campaign that was big and had an impact.

324 thoughts on “Act in two weeks or we will meet in the streets – students warn Mutharika

 1. Education is said to be a human right not as it is seen today as aprevillage ,and in my vie to commercialise it will promote socialism ,,i thank you

 2. Makape inu,u think becoz u r in university then u can rule the world?inu mungalephele kulipira Dora imeneyo?how much were u paying Ku secondary school….think again and see the real Malawi……mwagwa nayo?osapita mawa bwanji Ku streetko?mpaka two weeks??makape

 3. Government has gone into the hands of dogs. Give loans to the students.

  Dunderheads are complaining as if these monies are bursaries or grants, be reminded that these are loans. They will be repaid with interest.

  The government should just learn from other countries how they employ the strategy for practical recovery.

  Those who argue against, their thinking are like a chicken whose head has just been suddenly cut off and run brainless.

 4. Boma likulipilireni fees,lokhanso ngongole likupatseni kenako mukamaliza school mkumathawira mayiko akunja Ngongole osabwezanso kufuna kusaukitsa dziko eti.Ine kukhala president sindingakupaseni ndalamazo asakufuna adzimange makape inu

 5. First it was school feez now this….lets hope akumvetsetsan but if they choose the latter am afraid they gonna send you home…again.. Coz you gotta know when to hold em..n when to throw em when you are a gambler…clearly you dont….its just my opionion no hard feeling…i get your point koma…..but if you think education is expensive try ignorance…that same govt you are pushing has trained medical personels for three years others four years after qualifying they said they can not employ them….imagine …nde mukuti chani pray the plan doesnt backfire

 6. iweyo ndi amene uli abroad,uli pansi pa nyanja ndi umbuli wakowo ndipo udzafa nawo umbuliwo,mpaka pano u dont know de relationship between the leader and the govt? go back 2 sch

 7. Ndalama zimene mukufuna kuti boma lizikupasani ngati ngongole ndi misonkho ya ife mbuli amene tidasiira sukulu std3. Mzipatala mulibe mankhwala, bursary yaku Secondary kulibe. ndiye kuti ofunika ndinu aku University basi. Ife osaphunzira tikupanga komenti chifukwa ndalama mufunazo sizakwanu nza a Malawi amene ochuluka tidasiira std 3. Pitani kunseuko. Koma kumbukirani ROBERT CHASOWA

 8. Ndalama zimene mukufuna kuti boma lizikupasani ngati ngongole ndi misonkho ya ife mbuli amene tidasiira sukulu std3. Mzipatala mulibe mankhwala, bursary yaku Secondary kulibe. ndiye kuti ofunika ndinu aku University basi. Ife osaphunzira tikupanga komenti chifukwa ndalama mufunazo sizakwanu nza a Malawi amene ochuluka tidasiira std 3. Pitani kunseuko. Koma kumbukirani ROBERT CHASOWA

 9. some pple are devoid of intelligence thats why their comments r dirty,if the whole village can go 4 UNGA and parliament buying expensive cars,why then failing 2 provide enough loans 4 de stdnts? mphaka atha kukhalanso wanzeru kuposa anthu enawa,masavage,who just comment 4 the sake of commenting. foolish!

 10. mwakhuta bibida uko ndikumakomenta zinyasi apa….mbuli zachabechabe, chifukwa choti inu mulibe mwai wopita ku university nde mudzitipangira phokoso? muonanso kuti two weeks ikatha mavuto athu asanathane nawo tikumana mtaunimu….malawi ndi wathu, we deserve better for our hardwork

 11. Ameneyo ndyefodyayo mwanawasukulu akapatsidwe ngongole azabwenza liti??kamunthukalibe olondinkhukuimene komaatikafuna ngongole kkkkkkkkkkkkkk upite kuFINCA akakupatsawamva ndikuphunzrakwakoko

 12. Ameneyo ndyefodyayo mwanawasukulu akapatsidwe ngongole azabwenza liti??kamunthukalibe olondinkhukuimene komaatikafuna ngongole kkkkkkkkkkkkkk upite kuFINCA akakupatsawamva ndikuphunzrakwakoko

 13. Ana aschool munali kale pano mmangotokota pakamwa tikufuna strike yeni yeni ife the way amapangira munthawi ya muluzi aaaaa zoona maloan kupatsa 90 students only sankho bwaaaa inu ndinu future la malawi kkkkk

 14. These are d suspect in chelsea’s recent downfall case 1 The sacked doctor. 2 Peter Cech 3 Ronaldo (Since Mourinho compared Hazard 2 him, there have been problems) 4 Harrysong: The guy who sang, “After d reggae play d blues”. (Since d song was released, Chelsea hasn’t won a match) 5 Arsene Wenger (Since Mourinho called him specialist in failure, failure has been following Chelsea) 6 Falcao. (Everybody knows why dis guy is a suspect). 7 Drogba (Whenever he comes, Chelsea will win, he leaves & they drop. People says he has ‘juju’) Which one of dis guys do u 2 think is causing recent loss of matches by Chelsea?

 15. Hey, this thing about taking to the streets, I don’t like itooo. As an ordinary man, why should I be disturbed and delayed from reaching my destination for something I know nothing about??It’s not fair oh…

 16. ndiye mukapita ku mseuko ndiye nkumene kukapezeke ndalama.osangokambilana bwanji?pitani utsi ulipo okwanira oti udzakukwanirani.

  1. Et et asamapange ngat ndiosaphuzra akanayeneka kukhalrana pans ndkukambrana bas

 17. Vuto nlakuti atsogoleri athuwa adaphunzira ulere ena pangongole nthawi ya kamuzu ndiye lero apondereze ife? Ndalamazotu sizawo koma zadziko la mw. Kodi ng’ombe yoonda amaikama mkaka?

 18. Sukulu zangongolezi nde muzitha zaka zambiri mbiri mbiri mukadali ma student.sukulu iziwawa izitopesa.zatelemu zayamba coz pomaliza ma disagreements amenewa ndi nthawi and muyembekezere izi chaka ndi chaka.Iam sorry

 19. “We have information that out of 3,000 students from the Polytechnic who applied for the loan, only 96 students have been given the loan,” Is this true???? Statistics from Poly show that 730 students have been given the loan……

 20. Ana asukulu musatikwane kodi munsewumo ndi komwe kukutayidwa ndalamazo amene akukukanizani ndalamawo komwe amakhala simukukuziwa musatisowese ntendele pitani kusanjika, capital hill, or kuparliament mukazipeza ndalama kumeneko koma nsewu sukuziwa zoti mukumanidwa ndalama act lyk educated ppo

 21. kodi ndiinu apa poly ?aaa palibe xoolyi chomwe ikutithandiza amalawife,mukamaliza mumapangachani munno palibe,mumaphunzitsidwa za injiniya koma ndinomwenunso mukulephera kutithandiza kumavuto azaluso ku Malawi kuno,magetsi akuvuta vuta inu akupoly osati tsoolera ku inoveshoni ya another source of power , musapite pa nseu muzipita kwanu kkkkkkk just joking

 22. The Govt has lost billions of kwachas for the same loan issues so i wonder about all these noises… Why we malawians we don’t want to learn from mistakes??? They say education is a very expensive commodity that a poor country like malawi can not afford… Pliz let us sove this problem in a profesional manner… Demos will not bring money in our pockets… Tit 4 tat for parents chonde ana tisabeleke ngati agalu coz zotsatila zake ndizimenezi

 23. iiiiiiih koma ana inu ndiopusa bwanj!! mumasangalala ndikukhala pakhomo et!? mwaiwala kale pompano kuti in Bingu’s era kuti Chanco itsekedwe nthawi yayitali minister of education anali ndani? nde pano he is president, mukuganiza zikukomelani?? #kapena #mukumapangila #dala? tangopangani za xool mumalizepo mupezeko katsamba apa

 24. A Million ,ngati Mukuganiza Kuti Mudaphunzira Nokha Mumadzinamiza.After all What Is Needed Is Money.Zikutheka Bwanji Munthu Wa Std 3 ukunenayo kukhala billionaire?can i give u examples ?Ophunzirayo Nkukhala Wamasauzande Ochepanso.Please Make Sure That U R Not Provokative.

 25. zoona Grecian,mbuli Zachabe nkumakomenta,eish!,let the intellectuals comment coz r the ones hav drunk a lot of ink

 26. Mukabera za South Africa tvulala coz our country iz poor. our president iz tryin 2 put every thing az pvt so dat we can divorce donarz.we need 2 take an example of China&Russia they suffered 4 5–10 yearz in the end they were rich lets just gv our gvt sum tym so dat we c @ the end wat their planz r

 27. Ndimmene Malawi iliri panopo nzovuta kunthandiza aliyense pasukuluyi, koma bom likuyenela kukweza chiwelengelo cha owathandiza pafupifupi ndi theka. Ambiri sangakwanitse kulipila paokha kungokuona patulako ochepa chabe ndiwomwe angakwanitse

 28. By the time Zuma said “YES” to the demand of stue, the SA currency falls. And Rand is no longer valued like before. As a result, parents will suffer to manage the needs of family.

 29. Inu musatinyase mwamva kuphunzira ndkwanu bt let mi mind muzafa muli amphawi ngat kumalawi kuli ntchito. Mupite ku state house nt musewu, tizachedwe kupita ku business athu chifukwa cha inu?

 30. Ndangomvetsedwa kut UNIMA pano ili ngati PRIVATE COLLEGE aash,,,even ka bungwe kawo akuti kakupereka ma loan kaja kaya kalikuti mmm my Malawi,

 31. They think Mutharika is their father,let them do what is right in their eyes but if its not right,they will die for their shit.

 32. Romeo I believe u dot know wat you are tokn about…! wat u expend at a university within a year may b close to a million. … den de govt came up wid a plan to end govt sponsorship hence de implementation of loans but is only a few dat have been picked…..nde where are dey going to get money from since the loan issue was de only soln to dem….go on guys with dat issue abt demos may there wil b a change

 33. Its sad kuti in malawi we wear educated faces pamene tili mbuli,the big university in africa,stellenbosch in capetown,they are also doing their demo,koma them they want free studies,south africa ndi dziko lomwe anthu ali ndi ufulu oliwuza boma zomwe akufuna and it can happen,in malawi we are still poor,goverment cant afford us,pliz we are the ones we making kuti dziko lizisaukilabe,imagine aliyese pa poly loan nanga azanthu akumudzi,zipatala ndi zina zambili apanga chani,thick of azibale omwe ali ku mudzi.

  1. Iwe ulibe nzeru ana a school ayenera kupasidwa zofunikila morw especially a ku college, mumakondwa president azitenga anthu more than 200 ku foreifn trip ndikumaononga ndalama zambiri koma ana a school akuvitika, don’t talk shit here ana a school ndi amene amatukula dziko akamaliza school chifukwa they Work, on the ground pamene president amangouzidwa zomwe zikuchitika, give the loans out pliz.

  2. Kno dt those students @ university r oso akumudzi many of dem. So which ppl r u refering “akumudzi”? u give dem fud today, dey wil eat n xpct 4 mo tomorrow. So i suggest d money to support doz students 4 a hope 2moro. I ws der n i kno wat t z 4 a loan.

  3. Totally agree with Eliza komano there is one thing timalakwitsa amalawi..being educated doesnt mean you are always right ….if you got a degree o whatever doesnt make you dolo….thats y this country is poor…most pipo who are educated are just idiots….sorry i gotta use that word….some of pipo who are not educated in villages are much better at using resources….students ….its all about booze…shows..social weekends…nonsense

  4. Totally agree with Eliza komano there is one thing timalakwitsa amalawi..being educated doesnt mean you are always right ….if you got a degree o whatever doesnt make you dolo….thats y this country is poor…most pipo who are educated are just idiots….sorry i gotta use that word….some of pipo who are not educated in villages are much better at using resources….students ….its all about booze…shows..social weekends…nonsense

  5. Denis thanks alot,am 100%with what u have just said,in malawi we believe that those who are educated are the ones who went to university but thats not true,they were educated faces, look what students are demanding from goverment,yes they study everyday in their studies about economic clisis in mw.

 34. koma ma comment enawa akuchita kuonekeratu kut olemba ake sakudziwa chomwe akunena, so pliz, if u hav neva bin @ university en u know nothin abt basery, pliz jst shut up, wa standard **** nawenso mpaka comment? kkkkkk bulshit!!!!

  1. Don’t stop if we know what we are fighting for.APM is a dog that does not know what poverty is

 35. ngati ikupanga ma demo university ya yikulu mu africa muno ya ( university of stellenbosch) ku capetown southafrica pa nkhani ngati yomweyi ,nde ya malawi ya lakwa chiyani? Asiyeni apange mwaufulu wawo. Kapena mumafuna azitchola ma shop inu musiye kuitanira ma buss muzikaba katundu?

  1. Kodi Eliza Ukuti chani?! These people are taken as ‘Government sponsored’ but the government is falling to give them so they are asking what they deserve.. is there anything wrong here

 36. Tiyen kumsewu komweko basi,mapwiya sakumva uyu pofunika amve mkwangwa iki kukamwa kwake konyasako

 37. Ngati munthu ophunzira chonchi zikumuvuta what about munthu oti adakalibe 4 sanapange graduation ndikomwe. Zimuvuta bwanj. nsinje wa tikanena unathera mu sizi

 38. kupempha sakakamiza,loan isnt it ?but something has to be done immed, dont forget chanankholowa chizolowezi mbatata chinazulittsa

 39. I fully support the course taken by the university students. Most of our students are needy and need the loans.Government must prioritize education if we’re to develop as a country

 40. ok mwapasana zmimba ndye mwat koma mupeze dola yokayambla banja aaaaaaaaaa agwape iwalan zmenezo ngongole amapasdwa ana a schol muzabweza chan makaka inu nd mbuz ett

 41. this issue its for youngisters we are at xool though you are saying that we will die but am Sure they will hear us or else its. Do or Die Game mpaka kundende tikafika y they select us to continue our educa at unima and we kn that this demos we will fight fo ur sons and daughters hu are coming after us so Zip ur mouth and cheCk class u dd

 42. Mu matchen ameneyo ndarama zilipo amapanga bwanji hire ndege akamapita kum’sokhano ndizimene akafuna sibora osakafulara

 43. Tilekeni awo tili ku univ tichite izo tafuna….dnt talk shit as if for once u kno wat challenges we face….mxiiii stupid federation…..alekeni awo akudziwa ayankhile..enanu musoke kamwa zanuzo.

 44. Anthu osowa chochita amakhala pa fb comenting on issues of whch they dnt have enuf data.udalekeza std 3 koma ukukacomenta nkhan yokhudza university,enanuso ndisanje chabe popeza idakulepheran!..
  Koma mufune kaya musafune schul tmaliza wth that money govt is denying us…..

  1. Cosmas dnt waste ur tym argueing wth intellectuals.u d have no salt to tel them,they kno wat is ryt and wat z wrong or can u prove that wat u r talkng is more right than theirs??

  2. Intellectual iweyo Grecian!!? Hehehe intellectual my foot? Go to the streetz…and tiomberana indeed. You will be ma heros muli kumanda. Go ma intellectuals Go!!!

  3. Ine aise intelectual weniwen…..nTie tkakumana komweko tkayambira kulanda kamene umadalirako then ndikuponda iweyo…ndpamene ukadziwe kt mwamuna mzako mpachulu.ndie ife tmapheratu otiyamba

  4. Ine aise intelectual weniwen…..nTie tkakumana komweko tkayambira kulanda kamene umadalirako then ndikuponda iweyo…ndpamene ukadziwe kt mwamuna mzako mpachulu.ndie ife tmapheratu otiyamba

  5. Intellectuals Woyeee! Go Ahead. By The End of The Day, NO DOUBT, U’ll Be Loosers. ” I prefer DIALOGUE”

  6. kkkkkkkkkk…..Koma ndiye if astd 3drop out can understand isues better than so called university student then its better for these drop outs to be making decisions for the nation because we can move forward….Do not cheat ur self that if u are at public university of malawi then u r above every one..NO NO NO NO NO NOT AT ALL…U dont make any difference on the market at all bolanso wakukoleje ya utelala ukumunenayo…Uguys before u respond to any comment think because u dont know who is on this forum…Similary dont expect everyone to be on ur side so that they shld be called intellectuals…..aliyense yemwe sanapite ku University ya boma u mean ndi mbuli kkkkkkk…revisit ur library….if u were real intellectuals u could hv smelled the rat kuti these demos,some politicians are behind so that they fulfil their mission thru u….stop day dreaming ….no sense!

 45. Page iyinso nde sitizikukhulupilirani nkhani zanu, mesa masana munalemba kuti ma students sanapite ku parliament chifukwa boma lapeleka ndalama ku university za loan. Apa mukulembanso nkhani inanso. Pliz be serious.

 46. Boma lipeleke ndalama maiko ambiri ku university kumakhala loan chifukwa amadziwa kuti ma students ena amachokera kuma banja wovutika oti sangakwanitse kulipila fees, after all ndalamai imakhala loan yoti amadzabweza akayamba ntchito sikuti ndiyaulere ayi, nde enanu kusaphunzira kwanu ndi abale anu omwe chisakhale chifukwa choti anzanu asaphunzire

 47. umbuli wa anthu ali pamenepo,malo mosova zinthu mwamtendere mukufuna kuphwanya parliament, nde chomwe boma limachita lisiya vuto lanulo nkupanga maintain parliament yo pamapeto muzapeka oluzabe,kutero wina imfa yake yanunkhira kuteroko kkkk

 48. dont waste ur time this man(petera) does not care,ask your broz & sis who were there when he was minister of edu

 49. the goverment can spend 3billion on luxurious cars n u think we dont have the right to demand that amount of money to educate us n bring it bac in doublefolds??? think…

 50. ur request it has to be solved & is true their have to do something for that.wait & see .prz am not belong to any part.peace,justice & trueth is what i like.

 51. Zofuna zapittala sizo kenaka zizakhala malawiyonse mademo kkkk bwelani muzaone munthu uja akantama kt ndiowophunzila ziko lankanika usovenge pitala

 52. Aaaaah,m’malo moti alonjeze kuti azapita ku pariament olo kusatira konko kutsanjika,akuti tizakumana mumsewu,ndechani ana asukulu,muzakumana ndindani mumsewu!,muganize kawiri apa,kufunakulakwira anthu osalakwa basi,ngati kulikuika miyalayo kaikeni kunyumbayamalamulo olo kutsanjika,ndinudi ophunzira koma mutsazatisowetse ntendere mumisewumi.

 53. mmh u pple u were at home past days.why u are busy i bealive ur mature enough think befor u act.ths spirit is not of God.if u fear God think befor u go.to be first it does not mean that ur better but ur responsible.ur sawing seed no matter what.gvm is u

 54. If you don’t know the role of government on education shut up your mouth and don’t ever comment again. They are the same people who benefited from free university education, now they are busy kupondereza anthu osauka so that they cannot access university education by increasing fees. Shame on you

 55. i thought priority goes to the needy students,not all are subject to,or do they qualify for the loans.ena amayenelabe apange dig from their pockets,especially those who from well to do families.however guess its their right to express themselves.

 56. ngati boma ludalira money from donors wat about enafe……enanu muyankhula ngat akutumani..if u have money sialiyese Ali nazo……sionse ops ga mademo afuna nao loan..ena thy r fighting for their friends…Hahahahah tikumane ku capitoloko n two weeks time

 57. useless students,they think they are first to go to university. let them do what they want to do after that 2wks. we will smoke them out wth teargas. bullshit

 58. Guyz,cikuvuta ndiciani kuvomereza ku w r all in a daze due dis finacial predicament.Should I judge by cover to say we dn’t make use of wat we learn from our hundsom & beautf xool ? Should I say u’v neva eva com acros dat hundsom life skill of ‘acceptance’ wen thingz go upsid down.DZIWANI ICI anzathu ozindikranu,muukali nthaw zonse mulibe yankho………

 59. Alwz Ukakhala Kuti Kwanu Kulibe Adabita Ku University Kapena Iweyo Ukakhala Mbuli U Coment Nosense.Mesa Agalu Anu Mukwabakila Adaphunzila University Zolipilidwa Ndiboma.Uzingolimbika Kuti Udzakaponde Ku University

 60. Vto ndilot xul fees m’mene imakwera anthu akaombela m’manja kudalira ngongole lero ndiz mwaziona kuipa kodalira zawen osauka ali pamoto

 61. Let the concerned parties express their views on this post not myopias with magnum mouths only they much know is babbling nonsense..even at Harvard University there r students who r paid by govt..so stop ballooning this simple and clear issue

  1. Hahahahaha, u r so funny….. U cant compare Havard university with our Univesities my friend. We r far behind, and i wonder if our universities r under 100 on the World list of universities. The other thing is USA and Malawi r two different countries with different economic stability, even if u can compare with South Africa, we r far behind.

 62. Will the demos bring the money ? Dont u kno wat z happening in your country ? Maybe u were abroad, u dont kno anythng….

  1. An Example; Bambo ako achotsedwa ntchito and aliyense pakhomopo akudziwa kuti madala sakuvepa. So, from nowhere ana abwele ndi ma demand awo ofoyira when dey kno kuti madala awo zikuwavuta ? Think twyc

  2. @Langwani. Ati zokwela a speaker, leader of opposition, etc…..kkkk. I wonder wen dey preach abt austerity and yet dey want to b usng d vehicles….eish

 63. they called themself ana a school. koma akuti akufuna ngongole. mupanga nazo chani ndalama a pusi inu mufuna muzingonyengela kenaka mufe ndimatenda agalu. anthu tikukamba serious matters. mankhwala m’zipatala mulibe. njala ku malawi plus anthu akubvutika m’mamidzimu inu mukufuna boma likukongozeni ndalama. za ziii. akupatsani poti presdent wa leloyu ndi chi bwampini

 64. Kuti mufufuze amene akusogolera zopusazi ndi ana omwe makolo awo ndi ochita bwino and secondary yao anawa amalipita feez yoposera ya ku university…….Iweyo amene ukusatirawe asakupusise wachoka kwa nyezerera kuphalombe,,,ku Hora in mzimba,,,,ku enukwenu kutchire kwinakwake and kuti ufike ku university kugulitsa ziweto mix kachasu.was the older of the day.now today ..mmalo modikirira ngongole ya boma uli bizy kulowerera mademo omwe oyambisawo akuziwa omwe awatuma ….akakutibula ku msewuko angangako ku ntchenantchena /mpalare uwasiye pamoto …..Shame on u ndi omwe akukutumaniwo anamulkuveve!

  1. These guys are so stupid kodi mesa school ndiyao y don’t there parents support them or even them supporting themselves??? Dzipatala mulibe mankhwala uko, last year we didn’t produce enough zikudalira boma kuti ligule chakudya to feed the people nde poti ati ku college /University asatinyasepo ngat asafuna asiye sakuwakakamiza to be in school

  2. Well spoken Thisa….amnzawo tangochoka kumene mu chimpwirikiti cha feez…awa afune azikhala ngati ali ku orphanage….ati kubisala mudzina loti amphawi Zopusa zenizeni….Malawi ali ndi mavuto ochuluka oti if we.were civilised enough we could be sympathising with our gvt….Abig question is.after ma.DEMo so what?????

  3. Well spoken Thisa….amnzawo tangochoka kumene mu chimpwirikiti cha feez…awa afune azikhala ngati ali ku orphanage….ati kubisala mudzina loti amphawi Zopusa zenizeni….Malawi ali ndi mavuto ochuluka oti if we.were civilised enough we could be sympathising with our gvt….Abig question is.after ma.DEMo so what????

 65. Hay,ana Inu,ku Ubwana Mkuchilondadi Eti.Mukulirira Msima Pomwe Ufa Palibe.Mukuona Kuti Kulirako Mupeza Zofunikirazo?Osakhala Ngati Mafolenazi Ayi,mavuto Adzikoli Mukuwadziwa.More Over Mukuti Mukufuna Ngongole.Ngongole Amakakamiza?Kulani Ka.

 66. Go guys its your rights to do so,but remember that this is the worst govt than ever before,we are being sailing with a leader who has no vision for the country

 67. kodi pa school umalipidwa kapena umalipila ndiwe mwana wa school kwinaku kumakhala kusaganiza ada ngopita ku university without knowledge may God protect malawi

  1. ndawona muto la amalawi ngati inu even mutatukwana koma ngati muthu wayika decision singasithe cause mukupanga mademo mayaz just need kukhalapasi kukambilana zithuzi chomwe chimandisekesa ndichakuti muthuwe wagweredwa vuto koma kuti mukambilane umawona kuluza one u need the thing ooooh God may protect us

  2. By the end of the day akutsekelaninso xuluyo. Muzipitaso kwanu, thus why this guy was asking you kuti….kodi mumati lero ma demo mawa mademo xul mmaliza liti???penaso mziganiza ngati ma academicians and intellectuals, patience imafunika pena pake , what about the events in south africa….???wat were the results???everything was suspended…now even the poorest students are suffering. Personally i know what it means to be a student a boarder or non-resident i have been there and i understand, but you gotta be patient sometimes, you don’t just take to streats everytime, greeks are doing that zikuwathandiza chani???and understand the present economic position. Koma osamatukwana, cursing is not morally right, unfortunaly as students at that age we love that and emrance it even when we know its not right. Am very sure that somewhere-somehow all is not well with transactions but this money will be given to those that have not received….unfortunately so often xul authorities and adminstrations always do not want to clear things fast and in honest, and so often delays which has to change to avoid such scenarios.

  3. Come on Romeo, its the duty of government to educate its citizenry, u might have your reasons not to agree with wat they r doing but if u can look into the statistics Malawi is the most expensive country as far as University education is concerned in Southern Africa. U shud feel the pain these niggaz r passing through Romeo coz its not all that come from rich families n can afford to pay 275. God save this Country

  4. Tinavaya ku college tili mafana nde olo atamatseka palibe nchito tizamalizabe fast mix ubwino osabwerezapo nkukhala chi engineer chovayilila

  5. Thanks #Romeo and thanks #Enerst for the honest point, u are right in some way though. But here is just a snap shot of a very sad story, i lost a very good and intelligent friend 6yrs ago, he was@Chanco. During demostrations he was tear-gassed, xul was closed they were called back a 2months later but he had developed eye problems, and upon revelations @de hospital he regreted everything. Then another demo came he was nt involved in the demos, but the xul had bn closed again and due to financial challenges he could not afford a lot of stuff as many had expectations from him he developed lung problems, during that period out of frustrations he started drinking heavely, a car accidentaly hit him…he survived though, but my friend had a lot of problems now his eyes cud barely see, lung cancer, and now this accident he died a couple of months due to internal injuries while on one of his xul recess…anyway there are many risks that may nt be noteced right away but wth time they have an impact…..sometimes we get carried away easly without thinking thro-watch close friends sometimes-for they contribute to our early departures…i have been there…: just saying…….i pray that things should be sorted though.

  6. Demonstrations??? What4; and u say why?? thats obviously outdated!!! think of other altenative ways coz its u who can feel the pinch of those so called {demon}`strations!!! never say people never advise uu!!! (used to subsidies) kkkkkkk

  7. guyz mukungothaisa nthawi yanu pano mwamva zomwe anena mdala uja wamulomo wake ngati amumenya…I hop mwamuziwa….et akut

  8. university material imeneyo kutukwana kkkkkk anthu ndinu mukumakhala ma iresponsible bosses/educated savages mma office….Pali chifukwa chotukanira apa???….onsewa akukuthandiza maganizo kuti

  9. Godfreyuniversity material imeneyo kutukwana kkkkkk anthu ndinu mukumakhala ma iresponsible bosses/educated savages mma office….Pali chifukwa chotukanira apa???….onsewa akukuthandiza maganizo kuti

  10. Generally you have to pay for your own education. Ana a pa poly kupusa.
   Mumina , kudzimva ngati kuti you are the 1st who stepped @ vasity.

  11. In malawi pipo can go to university but they are still wearing umbuli pamaso pawo,even maiko olemera they dt need loan wen they are studing,i v been styding at U,C,T in Rsa,i have never been paid,south africa being coutry which people have freedom to expless their needs,what about poor malawi?

  1. it’s sad because there so many smart and brilliant people who began their first year but a degree that’s supposed to take 4 years is being done in 6 years simply because of these demonstrations which always lead the university being closed down

  2. I don’t study in Malawi for this very reason .. The course I wanted is available at poly technic but I figured I will be there 6 to 7 years to do my degree which should take me 4 years to do … Remember chancellor collage faces the same thing as poly yet poly wants to seem special in a certain way .. Best plan is to suffer now and do your school , get your degree and make your own money … It is pointless to fight this government because every cry will fall on deaf ears .

  3. Njema boma ngati likutiainzitsa tangoyenera kuraiza… mind you, ku poly fans ina mpaka lero malswitch sinalowe and akungokongola dollar

  4. must university tuitiona yokha imaonetsa kuti ambiri ndima merchant koma ife ma ghetto youth aku poly tangoyenera kuathira ma wise akuluakuluwa mix asamasinze… komabe ma ghetto mubwere social weekend imeneyi tizawalewale

Comments are closed.