Mutharika angers Nurses

Advertisement
Dorothy Ngoma

Malawi President Peter Mutharika’s directive to ban local health public relation officers from speaking to the media has sparked anger from the National Organisation of Nurses and Midwives of Malawi (NONM).

Dorothy Ngoma
Ngoma; Blasted the decision.

According to a memo signed by ministry of health principal secretary Mcpherson Magwira, district health spokespersons are now to seek permission from the ministry before granting information to journalists.

Reacting to the news, NONM Executive Director Dorothy Ng’oma said the development is unhealthy to a democratic country like Malawi.

“Local PR’s are very important because they give real, current issues that are on the grounds, I don’t think someone at the national level can give information about Nsanje, this doesn’t make sense.”

“But we are not surprised, we have a government that does not know what to do, no fuel for ambulances, no food for the patients.”

“They have failed all that and they also want to take away our voice? I think is unhealthy to a democratic country like Malawi,” said Ngoma.

The development has also been deemed to be a threat to access to information bill, advocated by media practitioners in the country.

Advertisement

112 Comments

 1. Dikirani Ndingopanga Zomwe Ndinampanga Bingu.He’ll Not Be Wth Us Before 20 Dayz.But The Problem Is Running Mate Wake Ndimbuziso Yamunthu Yot Singalamulire Dziko.Nde Tiziona.

 2. Amalawi munadzolowera kulira pakakhala vuto koma osapeza njira zothetsera mavuto anu. Kutukwana mtsogoleri wadziko ndi yankho lamavuto anu? Kodi otukwananu mutakhala atsogoleri mudzasiya kutukwana zasatanazo?

 3. A Ngoma imakula ndi nsanje, paja munalitu m,momo sikale. Ndipo ndikudabwa anamwino onse palibe wina wa nzeru woti atha kukusogolerani anachoka ku bwera mwamusankhanso nkhalambazi zikuchitilana kaduka, sizikuthandizanani! Dzukani kwa cha!

 4. I dont see anything wrong, because everybody knows dat donors pulled their funds to Malawi becoz of cashgate. Now, if u keep talking abt d problems in hospital on platform, will it help in solving out d problems ? Sometimes a Malawi, lets learn to love our country despite political afiliations. Accusations will not lead us anywhere, lets take a step to map d way forward in one spirit and conscience mind, politics aside

 5. MUNASANKHA NOKHA PRESIDENT YO NDIYE LELO MUKULILA, A MALAWI MULIBE MZELU OLO PANGONO NDINU. MUKUDZIWA KUTI BIGNGU MKULU WAKE AMAKUZUNZANI LELO MUKUSANKHA MPHWAKE MUKUGANIZA KUTI PAMENEPO ZINTHU ZIKAYENDE BWINO? A MALAWI MUMATENGA CHIPANI NGATI MPINGO WA CHURCH KOMANSO SIMUCHEDWA KUTENGEKA KUTENGEKA

  1. Ndwe M Bulund Iweyo?Zot Pitala Adamusankha Nd Ma Computer Suziwa?Zot Adabera Ma Votes Nd Ma Computer Osat Anthu Suziwa?

  2. Ndwe M Bulund Iweyo?Zot Pitala Adamusankha Nd Ma Computer Suziwa?Zot Adabera Ma Votes Nd Ma Computer Osat Anthu Suziwa?

  3. Computer ili Ndi manja bvuto lainu a malawi simuchedwa kuiwala mukhaula ndi peter yo, nonkha mumamuchemelela lelo mwayamba kulila , joyce banda mumamunyoza lelo wapita mwayambaso kumulila, mulila zenizeni. Simunati

  4. Mukayamba kulila ndipamene mikunamizila ma computer umaiziwa computer iwe kuti imagwila ntchito yanji? Compute imaba bwanji, nanga anthu ayanganila anali kuti bwanji sanali kuiwona computer yo, Nanga iwe ukuti computer iwe unali kuti panthawi imeneyo? Mwasowa chokamba. Kutengeka Ndi chips and chicken ndizimenezo

  5. Am Not Pat Ov Zandale My Friend Ndpo Pamoyo Wanga Cmnavutikepo Coz Ndmadalira Kwambri Olenga Iwe Nd Ineyo Mot Usathe Mawu Aixee Ndiine Uchedwaaaa

  6. Kikikikikiki I, don’t understand wat a r u talking about, apa tikukamba zobvutika olo za president wakoyo, wangosowa chokamba eti, Nanga ngati uli otchedwa Nanga ine zikundikhuza, if u have nothing say plZ JST zeep U r mouth

 6. Kkkkkkkk inu mukumuyamba dala Peter. Kkkkkkkk Mukufuna achite chani yet ndinu nomwe mudapangitsa kuti mkulu wake amwalire? Iye si bingu or amayi please. Kkkkkkkk kkkkkkkk simudati

 7. Tidanena ife uyu yayi koma kusamva a malawi ndipo mpaka 2019 ,ndichiyambi chabe kenako tiyamba kulipira mzipatala za boma.Boma ili ndilokumpha likuyenera kusintha dzina , Koma Mulungu akuona zimenezi

 8. koma yea!! Fair is not fowl n fowl is not fair,you’ve not seen Democracy limit and udindo wake.kodi inu mudavotela ndani paja?Hha-ha-hahaha!!!!!che Nanthambwe anazitengela ndi kunena kwa?????

 9. Zosaveka izi cholinga ndikuti anthu asamadandaule olo tiziva kuwawa , Bwana munatipeza ndipo muzatisiya ,Bwana olo mutachulutsa mkwiyo motani simungakwanitse kuphimba choonadi, tinene kuti musintha khalidwe mwayambali? Kapena tipemphe kwa Yehova kuti atilandile tione zina

 10. Musova, aphunzitsi ambirimbiri sakulembedwa ntchito nde popeza ma nurse nawo salembedwa ntchito nde mwapeza cholemba? osalemba za aphunzitsi akungokhalawa bwanji? kupusa eti!

 11. Duyz Chikha Mbewu Ya Chimanga Bezi Titakazinga Yonse Osasiyako Oloko Chimodzi Koma Pokha Ndi Anthu Tingoti Mulungu Awakhululukile Popeza Sadziwa Chomwe Amachita.

 12. Mwana akamalankhula zolakwika amene amavutika amakhala kholo ndiye ngati kholo lili ndi ufulu woletsa mwana kulankhula zotukwana ngati kuti nayenso amasaka nawo ndalama!!!

 13. Musavutike, akabwera Ku chipatala mukangomubaya nyereti yovutilapo

 14. waucape nyani ameneu m.balewako analimomo ndipo analiwamakhani kwambili onsati iwe nyani iwe pagongopako.usati nsananga wutha muwava kutina amw .unya iwe chitsilu

 15. akulu mukumawatchula A P M awa ayamba kupanga za late brother wake Bingu akungopanga zofuna yekha in short MR KNOW IT ALL imagine no fuel for ambulances and food for patients whats that koma we dont loose hope our God is a listen one amapanga njira popanda anthu sangamadandaule chifukwa cha munthu m’modzi. DPP WOYEEEEEE BOLA AMAYI OMWE AJA NDITHU odi ukoooooo amayi adutse

 16. Zitachita kuvuta kaya kutani ameneyi zomwalira kapena nditi kufa osatheka.Simunati munyera muona mpaka 2024 tilankhula ,tinyoza kutopa ameneyi akulamula mpaka 2024 mukhulupirira.Bingu salikumanda akumuyimirira ameneyi muvomereza

 17. Who has a hand grenade,a bazooka and a machine gun for sale?I need them badly.please!

 18. Kale kalelo; kuchipululu adasankha olakwikaaa..!!!!!
  Mwa umphawi ndi umbulii…adasankha molakwika…
  Kwinako sindipitiriza…
  Vuto lidali ati kusankhira chikuwawee!!
  Oyamba kulira adali Mbendera pa Comesa…..
  Lero MALAWI THE FLAMES ALI LAWILAWI!!!!!!

 19. koma peter utipha tonse, tikamafika next year udzakhala kuti watsala wekha ndi mkazi wako Gertrude. mwinaso mkazi wako she is now regrating kuti anakwatidwa ndi munthu was nkhaza. ndiye bolaso bingu nkulu wako uja.

Comments are closed.