Mutharika fails to honor MCP ultimatum

Advertisement
Peter Mutharika
Jessie Kabwila
Kabwila says Malawians need to know the truth.

The Malawi Congress Party (MCP) says the five day ultimatum it gave government to reveal the names of over 100 people who accompanied President Peter Mutharika expired on Wednesday.

There has been a battle between MCP and government over the issue that government took a bloated delegation to the 70th session of the United Nations General Assembly (UNGA).

MCP spokesperson Jessie Kabwila said government has failed to publish the names of the entourage alongside companies who sponsored them meaning that government knows that they used taxpayers’ money.

”We are trying to hold government accountable and transparent and we are hopeful that government will comply and we will communicate the reply to Malawians,” said Kabwila.

On government’s part, Minister of information Jappie Mhango said that government will not bow down to MCP’s call for it to publish the names as president Mutharika already responded that some people were sponsored by the UN.

 

Advertisement

153 Comments

 1. guyz ziwani kut Kabwila ndi wamitsala coz l remember dere z dis other day sh said pablicaly monyoza omwe akudwala HIV/AIDS kut boma likanatenga ndalamazo nkugulira makhwala kuti omwe afa kalewa mwina nkupulumukako.kumeku kunali kuyankhula kwa bwino?koma akanakhala a DPP ndiye bwenzi mutamva ZBS itanyamula nkhani yonseyo pamutu pawo koma choti aziwe ndiichi even 2014 radio imeneyi +ena otelo sidapangire DPP Campain kotelo azachita manyaz coz anzawo ananyoza maliro pano amanong’oneza bondo

 2. paja a MCP mwanenesa kuti muliika boma pa Pressure, so mwayamba kumaotcha misika cholinga muziti boma lalephera kuthandiza anthu okhuzidwa ndi kuphsya kwa misika. Munya a MCP inu tikukuuonani, misika yokuphyayo ikhala choncho, muisovenge, the govt is to solve very cricial issues not za misika. Muzingowapwetekesa anthu amalonda za ziii. Nanuso amalonda mungoombera mfiti mmanja akkukuonongani. Zanu izo muisovenge.

 3. ngati MCP ikufuna u president, izawine chisankho, tizaone ngati iyo ingakwanitse, governing a country is not a joke, even if Chakwera atakhala president lero, he will face the same issue of economy and others.

 4. Mcp ndikachaninso mphamvu zofunsa zinthu zimene pulezident atiuuza kale ngati mtundu wa amalawi mwazitenga kuti? Mukuganiza angayankhe zopusazo kagweleni uko

 5. A DPP you are the main cashgatter nde musamayankhule za cashgate, za nduna zakuthambani kafukufuku amapangika koma amathela mmalele sichifukwa cha MCP, koma ngakhale DPP idziyelese sizingatheke chifukwa cha mwazi wapa 20 july.. ndale uko now serious business,, list yomwe ikunenedwayo sikuti njopanda phindu kwa aMalawi ayi, zimenezi ndi ndalama zathu ndithu tiyenela kuzitsata mmene zikugwilila ntchito choncho nkofunika kudziwa kuti paulendowo John beseni anakagwila ncthito yanji ndipo kunali koyenela kumutenga paulendo? kuchitila kuti pa mawa a Chakwela akadzalowa mmboma asazapa mamistake owononga misinkho ya aMalawi. Mwina ndingofusa kuti nonse a mene mukuti MCP i kulakwitsa munayamba mwagula katundu ndikufusa lisiti la MRA n’kuwona pa mene alemba VAT, makobidi alipamenepo mukowona kwanu ngopanda ntchito? Komanso ngati simufusa lisiti inuyo ngoyenela kumangidwa,, ndiye muwone kufunikila kamsokho umenewu, ndemuzifuse kuti kodi kuvutikila konseku kuti ndalamazi zipezeke ndewina akangozi shopela ku America aliphee……..

 6. Mukuwotcha misika cholinga muzit peter zikumuvuta,NO!NO! No!NO!ma cometee amunsika amene anachosedwa alet gvt ndiamene akupanga zimenezo dara,azit peter akulephera kuyendesa dziko,chimene mungaziwe ndichot akut boma silimalephera timalephera ndife anthu.

 7. Chimene mungadziwe ndichot,palibe amene angakhale 100%,kukazabwelanso boma lina nalonso lizakhara ndimolakwisa mwake.ndipo azizatinamizanso,siyan kumalowera za Ndare,sitimadya nawo ife,olo tilalate ovutikabe ndiife tomwe.ife ndiye onamizidwawo

 8. Kabwila anayankhula ngati zanzeru koma Pena zikumandipatsa nkhawa kuti if it was them,they cudnt hv done much better.I mean,to me it sounds more like,”Can MCP pliz get its turn to mess this country up?Thank you!!”

 9. Tinene kut it z,unprofessionalism pa utolankhan?daily politics basi?nanga ife pot zandale ai,cimungalembepo zot Busy signal wakana kubwera kuno iyai?mpiru otendera ndi deal than okazinga ndi mafuta?ximungalembe nkhani zachitukuko?zandikwana ine ndixingoona APM chani chani uko,aaaa!!akutumani?

 10. Pliz atolakhani pliz musasokoneze anthu simungalembeko zabwino za President koma always critsiz kodi mesa aKabwilawo anali mu deligation yomweyo samakana bwa kut anthu achuluka? shit jornalist & Politicians

 11. Stupid calls coming from stupid party,, and being supported by stupid idiots inthe name of support..To hell with u mcp ….tell this your grand parents,,,

 12. Peter to honour mcp its an believable but do u know whom ur talking to?u already said de presdnt so how can apresdnt honour his servants, ur totally idiots and u dont know wat u r talking .dis is peter remember.

 13. Mwina tingoti anapondako ndi mapazi satana ku malawi.nanga ngozi zikhale za moto zokhazokha kumaphyaso usiku wokhawokha koma one day i believe uzapezeka naweso zaziwe kuti mathelo ako akwana.mulungu azaweza

 14. kodi ma mp athuwa ncthito yawo ndichani komanso awa ma councillor chifukwa masiku ano ndikuwona aliyense akuyangana maso kusanjika nthawi ija tinali ndi achina nga Ntafu Anali Kutengapo Gawo Koma Apanopa awa Bola Zawo Zikuyenda

 15. how could one include both rice and sand in the same bag? Other people in that delegation were useless to the summit.

 16. Wachita bwino who is going to benefit from that list ? MCP shud provide solutions that will help the country regain its lost glory rather then talking shit when they received part of cash gate money kuti ziwayendere ndi amayi.

 17. mcp is a loser party…it will be in opposition for ever…kumangotsutsako opanda cha mzeru basi…let APM rule.olo apereke mayinawo what wil it benefit us?

 18. Mwano oyamwira kkkkk ndipo sadzatheka. chitsulo chikatha pa galimoto chimachotsedwa nkuika cha tsopano. apo bi galimoto limachita ngoz mosavuta! ndikunama amechanic muli apa?

 19. Koma Mcp Ndiye Ili Ndi Chiwewe Chofuna Kulamuliratu.Bwanji Kodi?U Think Olo Peter Mutharika Atamwalira Lero Monga Mwa Malingaliro Anu Mungalamule Malawi?List Ya Anthu Omwe Anapita Ku unga Ithandiza Chani Kumtundu Wa A Malawi Akakupatsani?Who Do You Think You R To Be Honoured By Gvt?Munali Kuti Mmene Anthu Amenewa Amalonzekera Ulendo Wo Simunatsutse Bwanji?Zausiru Basi.

 20. Typical of politics in Malawi, we cant help pulling our nation to move the mud it is swiming but busy strategizing on how we can make the govt loose popularity, pompous & greedy politicans

 21. Khani zina ukamava mpaka utatukwana nazo. Tawauzani awo mukuti MCP kuti kuyambula lero ndi chipani cholamula bas .ndaona ndi zomwe akufuna bas

 22. kodi ife tikudikila chija chomwe amati achichita koma sanachitchulechi tichione fotseki zanu ,tachitani tichione

 23. Please atolankhani tamalembaninso nkhani zachitukuko zomwe bomali likuchita. Kodi dpp ikungopanga zoipa zokhazokha? Tikudziwa kuti nkhani zodzudzula boma zimayenda kwambiri malonda komabe muzichita balance.

 24. Time ija kuzudzula mcp umaphedwa,ma eggs,cattle,goats,atambala akuda ndi zina zambili mudawabela amalawi.pamaulendo mumatengananso makamaka MBUMBA.Kunena kwake mwati mukuthokozana pa ntchito yokweza chipani kuyambila ku Aerial-branch mpaka National level.Mukumatenganso tianthu tanu tosaphunzila bwino kuwasomeka mma ministry ati ntchito kuthokoza makolo awo atolera bwino mandanda ndi kunyamulanso zithunzi za atsogoleri mmisonkhano.Anzanuwa akungosata zomwezo.Ndinu amodzi musatipusitsepo apa iyaaa!Akabwila mukanakhala okonda dziko bwenzi mukumakangophunzitsa apa,anzanuwo bwenzi akumakalalika pakuti kumwambako ndiye kulibe mavuto-mfumu YESU AKUTERO.

  1. Kusonyeza Kuti Pasakhale Checking Popeza Enao Amateronso. Mwati Mtendere Uli Kumwamba? Pitani Kumwambakotu?

 25. Malawi will be the poorest country on Africa/World because of greedy leaders
  since we gain independent still we face alot of challenges but we didn’t find solutions to problems

 26. kodi mesa apm adanena momwe adayendera ku un ndemufunano chani mukuganiza ngati muzalowaso a mcp adapolamila mwini wake chipani chimenecho chidatha iwyeso atangofa muyiwale

 27. A Malawi; munthu atanena kuti a Malawi ndi dzitsiru angalakwe? Pali zoti Peter aikilidwe kumbuyo apa? Angakhale atawauza a Malawi kuti anthu ena amene adayenda nawo anatumizidwa ndi mabungwe komanso ma company, chodziwika bwino ndichoti anthuwo adalandila ma allowance kuchokera ku boma osati mabungwe. Atsogoleri sadzasiya kutidyera chifukwa chatulo

 28. Cngratulations Mr President, MCP musaganizekuti amalawi tidayiwala nkhanzda zomwemumatichitira, Ahakwera simuzdakhalapo president, ask Mr Tembo what MCP was doing to Malawians

  1. Amene mukuti akuganiza ngati saizi ya nsapato ndi amene akuganiza bwino kuposa inu amene mukumunenanu. U think president angakhale opepera mpaka kumamvera za kabwira? Akazafuna azakuwuzani koma osati kuchita kumulamula, olamula akenso a mcp….

  2. Makape a mcp muzingoliralira mpakana kalekale coz palibe amene adzakuvotereni chifukwa mfundo zanu ndi zaupandu.DPP forever 2019 and beyond

  3. Munthu akasiyana nanu maganizo sikuti akuganiza moperewera ayi. That’s demcracy. People differ. Lero BB yaluza kodi tisanyadire civo chifukwa choti a bb ambwinda?

 29. ka mcp ndie katikwana kodi tizingomva zopuxa zanuzo? Mukhala oxuxa zili zonxe mpaka kale kale. Za nkhaza zanu tikuziziwa ife. Kagwereni uko. Za ziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii!

  1. Mcp ndipang’ono koma DPP yakwana aliyese m’malawi muno nkhza ziponse kuwotcha misika tsiku ndi tsiku agalu inu

 30. Mcp malawi christian party inalakwa yokha un’gonou’ngono utaona kuti sizili bwino mwina ndi mwina anaitanitsa atola nkhani,ndipo zinakonzedwa koma achakwera anati Dzuwa likalowa limatuluka ,kodi ndiye kuti silinatuluke? A Jessei?

 31. OK so what next ?,what are you going to do ? Tisave zoti Ku state house kuli heart attack, apo ndiye nkhondo yapachiweniweni ibuka ndithu panja ndi Bingu mumamupasa matsiku, tiyeni nazo ziwoneka zokmwe zithele

 32. nchifukwa chani dpp chitengereni boma, misika ikungophya…? Sizoti muziotchera dala misika kuti muzagwiritse ntchito pa campaign..misikayi afta all ikaphya anthu akumamanganso okha opanda city kulowererapo…misala imeneyo ithe pulizi….ngati ndi ndale muzingopanga pa radio osati kumawaonongera anthu ma bizness awo ngat kuti munawapatsa capital ndiinuyo…!!

  1. dpp ikumatumira dala anthu kuti aziotcha misika…msika uphya bwanji msika oti ulibe magetsi…? Pena pake ndale amalawi mumapembeza kwambiri azitsogoleri anu ngati kuti sazafa olo ngati kuti peter-yo ndi ka mulungu kanu…!! Sibwino koma…ndale zili apo, tonse ndamalawi…

  2. on tuesday this week ptc yaku chilomoni inaotchedwa, wednesday post office yaku mulanje yaotchedwa, wednesday yomweyo msika wa mzuzu waotchedwanso….koma dpp

  3. apa sindikumvetsani, mukuti akuotcha misika ckifukwa chani? Chifukwa mmene ndikudziwira ine chipani choti chikulamula singakhale busy kuonga zinthu.akaotcha akupezapo profit yanji? Ndipo akamati chiloweleni dpp misika ikungopsya Escom house inapsyanso muulamuliro wa DPP?

  4. for your information during dpp ya bingu ; 1. Msika unaphya ku limbe 2. Msika unaphya ku lilongwe 3. Zodiak car inaotchedw 4. Office ya rafiq hajat inaotchedwa 5. Msika ku karonga unaotchdwa 6. Msika unaotchedwa ku mzimba 8. Msika unaphya ku kasungu 9. Msika unaotchedwa ku zomba 10. Robert chasowa anaphedwa….fastforward dpp mu 2014 to 15..1. Msika unaotchedwa ku lilongwe 2. Msika waphya ka 5 ku mzuzu, flea market katatu, ku zigwagwa kawiri 3. mec inaotchedwa 4. Galimoto ya ACB inaotchedwa 5. Njaunju anaphedwa nkuotchedwa nkumukwirira 5. Chilomoni police inaotchedwa 7. Chilomoni ptc yaotchedwa 7. Post office ku mulanje yaotchedwa…..!!! Mutha kuonjezera kwinakooooo

   1. DPP is rubish with its president, am not surprised that most of the comments above are from lomwes. Idiots to be exact, complete idiots.

  5. #ben….chiwanda iweee…!! Ziwanda zimenezo zikufunika bushiri athane nazo….mtumbuka ndi ndani…? For yur info am from lilangwe, btaz not za utumbuka ukunena iwezo…

  6. Hahahahahahaha!!! Mr #Goodwinnie! Use your head and not your Balls. Cant you see that its the opposition doing this to discredit Dpp? People like you who twist the truth deliberately dont deserve any breath on earth. Dpp rulling = Misika kupsya Dpp oppostion = misika osapsya then if at all you attended any logic class, what does that tell you??

  7. #davi…if yu want me to answer your question logically, yu could have stated the implication first…should i use aristotlic square or what…? You mean dpp torched escom when it was in opposition..? Hahahahha….i can see you are have drunk too much mad woman’s menstrual blood….!! ye a troll

 33. Kd mcp ikufuna itani apa,skt bwana peter azingoyankha nzina,zilinzose ndi zopanda mchere,kd akanatenga mamemba a mcp kupita nawo ku msonkhanowo izi zinakaveka,ndipo ndikamava Za mcp ndimangoona magazi okhaokha

 34. WTF does mcp think they are to dictate and give ultimatums to gvt? The bunch of frustrated loosers be trying hard to stay relevant! Tinakukanani nthaw yachisankho now shut TF Up and wait for 2019.

 35. Am in Thambani at a place called pa M’phelanduna mizimu ya a Sangala , a Matenje, CHiwanga ndi Gadama iwuse mumtendere. A MCP sitidzakukhululukirani mpakana kalekale

  1. maphwala ako iweee….kabwira, chakwera, gustav kaliwo, belekanyama, olo iwe amene unaliko mu 1980 pomwe ankaphedwa amenewo…? Nkhuku iweeee….wamwa ma period ankaxi wamisala etiii…!! Tikukamba zoonongeka kwa chuma in 2015 iwe ukukamba za 1980…nde mizimuyo ikusinthirani chuma chadziko lino…? Chule iweee

Comments are closed.