![Sangwani Phiri](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2016/12/Sangwani-Phiri-235x176.jpg)
Boma ndi lokhonzeka kunyetsa onse ofukula mchenga
A ku unduna woona za chilengedwe, mphamvu ndi migodi ati iwo satopa kulimbana ndi anthu onse amene ali pa kalikiliki kufukula mchenga. Malinga ndi a Sangwani Phiri amene amayankhulila undunawu, iwo ati undunawu ndi okhumudwa… ...