![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/07/Kamoto-Airtel-235x176.jpg)
Airtel itsitsa mtengo oyimbira ku manetiweki ena
Kampani ya mafoni a m’manja ya Airtel Malawi yati kuyambira sabata ya mawa itsitsa ndi 1 kwacha mitengo yomwe makasitomala ake amalipira akamayimbira lamya kapena kutumiza mauthenga ku ma netiweki ena. Izi ndi malingana ndi… ...