![Kizito Tenthani](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2021/06/Kizito-Tenthani-235x176.jpg)
Dziko la Malawi tsopano Lili ndi mkulu wa kalembera wa zipani watsopano
A Dr. Kizito Tenthani tsopano ndi mlembi wa zipani zandale m'dziko muno. Izi zikudza kutsatira kuvomelezedwa kwa a Tenthani pa udindowu ndi nyumba ya malamulo. Potsimikiza za nkhaniyi, m'khalapampando wa komiti yosankha anthu m'maudindo osiyanasiyana… ...