![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/07/Chihana-enoch-235x176.jpg)
Fetereza sitigula ngati chitumbuwa – Chihana wauza boma la Tonse
…wati ngati atsogoleri sakudziwa kanthu za feteleza, afuse anzawo omwe akudziwa Mtsogoleri wa chipani cha Alliance For Democracy (AFORD) a Enock Chihana, wawuza akuluakulu a boma la Tonse kuti ngati sakudziwa zoyenera kuchita pa nkhani… ...