![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/06/Lilongwe-District-Council-235x176.jpg)
Khonsolo ya Lilongwe igwiritsa K2.5 miliyoni kusamutsa pholo la mbendera
Khonsolo ya boma la Lilongwe yati igwiritsa ntchito ndalama yokwana K2.5 miliyoni ya misonkho ya a Malawi pa ntchito yozula pholo la mbendera ndikukaliyika pa malo ena ku ma ofesi kwawo komweko. Izi ndi malingana… ...