![kamuzu stadium](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2016/08/kamuzu_stadium-235x176.jpg)
Bwalo la zamasewero la Kamuzu litsegulidwa Okutobala
Boma kudzera mu unduna wa zamasewero latsimikizira anthu okonda masewero a mpira wa miyendo kuti bwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre litsegulidwanso mu mwezi wa Okutabala. Watsimikiza izi ndi nduna ya zamasewero a Francis… ...