Breaking News: Ng’onamo, Kananji fired!

Advertisement
Nyasa Big Bullets

Be Forward Wanderers have sacked coach Eddington Ng’onamo and his deputy Eliya Kananji a month after leading them to Carlsberg Cup triumph, Malawi24 can confirm.

On Tuesday, the team’s executive committee had summoned the technical panel to an emergency meeting following a 1-nil defeat to rivals Nyasa Big Bullets on Saturday where they resolved to have the two coaches fired due to dismal poor run of form in the super league.

Kananji fired!
Kananji fired!

Currently on 10th position with 29 points from 20 games, the Nomads only managed to collect a point from possible 9 in their last three games. Wanderers finished on 4th position last year but they are yet to end their super league drought, having won the league in 2006.

The duo have been replaced by former Flames international Yasin Osman who will be deputised by former Nomads striker Bob Mpinganjira. Kananji has confirmed that he has indeed received the letter of his dismisal.

On Tuesday, Malawi24 published an article which revealed that Kananji’s first eleven was turned down by the executive saying the derby was ‘too’ big without former Flames captain Joseph Kamwendo. Eventually, Kamwendo was outclassed by former Nomads reject Kondwani Kumwenda who scored the only goal to inspire Bullets to the victory.

Advertisement

156 Comments

 1. Palibe chimene chachitikapo pamenepa sangachotse Kananji kulemba Bob mpinganjira ndipo Yasin zidamukanika kalekale pano chanzeru angabweletse ku wanders ndi chani? kupha team kuja ndikumeneku.executive yanji yolowetsa team ikaluza kumachotsa ma coach fire the hole executive muona kuti wanders iyamba kupanga bwino.wanders siya Jack ndi anzeke ayi koma ndiya ife oyitsatira poti ikaluza timanyozeka ndife

 2. Ine ndi wa noma koma zomwe mwapanga palibe chanzeru kodi yasin mesa tinamuchotsa lero ndi dolo kodi kananji walakwa chiyani mukanachotsa ng’mnamo osati kananji. Komaso ngati mukufuna zigoli coach wa zigoli ndi ramadhan. Osati ayasini kaya poti mwatelo

 3. pokhapokha mudzalembe ntchito wenger kapena morhio mudzawina lig otherwise mungodana ndi makochi ose kumalawi kuno chonde vuto simakochi musadanitse bb simudzaiwa mpaka kalekale

 4. kakhalidwe komangochotsa ma coach mwachisawawa kaonjeza guys vuto si makochi vuto ndi ma player mundivonereza zinthu zitaipiraipira nose mufuna ntchito mu tnm super lg a leo mpulula kozekani chifukwa a yasn angomali season basi amutayaso za champion muyiwale

 5. Neba Kkkk Chigoli Cha Kk Chakusowetsani Mtendere? Inu Akananji Mumati Mutani Imeneyo Ndi Team Mmafunayo? Musabwere Ku Pps Team Maule Coz Kuli Coach Amene Akutimwetsa Wa Mkaka Each & Every Game Kkkkkkk Mauleee Chimoto Kuti Boooooooo Kananji Kugwa Kuti Phiiiiii !!!!

 6. weniweni wa noma kma na khani yokhayi am very xry kd guys when noma beaten by mafco 2 nero bwnj sadawachotse nthwi imenyo? both tech panel and Adm Abwera Poyera Tisamangonamizana Apa Wataniso Noma

 7. Let Me Help U Neba, Kananji Ndikoch Wabwino, Taunikilaninso Kumipandoko Nthawi Ilipo Ndithu, Mutha Kumalizira Mu Top Five, Infenso Zinali Momwemo, Pendapenda Sikugwa Mukudziwa Inu.

 8. ine sindikuona chifukwa chonchosela coch.bola inakati yakuchinyan ndiwizald,koma Bullets aaaah nditimu yayikulu kaya coch munali naye chifukwa ndikale.kkkkkkkk mwanya kut mpeeeeeeeeeeee

 9. No! No! No! This is a very nasty timing ever, sacking kananji & Ngonamo would mean nothing at the moment, Look at who have been re-employed, to my notion, nothing will change, you noma Executive you could have make use of logic, a bitter pill has been added here, believe me, even fisd will fail us.
  The fired were still second to none in Malawi soccer, I personally fire the Executive right now. The Executive have failed the Administration.

 10. Neba this is wrong turn apa wadupha nchiwaya kugwela pa moto Kananji mwanyika kumuchosa ntchito.
  Komanso wapanga mbiri yopweteka kwama supporter ako yomwe iziwawa kwambiri pa nkhani ya mpira.Apa wapitiliza kuitchukisa BULLETS kkkkkkkkkkkkk.
  Vuto ndiloti ma player mukugula daily kodi ma coach nthawi yosakha osewelawa ayipeza kuti?.Ma player amagulidwa mu off season kuti ma coach akhale ndimpata owanziwa ma players.Kugula ngati mukufuna kumenya CAF?????? Musova season yake ndi ino.

 11. Zakhala Bwino Tikamakonza Vuto Sitimawelenga Kuti Uyu Anatengetsa Carsbeg Cup. Ngati Pali Timu Yomwe Ili Ndi Mapuleya Abwino Nde Ndi Wanderes Koma Pakungosoweka Ukadaulo Wa Makochi. Kochi Azidziwa Kuti Uyu Ndikamuseweletsa Ndi Uyu Malo Akutiakuti, Zinthu Zikhala Bwino. Osamangolowetsela Dzina La Puleya Ayi. Mumasiya Mapuleya Achisodzela Abwino Monga; Thedi Sumani, Isaac Chair Kaliti, Jabulani Linje, Mike Kaziputa, Khumbo Nga’mbi, Peter Nselema Ndi Ena. Mutamatenga Anyamata Amenewa Mkutenganso Mavetelani Puleya Awiri Atatu, Mkuasakaniza Mukhoza Kuzaonanso Mmene Tingamachitile Bwino. Komanso Kuchotsa Makochi Okha Its Not Enough, Kuti Zinthu Zikomzeke Pakufunika Technical Pannel Ndi Exective Ipangidwenso Reform, Nkhope Zina Zichokemo Chifukwa Wina Aliyense Asamakhale Ndi Tean Yake Kapena Ma Player Ake While Timuyo Ndi Imodzi. We Need Technical Pannel And Exective That Will Give All Power To A Coarch Zinthu Zizayenda Bwino. Tikamangoluzatu Zimatiwawa.

 12. Vuto simakochi kuteam yanga koma amene amatsogolela kumbuyo kwa ma coach,komaso ma players coz its only 4 -5 players omwe they ar for noma,samafela game alimbe mtima ofuna kuwina a Osman alephela kangati? kulakwa anthu owononga mkumawadziwa mukachotsa ena kulakwa.Tonse timasapota koma sitinalandilepo or 1tambala koma kuli ena omwe akumadya ndalama,player or yaka palasa alimbe mmakakamila maudindo kulemphelaso mwamanga nyumba, makasu anuwo mkunalandila pa 16!!!? shame. Kumagula maplayer opanda tchito,tikudwala mmiba,kupeleka aziwengo.Mukutipweteketsa mutu atsogoleli adyela ku MW.

 13. Vuto simakochi kuteam yanga koma amene amatsogolela kumbuyo kwa ma coach,komaso ma players coz its only 4 -5 players omwe they ar for noma,samafela game alimbe mtima ofuna kuwina a Osman alephela kangati? kulakwa anthu owononga mkumawadziwa mukachotsa ena kulakwa.Tonse timasapota koma sitinalandilepo or 1tambala koma kuli ena omwe akumadya ndalama,player or yaka palasa alimbe mmakakamila maudindo kulemphelaso mwamanga nyumba, makasu anuwo mkunalandila pa 16!!!? shame. Kumagula maplayer opanda tchito,tikudwala mmiba,kupeleka aziwengo.Mukutipweteketsa mutu atsogoleli adyela ku MW.

 14. Abale Anga Yangokhala Kuti Teamuyi Ndiyotemberedwa Kodi Ma Coach Awawa Anali Kuti? Si Anali Ku Bullets? Kuti Aziwatenga M’mesa anaona Zintchito Zawo? Ok Ma Player Amene Akumakulizaniwa Si Ndiochokera Komweko Mumati Ndiosatha Mpira? Lero Mudziwe Izi Bullets Ndi Team Yayikulu M’malawi Muno. Uthenga Opita Kwa Ma Player Onse A Nyasa Pitilizani Kugwilizana Olo Mukumane Ndi Mavuto Otani, Ife Timakunyadirani Koooopsa.

 15. Kkkk neighbour sayamika,ma coach akuwatengawo anali komweko ndipo nawo anachosedwa chifukwa cholephera panopa akubwelera komwekonso

 16. I think these guys mabodza heve…. Wina akuti amusokonezera line up first choice … Ena akuti kamwendo sangakhale pa thabwa koma kuyamba basi…. Tiziona… Always blues legend guy

 17. Mwangofuna Kuchotsa Makochi ,Kt Uyu Amati Nebayu Apeze Chonena Chifukwa Wadya Zambiri Za Sulumba , Pano Asulumba Ndi Bench Basi ,bola Kale! Kkkk

 18. Vuto simakochi koma executive ya dyela kulowelela pena paliponse why kumasapota mutokoseko zapa geti mutokoseko zama coach mulowelelepo iiiiii lelo mwachosesa anzanu ntchito sibwinoo vuto mukuliona koma mukuli lambalala.
  Munya muona NBB tizingokupondani basi Elube nkazi wathu iwe five years without knocking at the door of NBB kwa ayaya bwanji or ku makanjila bwanji nanga mafuta ankhumba aja bwanji nanga shehe wa mu Limbe anakuthandizani kutibela Carsberg onsewa sangapango kanthuuuuuuuu neba ku Lilongwe ukabwelako ndi 2 points. Osman sali active pa za mpila nkhalamba iyi iiii how many times wakhala akubwela nkupita

 19. Tinamuuza Kananji timu yomwe ukupitayo llibe khalidwe lero ndizimenezi, Kananji akapanga lineup anthuena kuiphwasula timu lwina bwanji, kuteroko naye Jaffali Chande amuukira pompano

 20. ine ndinadziwatu kuti tikangokusendemurani muchotsa ma coach,ma player anu si akunyanyara training,dikiran muone mmene mutasendebwele,,first round ijatu tinapanga dala kt game ithe 1-1 tikanakusendani team ikanasokonekera

 21. Chigoli Chakondwani Kumwenda Chathetsa Ntchito Ya Kananji Ndi Ng’onamo.Mbali Inayi Chachititsa Kuti Anyamata Anoma Azindikile Kuti Sakuwapatsa Ma Allowance Mpaka Kuyamba Kunyanyala Training.Kkkkkkkk Koma Ndizoopsya.

 22. Zochitisa manyazi kwa ma player osakonda team yanu anoma bwanji sizikuwawani tikamalira inu amene oluza nkumasangalala ngati simufuna kumenya timakana tsiku lina ndizakutukwanani ndi amanu omwe basi ndakwiya

 23. Koma ku Nkhumba FC ndiye kuli mbuli eish. Vuto si ma coach. Anyamata anuwo asewera bwanji mpira mmimba mulibe kalikonse? Ndalama simukuwapatsa & apa mukunamizira ma coach. As far as am soccer is concerned, Eddie is the best ever. Kaya mwina Kananjiyo. Mutha anga makatani. Simunati

 24. Vuto simakochi koma technical,tikhala tikuyesa maplayer mpaka liti?muwasiye makochi agwile ntchito yawo.osawanjenjemeletsa.

 25. Firing coaches is not a solution at all.Both Yasin and Bob had their time at lali luban but failed to put noma on the map.Masenga abwerese pano ngotani.Dont make noma _a Coaches Prostitutes Club!!!!After all those glories Elia brought to noma, today this innocent man is ruthlessly dumped like a used condom.Elia _dont worry God is still in control. Amen!!!!

 26. Mayooo ine,neba wapengaa ndi kachigoli ka KK mpaka kuyinga ma coach onse. Neba waganiza bwanji?Pepa neba usatero ungolimba mtima basi.

 27. Try to sign Nigeria coaches my they can change things in manoma.kkkkkkkkkkk.ngati akulephela osewela ochokela komko.noma goats

 28. Neba zakuvuta ,waona mawanga nkhanga mpaka kutaya nkhwali?eeeeeeeee uli mmadzi ,ife makochi athu alibe problem nyasa b oyeeeeeee!!!

 29. Neba zakuvuta ,waona mawanga nkhanga mpaka kutaya nkhwali?eeeeeeeee uli mmadzi ,ife makochi athu alibe problem nyasa b oyeeeeeee!!!

 30. Bola pamenepo…..Ramadahn paja anati ndiwokenzeka kuthandiza timu ina iliyonse pano pa flamez….ngati morinho anachoka ku Chelsea kupita ku Man-u….i see this Burundi guy coming to rali lubani….

  Either way,removing the coaches is the best manoma has done so far

 31. u can’t compare ngonamo and kananji wth mourinho and LVG, Mourinho wakocha ma team akulu akulu okhaokha ma league osiyana, and kutenganso league, same to LVG, Ka ngonamo ndi kananji apanga chani chodziwika pa dziko lonse la pansi ku mbali ya mpila, oro kumbali ya zitsamba or kut ma qualification, sangafanane konse, ndiye osayelekeza kupanga compare.

  1. Koma zowona ma coachwa mmawayesera game yake imeneyi? Mwawalakwila.koma munawauza kuti ntchito zithapo before gameyi? Bola munakawachosela game ya ku dwangwa ija pls.iyiyi nonse mumaziwilatu zosatila zake.patenga zaka zingati pomwe munachinyapo NBB mu ligi.ayi ganizani mofasa.nde mukuwona ngati zinthu zisintha?

Comments are closed.