Magistrate condemns mob justice


Blantyre Mob Justice

Midima first grade magistrate Ben Chitsakamile has deplored acts of mob justice in the country saying the malpractice is a dangerous way of curbing crime.

Blantyre Mob Justice
One of the recently killed suspected thieves.

Chitsakamile was speaking on Thursday during court proceedings at Midima first grade magistrate court in Blantyre where he passed sentence to 39 year-old Lloyd Kavuluza who is a victim of mob jusice.

The magistrate sentenced the suspect to 12 months imprisonment with hard labour but the sentence was suspended to 24 months during which time he should not commit similar offences.  

Kavuluza sustained serious injuries after a mob attacked him when they caught him stealing.

“People should not take the laws into their own hands. Mob justice is a dangerous way of curbing crimes. It leads to serious injuries and death,” said Chitsakamile.

In recent months, there have been an increase in cases of mob justice in the country.

Malawians claims that the malpractice is increasing because they have lost trust in the Malawi Police Service who have failed to crackdown on some serious crimes.

According to the Police, at least 16 people have been killed in mob justice attacks in the past three months, the most reported being in Nsanje where seven suspects were attacked and set ablaze by a mob for being found in possession of human bones.

Recently, the United Nations Commission for Human Rights expressed worry over the killing of suspects and called for speedy prosecution of the culprits.

55 thoughts on “Magistrate condemns mob justice

 1. Kodi ndani amakondwa ndikubeledwa?choti mudziwe inu ma judge ndi apolice akuba ndianthu wopsa kwambili moti pamene akubwela kuzaba ngati ungapange makani pofuna kuteteza chuma chako amakupha mosakunyengelela ngati galu wachiwewe omaliza amakupasaso banyela umangomva mkazako akukuwa iyiii akulira amuchita chisembwele.tsopano chomcho ndibwino?tikati tionese chilungamo munthu tagwila kupita naye ku court mumampasa 2yrs in prison ndizoona eti chomchi umbava ungathe?

 2. Kodi ndani amakondwa ndikubeledwa?choti mudziwe inu ma judge ndi apolice akuba ndianthu wopsa kwambili moti pamene akubwela kuzaba ngati ungapange makani pofuna kuteteza chuma chako amakupha mosakunyengelela ngati galu wachiwewe omaliza amakupasaso banyela umangomva mkazako akukuwa iyiii akulira amuchita chisembwele.tsopano chomcho ndibwino?tikati tionese chilungamo munthu tagwila kupita naye ku court mumampasa 2yrs in prison ndizoona eti chomchi umbava ungathe?

 3. while we might be blaming the police on their softness on cracking down crime, the courts are to blame too. their leniency in giving punishments to serious criminals makes people resort to mob justice

 4. Inenso sundikuona chifukwa chowasiyira ndi moyo.akuba ndi zirombo…amene akuletsayo ..ize man…muzakwera yathuyi akazabwera kwanu…kutenga katundu yense popanda opikitasana naye…kukugogodani kunsanako….akazanuwo ndikuwapanga ujeni. Pompo muzasintha malingaliro oti akubanso ndi anthu

 5. Sinanga olakwawo mukawagwira, zikuoneka ktti malamulo sakugwira ntchito chifukwa sakulangidwa mokwanira ndiye mukuti anthu atani? Alanga okhatu basi

 6. stupid Human Rights activitists if I’ve spent months and loans to buy a TV screen and somebody comes armed, and snatch it away and is mob justiced you’re saying that’s not on, are you serious? Where was him when I was toiling in the jungles and where were you stupid activists to sensitize the stupid thief about importance of hardworking, you are now here talking nonsense, police sensitize people about hardworking otherwise mob justice is lasting solution sitingasekelere zopusa kuti somebody stupid andidyere thukuta manga, wina ayelekeze kubwera ku nyumba kwanga mudzanyamula.

 7. Palibe chifukwa chowasiyila ndimoyo akagwidwa aphedwe basi even atakhala mbale wanga aphedwebasi otsawasiya ufulu mpaka kuwakuba malawi siuzalemela umangotsatila zilizonse

 8. That’s why maiko achisilamu akapeza munthu wakuba am adulation manja either miyendo kotero kuti kulibe akuba
  Munthu you can left Blantyre going to lilongwe left yr shop open no one can steal.
  Tsono anthuwa kwathuko adzasiya kuba akamaona anzawo akuphedwa. Akapeza nawoni

 9. Enawa zakuba amangonvela aneba muzanva madzi sudya sima sugona olo zabwino zimakhala zoipa.

 10. mbudzi zomwe zikumva chisonidzo sidzinabeledwe munthu amamutsetsera mbudzi zonse mkhola tidziwaotcha pa braal amenewa mphoto ya uchimo ndi imfa

 11. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 12. MAlawi ZIKOMO popha mbabva zowopsyazo Zimmer zikamangidwa zimakhara masiku ochepa ku ndende .Akapezeka lphani achepeko ZIKOMO woberedwa wolira

 13. Amene simukugwirizana nazo Mudzagwirizana nazo akadzafika mnyumba mwanu . anthuwa ndioipa! Amasesa chilichonse mnyumba ngati ground .ngati iweyo wasamukapo! Inu muli ndi zibwana!!!!!!! Pomaliza kugwirilira akazako,!!! Iweyo ukuombera mmanja. Udzaziona akafika kwanu.

 14. Anthuwa ndi oipa alive chisoni!! Ineyo andithyolera nyumba Last week kutenga katundu wa ma kwacha ochuluka .amene sindingakwanitse kumpezanso kwa zaka zinanso ziwiri..Akapezeka !!!!!!! Ine ndikugwirizana nazo aotchedwe basi afe imfa yowawa.adulidwe mwendo kanako nkono kumalizira Mutu pomaliza azifa.mwina anzake akaona ayamba kulapa.mfiti anthu oipa! Ma Court athu aaaaaaah achuluka chisoni amamunvera chisoni munthu wakuba. Zaka zitatu Ku ndende!!!!! APHEDWE BASI .OSAWANYENGELERA .

 15. Vuto lomwe limakhalapo ndi loti zigawenga zoopsya zopha anzawo kapena okuba mwaupandu akamangidwa amangokhala 2 days kenaka abwerako nkumapitiriza zomwe ankachita chotero zatikwana akagwidwa ayatsidwe basi kaya kuwadula miyendo ndi manja otherwize palibe chomwe chingachitike

 16. Vuto lomwe limakhalapo ndi loti zigawenga zoopsya zopha anzawo kapena okuba mwaupandu akamangidwa amangokhala 2 days kenaka abwerako nkumapitiriza zomwe ankachita chotero zatikwana akagwidwa ayatsidwe basi kaya kuwadula miyendo ndi manja otherwize palibe chomwe chingachitike

Comments are closed.