FAM ‘suspends’ Jaffalie Chande


Jaffalie Chande

Midfielder Jaffalie Chande will have to spend his time on the sidelines until the Football Association of Malawi (FAM) determines the future of the saga involving disputed contracts at Nyasa Big Bullets which saw him switch to rivals Might Be Forward Wanderers.

Jaffalie Chande
Jaffalie Chande: To be on the sidelines.

A press statement signed by the FA’s General Secreatry, Sugzo Nyirenda states that the football body together with the Super League of Malawi (SULOM) have concluded the round table meetings regarding Chande’s disputed contract with Nyasa Big Bullets F.C.

”The two meetings (held on 5th and 12th April 2016) were aimed at finding a solution to the standoff between the two parties. However, FAM has managed to gather enough information and documents that will be passed on to the Disciplinary Committee to determine the future of this matter.”

”In the meantime, the player will wait for the determination before returning to the field of play. It is expected that the FAM’s Disciplinary Committee will meet in due course to determine the issue at hand.” part of the statement reads.

He has been involved in disputes with the Peoples team on matters of the duration of his contract at the culb

267 thoughts on “FAM ‘suspends’ Jaffalie Chande

 1. Had it bin Chande z switching Nomads to Bullets zikanatheka, u check the fate of Dedza & Wizard , simply means no + ve governing bodies that’s y we hv stupid performances even at national levels kodi chande nawenso ukung’olimbana ndi matimu opanda tsogolo . Ufumu sapasa walendi ( akulephera kukhala ndi ground matimu anji momsemuja) kumangoti afuko . Aaaah wafuko sakhala walendi.

 2. Had it bin Chande z switching Nomads to Bullets zikanatheka, u check the fate of Dedza & Wizard , simply means no + ve governing bodies that’s y we hv stupid performances even at national levels kodi chande nawenso ukung’olimbana ndi matimu opanda tsogolo . Ufumu sapasa walendi ( akulephera kukhala ndi ground matimu anji momsemuja) kumangoti afuko . Aaaah wafuko sakhala walendi.

 3. Koma butao wayankhula ngati wanzeru pa nkhai ya cande, koma ndiwe opanda nzeru, osagaiza mmene munamulangira henry kabichi? Season yooooonse mwana osamenya mpira, lero inu mwasanduka angelo akuunika?kkkkkkkkkkk komadi satana amazionesa ngati mngelo wakuunika

 4. Bullets ndi bullets basi ngakhale ena akulankhula zosamveka mkamwa monunkhamo tawaduduluza loweluka lapitali ziwiri ku duuu lero mkumalankhu zosakwana ngakhale mutamutenga chandeyo kwathu ndikukutsikitani basi osakuchitirani chisoni

 5. Chande,musiyeni,apite Ku B Forward,ndkumene,akapexe Ndalama Yogula,nyama, Watopanawo Anandolo. M,mumpase,osakwatilayo,kapena Kut,agogooo Or,fi….Sha.

 6. I wonder why Nomads behave as if they own the player.The wrangle is between Bullets & Chande.Fible-minded people accusing FAM of biasness,how?We can’t all be leaders at the same time.Nomads blame urselves 4 misleading Chande those are the consequences.Forgery is case before the court of law.A word to Chande”harakaharaka kutangulia sikufika”.

 7. chande anadya mfulumila.. plz ma player aku malawi tapita ku school muchose mamina mmutumo it seems jafali schoo
  l ndiyochepatu apa….

  1. And this tme around his performance has gone down. He won’t be Jaffalie Chande amene anthu amamuziwa uja. Kudya mfulumira!!!!

 8. Chande ndi Tambwali ndiye wakumana ndi atambwali anzake. Akanawauza chilungamo anoma kut ali ndi contract ku bullets. Komanso a noma phuma mukanafunsa kaye ku bullets ngat amkakuzani chandeyo zinali zoona.

 9. Chande ndi Tambwali ndiye wakumana ndi atambwali anzake. Akanawauza chilungamo anoma kut ali ndi contract ku bullets. Komanso a noma phuma mukanafunsa kaye ku bullets ngat amkakuzani chandeyo zinali zoona.

 10. Mercy zampila ngat siukuziziwa ndbwino kukhala chete player osiya team yake adakali ndi contract amayenela kulandila chilango bwela kuno ku RSA uzaone mene amawakhausila ma player otelo kapena maiko ena adzungu ukaone zilangoo zakezo

 11. written documents ndizimene zikupangitsa ndiye ayenera kutsata malamulo ngakhale mwendo uli wake koma contract ndiye pagona nkhani iye ankasayiniranji contract yo

 12. Vuto ndilakuti afam ndi solomu ose ndi a bullets ndipo ndi mbuzi angoleka kuyendets mpira pali chimene akuchita khani ya chande yalowa ndale munthu aliyese ali ndi ufulu wopita kumene akafuna aliyese

 13. Vuto ndilakuti afam ndi solomu ose ndi a bullets ndipo ndi mbuzi angoleka kuyendets mpira pali chimene akuchita khani ya chande yalowa ndale munthu aliyese ali ndi ufulu wopita kumene akafuna aliyese

 14. Vuto ndilakuti afam ndi solomu ose ndi a bullets ndipo ndi mbuzi angoleka kuyendets mpira pali chimene akuchita khani ya chande yalowa ndale munthu aliyese ali ndi ufulu wopita kumene akafuna aliyese

 15. Anthu ena amangopanga comment coz apeza mwayi opanga comment. Koma chifukwa chenicheni chopangira comment amakhala kuti alibe. Or chifukwa choti ndi Bullets. Chande ali ndi ufulu coz ali, or anali ku Bullets. Akanakhala kuti anali ku Noma, ndipo wapanga zimenezi, mukanalankhulabe kuti alindi ufulu??? Zisamakomele mbuzi kugunda galu. A Bullets akumukhomelera bwanji? Pachochitika chinachilichonse pali lamulo lake and I hope lamulo lofanana ndi lomweli ku Noma liliko. Alindi ufulu ochoka inde koma akuyenera kutsata lamulo. NB.Ngati zampira simumadzitsata ndibwino kungokhala chete.

 16. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life, this is what i caused myself, for allowing my fiance make sex to me unsecured without protection, although i never knew he is HIV positive. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the traditional healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS…

 17. Aaa apa ndie zangooneseratu kut awa a nyasa mitu sikugwira nawoso a Fam akumalora bwanji anthu afodya kumawapagirazochita?musiyeni mwanayo apite akuthawa kusutanawo chingabwe awasiye a china yami,sulumba osaiwala fisher

 18. a bullets nd a fam pa……….. panu mugawane mtima wa nkhidzi md kaduka siulemela nawo mzingokhala nd mimba zanuzo chande has a bright futr wether noma o kwnina kose no matter hw mtamuchingila agalu inu

 19. Khalidwe limeneli anyugwi muzalisiya liti?Player amachoka kukamenya team ina basi.koma inu ayi mumuopseze basi bwanji kodi?

 20. Chande this Chande that, who is he n what has he done to Malawi football? xul us osautsata mpirafe timangodziwa Essau Kanyenda as far as Malawi football is concerned

 21. Chande this Chande that, who is he n what has he done to Malawi football? xul us osautsata mpirafe timangodziwa Essau Kanyenda as far as Malawi football is concerned

 22. Chande this Chande that, who is he n what has he done to Malawi football? xul us osautsata mpirafe timangodziwa Essau Kanyenda as far as Malawi football is concerned

 23. Chande this Chande that, who is he n what has he done to Malawi football? xul us osautsata mpirafe timangodziwa Essau Kanyenda as far as Malawi football is concerned

 24. Zonsezi ndi awa oipa a bullets Sulumba alikwanuko bwanji nsanje player akachoka pakuti ma player siyeni a team ai koma ma surpoter ndiye ma player muziwalora kuti apite komwe akuona kuti athandizika shame

 25. Zonsezi ndi awa oipa a bullets Sulumba alikwanuko bwanji nsanje player akachoka pakuti ma player siyeni a team ai koma ma surpoter ndiye ma player muziwalora kuti apite komwe akuona kuti athandizika shame

 26. Zonsezi ndi awa oipa a bullets Sulumba alikwanuko bwanji nsanje player akachoka pakuti ma player siyeni a team ai koma ma surpoter ndiye ma player muziwalora kuti apite komwe akuona kuti athandizika shame

 27. Zonsezi ndi awa oipa a bullets Sulumba alikwanuko bwanji nsanje player akachoka pakuti ma player siyeni a team ai koma ma surpoter ndiye ma player muziwalora kuti apite komwe akuona kuti athandizika shame

 28. what i new iz bullets simaluza mlandu akuzitukumur ngat akachitako zinthuzinthu ku behind foward ife tili ndi choliza wana chi sulumba man of ze moment!!!!!!!!!!!

 29. what i new iz bullets simaluza mlandu akuzitukumur ngat akachitako zinthuzinthu ku behind foward ife tili ndi choliza wana chi sulumba man of ze moment!!!!!!!!!!!

 30. what i new iz bullets simaluza mlandu akuzitukumur ngat akachitako zinthuzinthu ku behind foward ife tili ndi choliza wana chi sulumba man of ze moment!!!!!!!!!!!

 31. what i new iz bullets simaluza mlandu akuzitukumur ngat akachitako zinthuzinthu ku behind foward ife tili ndi choliza wana chi sulumba man of ze moment!!!!!!!!!!!

 32. JAFALI CHANDE sanamupange suspend ayi. Chomwe chachitika panopa ndichakuti nkhani yonse asiya mmanja mwa disciplinary committee kuti azapereke chigamulo kuti olakwa ndindani pakati pa Chande ndi Bullets. panopa Fam komanso SULOM amva kale umboni kuchokera mbali zonse ndipo Chande komanso Bullets azidkilira chigamulochi. MALAWI 24 muziwauza anthu zoona.

 33. Ngakhale Zonda zidali choncho from Epac koma sitinaone zotelozi.Chande mtima wake uli ku Noma basi leave him apite

 34. Zampila izi nanunso aFAM Vuto loopa pochita zinthu tagamulani nkhani yosavuta iyi mukufufuza zichani? Nkhani simaumboni basi,pepala ya bullets,pepala la Sulom,pepala la Chande pamapepala atatuwa chigamulo chilipo zakula ndi ndale et?

 35. Zampila izi nanunso aFAM Vuto loopa pochita zinthu tagamulani nkhani yosavuta iyi mukufufuza zichani? Nkhani simaumboni basi,pepala ya bullets,pepala la Sulom,pepala la Chande pamapepala atatuwa chigamulo chilipo zakula ndi ndale et?

 36. Timanena kut no player is bigger than a Club,ndie achande apa mwaziona2 ndikukonda dollar kwanuko2.ndipo amene mukut NBB ikukamira chande ndinu makape coz ife we are only following constituion not Chande’s Shit

 37. a malawi vuto lili pati poti iye wasankha kopita munakango mulangiza kapena kukonza pamene iye walakwisa muziwe kuti iye pamenepo ntchere wake waima zambiri zamoyo wake zaima mukumuphela ufulu amalawi sitizapita patali ndi mpira

 38. BB musiyeni chande acite cifuniro chake posankha team yomwe akufuna kumtima kwake.kodi mukufuna kuti acite dzimbili?adzakubayanibe a bb chande,ndatha kuona kuti mukucita naye mantha chande.

 39. Chigamulo ncholakwika,coz akuyenera kumumvetsa player yo than kungopeleka chiganizo chosaenera.Chinthu china nchoti ngati angamuuze kuti Chande asasewere mpira nde kuti akuononga carrier yake coz akanakhala mmodzi mwa maplayer omwe angazathandize kukonza team yadziko lamalawi

 40. Bullets should let the player to choose his destination or they should give him a K3.5 million contract, that’s the best solution rather keep him on bay and mind you Jaffalie Chande is a good player and he needs to be respected.

 41. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 42. Umbuli umaonadi wamnzako what is suspension? The way I know suspension itha kupelekedwa even kwa magpies, player akachita accumulate 2 yellow cards amati has been suspended for next game so chande has been suspended until chigamulo so Malawi24 is right omwe simukunvesa ndinu anoma muli mu denial stage kulikonse malamulo amayenera kusatilidwa akananena kuti ndikufuna kuchoka but this is my contract anoma ndikupanga zigula player ikanakhala nkhani ina koma akufuna zachinyengo no vomelezani procedure has to be followed

 43. Guys musamupusitse mtola nkhani apa wafotokoza momveka bwino kuti “suspend”inu mukufuna anenebwanji?inuyo ndi amene simukudziwa kutanthauza bwino,angakhale game imodzi… thats suspend….mudzimvetsa zinthu..

 44. ine i wonder ndi anthu amene mukunena kuti alakwisa polemba kuti suspended,,,kodi mesa akati suspesion ndiyekuti munthu waimisidwa pachithu chimene amapanga,,ndiye chalakwikapo ndichani apapa poti jafalie chande waimisidwa kaye kuti asasewele mpila until sogolo lankhani yake litaoneka pothela,,,anthu enanu munangozolowela kunyazisa azanu basi,,,

 45. malawi football adminstrators they need man to man initiative by fifa

 46. Inu a malawi 54 ndinu abodza hev.kumamva zimene a FAM anena.remember,tate wa bodza ndi satana,so you belong to the devil.Pali phindu lanji mukanena bodza?with ur lies u turnish the good image of malawi.we have ……..news 24 not stupid people like you.

 47. Chande ndi machine chonde FAM musafwifwise mpaseni mpata woxisakhira tmu kaya nyelele /silver/fisd/chilumbaballacks

 48. adonkey can carry aworrior to the battle field,but it can`t fight! IT IS FINE TO GO TO JAIL FOR A GOOD CAUSE!leave Chande alone

 49. A very lovely fellow, a good friend and ya, its his decision to move on with his life. I am a bullets fan but I do respect his decision. FAM is being run by pure idiots. Mpira pa malawi ndi mbola anyway and Jafa says this now and again. He just wanted a good offer to support his basic needs that’s all and if any foreign team is interested in his services I assure u that he’ll go for sure.

 50. mukupha tsogolo la mwanatu apa, why should he wait again when the committee mate already? they know the verdict

 51. NKHANI YOMWEYI MAWA AZATIUZA KUTI ‘CHANDE’S DONE FINALISED’ KOMA content yake yomweyi yoti akukambilana.

 52. The problem is that FAM n superleague officials r corrupt.Most of these pple r of the view that chande shud go back to bullets fc.A development that is against player’s intensions.

 53. Chande pansasa sayipisila pita ukakwilire zoyipazo nkukapitiliza bwino ulendo wako.Ntchenthe imati patsogolo mpabwino pambuyo mpabwinonso.

 54. aaaaaaasaaa ali ndi ufulu koma mumati azipanga zachisawawa? ma player atati azipanga phada wapangayu zingamayende? we need professionalism in football!

  1. Gaba was proffessional enough! He signed a pre-contract with another team in the last 6 months of his contract. His parent club was not amused but according to FIFA statutes Gaba was right. This is also what Steven Gerrald of Liverpool did by signing a pre-contract with a LA Galaxy when he remained with 6 months on his Liverpool contract.

  2. Gaba was proffessional enough! He signed a pre-contract with another team in the last 6 months of his contract. His parent club was not amused but according to FIFA statutes Gaba was right. This is also what Steven Gerrald of Liverpool did by signing a pre-contract with a LA Galaxy when he remained with 6 months on his Liverpool contract.

 55. Eishiiii atolankhani enawa koma,,,,sukulu yake ya kuti mudakaphunzirako za ukazitapewo??? heshiiiiiiii mwati suspend?? kwanthawi yaitari bwa??? nkhani walemba wekha koma kukanika kuimvetsetsa iwe iwe aaaaaaa ndikadakhala bwana wako lero utapachira ndithuuuuu!!!!!!

 56. koma bungwe la fam ndi sulom aziziwa kut popanda player iwonso alibe ntchito akumakhutisa mimba zawo pamene player akuvutika mmasuleni chande palibe nkhani apa!

 57. Malawi24 is a source of maboza okhaokha palibeso angakhulupilire inu ndpo ife tikuziwa kt khani itha lero czamabodza zanuzo

 58. Meaning FAM and Sulom has failled to resolve the matta as soon as possible?;
  This is not abig problem which two soccer bodys cant find solution,, be serious gyz anthu aphanatu awa .. Am crying for my friend Jaffalie ur losing direction with ur Future just bcoz of Money that cant even buy ur perfect future

 59. Jaffalie Neymar Chande should go back to bullets not to play but sit down with the team tell them he wants out. He must tell them what is in his mind not through the papers. What he must know is when leaving a parent house you must get the blessings olo atakulakwila bwanji.
  WHY am I saying this? Tony chitsulo deleted himself on the soccer scene after he made a mistake like this one leaving silver strikers mwachipongwe. So Chande must sit down with Bullets get the paperwork done and join the Nomads. Koma kuti pakhale kukokana chonchi believe me someone will press the wrong button and the memory card will be deleted.

  I feared this for Jaffalie Neymar Chande any way let’s wait and c. I will stick to my statement above. Chande must sit down with Bullets

  1. ndi choncho kumene Mr.. Komanso awa a Nomawa akumbukire bwino bwino kuti Chande pobwera ku Bullets sikuti anangobwera ulele ndiku kumbukira ine Epac nso inavuta kwa basi! A Bullets anamugula movutikira kwambiri chifukwa nthawi imene ija chuma chimavuta cz kunalibe sponsor!! Ndiye chinthu wachipeza movutikira wina wake angobwera mkuzakulanda ulere basi! Ngati ali Sulumba akuwapweteka anomawo ndi bwino iwowo azikangana ndi a Blantyre United chifukwa ndi amene anamugulisa ku Bullets nthawi ya loan yake itatha ku wanderers ko!!

  2. Chanzeru palibe wait 4judgement coz mudzakhumudwa olakwa muli inu. A person z innocent until proven guilty. If ppo say u’r foolz are they wrong kkkkkk

  3. Brother, this is the kind of thinking I have always wanted to align myself to. Well articullated advice that everyone should have been preaching regardless of their inclination. Keep the good work up !!

  4. Ofcouse sanagamule koma ngat akhale kanthawi kudikira chigamulo it’s a disadvantage to him coz amzake akhala akukankha chikopa kuyambira saturday’li. Ndie mumadziwanso akat “until further notice”, ndi chaka cha mawa chimenecho

  5. Ofcouse sanagamule koma ngat akhale kanthawi kudikira chigamulo it’s a disadvantage to him coz amzake akhala akukankha chikopa kuyambira saturday’li. Ndie mumadziwanso akat “until further notice”, ndi chaka cha mawa chimenecho

  6. sanagamule kuti ndi olakwa koma ngati ampanga suspend zikusonyeza kuti ali ndi mulandu pena-pake…iye ngati sakuifuna Nyasa akanatsata malamuro moyenera sizomwe anapangazi ayi

 60. Nthawi.zina a Malawi 24 tazionani kuti mutu ndinkhani zikugwirizana..Apa mukuona kuti zimene muķukamba ndimutu zukugwirizana.???????Maedita koma aliko kumeneku????

  1. Mbuli inu that z why u failed 2secure certificate ya club licencing. Inu koma nsanje basi the whole team kulimbana ndi 1player kkkk shame on you big fools.

  2. Cassm ndiwe chitsilu ,mwapindula chan ndi club linces? Bullets is far better than chande kunalitu gaba amamenya anapta maule anatha? Norma takumenyana without chande we dnt depend on one player big fool,team work,jafali atha amene uja mark my words.

  1. Does he beg u? Mwinaso barman ndionjoya than you lyf doesnt end in football. He haz a car now koma zakuwawani. Shame

 61. immmmh Malawi 24 tamvesesani zinthu,, akuti zokambilana zonse zantheka ndipo maumboni apezeka ndie podikila chigamulo iye(Jaffelie Chande) adikile asamenye mpaka atapeleka chingamulo,, not suspended as wat u said on headline

  1. @chikutumbwe ngati banjalo munangotola munsewu opand dongosolo its okey,koma ngati lili lovomerezeka mumayenera divorce kaya katundu kugawana bwinobwino or else mamuna atha kupanga zoti usazakwatiwenso mwina sukuziwa

  2. Jonathan Kaipa Kachilambe Chikutumbwe Waku CZ we do not condone sexist, demeaning comments. We will delete your comments unless you edit them and debate with dignity!

  3. @malawi24 you may proceed to delete my comments if you feel like they are sexists,i don’t see problem with them ,you may even proceed to remove me from your page,much obliged.

  4. Mercy am sorry for all the for all the bad comments thrown at you..But i jus want to let you know that chilichonse chimakhala ndi malamulo and no player is allowed to do what Jafalie did,ngati contract yatsala nd 6 months umaloledwa kumakambirana ndi team ina and you can sign a pre contract not real contact but if leave your team ndikupita ku team ina uli ndi contract ku team yako yakale pamenepo waphwanya lamulo and team yomwe wapitayo yalakwanso,imalandira chilango….monga ndanenera ndikupepesa kaamba ka mayankhulidwe ena osakhala bwino omwe achitika apa

  5. Palibe zimenezo zomunyoza Mwaliyu khaya kuphikira,kupereka Mwendo kwa Amuna ake inu Zisakukhuzeni. nkhani ndi ngamo baasi Wathoka ngamo mukuwonjeza kumukhomelela Mwanayu.iye Sakufuna kusewera team yanuyo Musiyeni Awone Zina.

  6. I don’t see any problem with Jonathan’s comment #Mr_Malawi24 u just need to understand the meaning, its a straight talk nothing like sexists.

  7. Chande phuma ndi agent wakoyo siwunawone Sulumba akugagada timu iyo.Lamulo basi lisatidwe uzingokhala kaye wamva chande anzako akupita cha apo.Iwe ukukangana ndi Malawi 24 ndiwe wa Noma eti ?bwino ungafe mozikhwezatu zampira iz

 62. Anaonjeza kwambiri kudzitukumula,kodi amaganiza kuti basi angopita kukuyamba kusewera ngati alibe contract nd Nyasa Bullets koma ya ichi chakoma icho chakoma wagwa nawo chagada kkkkkkk.

Comments are closed.