Bullets want justice in Chande contract disputes


Jaffali Chande

Nyasa Big Bullets General Secretary Kelvin Moyo has called on Football Association of Malawi (FAM) and Super League of Malawi (SULOM) to intervene in Jaffali Chande’s proposed move to Mighty Be Forward Wanderers.

Jaffali Chande
Jaffali Chande fueling rows.

Bullets, FAM, SULOM and Wanderers are in a tug of war over Chande’s controversial transfer to Nomads as SULOM, FAM and Wanderers are all saying the player is a free agent while the people’s team are insisting that the player is under contract with them until August.

Bullets now want Wanderers to buy out the remaining months of the contract for K800,000.

Speaking with a local media house, Moyo stressed that justice must prevail from all angles of the story.

“Justice must always prevail on everything. We submitted the contract papers to SULOM and FAM and today we are told that Chande is a free agent, what do they want us to do?” he queried

“We know that there is a reason why they are hiding the contracts documents from us, but they are not punishing us, instead they are punishing the player because as Bullets we will not sit down and allow Chande to play for Wanderers before his contract expires,” he added.

154 thoughts on “Bullets want justice in Chande contract disputes

 1. The truth is with Chande, he has contractual papers of which BB does not have so FAM and SULOM act professionally by not being interested parties on this matter. Last season, u advised all players to have a contract in order to play in the league. Jangale pull up your socks its ur office which is messing things. Clear Chande basing on his papers and be serious in order to a achieve our goal of professionalizing our league.

 2. Listen ladies and gentles,Jafali Chande signed an eighteen months contract in August 2014 to Feb 2016 which means chande is a free agent.Chande himself has produced his original contractual papers.Kondi yesternight on Galaxy radio said this,”In 2014 Chande demanded one million from Bullets camp,bullets was unable to give out that huge amount of money,instead Kondi gave out half million kwacha from his pocket for 18 months”, now this time around Chande demanded 3 million and Bullets failed too as usual,the battle is on contractual papers of Chande and Bullets as well as from FAM and SULOM.Chande is a hero,bcoz he knows football is money,i applaud you Jafali,osamagona tulo,kufela timu yayikulu koma no dollar.Mufunse Ganizani Njoka Malunga.

 3. Listen ladies and gentles,Jafali Chande signed an eighteen months contract in August 2014 to Feb 2016 which means chande is a free agent.Chande himself has produced his original contractual papers.Kondi yesternight on Galaxy radio said this,”In 2014 Chande demanded one million from Bullets camp,bullets was unable to give out that huge amount of money,instead Kondi gave out half million kwacha from his pocket for 18 months”, now this time around Chande demanded 3 million and Bullets failed too as usual,the battle is on contractual papers of Chande and Bullets as well as from FAM and SULOM.Chande is a hero,bcoz he knows football is money,i applaud you Jafali,osamagona tulo,kufela timu yayikulu koma no dollar.Mufunse Ganizani Njoka Malunga.

 4. Listen ladies and gentles,Jafali Chande signed an eighteen months contract in August 2014 to Feb 2016 which means chande is a free agent.Chande himself has produced his original contractual papers.Kondi yesternight on Galaxy radio said this,”In 2014 Chande demanded one million from Bullets camp,bullets was unable to give out that huge amount of money,instead Kondi gave out half million kwacha from his pocket for 18 months”, now this time around Chande demanded 3 million and Bullets failed too as usual,the battle is on contractual papers of Chande and Bullets as well as from FAM and SULOM.Chande is a hero,bcoz he knows football is money,i applaud you Jafali,osamagona tulo,kufela timu yayikulu koma no dollar.Mufunse Ganizani Njoka Malunga.

 5. Listen ladies and gentles,Jafali Chande signed an eighteen months contract in August 2014 to Feb 2016 which means chande is a free agent.Chande himself has produced his original contractual papers.Kondi yesternight on Galaxy radio said this,”In 2014 Chande demanded one million from Bullets camp,bullets was unable to give out that huge amount of money,instead Kondi gave out half million kwacha from his pocket for 18 months”, now this time around Chande demanded 3 million and Bullets failed too as usual,the battle is on contractual papers of Chande and Bullets as well as from FAM and SULOM.Chande is a hero,bcoz he knows football is money,i applaud you Jafali,osamagona tulo,kufela timu yayikulu koma no dollar.Mufunse Ganizani Njoka Malunga.

 6. MUZIONETSETSA NKHANI ZANU NGATI ZILI ZOLONDOLA ZOTINAMIZA IFE AYI…CHANDE CONTRACT YAKE INALI YOTHA CHAKA CHINO MWEZ WA {FEB}Osat za august zikunenedwazo mmmm..BE HONEST

 7. MUZIONETSETSA NKHANI ZANU NGATI ZILI ZOLONDOLA ZOTINAMIZA IFE AYI…CHANDE CONTRACT YAKE INALI YOTHA CHAKA CHINO MWEZ WA {FEB}Osat za august zikunenedwazo mmmm..BE HONEST

 8. Amalawi m’pira umativuta,tizingotukwanana zamkutuzi koma NationalTeam umakhaula popanda mpikisano omwe imachitako bwino.Kumaluza Chandeyo alikomkuno ngakhale akutiwawitsa mutu.

  1. No development in Nkhaza let him go, Youth what will change if Chande is punshed? This is not a permanent property. Sulumba was at Blantyre United he went on to Wanderes today is at Bullets. If there are people at Bullets Chande will do what is best or him

  2. Punishment will come when he will not play for 5 months ,remember what happened to Aaron Nyasulu. Sulumba was a loan material at Nomads he wasn’t their player Chande was a Bullets property

 9. BB ndikawawa,Just think peoplez team,Ndiye Chande ndiwachani musiye akathele komweko we hav alot of prayez at bb,Noma ndi akazi athu ndi CHANDEYO onse tiziwakwatira limodzi,alira chaka chino akatenga mzungu amene amatolera mipira ikatuluka akuti ndi player akwatidwa onsewo..2016 BB i lamulaso mufune musafune.

 10. Chande will never be Chande by himself he is Chande coz of 10 other players. Now i think if he goes to MIGTHY and there are no other guys to help him, he will be out of value. Just let him choose where he wants to go

 11. Vuto liri ndi atolankhani anthu amangova koma umboni weniweni alibe.Chande chilungamo akuziwa yekha ndiponso a BB chilungamo akuchiziwa okha.Chomwe iee tikufuna ndi mpira osati zanuzo

 12. A BB tangomusiyani apite basi Chande.Ng’we ng’we ng’we chifukwa wapita ku Noma?Nkhakamila bwanji chonchi,munthu akukukanani koma inu ka ka ka!Umbuli eeti?

 13. Koditu umboni ndiyekha coz iyeyo ali ndi copy kondi ali kuti akayankhe. Kodi contract amasayina kawiri? Fbb kupereka contract ya fake wt a game.

 14. Koditu umboni ndiyekha coz iyeyo ali ndi copy kondi ali kuti akayankhe. Kodi contract amasayina kawiri? Fbb kupereka contract ya fake wt a game.

  1. Koma nawe iwe. Sungaganize kuti Chance ndi yemwe Wa apatsa a Noma contract yo.

 15. Chimene akufuna A NBB ndi chilungamo osati kufuna chande ai inu awandazi mukuzowera chitidwe oipa podalira wota galu zangayo

 16. nkhani imeneyi yatikwana kod CHANDE waziwika liti? kupanda #NYASABULLETS munakaziwa kut tilindi CHANDE? #NYASABULLETS ndi timu yayikulu dziko Muno ndi timu yokha idapita ku Europe kumangalanda just to remind you ma newcomers nyarere manoma itapitako ku overseas? nanga ilindi zikho zingt ngt mumazitsata?

  1. A Shad Nanu Mungokhala Ngt Simumazisata Bwanji,inu Munamvapo Kt Contract Ikukatha Mu August Chonsecho Super League Imakhala Ili Pa Climax?

 17. Km guez mukuziwa kut chande wanuyo kaya ndi wa BB or NOMA kaya this tym alibe team km mukumpasa matama?? Kd iyeyo mukufuna akhale ngati ndani ku malawiko?? Any page ungaiwone nkhani yake Chande,Chande,Chande…wabwera liti mu super league kuti mpaka asowese mtendere malawi yonseyo? Kd ku BB ko tym yomwe kunalibe Chande simumatenga zikho even ku NOMA ko simumatenga zikho?? Mukuononga nthawi komaso ndalama coz 1 player km simukuziwa kut mufoora ma player enawo,,eish,,tatopa ndi nkhani inemeyi

 18. mmmmmmmmmm m’bale wanga #ganert kamtima kenako mukumufuna mwanayu maboza apa ai.muziwe lero kut inu a bb mukangozayerekeza kutengera nkhani yanu ku fam bas muzaziwe kut chathu palibepo apa kkkkkkkkkkkk musova mukanayalukaditu naye mwana ameneyu kkkkkkkkkk

 19. ngati ikusowa contract paper kulibwanji ndalama zapageti? musatinamizepotu apa kumeneku mkupititsa mpira pasi tizingolimbana chfukwa cha inu afam ndi sulom simuyendetsa z2 mwadongosolo lenileni

 20. Point of correction Malawi24, the one in need of justice is the player himself not Bullets. Let the truth speak for it self.

 21. Afam ndi Asulom mwasowesa dala contract ya Dyafali cholinga apite waulele ku Noma mutanamizana ndi Water Wamilandu mwagwa nayo ife yathu ndiimeneyo ng’oooo! Maule woyeeeeeeeeeee!

 22. Can You Remind Me how much Bullets paid Epac for Chande? And I remember GS wa Epac anachita ku sangalala kunena kuti if all big teams were lyk dat bwezi zili appreciating how fair business did with them on chande

  And tell me how wd Bullets buy a player n leave th player unattached? And ma fanz ena ua saying just leave him ….Noh..Bullets shd try as much as possible to come out with sthng out of this because they have got a strong case

  And even looking at Wanderers on how they bought Chande ….They did some 2003 business there and they must pay for this sin ..just buying Chande as a reply for Sulumba transfer in dat way with no proper clearances was inconsiderate for th Lali Lubani Club

  Lastly Fam and Sulom clear ua house b4 going to these clubs komwe mwasokonezera zinthu ranging from ma appointment amene a ma coach omwe nd osakhala bho and nkhani ya contract mu malimbikisa ndinu Ngatidi copy ya Contract yasowa please come out clear on this current issue just tell whether Chande indeed had contract with Bullets
  and Bullets lose case closed

  1. Akulu mpila simuutsatatu apa , n khani sikukakamila ayi koma malamulo a fifa samalola kut munthu akhale ndi ma contract awilili ina isanathe, komanso Chande sakumenyanso team ina iliyonse mpaka contract yake ithe, ngat anoma akufuna kut iye asewere panopa akuyenela kumugula bas, ngat sizitelo bas Chande sakumenyanso mpila ku NBB atangokhala player wa NBB wadzinalokha ,mwina wanvesesatu apa et.

 23. Mpase mwai azipeter musamuchukise ngati Malawi yose alipo yekha akanakhala oziwa bwezi atapita Ku matrayo kunja kunali agaba Ali kuti musiyeni ayenda mpaka mzungu wa Ku Japan akudabwa kuti ine sakundikhukupilila?

 24. we have the computers to keep soft copy of a contract.the question of missing of a hard copy does not hold all this is football politics and wonderous should not be involved in the discussions.

 25. Chilungamo chidziwike pa malawi footbal afarm osamagona kumeneko copy Yachande isowa bwanji ku farm..NBB SIKUNAMA IWOWA NDAMENE AKUDZIWA ZOWONA ZAKE MWANAYU NDIWAWO

 26. wonderous can not have a copy of contract from a prayer of another team. where are players agent ? Do the players sighn contracts without a lawyer” go back to drawing board .Fam was not supposed to call for a meeting but make a ruling based on submissions from Bullets and the player.

 27. Koma nkhani imeneyi idzatha anthu akuba awa a FBB ngati amaba ndalama zawo angalephele kukaba ku FAM? CHECK.Koma ife tikuti Nomaaa moto kuti buuuuuu

 28. Anoma mwayitenga kuti copy ya coctract ya chande ndiye mumamusayinitsa bwanji mukudziwa. chilungamo chake chioneka NBB Maule kuti moto buuuuuuuuuuuuu

  1. Noma siidamupatse Chande pepala la Bullets ayi, iye Chande pepalalo ndilomwe bullets idamupatsa atasaina contract yake, komanso ku Fam kumbuyoku samalandila ma contract coz system imeneyo inunso mukudziwa kuti yayambika chaka chomwe chino. Billy Tewesa anapeleka contract yabodza pomwe Chande wapeleka copy ya Original

 29. Nde wina akapita kukhothi muziti za mpira sapita ku khothi chinyengo mukuchiyamba nokha

 30. A Levie Mumafuna kuonetsa ngati mpira mumautsata koma ayiso muliso ndimtunda kuti muzitsate bwino .This year team ya bullets yapeleka ma contract ya tsopano kutengera kuti ali ndi ndalama zochuulukirapo. izi sizachilendo ayi mngakhale ma team odziwikaso nthawi zina zimatengera ntchito yomwe player akugwira mu teamyo..ndiye sikuti kupatsidwa contract ina zikusonyeza kuti yakale yatha ayi.naye chande sadanenepo kuti contract yake inatha ayi koma zinthu zangulowa chiptwilikiti akulu. osalalata msanga mungadzapuse mawa lino. tonse tidikire sooner or later chilungamo chidziwika. za Mpira izi kkkkkk

 31. Bullets,FAM,SULOM & Chande mwatikwana ndi nkhani yanuyo, kodi a chande munawapasa ngilimbo yanji a bullets yoti mpaka ku panga fotokope contruct ya zakha 3?

 32. Nde mulilira chan ngt chande asali kanthu? nde bwenz akufuna kuthetsa nbb kuli kumulira? kulani km ndizampira izi playr amabwra amapita nanga inu bwanji aaaaa km guyz

 33. Copy ya contract yasowa bwanji ku FAM????….??? Ndiye kuti ena amagwirizana ndi Bullets ayisowetsa kut a FAM adzasowe mboni… Bullets yaenda pansi pamenepo. Nchifukwa chake a Bullets alimba mtima kuti aonetse ma copy a contract ya Chande ndi iwowo

 34. Ndiye zitha bwanji poti madzi achita kale katondo,nga sipalowa njoka kodi?.Ine nyelele zapumula kuluma-luma ankhwele ndipo tiwonana masiku akubwelawa,GO WONDERES DE NOMARDS FOWARD -FOWARD

 35. Mbuyo mwabwino mtsogolo mwabwino, konza kapansi kuti ka mmwamba katsike,usatukane apansi sukuziwa mmwamba ukukweramo muli bwanji.

 36. Ngat Chande anali ndi contract bwanj amafuna kumusainisa contract ina yet inayo ikanali ndi 2yrs kut ithe? Izi zikungoonesa kut mpila kwathu kuno tikadali nawo kutali n zoyenera kupanga sitikuziwa.anthu amapanga terminate contract n kumupasa clearance player.y a Malawi?

  1. Christiano Ronaldo ankafuna kuchoka ku Madrid contract isanathe adasayinira inanso thats wy ali konko timati extension of contract kwathu kuno chifukwa chosowa ndalama nchifukwa chake timasayina contract itatha

  2. Even Ozil contract yake ku Arsenal izatha 2018 koma panopa iz in talks wth Arsenal for an extention nde inu mukuti bwanji?………..

  3. only thse who follow Malawian fotbal wil agree wth me… kwathu kuno player samasaina contract ina atatsala ndi chaka or two to his current contract… team are alwys afraid to lose mor thts why ma contract amakhala a yr or two basi

  4. Koma Kwathu kuno Sizidacitikepo Ndie Musamupangile Cande Ayi 500,000 Munthu Sungasewele 3years Mu Club Ayi Ndie Wakulutsani Madzulo, Mr Kondie Msungamatu!!

  5. Amene mukufunsa mafunso oti ‘ngati anali ndi contract ndichifukwa chani amafuna kumusainitsa ina ali ndi contract kale’ I bet zampira simudzitsata ndipo musiire aini ake zimenezi. Player amatha kusaina contract ina ngakhale yakaleyo isanathe malingana ndim’mene club-yo ikuonera kapena kuti m’mene ikufunira ma-service a-player-yo.

 37. Why cant Bullets let this player go? Bullets inalipo ….ilipo….idzakhalapo the next 200 yrs……..its not lyk bullets will cease to exist if they let him go……. #phokoso

  1. Look at how many contracts are out. Wina akuti yotha this year wina akuti ya 5 yrs FAM I kuti contract yasowa aaaaaaah zikuchititsa manyazi

  2. Winau ndi umbuli chabe playr ali ngt mame aaa abb bwanji kutichitsa manyazi ifetu timat ngt pali team mmalawi muno yomwe mwina ingamapange zachikulu inu abb kmnso noma km inuyo inu abb nu aaa ndalema nanu

 38. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 39. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 40. inu muksmba zambuyo bwanj nkhani ndiyot contract yomwe wakaonetsa chande dzulo ku fam yasiyana ndi contract yomwe a bullets ali nayo coz ya chande inapanga expire mu feb pomwe ya bullets akut ipanga exp next year mu augst zomwe zapangisa a FAM kunena kut apeleka chigamulo chawo lachiwiri next week cholinga chot afutse kumbari ya kondi sungama and forty coz ndi omwe anasaina contract ya chande

 41. MAULE OSAFOOKA, CHILUNGAMO NCHOVUTA KUCHIBITSA. Zaziwika kuti contract yomwe Chande anakapereka ku FAM ndiyachinyengo. Izi zaziwika pomwe akulu akulu a bullets apanga kauniuni PA ma contracts omwe anapelekedwa mu chaka cha 2014 ndipo ma copies ena onse akufanana ndi contract yomwe bullets inakapeleka ku FAM pomwe copy yomwe ili ndi Chande ikuonetsa kuti ma pepala ake ndi a 2015-16. “Achina 40 asaina zulo contract ndipo ikusiyana ndi ena onse a 2014 omwe anasaina anyamata ena, Tilinawo achina nzonda zikufanana ndiyomwe tatura ife” watero Stone Mwamadi. Nde asaone ngati ku Bullets kuli anthu osazindikira.

  1. anasayina limodzi ndi Manyenje ndiye the mas jst check for Manyenje one Bullets we will believe me ngati achina msungama apatsidwa ndalama kuti asayine kachikena pali ma prayer ambili omwe anasayina 2014 akasintheso watch out achina fote

 42. Apa zikuonekeratu kuti popanda Chande Chingambwe F C singachite bwino. kodi mumaona ngati maplayer mumatenga ku matimu ena aja eni ake zimawasangalasa moto umapita kwasala ntchire mwamva asasamba inu

Comments are closed.