Black Flame unites artists in a tribute to Grace Chinga

Advertisement
Grace Chinga

The best thing about being an artist is that when you die, you leave footprints through your work. As good as Grace Chinga was, and dying as she was about to release new music, people should anticipate for the biggest scramble for songs as far as Malawi gospel music is concerned. The moment the songs will be out they will be the talk of the town. The CDs and the online uploads will be hunted down by people who would love to have a feel of their fallen gospel songbird.

The songs were being recorded and produced by Khathwa Aligiza of Alimoso Studios. This man has been in music production for years. It is no wonder that Grace Chinga trusted him to have a touch on her album after a six year absence. Khathwa right now is one of the most privileged people in Malawi. He is one of the very few who have had a full idea of the new songs.

But for those who are losing heart over their wait for the songs, do not worry. Here is a clue to the new songs. In the trending tribute to Grace Chinga, the ‘Ndulu’ remix, which was sung by a host of gospel artists, there is a path that somehow leads you into what to expect from the upcoming songs.

In the song, the beat was originally done for her song to be found in the albums she announced before her death. The opening female voice is that of Grace Chinga.

From the few lyrics that Khathwa allowed to be part of the tribute song, Grace Chinga is telling a story of a person going through bitter experiences; a woman who is being ridiculed because she is not married and childless. Other married women are not allowing her to be near them for fear of her snatching their husbands. They are looking at her as cursed. And the whole experience of not being loved is bitter for her, as it can feel if one bites the Pancreas (Ndulu). It will definitely be bitter. The guess can be that in the following verses, Grace Chinga talked of other issues, all relating to someone feeling the bitterness of life.

Grace Chinga
Chinga still being mourned.

‘Ndulu’: The choice of the word was perfect as far as the situation being sung about is concerned. That was what Grace Chinga was good at: She always came up with new kind of expressions, not common in other gospel songs. Aside the message, the beat itself was done well. It is soulful, and it went on well with the message in it.

No wonder it was the choice for the tribute song. Grace Chinga was an expert at expressing the daily experiences people go through. Three years ago, I overhead one woman telling another that what Grace Chinga sung in her ‘Thandizo Langa’ song happened to her: Being falsely arrested by the Police.  Then in turn the same Police escorting her home using their car after finding her innocent. In ‘Ndulu’, the experience will be the same for certain unmarried and childless young ladies.

Despite being absent with new songs for six years, she still had it. The song tells that story. She was still the best at what she was known for. As the songs will be coming out, we should expect one of the difficult-to-handle demands for music. With her last single ‘N’dzaulura’ breaking the Malawi music download records with now close to one hundred and thirty thousand, it has just set the pace for what is about to happen soon.

About the writer: Wonderful Mkhutche is an author, a political scientist and manuscript editor and developer.

 

Advertisement

136 Comments

 1. Mama Grace u dd ur part… Pempho lathu ndiloti Yehove akuchitireni chifundo. Za imfa yanu sister akudziwa ndi namalenga. Mukause mu mtendele. Wil always mic u

 2. kodi inu wayamba kumwalila ndi iye yekhayu mose mwayambila muja panopo Fb ikuchita kubowa nkhani yomweyomweyo kumangobweleza tamusiyani mwana waweni akapume abale nde kodi achimalewo adzingova zimenezi atothola bwanji nanga chonde pezani ina iyi yatha

 3. Muchimwapo apaa,,,,,tangolapani Ambuye anakali pa mpando wachisomo okhululukira anthu,i mean repent before it is too late

 4. Nthawi yanga imangodikila,kuti ndimalize ntchito yanga, yomwe mulungu anandituma kuti ndigwileee.Abale ntchito yosiya wina,ndiyovuta kuti wina amalize,poti masomphenya amakhala osiyana.Nsambi chaabeee……….eish Grace keep on resting in peace. ……

 5. zochitika mmoyo mwanga zabwino pena nzoipa.. pot opusa ndiyemwe mbili yake yaipisidwa.. lelo lino ndiwoyela poti zako zabisika iwee.. dzudzuleni mwachikondi osati mondiweluza.. musanandisonye ndi chala mu fuse kwa chauta iwee… mundisungile moyo mundisungile kolona… wavaladi kolona mama grace.. Will miss you. Always rest n peace. Ndipo amavala bwino nzimai uyu natural beauty.. Sungaone olo ndolo olo… My lomodel.. U wea simply the best.. Not matter wht pp cd say about you.. U never slide back.. Lots love mmmmm

 6. musataye thawiyanu pangani zamoyowanu kuti mukafikilakuti mwaiwala zamachimo anu mukukamba zaazanu iyeyo kwake kwatha usamuweluze mzako pakuti iweso ukudikila komweko panga zaoiwe ndi mulungu wako kuti likafikaso tsikulakoloteleli ukafikilakuti musataye thawi yanu ndi kukamba za azanu iyeyu kwake katha pangani zanu ndi mulungu wanu

 7. RIP GRACE, you have done alot to us.I hope you will do the same in your given heaven office.Amen.

 8. i must point out something that seems to rather be ignored,to all that have heard the song to be talk of controversy,because simply the late was well known for gospel music but what about this “ndizaulula” song is saying it is agospel song….before u turn on me,judge me or criticis me, please listen to the song,listen & hear…then in earnest analyse & compare to the music u qualify as gospel,there are common aspects,elements,contents,is the song in question holding true to such???

  1. that song is carryin a great message,,,if u can listen very wel u wil see dat da one whu is saing Ndzaululu its not Grace hersef,its God dat if u wil not repent i wil disclose every evil u do,koma ukalapa machimo ako akhululukidwa,,,,,,,,listen to dat song positively,,,it is a messege for everybody to repent

  2. aparrently there is a verse 2 to that song that i did not listen to,my bad for jumping to conclusion,i accept when am wrong & seems i may have been terribly so this time around.

  3. aparrently there is a verse 2 to that song that i did not listen to,my bad for jumping to conclusion,i accept when am wrong & seems i may have been terribly so this time around.

  4. Grace Chinga’s album have always had such songs that seem controvential. Remember MUNDISUNGILE KOLONA: it was once talk of the town, people asked where is the gospel in this song as some even assumed that Grace amamuimba Ethel blablabla……. So Grace has left this message; may be she would have enlightened us more about the song on stage during Launch/live performance if she were with us. sob sob sob

 9. ngati ndinu a chikondi agalu!olo CD munali ndi ya pirate ndiye mukuti mumamukonda.Mesa bwenzi mutamagwiritsa ma CD ake a original osati zobenazo,ndiye muzisokosera ngati mumamukondadi afisi achabe chabe inu,zinjoka mu udzu

 10. Ine sindikusamala kut ntchito zake zinali zotani izo akuziwa ni Ambuye koma chomwe ndikuyang’ana ndi utumiki wake wamayimbidwe omwe amandisuntha nawo ndipo ndizamudakumbukira mpaka kale

 11. Ine sindikusamala kut ntchito zake zinali zotani izo akuziwa ni Ambuye koma chomwe ndikuyang’ana ndi utumiki wake wamayimbidwe omwe amandisuntha nawo ndipo ndizamudakumbukira mpaka kale

 12. Munthu akamakambidwa ndekuti amachita chifunilo chamulungu enanu kaya mwasowa zolemba pa fb ziwonani zamavuto anu sikuti mutchuka chifukwa mukuipisa mbiri yamuthu ,kuweluza ndikwa mwiniwake ndiwendani kuti ukaweruze? Osachita manyazibwa ambiri akukamba zaobwino wake iwe kaka pazinthu zoti sungaonjezere even tsikulimozi pamoyo wako, iwewabwinowe wanganji choti anthu akuyamikire ndimbiri yanji yomwe uzasiye? Kambani zina ziveka naga iziii mungouyika usatana wanu pantunda. Atamwalira macholowe bwanji simunakambe zambili? Ali m’balewanu mungakondwe nazo anthu atamafalisa nkhani ngati zimenezo?

 13. SHE WAS GUD KULEMBA NYIMBO KOMA SHE WAS A STRONG WOMAN WHO KNOWS WAT SHE WANT WITHOUT FEAR OR ANYTHING BUT GOD OLNY R.I.P GRACE

 14. SHE WAS GUD KULEMBA NYIMBO KOMA SHE WAS A STRONG WOMAN WHO KNOWS WAT SHE WANT WITHOUT FEAR OR ANYTHING BUT GOD OLNY R.I.P GRACE

 15. By the Grace of God , Grace Chinga was given to Malawi to share God’s Grace. May your soul rest in peace, Grace.

 16. Kwa iye anatembenukadi mtima imfa siyoopya koma tsoka kwa iye odziyeletsa mmaso awanthu pamene dzintchito dzake ndinyansi pamanso a mulengi ubwino wake sayang’ana nkhope mulengi hahahaha kodi inu ndi ine tilipati? uyu kwake kwathatu olo tingakambe dzomuyeletsa olo dzomudesa kwa mulengi ndi zina!

 17. Okamba muzikamba;Ozonda muzizonda;oye analibe Pulobulemu;uli ndi pulobulemu ndiiwe ukukamba zoipa zake;kuiwala zaubwino wake;She was a star beh;ankatiimilira….Continue resting in peace MAMA Grace….

 18. Mzime Wa Gwetah thanks for your comment and am proud of you. If you understood my comment very well, u could agree with me that wina aliyense ali ndi mavuto. Now, munthu akamwalira ambiri Amakonda kunena zabwino zokhazokha.Koma ndi bwino nthawi zina kumanenanso zofooka zake za munthu. Am not trying to judge GRACE here koma monga mwanena nokha, wina aliyense ali ndi zofooka ndiye ine chofooka cha GRACE Chinga chinali chimenecho. Hope mwatha kundimvetsa.

  Thanks Abwino Mulaunzi for walking together with me.

 19. @ MacKnowledge Achair Maliro aliyese amakhala ndi zofooka moyo ingakhale uyimbe bwino upephere kwambiri as long uli pansi pano zofooka zambiri pamoyo koma tidzapulumukila chisomo cha mulungu…ndipo palibe wolungama padziko ndi mulungu yekha basi

 20. Athu amathoka shit zikakhala kwa anzawo the woman was talented chifukwa nde eeee ankatha gone but not 4goten kwatsala tchile ndi kumene kukupita moto rip chinga

 21. so many things has been said,connected to the death of Grace.but its only God knows the trueth.inu ndi ine tikamayankhula zambirimbiri titangolakwapo apa.zagwa zatha.

 22. Zuzuleni mwachikondi osati kuniweruza,pot opusa ndiemwe mbiri yake yaipitsidwa lero iwe ndioyera pot zako zabisa,,,musalimbane nkuipisa mbili ya nzanu pot zanu zabisika alipo yemwe sanachimwiko atole mwala amugendeeeeee,,,

 23. Alipo sanachimwepo?????? Anali munthu tu paja. Aliyense amakhala ndi zofooka zake olo mwini wake nso amatba kunena. Kwake kwapita kwatsala kwa iwe ndi ine. Bola iyeyo mbali ina anayesetsa kuflitsa uthenga iwe nanga wapangapo cha pa ntchito ya Ambuye?????? Udzifunse wekha!

  1. Akhonza kufalitsa uthenga kma iye mwin uhengao osaumva and chpulumutso kukhala nacho kutali. Usaiwale mau amat: si onse akunena Ambuye Ambuye adzapulumuke kma yekhayo wakuchita cifuniro cha Mulungu

 24. Amayimba bwino. Zodandaulitsa kwambiri koma she had lots of scandals. Vuto lake linali lomwelo basi. She was not stable pa nkhani ya banja.
  Bushiri, Moffat,kaya akuti Josephy Tembo, etc mmmm. Anyway.

  1. eyetu sinanga tonse tilipasi pano ndiye palibe wabwino olo bible likuti “tikazitcha olungama tizinyenga tokha”ndizambili tikuchita kuposa anapanga Grace kuimba ndi mphatso basi osati kuyela ntima ayi nkhani yotembenuka ntima ndi nkhani ina

  2. Mmmm guyz,nthawi zinazake ndibwino kuyamikila pazimene nzathu anapanga,komaso tisamaweruze azathu,your saying a lot of things kuti she was dating bushiri komaso josephy tembo,zithu mukunena apa ndizopanda umboni mwinaso nanu munagova kwa anthu ena,so guyz let’s respect her soul to rest well mulungu ndiye oweruza zimenezi komaso ndiamene amaziwadi zoona zake zamuthu,thank u my good pple stay blessed!!

  3. Bwanji osangotiuza the good and bad side of her, in this way zibalansa. Pipo r fabricating stories chifukwa anthu mukubisa her bad side. We all hv weaknesses palibe alibe the bad side. So someone with infor write the article muona palibe atachite comment coz it will be the plain truth. Anthu r saying things coz only gud side is said as if she was all holy!

  4. Bwanji osangotiuza the good and bad side of her, in this way zibalansa. Pipo r fabricating stories chifukwa anthu mukubisa her bad side. We all hv weaknesses palibe alibe the bad side. So someone with infor write the article muona palibe atachite comment coz it will be the plain truth. Anthu r saying things coz only gud side is said as if she was all holy!

 25. Wakumudziyo ngati amayimbi kunyumba kwawo ndeumati adziwika bwanji kuwanthu? Iwe ungamphuzire school mkulandila ma paper ako abwino nde mkukakhala kumudzi job uyipeza? Suzutengera Gra poti amakhala m BT ayi ndayankha iwe wanena zawoyimba wakumudzi

 26. Dead and gone away!! kuti amwalile oyimba wakumudzi you can’t keep on posting! koma poti ndiuyu hahaaaaa like she was a president!!! its too much guys now

  1. tell me now what is the different between wakwanu uja anamwalila ndiyeyu? and you @Kettie ukadzawadziwa mawu amulungu ndipamene udzasiye kumuwuza wamoyo nzako kuti wa satanic!!! being a hero its nothing @ melvin zake zonse zanthela pamenepo!!! kuti mukhulupilile kunali life president Dr H. Kamuzu banda and Bingu wamunthalika Anthu amene amati akamadutsa pamalo anthu kuchita Salute!!! Anthu amene akongoletsa Malawi kuti afike pamenepa!!! lelo ali kuti? hahaaaa bible limati Zonse zadziko zidzapita koma Mawu a Mulungu sadzapita kufikila atakwanilitsidwa!!! chilungamo kuwawa

  2. Ur just busy accusing each other,Mmmmh guys the woman is gone,some of you u r just supporting her coz she is gone the time she was alive u were not,even DVD yake mulibe.#Emmanuel ukunenezoona there is no nid kuti muzimuchulachula mwina wake Ali phee kumanda,basi mma news adakalembabe.mmamunyoza Ali moyo lero muziti anali hero shame on u guys.my condolence thou

  3. Vuto si omwe akumutchula tchula, vuto ndi inu amene mukumawelenga ma post amenewa. Us for me I don’t see any plobrem becuse Grace was a celebrity. She deserved such a talk. People can talk even for 2yrs,no problem. Koma akanakhala michael jackson? A malawi a nsanje inu. Kaya mukomoka,kaya mukagona mu ntengo; still people will keep on talking and showing sympathy on her.

  4. kakolope kmnyanja iwer! yemwe zikukubowa,Grace ndi grace bas & wil continue to preach to us the gospel coz nimbo zake tizigulabe,was indeed my favourite, eeeh kundidalisa kokhako!!

  5. emmanuel u r ryt….only stupid people osowa zochita atha kuma kambabe za ntembo oti wayamba kale kunukha pano…malo moti apeze zina zochita…….Ndinavaso kuti anali Hule munthuyu…koma anthu akusiya kukamba za uhule kumanena za satanic…ku nyasalande anthu onyasa ndi zelu zomwe

  6. Koma ngati omwe a kukambabe za Grace ali zitsilu, ndiye inu a Ndeule tikuyikeni gulu liti popeza apa mukukamba nawo. Mokupemphani bwanji mungokhala a Head master a Zitsilufe?

  7. Grace anali odziwika akuyenela kulilidwa munjila iliyose yomwe anthu omukonda aganizila popeleka ulemu kwa malemuyu,and sungamufanize ndimunthu wakumudzi oti wango yamba kumene kuimba,bwanji kodi? awa ndimalo amene anthu akuonetsela kukhuzidwa kwawo pa infai and tidakalilabe so enanu tulukani ngati zikuwawa

  8. Kodi Amalawi Vuto ndi chani? Malo molimbana ndi njara yabuka Mziko munoyi basi mulibusy kulimbana ndimunthu oti kwake Kwatha? Mukuganiza kut akanapanga zoti zisangalase M’Malawi aliyense? Abale mulibe manyazi kumaujeda ndi mtembo omwe? Eish,,,,ndilindichisoni kwambiri Ana azinkhanira Inu. Ngat imfayi yatizizimutsa, Mesa unali mwayi wathu kuti tikonze mitima yathu? Bolatu iyeyo mutu unamupweteka koma winawe udzafa uli kuchigololo, Uli kokuba, akupha Alubino, utaledzera Mowa, Uli kotamba, even nthawi yolapa mwina sudzaipedza.Nde Malo moti tilape tilibusy kukamba zamunthu oti wapita zonse zake athananazo ndi Mulungu Nde tikupindulapo chani? TIZIGANIZIRE,,,, or munditukwane Ndilibe Nazo ntchito bola M wamva. Iyaaaaaaa

  9. Kodi Amalawi Vuto ndi chani? Malo molimbana ndi njara yabuka Mziko munoyi basi mulibusy kulimbana ndimunthu oti kwake Kwatha? Mukuganiza kut akanapanga zoti zisangalase M’Malawi aliyense? Abale mulibe manyazi kumaujeda ndi mtembo omwe? Eish,,,,ndilindichisoni kwambiri Ana azinkhanira Inu. Ngat imfayi yatizizimutsa, Mesa unali mwayi wathu kuti tikonze mitima yathu? Bolatu iyeyo mutu unamupweteka koma winawe udzafa uli kuchigololo, Uli kokuba, akupha Alubino, utaledzera Mowa, Uli kotamba, even nthawi yolapa mwina sudzaipedza.Nde Malo moti tilape tilibusy kukamba zamunthu oti wapita zonse zake athananazo ndi Mulungu Nde tikupindulapo chani? TIZIGANIZIRE,,,, or munditukwane Ndilibe Nazo ntchito bola M wamva. Iyaaaaaaa

 27. give us a link to download…..mwina mkuwadziwako a black fame kaya mukutero kaya!….tiwadziwa nthawi yazovutayi

Comments are closed.