Bullets players on a road trip selling cigarettes

Advertisement
Big Bullets
Nyasa Big Bullets
Nyasa Big Bullets players at one of the promotion tours.

Malawi super league giants, Nyasa Big Bullets players have been on the road selling Nyasa Manufacturing Company’s (NMC) merchandises, fueling concerns that preparations for the new season will be affected.

As part of their sponsorship agreement with NMC, Bullets players have been traveling all over Malawi for sales promotion. Due to the road trips, some senior players have only managed to report for training once or twice even though the team started pre-season preparations two weeks ago.

The development has angered a section of the team’s supporters.

“Our friends are busy preparing for the new season yet some of our players haven’t had a day to rest because they are promoting NMC products. It’s not wrong but with the new season coming ahead, it’s very good if they can be released to start training with their teammates,” worried one Bullets supporter.

But reacting to the news, Bullets vice general secretary Kelvin Moyo said the team’s executive is doing this in order to allow the players to rest since they did not rest during last year’s pre-season due to the club’s CAF Champions League commitments.

“This won’t affect our preparations at all. We are doing this in order for the players to rest. Ask Yamikani Fodya on how many games he has played this season.

“The new season is fast approaching but we can’t risk our players too. Let them rest,” explained Moyo.

Bullets clinched a K500 million sponsorship deal with the cigarette manufacturing company last year.

Advertisement

514 Comments

 1. Tikudabwa Nazodi Zimenezi Eti Mpaka Kumati Akafika Pa TC Akumachita Kunena Kuti Asute Ndudu 10 Pa Mphindi 20 Alandila Catton Imodzi Ya Ulele ya 2010 Koma Chosecho Pali Ana Asukulu Okhaokha.

 2. Tikudabwa Nazodi Zimenezi Eti Mpaka Kumati Akafika Pa TC Akumachita Kunena Kuti Asute Ndudu 10 Pa Mphindi 20 Alandila Catton Imodzi Ya Ulele ya 2010 Koma Chosecho Pali Ana Asukulu Okhaokha.

 3. Nde kumakhala busy kunyadila sponsor nkhani zake zopeperazi mmalo mopanga zampira kumagulisa ndudu zopoila ,ma player komanso ma supporter a bb chitanipo kankhu if u love ur team izi sizoona AI guys am nyerere fan koma izizi nde AI mmmm,

 4. Nde kumakhala busy kunyadila sponsor nkhani zake zopeperazi mmalo mopanga zampira kumagulisa ndudu zopoila ,ma player komanso ma supporter a bb chitanipo kankhu if u love ur team izi sizoona AI guys am nyerere fan koma izizi nde AI mmmm,

 5. Eya ngati mukufuna kuti tikuthandizeni muzigulitsa fwaka m’misewu. Malonda akavuta muzisutakonso koma siwulere tizikudulani mwezi ukatha mwamva eeeeee! Iwe Sulumba bwanji sukuyankha tidakuwuza ndife kuti uchoke kuja amagulitsa galimoto? Nesa paja m’machita kundinyengerera hihihihihi! Pepa usalire Muha.

 6. Eya ngati mukufuna kuti tikuthandizeni muzigulitsa fwaka m’misewu. Malonda akavuta muzisutakonso koma siwulere tizikudulani mwezi ukatha mwamva eeeeee! Iwe Sulumba bwanji sukuyankha tidakuwuza ndife kuti uchoke kuja amagulitsa galimoto? Nesa paja m’machita kundinyengerera hihihihihi! Pepa usalire Muha.

 7. If this is a way to go for the sponsors to use the players advertise their merchandise then our sports council has to do something about it. Football is highly rated by our young generation. It doesnt make sense to see the young star encouraging his fellow to smoke in the name of making money for the sponsors, this will lead to moral decay at the end. The club need to re-strategise.

 8. If this is a way to go for the sponsors to use the players advertise their merchandise then our sports council has to do something about it. Football is highly rated by our young generation. It doesnt make sense to see the young star encouraging his fellow to smoke in the name of making money for the sponsors, this will lead to moral decay at the end. The club need to re-strategise.

 9. If this is a way to go for the sponsors to use the players advertise their merchandise then our sports council has to do something about it. Football is highly rated by our young generation. It doesnt make sense to see the young star encouraging his fellow to smoke in the name of making money for the sponsors, this will lead to moral decay at the end. The club need to re-strategise.

 10. neba akugwira chibalo ndeukhaura umangova siponsa sunati ukachokapamenepo tikawonana pa ground amuhamad akafela zaen, dzofiyira wati.

 11. kkkkkkkkkk ndie kumawiko aziona zinachitika kut? zachilendo izi! instead kut azicheza ndi mabanja awo! ena ndi a seventh day iiiiii kulakwitsa bola NOMA BFORWARD WANDERERS NDI MORE!

 12. Hahahaha bola kugulisa amphaka, nakha ndudu, Ana amasiye forever!! KUPEZA CHINGAMBWE!! kupeza Thom-thom, KUPEZA EMBASY, kupeza 2010, KUPEZA MUTU WA MBALAME KKKKKKKKKK

 13. Kkkkkkkkkk, izi sizinachitikepo mu mbiri ya masewero ku Malawi kuno. Kkkkkkkk, Bullets why? Kuyifera kumeneko? Kkkkk, mukukwanisa ndithu……,, asangalatseni mabwana anuwo

 14. Think twise b4 talking shit,popanga bussines pamafunika plan zomwe apanga anyasa sizikutanthauza kut azikhala akutenga ma player mkumaka gulisa fodya kumeneko kunali kuitanila malonda,inuyo simunayambe mwamvapo kut guest wathu pa mwambo uwu ndi uyu simunazionepo? Muzikula amalawi tisiyeni ndi sponser yathu ndipo ndramazo zikuthandizilaso team yathu bb

 15. Kkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk sono fisher mukumupasa ndudu kuti azigulista? Nduduzo mukufuna kuti agulitse kapena asute zonse iyeyo alindichibaba ndenkumpastanso ndudu eish fisher achokepo pogulitsa ndudu.Nyerere ndi more fire moto wambiri NAKAMURA AKUBWERAYU neba unyanayo bibi kkkkkkkkkkk manoma ofewa

  1. Hahahahahahahaha! seriously? instead of yomathandiza kuchepetsa kut anthu asamasute mukumalimbikitsanso koma mumafunira anthu anu zabwino? kkkkkkkkk team yafuko ija yasanduka yoonjezera lung cancer lol.

 16. Yes last week they were in Mangochi selling tobacco may be its in their memorundum of understanding and articles of association

 17. Hi, Are u a graduate, school drop out, and u are looking for job/work to do? Don’t worry again we can’t waite for our government to create jobs. U can start working on ur own and make good money for urself is free. Make up to 2000 US DOLLAR per week right inside ur house anywhere anyday anytime. Hurry now and become who u want to be in life is free. Earn good money online by working as a part time job, u also earn up to 2500 US DOLLAR weekly guranted it’s free no harm join me at http://job4america.xyz/?user=7301

 18. Hi, Are u a graduate, school drop out, and u are looking for job/work to do? Don’t worry again we can’t waite for our government to create jobs. U can start working on ur own and make good money for urself is free. Make up to 2000 US DOLLAR per week right inside ur house anywhere anyday anytime. Hurry now and become who u want to be in life is free. Earn good money online by working as a part time job, u also earn up to 2500 US DOLLAR weekly guranted it’s free no harm join me at http://job4america.xyz/?user=7301

 19. Hi, Are u a graduate, school drop out, and u are looking for job/work to do? Don’t worry again we can’t waite for our government to create jobs. U can start working on ur own and make good money for urself is free. Make up to 2000 US DOLLAR per week right inside ur house anywhere anyday anytime. Hurry now and become who u want to be in life is free. Earn good money online by working as a part time job, u also earn up to 2500 US DOLLAR weekly guranted it’s free no harm join me at http://job4america.xyz/?user=7301

 20. lilongwe ndiozindikira singauze silver to sell tobacco ife timauza kuti azikapanga nsalamazo nkumakazisiya ku lizevu bank.

 21. lilongwe ndiozindikira singauze silver to sell tobacco ife timauza kuti azikapanga nsalamazo nkumakazisiya ku lizevu bank.

 22. lilongwe ndiozindikira singauze silver to sell tobacco ife timauza kuti azikapanga nsalamazo nkumakazisiya ku lizevu bank.

 23. Ngati ma player akutha ku malawi ndi chifukwa cha fodya ndi mowa .Ndiye apa zachita kuonetsa pooela kuti company ya nyasa ikufuna kuononga bullets

 24. Ngati ma player akutha ku malawi ndi chifukwa cha fodya ndi mowa .Ndiye apa zachita kuonetsa pooela kuti company ya nyasa ikufuna kuononga bullets

 25. Ngati ma player akutha ku malawi ndi chifukwa cha fodya ndi mowa .Ndiye apa zachita kuonetsa pooela kuti company ya nyasa ikufuna kuononga bullets

 26. Mtolankhani walemba nkhani iyi samakondwa akamaona BB ikukwapula matimu mosayang’ana kt awa timamwera limodzi m’chilobwemu. Supporter wa nyerere uyu, shupit zake.

 27. Mtolankhani walemba nkhani iyi samakondwa akamaona BB ikukwapula matimu mosayang’ana kt awa timamwera limodzi m’chilobwemu. Supporter wa nyerere uyu, shupit zake.

 28. Mtolankhani walemba nkhani iyi samakondwa akamaona BB ikukwapula matimu mosayang’ana kt awa timamwera limodzi m’chilobwemu. Supporter wa nyerere uyu, shupit zake.

 29. Kkkkkk tayendani a Noma mugulitse magalimoto akaunjikawa kkkk no future in the Be Forward wanderers partnership…no gains on part of the kaunjika vehicle dealers bola fodya emweyu

 30. koma zaonjeza player ndimunthu olemekezedwa kwambiri ndisapota ngati player akumutchipitsa chonchi do you think ma player athu akhala osiririka

 31. imagine being aplayer,thinking preperations for traing,to other side fodya(hona)selling.ok when the performance of a player goes down you blam a player.kma bb mmmm chfukwach limban vpuli sabwera ndangonena ine wa mabanker

 32. Munkaesa ndimasewela mugulitsatu ndudu zimenezo yamikani fodya mwadzina lake adabwela pakalambo weekyatha kudza gulitsa ndudu zimenezi

 33. Ndmadabwa2 Ine Apa Nde BB Yatha Bas Prayers Kugulisa Cigarates For What? Mukangosya Kuthandzidwa Bwanj? Mukuzuzika 2much!

 34. Koma ndiye kubalarikatu aaah kugulisa uku kumasutaso iiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii
  kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk mwakula mwatha muziona zikaipa ziwa nyimbo kkkkkkk mpaka pamenepo mwatonyanya kumuziko nebar aaaaaaaaaaaaaaaaaaaaa ai kkkk

 35. Pepan ife talandiraso ujau. Kaya mukugulitsa kaya simukugulitsa zanu izo ife ndie ndi wamkaka

 36. Mukunyoza a malawi24 lero,akalemba zabwino zainu mumvekele zili bo,akalemba zokhudza noma ma comment mbwee oseka noma lero 24 omweo akuonani mukutakata rali ndi laif mukut zabodza zoona?chaka chino mulemedwa ndithu ma memory card mbali ina fodyanso mbali kkk ma sponsor enawa bolanso fisd

 37. izi ndiye zachilendo mu mbiri ya mpira sponsor ship yanji imeneyo akupanga anyasaland aaaaaaa ndadabwa nazo ndiye mwati Muhammad sulumba aliposo kogulisa chingambwe

 38. koma choncho Siboo!! mukusisa molalo ya maplayer Sipangapezeke njira ina Apart 4rm iyiyi. ine ndi Wanoma koma Sizikundiwaza izii olopang’ono.

 39. No Vending Fodya Allowed @ Lalilubani Road,coz Smoking Z Hazadous 2 Player’s Life(by Management “Noma”)kkkkkkkkkkk Odi Uko Noma Ipazeko Kkkk

 40. Kachinjika Palibe Chanzeru Ukukamba,zinazi Tamavomerezan Imeneyo Sponsorshp Kkkkkkkk Odi Uko patukani Ndi Fodya Wanuyo Noma Idutseko Kkkkkkkkkkkk

 41. A MALAWI 24 nanuso mumasuta, mukuyika chithuzi choti anthu ali ku ground nkumanena za kugulitsa fodya, za Ganja basi . Awoneseni ma players atanyamula fodyayo ngati ndinu atolankhani enieni mntshwiiiiiiiiiimmm #NYASA_BULLETs_more_FIREEEEEE

 42. A MALAWI 24 nanuso mumasuta, mukuyika chithuzi choti anthu ali ku ground nkumanena za kugulitsa fodya, za Ganja basi . Awoneseni ma players atanyamula fodyayo ngati ndinu atolankhani enieni mntshwiiiiiiiiiimmm #NYASA_BULLETs_more_FIREEEEEE

 43. Kodi ma player athu olo akugulsa malondaa inu amatimu ena chikukhuzani ndi chani?kaya ndi ma vendor kaya chani koma team iyi imakuchinyanitu,mind yur busness ku ma team anuko,BB ikuziwa chimene ikupanga bwebwebwebwe chani apa?team ikhale yopanda sponsor muyitonze,yapenza sponsor mukulongolola BB imakusowesani mtendere kapena?Fotseki zanu ndithu,imeyi ndi nkhani

 44. Kodi ma player athu olo akugulsa malondaa inu amatimu ena chikukhuzani ndi chani?kaya ndi ma vendor kaya chani koma team iyi imakuchinyanitu,mind yur busness ku ma team anuko,BB ikuziwa chimene ikupanga bwebwebwebwe chani apa?team ikhale yopanda sponsor muyitonze,yapenza sponsor mukulongolola BB imakusowesani mtendere kapena?Fotseki zanu ndithu,imeyi ndi nkhani

 45. koma kunene zoona izi zomwe apanga acampany yanyasa sizabwino ai kulibe team muno mu africa imapanga ngati izi ai tikhoza kuona kuti akutithandiza koma kulikupha tsogolo la mateam kuno ku malawi chifukwa ngati akufuna kuthandiza akanapezela njila ina yoti nawonso team iziwapindulila osati kuwagwiritsa ntchito anyamata ntchito kaamba kofuna thandizo ai chabwino maplayer ena zipembezo zawo sizimawalola kugulitsa fodya ai malinga ndi Bible limanenela koma lelo akuwagwiritsa fodya komanso monga iwo achinyamata sinkhani yabwino azikaima pastage ndukumakamba za fodya ai nanga momwe akupitamo muli anyamata ena ngati iwo nde nkumawauza chani za tsolo lampira kodi bwanji osasankha kucommite komweko anthu ena monga masapota ena okhulupilika kuti azikagulitsanawo uku maplayer akupanga training bwanji chabwino ngati training akupanga pakepake nde kuli ena achilendo atolelana bwanji poti akupanga matsiku olekalekana pls akuluakulu kambiranani bwino pankhani imenei chifukwa ndikudziwa zonsezi zikuchitika kaamba kofuna sponsaship ndi campany

 46. koma kunene zoona izi zomwe apanga acampany yanyasa sizabwino ai kulibe team muno mu africa imapanga ngati izi ai tikhoza kuona kuti akutithandiza koma kulikupha tsogolo la mateam kuno ku malawi chifukwa ngati akufuna kuthandiza akanapezela njila ina yoti nawonso team iziwapindulila osati kuwagwiritsa ntchito anyamata ntchito kaamba kofuna thandizo ai chabwino maplayer ena zipembezo zawo sizimawalola kugulitsa fodya ai malinga ndi Bible limanenela koma lelo akuwagwiritsa fodya komanso monga iwo achinyamata sinkhani yabwino azikaima pastage ndukumakamba za fodya ai nanga momwe akupitamo muli anyamata ena ngati iwo nde nkumawauza chani za tsolo lampira kodi bwanji osasankha kucommite komweko anthu ena monga masapota ena okhulupilika kuti azikagulitsanawo uku maplayer akupanga training bwanji chabwino ngati training akupanga pakepake nde kuli ena achilendo atolelana bwanji poti akupanga matsiku olekalekana pls akuluakulu kambiranani bwino pankhani imenei chifukwa ndikudziwa zonsezi zikuchitika kaamba kofuna sponsaship ndi campany

  1. ndithu braz ine zikundikhuza poona kuti izi ndizachilendo kumacampany othandiza kapena mwina akanawalemba ntchito tikanati akupanga ticket yake yatsiku koma gulitsa malonda player katundu wasponser ndizachilendo ine kunva zimenezi, mundilole ndikambepo mau olakwika awa: kumene akuyendako akuyenda pachitsulo chopanga munthu wanja ake mwina mwatsoka ndukuchita ngozi ndie adzalandila compasetion poti sintchito chifukwa ndukukamba izi satana alipachintchito padziko lonse lansi ndipo akutenga myoyo yawanthu munjila zosiyanasiyana ndie ine sindikuona chanzeru player kumanga zimenezi ai ngati ku RSA kuli mateam ambiri koma ine kumeneko sindinaonepo player akugulitsa katundu wa sponser ai ndimamunela player paground or pa TV akusera mpira basi koma izi ai ndithu sizabwino konse koma langa ndipempho basi kwa akulu a team aganize bwino ine ndukuona bola mateam aja amati tikakutenga tikulemba ntchito limenelija nditsolo labwino chifukwa or player yo atatha sikuti angamuchotse ntchito ai iye walo m,boma basi mpaka mtsolo koma awa mmmmmmm.

  2. ine ndiwa NOMA izi ndikukamba ngati ine munthu modzi wa amalawi kunvera chisoni anyamata athu adziko kupatula zatimu yanga ndithu bwana

  3. ine ndiwa NOMA izi ndikukamba ngati ine munthu modzi wa amalawi kunvera chisoni anyamata athu adziko kupatula zatimu yanga ndithu bwana

  4. ine ndiwa NOMA izi ndikukamba ngati ine munthu modzi wa amalawi kunvera chisoni anyamata athu adziko kupatula zatimu yanga ndithu bwana

 47. Ineyo ndi wanoma koma ngati zogulisa fodyazo angwizana pamenepo analakwisa mpaka player kugulisa fodya??????maplayer enawo mipingo yao silola zimenezi mukuwachimwisatu.

 48. Koma sizelu ma prayer azikhala akungulitsa fodya? Mpaka kukana kuti sasewela mbonaza cholinga adzingulitsa fodya mmmm very bad! Osamaiwala kusuta kumaononga moyo !!! mukukweza chiwelengelo chaanthu odwala cancer ndi TB

 49. ma bwana a bb aganizileni mapuleya akhalila kukazinga chimanga kusuta chamba lelo mwayandikisa fodya zooona akamamusuta muziti sizikuenda mgraundi?5

 50. ma bwana a bb aganizileni mapuleya akhalila kukazinga chimanga kusuta chamba lelo mwayandikisa fodya zooona akamamusuta muziti sizikuenda mgdi?5

 51. Kkkkkkkkkkk, Nyasa company ndiyochenjera kwambiri. M’malo molemba anthu ntchito yowalipira, aganiza zotuma ma player to sell fodya wao without paid.Kaya, zanu izo.

 52. Nyasa ndiya amwenye nde mukhaulatu mmangololera sponsorship wtht memorandum of understanding…thats bullshit ,the playerz ntchito yawo ndi mground not ma salesman a fodya ,osangolemba mavenda akundix ndi bangwe buaj

 53. Akapitilira choncho mzamva kuti wina wagwidwa coz maplayer ena azigulitsa chamba ndi ma drugs kunamizira nduduzo komanso adzasokoneza ndalama.Apaseni ulemu maplayer chonde msawanyozetse

 54. Penapake mukakhala kumaunikora bwino ximafunika osamangokomenta zopanda mutu CX ya bullets si sponsorship koma partnership nde olo atagulitsa chingambwe ndipomwe akudyera pamene iweyo ukuwanenewe ndinena olo ndi chithu choti uloze ulibe ntchito kukhalaira kupepha ndikudzitukumira ngati uli ndi kathu .iwe ukuti ukuyendera motorcar ya b4wrd galimoto lake unenero nde liti????? Muchikhala ndi ndalama sibwenzi xulumba wanuyo atathawako ndikupita Ku team ya anthu ogulitsa chingambwe , anatha mkulingalira kuti kumeneko kulibe moyo nde palibe chabwino chomwe chimabwera usanachigwirire ntchito mayb u shu go end consult ma dictionary anu da different btwn sponsorship end partnership koz mwaonetseratu umbuli ndipo mudzakhala choncho amalawi ximidzatukuka pakuyang’ana ntchito yomwe nzanu akupezera ndalama olo utakhala kuti ukuseta khalamba bola ukulandira pamene winawe ndiwe spoon umadzi kudya ndikukanyera chepetsani kunena anzanu momwe mukugundika kuwanena APA Iwo akufuna ndalama pamene iwe ukudikira amum ndi adad kuti akudyetse samalira pakamwa pako

  1. iwe ikuona ngati ndine ndani????? mxilll ndipo iweyo mkandanoso???? did i metion ur name?????? shupit ukapangire wina zimenezo mwina ngati umachita zopeperazo ndi gal friend wako konko mxilllll

 55. Wy do this news forums post negativities abt their homelands, if selling in the streets can solves th cash crisis at club and make them put something in their pocket so what is wrong

  1. We are living in different world my frend,u dont compare yorself with all world of sports country,yet Malawi is struggling to its food as a nation,hw abt a company tht produces cigarettes can copy up th standards of real footbal,in aditional if money is in their pockets it cant go by repoting to evryone tht it hav bn obtain from street vending

  2. We are living in different world my frend,u dont compare yorself with all world of sports country,yet Malawi is struggling to its food as a nation,hw abt a company tht produces cigarettes can copy up th standards of real footbal,in aditional if money is in their pockets it cant go by repoting to evryone tht it hav bn obtain from street vending

 56. Izi nde ziti?? Ma players mwawasandusa kukhala ma sales rep. No no no thus not the way to go. Mwagwirizana zopusa. Nthawi ya china Kinna munamvapo kuti ankagulitsa nsapato za Bata?? This is degrading.

 57. Week yatha Jar Man ndi Yamikani Fodya pa Lionde uku akugulitsa fodya kkkkkkkkkkkk
  azunguwa ationerera kwabasi!!!
  Anthu amamumvera chisoni Fodya malingana ndi age yake kumapanga zimenezi!!!!

 58. Pamene ena ali busy ndi magalimoto, ena ali pikitipikti ndi ndudu kuti mwina angagule kabaza.Kumaona ma sponsors. #team wanderes

 59. Ine ndinaona pa Mpale MANGOCHI pa 5 Feb 2016 ma 5 pm. Umanewu si mpira Kodi tikuwawonongeranji ma players. Musiye zikutinyasa komanso sizovomerezeka

 60. Kkkkkkkkkk mukhalila yomweyo ife tili m galimoto pano ya B Forwad muledzela komko ndimowa kkkk mwayamba geni kodi mmalo mopuma kuti okuthandizani alipo bolaso kukhala single

 61. Iwo akugulitsa fodya ife tikugulitsa ma galimoto. Nde Mr Yamikani Fodya nayenso akugulitsa nawo fodya? Akugulitsa m’dala wake

 62. Iwo akugulitsa fodya ife tikugulitsa ma galimoto. Nde Mr Yamikani Fodya nayenso akugulitsa nawo fodya? Akugulitsa m’dala wake

 63. Ma supporter a Bullets, chonde, tafufuzani kwa akulu akulu. Osamangopanga phokoso. Sizowona kuti Yamikani ndi anzake adzikagulitsa malonda pamene masapota mwangokhala. Ndiye pamenepa ma player akupuma? Poverty in freedom is better than riches in bandages. Ndatukwana apaaa????

 64. Ma supporter a Bullets, chonde, tafufuzani kwa akulu akulu. Osamangopanga phokoso. Sizowona kuti Yamikani ndi anzake adzikagulitsa malonda pamene masapota mwangokhala. Ndiye pamenepa ma player akupuma? Poverty in freedom is better than riches in bandages. Ndatukwana apaaa????

 65. mmmmmm its brand selling not that the player are selling cigaretes. it happens everywhere in the world,the problem is the reporter for he is trying to take the issue to suit his mind- poor reporters

  1. Owen, iweyo koma wawawonako? Zina osamatsutsa ngakhale kuti chinthucho umachikonda. Zikuchitiks apa ndikutoza ma player a Bullets.

 66. mmmmmm its brand selling not that the player are selling cigaretes. it happens everywhere in the world,the problem is the reporter for he is trying to take the issue to suit his mind- poor reporters

  1. Owen, iweyo koma wawawonako? Zina osamatsutsa ngakhale kuti chinthucho umachikonda. Zikuchitiks apa ndikutoza ma player a Bullets.

  2. Vuto laku Malawi we always like negative reporting. It could be Nyasa’s markting strategy in marketing their merchandise using BB players to gain the market share. So apa palibe nkhani , bwanji a first Lady akasesa nawo pa mseu all the negatives samamvekapo.

  3. @ mcfield, i met them and none of the player carried the cigaratte packet but they only had words for the products

 67. Guys this nt sponsorship but self sponsoring.kungoti somewhere excutive ya BB siyimaganiza they could do this on their own ndikupeza more money then the clud could move on even without sponsorship.koma akudikira anthu ena a nzeru ngati a Nyasa manufactures awaganizire and making more profits pa mutu pawo.Eee nafenso tawawona ku LLs akuwoloka LL bridge we dont know were they ar going nw.zopatsa manyazi.ukapolo chani?kkkkk.

 68. Guys this nt sponsorship but self sponsoring.kungoti somewhere excutive ya BB siyimaganiza they could do this on their own ndikupeza more money then the clud could move on even without sponsorship.koma akudikira anthu ena a nzeru ngati a Nyasa manufactures awaganizire and making more profits pa mutu pawo.Eee nafenso tawawona ku LLs akuwoloka LL bridge we dont know were they ar going nw.zopatsa manyazi.ukapolo chani?kkkkk.

 69. Players cum ciggerate sellers!? This is player abuse and manipulation indeed! Sponsorship kuidyera kuwawatu uku!!!

 70. Players cum ciggerate sellers!? This is player abuse and manipulation indeed! Sponsorship kuidyera kuwawatu uku!!!

 71. Baseless!Write something that will have impact on people’s lives not thrash lyk w@ u’v scribbled here.Is it wrong do business?This is not eye catcher,seek guidance frm ur editor even ur lecture on hw 2 come up wth a hot article.

 72. Baseless!Write something that will have impact on people’s lives not thrash lyk w@ u’v scribbled here.Is it wrong do business?This is not eye catcher,seek guidance frm ur editor even ur lecture on hw 2 come up wth a hot article.

  1. this is very pathetic indeed! i saw fitcher at kasungu boma yesterday plying dat business enroute to mzuzu.Zinandikhuza.

 73. Vuto timaziwa kt inu malwawi 24 mumasapota Ayaya Fc chipezereni bullets sponsorship mwakhala mukunyoza BB chosecho mumafuna kt azivutika pakana kalekale mwagwa nayo popeza zomwe mumafuna inu Mlungu wakana siupindura moyo wasenje patumbo pamayi anu nose mukuvomereza zopusa apa

 74. Vuto timaziwa kt inu malwawi 24 mumasapota Ayaya Fc chipezereni bullets sponsorship mwakhala mukunyoza BB chosecho mumafuna kt azivutika pakana kalekale mwagwa nayo popeza zomwe mumafuna inu Mlungu wakana siupindura moyo wasenje patumbo pamayi anu nose mukuvomereza zopusa apa

 75. Hahahahahahahahahahahaha wandudu wandudu wandudu tabwerani tigule muli ndi embassy tilibe bwelera ife timasuta embassy hahahahahahahahaha siza mpila koma fodya.

 76. Hahahahahahahahahahahaha wandudu wandudu wandudu tabwerani tigule muli ndi embassy tilibe bwelera ife timasuta embassy hahahahahahahahaha siza mpila koma fodya.

 77. Auzen anyamata chisangalaro chikakula chimabala chisoni adziyenda Bo pansewo sitikufuna pomayamba czon pazakhale wina palibe asayende ataledzela

 78. Auzen anyamata chisangalaro chikakula chimabala chisoni adziyenda Bo pansewo sitikufuna pomayamba czon pazakhale wina palibe asayende ataledzela

 79. Koma gyz ndinee @Noma fan bt zomwe akuchita anyansa apaaa sibhooo m’malo moti maplayer azikozekera za czon ali bzyyy kugulinsa zingambwee nomwenuuu mumafuna mpira upiteee pansogoro uvaya bwanji pasogoro mpira mukumvutinsa maplayer chinchooo kuli ma bonanzer mwati ooo BB sitenga nawooo mbali pa bonanzer iliyonsee kuwapuminsaa maplayer apuma bwanji maplayer akupezeka ku mangochi kukagulinsa fodyaaa ishhhhhhh shame to u Neba with ur nyasaaa

 80. Koma gyz ndinee @Noma fan bt zomwe akuchita anyansa apaaa sibhooo m’malo moti maplayer azikozekera za czon ali bzyyy kugulinsa zingambwee nomwenuuu mumafuna mpira upiteee pansogoro uvaya bwanji pasogoro mpira mukumvutinsa maplayer chinchooo kuli ma bonanzer mwati ooo BB sitenga nawooo mbali pa bonanzer iliyonsee kuwapuminsaa maplayer apuma bwanji maplayer akupezeka ku mangochi kukagulinsa fodyaaa ishhhhhhh shame to u Neba with ur nyasaaa

 81. Koma gyz ndinee @Noma fan bt zomwe akuchita anyansa apaaa sibhooo m’malo moti maplayer azikozekera za czon ali bzyyy kugulinsa zingambwee nomwenuuu mumafuna mpira upiteee pansogoro uvaya bwanji pasogoro mpira mukumvutinsa maplayer chinchooo kuli ma bonanzer mwati ooo BB sitenga nawooo mbali pa bonanzer iliyonsee kuwapuminsaa maplayer apuma bwanji maplayer akupezeka ku mangochi kukagulinsa fodyaaa ishhhhhhh shame to u Neba with ur nyasaaa

 82. That’s why ku Malawi simudzatukukuka because we only focus on what kind of activity is someone doing to generate funds.
  After all I don’t see any reason coz akamanka napempha nomwenunso mumadzalemba yapa kut ndi team yopempha so what do u want them to do?.
  The players are setting a good example thus it’s another way of attracting more fans. Otherwise it’s not by compulsory whether one shud buy or not, what they need is money which in end the players are beneficiaries themselves.

 83. That’s why ku Malawi simudzatukukuka because we only focus on what kind of activity is someone doing to generate funds.
  After all I don’t see any reason coz akamanka napempha nomwenunso mumadzalemba yapa kut ndi team yopempha so what do u want them to do?.
  The players are setting a good example thus it’s another way of attracting more fans. Otherwise it’s not by compulsory whether one shud buy or not, what they need is money which in end the players are beneficiaries themselves.

 84. That’s why ku Malawi simudzatukukuka because we only focus on what kind of activity is someone doing to generate funds.
  After all I don’t see any reason coz akamanka napempha nomwenunso mumadzalemba yapa kut ndi team yopempha so what do u want them to do?.
  The players are setting a good example thus it’s another way of attracting more fans. Otherwise it’s not by compulsory whether one shud buy or not, what they need is money which in end the players are beneficiaries themselves.

 85. Wamogo ndudu ziwiri aaaa ndimawona ngati ndi Embasy zomwe akukumana nazo achina anong’a kkkkkk no pain no gain instead of football player to mogo seller tiye nazoni mpwimpwimpwimpwiiiiii

 86. Wamogo ndudu ziwiri aaaa ndimawona ngati ndi Embasy zomwe akukumana nazo achina anong’a kkkkkk no pain no gain instead of football player to mogo seller tiye nazoni mpwimpwimpwimpwiiiiii

 87. Wamogo ndudu ziwiri aaaa ndimawona ngati ndi Embasy zomwe akukumana nazo achina anong’a kkkkkk no pain no gain instead of football player to mogo seller tiye nazoni mpwimpwimpwimpwiiiiii

 88. This is cheap propaganda ! Sheet this newspaper always write false stories, last time you write za Mangichi district hospital, but on the picture you placed Machinga hospital it shows you employed unprofessional and unexperienced journalist ! To hell with your cooked stories kaya akutumani ndi a Be forward mumwa therere chaka chino mtima wanjiru !

 89. This is cheap propaganda ! Sheet this newspaper always write false stories, last time you write za Mangichi district hospital, but on the picture you placed Machinga hospital it shows you employed unprofessional and unexperienced journalist ! To hell with your cooked stories kaya akutumani ndi a Be forward mumwa therere chaka chino mtima wanjiru !

 90. This is cheap propaganda ! Sheet this newspaper always write false stories, last time you write za Mangichi district hospital, but on the picture you placed Machinga hospital it shows you employed unprofessional and unexperienced journalist ! To hell with your cooked stories kaya akutumani ndi a Be forward mumwa therere chaka chino mtima wanjiru !

 91. ndkamat bullets nd team ya ma vendor ndemuzkana……nanga player wa people team kmangulisa fodya ….mukfalitsa tb nd chancer

 92. ndkamat bullets nd team ya ma vendor ndemuzkana……nanga player wa people team kmangulisa fodya ….mukfalitsa tb nd chancer

 93. ndkamat bullets nd team ya ma vendor ndemuzkana……nanga player wa people team kmangulisa fodya ….mukfalitsa tb nd chancer

 94. koma maplayer athuwa nde ali pa ukapolotu yamikani fodya ndi Seventh Day koma akumagulisa nawo fodya guys nzabwino zimenezi

 95. koma maplayer athuwa nde ali pa ukapolotu yamikani fodya ndi Seventh Day koma akumagulisa nawo fodya guys nzabwino zimenezi

 96. koma maplayer athuwa nde ali pa ukapolotu yamikani fodya ndi Seventh Day koma akumagulisa nawo fodya guys nzabwino zimenezi

 97. Zovesa Chisoni Kwabasi,player Anamulemba Ntchito Yampila Pa Ground Akutiso Pita Kunsika Ukagulitse Chingambwe Pamozi Ndimandasiwa Kuti Ulipidwe.Sponsership Yaukapeeeeeee

 98. Zovesa Chisoni Kwabasi,player Anamulemba Ntchito Yampila Pa Ground Akutiso Pita Kunsika Ukagulitse Chingambwe Pamozi Ndimandasiwa Kuti Ulipidwe.Sponsership Yaukapeeeeeee

 99. Zovesa Chisoni Kwabasi,player Anamulemba Ntchito Yampila Pa Ground Akutiso Pita Kunsika Ukagulitse Chingambwe Pamozi Ndimandasiwa Kuti Ulipidwe.Sponsership Yaukapeeeeeee

 100. Iyayi ineyo sindine wa Bullets bt don’t devalue some of our National Team players lyk this inuyo a secretary ndi anzanuwo are responsible to do the advert NOT a player akuthawirani ku Moscotu mwatani kodi? Yesterday in morning Hrs. were in the Capital City Lakeshore minbus area station kubangula moipa

 101. Iyayi ineyo sindine wa Bullets bt don’t devalue some of our National Team players lyk this inuyo a secretary ndi anzanuwo are responsible to do the advert NOT a player akuthawirani ku Moscotu mwatani kodi? Yesterday in morning Hrs. were in the Capital City Lakeshore minbus area station kubangula moipa

 102. Iyayi ineyo sindine wa Bullets bt don’t devalue some of our National Team players lyk this inuyo a secretary ndi anzanuwo are responsible to do the advert NOT a player akuthawirani ku Moscotu mwatani kodi? Yesterday in morning Hrs. were in the Capital City Lakeshore minbus area station kubangula moipa

 103. Akuwazuza anyamatawa ndisaname. Vuto la umphawi ndi limenelo nanga anyamata abwinobwinowa kumanka asatsa chingambwe kwa anayamata anzawo? Sikuonong tsogolo la dziko uku. Kusuta kumaononga moyo osaiwala

 104. UNAMUSEMERA CHINYAU CHIWAMBO KUTI IWE UTASE . CHIWAMBO NDIYETU WOYENERA KUKHALA VICE GS WA BB OSATI IWEYO WA WANDERERS.

 105. thats not true moyo. let them join their friends now. from December to now they haven’t rested ? paja iwetu ndi wa Noma galu iwe moyo

Comments are closed.