Bullets in dire financial need

Advertisement
Big Bullets

Malawi super league giants, Nyasa Big Bullets has appealed to the club’s supporters to help the team financially during its pre-season training.

Bullets technical director Billy Tewesa made the appeal at Kamuzu Stadium when he addressed Bullets supporters who had gathered to watch the team’s first pre-season training on Tuesday.

“We need your support, assist your team with some cash so that we should be giving it to the new players who will be training with us as part of their transport allowances,” said Tewesa.

Big Bullets
Bullets need help.

The Bullets technical director added that starting Wednesday, the supporters will be paying K100 at the gates to watch the team train.

Tewesa then assured the supporters that they will see the club’s new signings in action before the close of the transfer window.

During the current transfer window, Nyasa Big Bullets have signed Muhamad Sulumba from Blantyre United as well as John Lanjesi and Emmanuel Zoya from Civo United.

During the meeting, Tewesa also tackled questions from the supporters on various issues affecting the club.

Responding to a question about goalkeeper Vincent Gona’s injury, Tewesa said that Gona is still not feeling ok and it will take a long time for him to be back into the team.

“Gona is still sick and we are not expecting to have him back soon. But I urge you the people’s team supporters to be paying him a visit from time to time,” he said.

Advertisement

162 Comments

 1. Iwe ndiwe nkaidi wa ntolankhani kwabasi akupeza masapota amatimu ena kapena ku nbb kokha, unaphunzira kuti sukulu ya atolankhani?

 2. U can talk all u want kaya munyoza Malawi 24 kma the truth is nkhaniyi ndiyowona and td wa bullets wathokoza masapota abullets so musamanyoze atolakhaniwa ine nditamva ndimawona ngati munapanga chiganizo chabho kuti mwina enafenso tikhoza kutengela zimene mwapangazi kuti zithandize ma team ambiri kma ndawona kuti fodyayu akupwetekani ndithu kkkkkkkkk

 3. U can talk all u want kaya munyoza Malawi 24 kma the truth is nkhaniyi ndiyowona and td wa bullets wathokoza masapota abullets so musamanyoze atolakhaniwa ine nditamva ndimawona ngati munapanga chiganizo chabho kuti mwina enafenso tikhoza kutengela zimene mwapangazi kuti zithandize ma team ambiri kma ndawona kuti fodyayu akupwetekani ndithu kkkkkkkkk

 4. sono bingi agwila thumba kuopa kugwesa mulandu kkk yawo ija yoyenda ndimilandu nthumba mulandu oyamba chibiliti chamachesi wachiwili rizla wachitatu nyasa nthumba kkkk

 5. ndimkadabwa anthu akamakudandaulani aMalawi 24 mwinaso kukutukwanani ndaonela momwe mwalembela nkhaniyi simunaike mutu wachoonadi musamayambanitse anthu pazazing’ono taonani tsopano momwe anthu ena akulankhulila kunyozana kokhakokha all this because of yu Malawi 24 naweso neba tatanganidwa ndi ZAKO, WHY BUZY ndizaweni?

 6. U Malawi 24 suck! If u hav reporters let them go bak to xul, I was there at the stadium n it was the sapotaz who agreed among themselves to be paying K100 to HELP as transport new recruits who come to try luck at BB and after that sapotaz made contributions to Jaffalie Chande who we learnt has new born baby.At no point did Nsungama say BB has no money

 7. U Malawi 24 suck! If u hav reporters let them go bak to xul, I was there at the stadium n it was the sapotaz who agreed among themselves to be paying K100 to HELP as transport new recruits who come to try luck at BB and after that sapotaz made contributions to Jaffalie Chande who we learnt has new born baby.At no point did Nsungama say BB has no money

 8. Tiyen tigwlane manja pothandza tim yathu kaya akutbela adziwa nd jehovah tisatengele zama tim enawa mpila ndye umenewo .maule woeeee !!!!

 9. Tiyen tigwlane manja pothandza tim yathu kaya akutbela adziwa nd jehovah tisatengele zama tim enawa mpila ndye umenewo .maule woeeee !!!!

 10. Malawi24 or whoever you are everheard of maximising revenue? Does it mean one is broke? Stop mercenary journalism you will lose credibility and fade like a party cloth

 11. Malawi24 or whoever you are everheard of maximising revenue? Does it mean one is broke? Stop mercenary journalism you will lose credibility and fade like a party cloth

 12. Mwasawukitsitsa mpaka k100 pa get kkkkkkkkkkkk nyasa bb imeneyo hahahaha heheheeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeedeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee!!!!!!!!

 13. Mwasawukitsitsa mpaka k100 pa get kkkkkkkkkkkk nyasa bb imeneyo hahahaha heheheeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeedeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee!!!!!!!!

 14. Koma ndiye zafikapo! kkkk…. chingambwe malonda avuta kapena? Nanga mkumati chiyani. Ok. why don’t u just be like ur neighbour? Mubwere ndikupatseni ntchito mugwire ndikupatsani ndalama zokwanira osangozolowera kupempha ayi.

 15. Koma ndiye zafikapo! kkkk…. chingambwe malonda avuta kapena? Nanga mkumati chiyani. Ok. why don’t u just be like ur neighbour? Mubwere ndikupatseni ntchito mugwire ndikupatsani ndalama zokwanira osangozolowera kupempha ayi.

 16. u Malawi 24 y do u like twisting stories? ihate u chomeneeeee supporters were paying those k100 for new players hu r not registered with the club n it was for the gud faith of supporters where else have u heard tht supporters r doing wat bullets suporters r doing? y do u like kuti muzitukwanidwa? and u mn u dnt have editors kuti aziona kaye before u post? shame on u Malawi 24

 17. u Malawi 24 y do u like twisting stories? ihate u chomeneeeee supporters were paying those k100 for new players hu r not registered with the club n it was for the gud faith of supporters where else have u heard tht supporters r doing wat bullets suporters r doing? y do u like kuti muzitukwanidwa? and u mn u dnt have editors kuti aziona kaye before u post? shame on u Malawi 24

 18. Hahahahaha Koma Chingambwe Bullets Mpakana Kulipilitsa Maliheso? Kkkkkkkk Pepa Neba Chakachino Kulibe Fodya Wakanika! Kkkkkkk

 19. Hahahahaha Koma Chingambwe Bullets Mpakana Kulipilitsa Maliheso? Kkkkkkkk Pepa Neba Chakachino Kulibe Fodya Wakanika! Kkkkkkk

 20. Mukutiputa a Bullets tiliphee,tikayankha nde muziti mavenda,mbuli,mabwana,madona,mapalestina,maulee,masapota olutsa.u malawi 24 give its noble respect NBB, research to find details not headlines

 21. Mukutiputa a Bullets tiliphee,tikayankha nde muziti mavenda,mbuli,mabwana,madona,mapalestina,maulee,masapota olutsa.u malawi 24 give its noble respect NBB, research to find details not headlines

 22. Apatu mukupanga Ma comment a chipongwe zingosonyeza umbuli,akuti ndalamayo its for the new players trying their luck,vuto munkathawa school kumakasewela bawo ndi agogo!

 23. Apatu mukupanga Ma comment a chipongwe zingosonyeza umbuli,akuti ndalamayo its for the new players trying their luck,vuto munkathawa school kumakasewela bawo ndi agogo!

  1. shoiab bwanali,dzina lokhalo likuonetsa kuti ndiwe mnchawa weniweni ukuchita kukanika kulemba Ma right spellings apa,inu muzikangoweza nsomba olo utelala musaoneke ochenjela pagulu,zankhope yanu sindikamba chifukwa ndiyomvetsa chisoni,zikomo!

  2. shoiab bwanali,dzina lokhalo likuonetsa kuti ndiwe mnchawa weniweni ukuchita kukanika kulemba Ma right spellings apa,inu muzikangoweza nsomba olo utelala musaoneke ochenjela pagulu,zankhope yanu sindikamba chifukwa ndiyomvetsa chisoni,zikomo!

  3. Iwe naweso anenapo za ma new players apo,,anena kut bullets is in dire financial need,,,,onetsetsa bwino mudala iwe

  4. Iwe naweso anenapo za ma new players apo,,anena kut bullets is in dire financial need,,,,onetsetsa bwino mudala iwe

  5. koma guys kodi phone yanu imatha kungowelenga heading yokha sitha kutsekula nkhani yonse?hihihihihi,tawelenga zomwe wanena tewesa musimo that is ngati phone yanu itatsekule!!!!!kkkkkkkkk!!!!

  6. koma guys kodi phone yanu imatha kungowelenga heading yokha sitha kutsekula nkhani yonse?hihihihihi,tawelenga zomwe wanena tewesa musimo that is ngati phone yanu itatsekule!!!!!kkkkkkkkk!!!!

  7. mun2 omvetsa chisoni iwe…ndiye kuphunzirako kuli pati ngati ukukanika kuwerenga zomwe ndalembazo…kuda ngati unachita kulozedwa

  8. mun2 omvetsa chisoni iwe…ndiye kuphunzirako kuli pati ngati ukukanika kuwerenga zomwe ndalembazo…kuda ngati unachita kulozedwa

  9. Hahaha!!!nanu phone yanu ikukanika kutsekula nkuwelenga what the Technical director Mr Tewesa has said bout kuti Ma k100 ngachani?hihihihihi!!!mwangowelenga heading yokha?hihihihihi!!!iwe sindilimbana nawe coz sinaonepo Mdyomba wanzeru,tizakangoweza msomba apa!!!hihihihi!!!!ndukumvetsa poti anzathu inu za xul izi simbali yanu,inu Koma kujoni kuseta Ana azungu basi.

  10. Hahaha!!!nanu phone yanu ikukanika kutsekula nkuwelenga what the Technical director Mr Tewesa has said bout kuti Ma k100 ngachani?hihihihihi!!!mwangowelenga heading yokha?hihihihihi!!!iwe sindilimbana nawe coz sinaonepo Mdyomba wanzeru,tizakangoweza msomba apa!!!hihihihi!!!!ndukumvetsa poti anzathu inu za xul izi simbali yanu,inu Koma kujoni kuseta Ana azungu basi.

  11. Guys ine ndamva dzulo kuti ndalamai its 4 the new player amene akuzayemwai ku Nyasa bullets kodi mesa ndizothandiza ma player anu womwe zimenezi sikuti ndizabodza mukanamvera Tnm soccer show pa zodiak dzulo mukana TD wanu anathokozanso masapota chifukwa chaganizoli

  12. Guys ine ndamva dzulo kuti ndalamai its 4 the new player amene akuzayemwai ku Nyasa bullets kodi mesa ndizothandiza ma player anu womwe zimenezi sikuti ndizabodza mukanamvera Tnm soccer show pa zodiak dzulo mukana TD wanu anathokozanso masapota chifukwa chaganizoli

 24. This Is Total Rubbish, A Malawi 24 Ndinu Mukupangisa Kuti Masupporter Azinyozana Chifukwa Cholemba Nkhani Zabodza ,get lost.

 25. This Is Total Rubbish, A Malawi 24 Ndinu Mukupangisa Kuti Masupporter Azinyozana Chifukwa Cholemba Nkhani Zabodza ,get lost.

 26. haha..its funny how you the malawi 24 guys twist stories to capture people’s attention…the way you dilute news is nauseous..i was there yesterday and it was supporters who agreed they should be paying on the gates so that the proceeds should be given to the trialists..if my memory is doing me justice i remember seeing no bullets official begging for k100s..haha..your journalism leaves alot to be desired..but somewhat i comprehend or these needlss gimmicks,you wanna more pple to like your page and site

 27. The money is meant for those players trying their luck at the club who are not registered by the club coz the club cant gve them anything

 28. Mukumbenso chimbudzi ku clubhouseko cholipilitsa. Ndindindi K100 wawawa K50

Comments are closed.