Former Malawi under-20 national football team wonder kid, Chawanangwa Kaonga, has refuted rumours linking him to two Blantyre giants, Mighty Be Forward Wanderers and Nyasa Big Bullets.
Kaonga who plays his football in Mozambique for Chibutu FC has revealed his position on the matter through a social media post.
According to the post that Malawi24 has seen, the player suggests that he will rejoin his former club if he returns to Malawi.
“My heart is still at Silver Strikers and not what you are talking about,” reads Kaonga’s post.
Since last week, people have been has been spreading rumours on social media that Kaonga is discussing with the two Blantyre clubs for a possible move.
Kaonga joined Chibutu FC of Mozambique Macombola League last year from Lilongwe based side Silver Strikers FC at a fee of about Mk7.5 million.
Silver imapangazake mosanyoza mateam ena kapena player koma mateam awirinu i don’t know. Ndichifukwa zochitikazanu simumasiyana ndima street kids mifunda yamateam mwasintha mwasinthaso. Mawa timva kuti ndi bb nyoni, timvaso inayo ndi noma pilirani. Weniweni mwanaochangilana wakuchibuku taven he heeeeer
Khala chete kape iwe ife mwatiputa dala
Osalimbana ndi mapulea gyz pangan zakoch chifukwa nde yemwe akulakwitsa mapulea

osadanda maule ife tiatenga ma star okhaokha makape, ana ayi maule woyeeeeeeeeeeeeeeeee!!!!!!!

kaonga ndi machine
kaonga ndi machine
Atha chomcho uyo.
Atha chomcho uyo.
Amkasewera kma ku bb alibeko malo
Amkasewera kma ku bb alibeko malo
Amene akunyoza chawa ndi mbalame ya munthu ndi chitsilu chenicheni ndi golo liti limene cawa sanaikeko chigoli kuno kumalawi ndiyambile iwe wa chingambwewe cawa wakuliza kangati chifukwa choti mwatenga league kawiri nde mutifute iweso wa nomawe iwe nde ngati pali team yokakanika nde ndiwe basi blantyre kungokhala mbalame za ma team baxi agalu achabechabe

Iweyo nd chawa wakoyo nose makape muzpanga zanu ngati akutha bwanji osamusayinixa contract ina watha ameneyp bax
Iweyo nde kape ndi wathu amene ija
Nde kuzindikira kumeneko
Amalawi tilindivuto lolephera medication makamaka masapota ama team awirinu bb ndi nyelele. Nkhani iliyose yosakukomelani mumasogoza kunyoza motukwana, kodi kumeneko ndikuzindikila zinthu kapena bwanji? Ine ndimawona ngatiumbuli otheletu chomatukwanila munthu ndichani poti aliyese ayenela kukhala ndi choice popanganga zinthu chosecho enanu mumatchedwa Ababa mukafika mumanyumba mwakwanu
Uwauze asama lembe zabodza AMalawi 30 wa wamva.

Ife timadana nd boza muuzane mwatiyamba dala nd ku daphuzra kwathuku a xul inu chamba chanucho ife ayi
Kkkkkkkk aaaaa Chawanangwa anathakale kale ndiye Bullets yake iti ingamufune mwina nomatu.

Kkkkk ndie mwati #Thumbidwa?
Kkkkk ndie mwati #Thumbidwa?
Ndatsimikidza kut atulankhani a Malawi24 ndimbudz unavako liti kuti Big Bullets ikufuna kumutenga mthumbidwa imeneyi akanakhala star bwenzi aliku moshko konko nanga walepheleranji ntchto ameneyo lol silevel yake NBBFC
WANENA ZOONA ATOLAKHI ATHU NI NIMBUZI

Afera komko kapeyo. Kodi akuzitenga ngati ndani?

Sanasayine contract ina ku Moshiko bwa? Phala lenileni ili

We don’t need him ………. we won the championship while he was at silver in 2014..he can go back there and continue clapping hands for us the champions

Amarawi Tikamasewera Npira Tizsewera Ndcoringa Oky

Kufalitsa nkhani zabodza ngati izi atola nkhani ambiri akhara akuphedwa pa dziko pano kamba molemba nkhani zanyansi ngat izi,,

Mpira wake wakuti omwe kape ameneyu ife a BB tingamunjenjemere adasewelako ooneka ku anthu ? za ziii

Mwana ozindikira chawa ndili panbuyo pako
Kkkkkk koma yah xul yavuta apa lol
Kkkkkk koma yah xul yavuta apa lol
Manyaka eni eni!!
Manyaka eni eni!!
Iwe ndiye wabodzatu moti ukuwanamiza anthu pamenepa zamanyi basi

And We Dint Need Him Omwewa Alipowa Bullets Nd Fire U Know

Samatha uyu
Samatha uyu
Hehehehehehehe koma ndi chizungu kkkkkkkkkkk ayi ndithu u stand us amalawi 24

Bwera ku mabluez,udzaone ku xintha.
Koma ineeee ma journerlist a pa Mw amandimvetsa chisoni ndi malembedwe awo a nkhani, no professionalism.

a malawi 24,kodi mukufuna kutchukisa kanganya uyu kwa ma big team bwanji? osangolemba za team yake ya silver yo bwanj

mumazitenga kuti kodi nkhani zopusazi?
mumazitenga kuti kodi nkhani zopusazi?
Anatha ameneyo ife ciukepa alipo
Anatha ameneyo ife ciukepa alipo
U should have reported that “former silver strikers forward has snubed bb and nyerere” not the way u did, that is bias at its best, dint he have a club when he left??
The one in sky blue kkkkkkk it doesn’t make sense serious
These janalists they report sports issues as if bb and nyerere are only clubs we have in malawi. Zimandikwana bwanj!

A Malawi 24 Pliz Musatiipitsire Mbili Ife A Bullets,,we Have Never Approached Chawanangwa Kaonga As U Re Putting It Bt Our Traditional Rivals Wanderers Are In Pursuit Of Former Silver Strikers Red-hot Striker…