Kanyenda shines in SA

Advertisement
Essau Kanyenda

Malawi national football team striker, Essau Kanyenda, on Saturday afternoon helped his club, Polokwane FC, to beat Jomo Cosmos in the Premier Soccer League (PSL) of South Africa.

Kanyenda scored an opener about 6 minutes into the first half and made the match to be 1-0 till halftime.

Essau Kanyenda
Kanyenda : Scored.

In the second half, Jomo Cosmos who features another Malawian player, Micium Mhone, equalised on 68 minute to push the score line to one all but Polokwane scored the winner 10 minutes before the last whistle.

Kanyenda is having good times in this 2015-2016 PSL soccer season in the richest Southern African nation as he has been helping his club to win games many times.

His performances in the PSL this season have impressed local clubs such as Silver Strikers, Big Bullets and Mighty Wanderers who have been approaching him several times to play for their respective clubs.

His contract with Polokwane expires at the end of this PSL season and according to reports, possibilities are high that the club will renew his contract.

Advertisement

82 Comments

 1. Timavera inu a Malawi mukamadandaula zambiri,zokhudzana ndi ndalama.Masiku ano ku Malawi ntchito idatha kwatsala ndi mavuto ofuna kulandira ulemu basi kuti”sir”osati ndalama zokwanira pa umoyo watha.Ine n’sidzalembedwa ntchito yongofuna ulemu kuposera ndalama zokwanira,Kanyenda was right to say like. that

 2. A malawi muli ndi vuto,esau walakwa chani? akanakhala kut wanena kut sazamenyaso flames bwezi mukulalata zanuzo koma iye akunena monga mwa tchito yake nd perfomance yake pomwe iye akuziwonela osati pomwe mkumuwonela inu, ikazasika perfomance yake pomwe azaziwonele yekha azamenya ma club akunowa komaso pokha pokha atamutaya ma club aku jon anachokela kuno ku via ku jon kenako rasha pano akubwelela rasha,jon kumalizila malawi masiku ano mpira nd dola osati wa nsima unatha, basi azivutika kufela poti nd ma club akwanthu praya akati wagwila dola yambili pa czon k2000,000

 3. Hazard ndiye amalandira ndalama zambiri ku chelsea,koma chiyambireni cha season wachinya chigoli chimodzi.Polokwane city imamenya mu league yayikulu ku joni.osamanamiza anthu apa.Kanyenda ndi star basi mukuyenera kuvomekeza ndithu zimenezo.

 4. Mthengo mudalaka njoka, sindidzanyoza kwathu jst bcoz am doing something out of my country. I can enjoy anyhow koma time will come for me to remember my home village. H. K Banda, how long did he took kwa aluya? Atamva mmimba anavaya kwao. Zifukwa nzochuluka that can make u remember home. Malipiro ochepa omweo ife momuno basi

 5. Kanyenda shud not spoke lik dat cuz he,s old and de perfomanc is down alredy,do u think which team in africa can take him? Only de un known teams.

 6. Tieni tiyamike kuti wapeza tchito kwina malo akewo enaso apezako mwai tchito, zoona zake ndizoti hmmmm kwathuko sikulibwino.

 7. Big up Mr Kanyenda, mpila wakuno mukhoza kuyaluka nawo, if its gonna be tym to retire do it konko. Ambili akunyozawa there the same azakunyozeni mutapanga zozasewra kuno. Be like Maduka enjoying life there. Kungoyerekeza kuzamenya matimu aku ull be like a sponsor to the club. ” tithandizeni ma boot, jersey yatha, player wina mumva pa den sipali bhoo, ndilibe airtym nde ma player akuno ku Malawi. Keep playin in RSA till u retire. Big Up! Esau Kanyenda.

  1. Man ine ndikuvomereza idea yanuyo coz kuno ndiye munthu owudoda atha kupusirakod.

 8. Ngakhale garden boy ku south africako akulandila malipilo oposa ma General manager ena aku Malawiko ,kungokhala dzina chabe kuti manager koma malipilo ochepa, tsono ngati mukuona kuti kanyendayo walakwa, papezeke team kumalawiko imuitanitse ndipo izimulipila ndalama zomwe wanenazo, nanga simukuona kuti iyeyo akukunyadilani, mpatseni malipilowo tione that’s only the solution, mumakakamila zinthu zautsilu zoti simungazikwanitse, am from pretoria.

 9. his job is to score goals. equally if he was a robber he could be robbing. there is nothing like kanyenda shines in SA.

 10. Never ask for what your country should do for you but rather ask for what you should do for your country. That’s what patriotism is all about #love for your home land.

 11. Nkhani siyochepa malipiro. Palibe paziko pano ndinamumva ine akuti malipiro anga ndi okwanira mundichepeseleko pang’ono ayi. Koma kuti mundionjezere. Ndalama yakunja sungaifanizire ndi yakuno ngati zinthu uzigula m’makwabha ayi

 12. Kanyenda, poti ndiufulu olakhula zomwe ungalakhule koma pachichewa pali mau amati tovi tonya mwana tinapaka wam’kulu.

 13. Olo azizakhals ku nyumbakwanu? Apangazake musalowese ndale sizachipani izi pila amasewera ngati ntchito ndiye eapeza malipilo omukwanila musamuzonde fokolo ee mbwe! Mbwe! Nensnizina zomwemufunila .

 14. Anakalamba asiyeni zelu zachepa madalao kunoso akudziwa kuti azakhala pa beanch, zake wina ndiuyu akukalambila pampando ku Ku Dr congo moti abwereko ataa kakaka

 15. Akunyada zichani? Mpirawo aphunzirira kuti? Club yake iti? Zigoli zake ziti? Chimodzi basi?

 16. Kumalawi kuno mavuto anyanya katundu amakwela mtengo koma malipilo osakwela nyanja yeniyeniyi timakanika kupitako kukasangalako moti ena amangoyiwonela pamap olo panyuzi chifukwa chochuluka mavuto ndiye uyu sanalakwitse kukana chifukwa mpila wakuno amatukuka ndi maoficiol osati maplayer

 17. kachigoli kamidzika ndiye timve mimba abale . a week of lst week team yake idakwapula super sport ndi zigoli 4 kwa 0 koma iyeyo ali momo ta kake ka chigoli,week yathayi team yake ina menyedwa 5 kwa Du! ndi wits iyeyoso ali momo koma anabwereramo osawona net. ndiye musanamuyamikire munthu mudziyamba mwaona work Rate yake.inde munthu akachitabwino ofunika kumuyamika kom osati kupopa ayi

 18. Mmm ozikonda uyu.kodi suja amasewera ku Dwangwaa uyu ndie azinyoza kumudziii.Adzabwera azatipezaa kunali anzake azatipezaaa

 19. Amkayankhulaso chomchi Ben Mackcathy, he finally made a U turn to Pirates, amufuseso Bernard Paker amkateroso lero aliku chiefs, off course yes malipilo ndiwochepa koma mau osiyiza anaombola kalulu

 20. ndi zoona ku Malawi malipiro ndi otsika koopsa moti olo kuti uchite survive pa Malawi simasewera, uone rent, xul fees ya ana, chakudya, transport ya ku ntchito ndi zina zambiri zofuna ndalama aaah mavuto ndithu osangalala ndiochepa pa Malawi, mabvuto tili nawo ndithu

 21. kulibe ndalama kuno musiyeni munthu apange tsogolo zakuno player kudwala mpaka kumwalira osamusamala? whats that? Malawi ali pa moto.

 22. Kunena zoona kumalawi malipilo akanalipansi kwambili pomwe zithunso ndizodula kwambili ndiye kwamunthu amene anailawapo rand ndikovuta kukagwilanso nchito kumalawiko

  1. There is a problem.he cud av jst said kt sakukhala bt to say wat he said,its wrong.he was brainwashed in malaw.kut akafke komwe aliko its all cz of malawian teams so to say wat he said,its totally wrong. remember,wen u boost urself,God can pull you down.evrythn wil end weaeva he is.azatipeza kwao nd kuno!!!!!

 23. Vuto ndiloti amalawi ambiri timadanandichilungamo. Kodi iyeyu akanati sindikufuna kusewelanso ma local cubs akumalawi. Kodimesaukanamufusa kutinchifukwachani. Ndiye munthu wakuuzani momvekabwino mukuti ngozikonda. Koma akanalankhulabwanji kutimuvesese? Enampaka kumanena zambiri no noooo its time for him to make more money for hiz future not just to pliz some1 like the way you talk now guys. Let’s jus accept that time changes. I do like this guy no matter wt.

 24. Amenewo nde star wa flames amene ndimamuziwa bwino since ndinayamba kuonela balls osat ma coach enawa samamuitanatu et, mantha basi

Comments are closed.