Breaking: Police shoot three vendors in Limbe

Advertisement
Malawi24 Breaking News

Malawi Police officers in Limbe, Blantyre have this evening shot three vendors who were doing their business at a restricted premise close to Block Buster shop leaving them with serous injuries, Malawi24 can confirm.

When Malawi24 rushed to the scene a few minutes after actual incident, it only found one victim who was shot on leg and by that time in great pain with the others already ferried to hospital by a speeding sympathizer.

Malawi24 Breaking NewsWhen this reporter tried to interview the victim on what really happened, he only managed to identify himself as Martin Masuwa and he failed to explain more because he was failing to speak due to pains.

But according to one eye witness, Andrew Mafude who was at the scene when this was happening said police were in a Blantyre City Patrol vehicle with some Blantyre City officers when the fired at the vendors.

Mafude explained that other two victims who were critically injured were taken to hospital using same vehicle (Blantyre City Patrol) and they left one at the place.

The two, a woman and a youthful looking young man were rushed to hospital by some ‘Good Samaritans’, according to witnesses.

The woman who was selling fast foods was shot in the head while the young boy was shot in the abdomen, Malawi24 has been highly informed.

“A polisiwo anasika mu galimoto ya City ndikuyamba kuwombwera nyamata yemwe amafuna kutenga ma face a phone (amuombera pa mimba)omwe amagulitsa kuti athawise kuti a City wo asamulande, kenako awomberanso mmutu mayi yemwe amagulitsa zitete zake kenako ataona bambo wina akuthawa ndi ma ambulera omwe amagulitsa anamuombera pa mwendo.” said an eye witness in the vernacular Chichewa and has narrated the whole incident.

Masuwa shot on the leg and bullet is still there was then taken to hospital by Malawi Indian Nationals.

Police were yet to comment, when this publication made this post.

MALAWI24 WILL KEEP YOU UPDATED ON THIS

Advertisement

516 Comments

 1. Anthu enanu ndizitsiru kwambiri chifukwa simuganiza mokwanira.inu mukudziwa kuti mwala umapha ndiponso mfuti imapha zikusonyeza kuti aliyense anakonzeka kuziteteza bcoz wonse anali armed.Do you think a police amapanga training yozinda miyala?A malawi zibwana kukabwera wakuba wa mfuti mumathawa yet mfuti yomweyo akatenga wapolice mumadelera why.musamanamizane palibe wapoli angatenge mfuti yopanda zipolopolo.mukapitiliza kugenda a police ali ndi mfuti mudziphedwabe until you learn to respect ur police.only those who have gone thru police training can understand kuopsa kwa angry mob.enanu muzingokamba za prossional yanu.

 2. I don’t know how to comment. I feel the story is not complete. It’s a long time since I heard that police officers have shot people like this. Tell us the whole story. Malawi24, you are experienced in writing stories that contain half-truths. Please be professional. If you haven’t captured the whole story, indicate in the story rather than pretending that you have investigated the matter thoroughly. You don’t have freedom to misinform Malawians. Wishing all victims quick recovery.

 3. choyamba ife anthu akumudzi tiyeni tiwapase wulemu apolisi fuso nali wapolisi angangochoka uko ndikuyamba kuwombera anthu?

  1. Iwe hule iwe ukhale chete ndpo mulonda wachita zimenezoyo ngat ali chibwezi chako umuuze kut palipose azyenda nd mfuti chisoni naweso ulibe mfiti yayikaz iwe Mulungu akulangen ndthu

 4. Please jonourlist, know that whatever you write is the cause of war or peace. Police officers are not mad people. They work according to their own risk and rules. Please. I understand that people themselves started to throne them, then in return they short people because they don’t have stones. The short wasn’t just a short but it was an exchange. Please give us true stories not this lie.

  1. Ada iweso uzyankhula bwino utakhala kit ndwe wawomberedwawe ungamve bwanji A malawi tiri nd ufulu osaomberedwa ngati talakwisa aztmanga malamulo azikagwira nthito not lyk dat

  2. Man, sindinatero kuti apolisi sanalakwe. Koma as a person of concerned, nkhaniyi ndaufufudza amwene. Apolisi amadutsa, ndiye mavenda anayamba kuwaponyera miyala monga mwa mchitidwe wao ku Malawi ko. Now, you think kuti iwowo ayang’anire kugendedwako? Ndu nzeru zopusa kulimbana ndi boma kwenikweni akapotasima ngati ife. Only that aomberedwa ndi osalakwa. Koma pali mwambi oti;paphya sitolo palibe kuwerengera.

 5. Kwa amene amapitapita mtaunimu sangakondwe ndi mmene amachitila mavenda tangoganizani mukamatsika mastep a pa shoprite paja kapena pa people munthu kulephela kuti udutse ndi kajumbo kako chifukwa cha anthu amene amagulitsa zinthu zao mmalo amene anapangidwa kuti mudzidusidwa ndiye pofuna kupewa zambiri anthu ogulitsa zinthu mmalo osavomelezekawa achokeletu.

 6. Munalephera kuthana ndimbava za mfuti ku OG industries mukungolimbana ndianthu osauka. Ngati mumadziwa ntchito osathana ndimbava zamfuti bwanji. Zoona muzilimbana ndikuombera ana ndiazimayi osasiya upolisiwo bwanji

 7. Kwa anthu omwe mukulemba macomment opusa onyoza police tinene kuti ndinu akumizi?munaonapo munthu akati walusa akugenda apolice?mmaziwa kuti wapolice ndimunthu ngati iweyo?akagendedwa amamvanso kuwawa kumvesesako akhale apolice okha osati iwe eti?zigendani aziona zochita okha uli iwe ungatani akukuphwanya ndi miyala mmutu?

 8. Kwa anthu omwe mukulemba macomment opusa onyoza police tinene kuti ndinu akumizi?munaonapo munthu akati walusa akugenda apolice?mmaziwa kuti wapolice ndimunthu ngati iweyo?akagendedwa amamvanso kuwawa kumvesesako akhale apolice okha osati iwe eti?zigendani aziona zochita okha uli iwe ungatani akukuphwanya ndi miyala mmutu?

 9. Kwa anthu omwe mukulemba macomment opusa onyoza police tinene kuti ndinu akumizi?munaonapo munthu akati walusa akugenda apolice?mmaziwa kuti wapolice ndimunthu ngati iweyo?akagendedwa amamvanso kuwawa kumvesesako akhale apolice okha osati iwe eti?zigendani aziona zochita okha uli iwe ungatani akukuphwanya ndi miyala mmutu?

 10. Malawi is just poor country so pple are trying to do small businesses to earn aliving in order to avoid stealing you are killing them instead of promoting them do you expect malawi to develop..?? These silly rules are not suitable for this poor nation,lets learn to act like we are human beings by recognising the human diginity of us poor pple we struggle for everything its unlike to you rich pple pls here our cry……!!

 11. kodi mungonyozi chifukwa chomwe anaomberera anthuwo mwachiva? komaso akanaphedwa wapolice mukanati osadziwa ntchito ufulu uli ndiudindo apoliceso ali ndi ufulu mavendanuso matama mumaonangati dzikoli ndilainu nokha mumatipinga mochoke ku flea markert ma sherter ngambiri mupite kukapeza

 12. Keep it up apolice.mumazisiya kuti nthawi yonseyi.
  Ma vendor ali ndi malo onwe ife timakawagula osati pali ponse palibenso nkhani apa. simunamuomberere pa bench pake. zisakomere mbuzi ku galu

 13. Paja zimakomera mbuzi kugunda galu inu mumafuna avulazidwe ndi minyala amaponya mavendawo nawoso alindi mabanja sibwino kumakhalira kuwagenda anthuwa sizinyama nawoso ndianthu mavenawo samaziwa malamulo opangilako malonda? inu simumaziwa kokagula malonda .

 14. Paja zimakomera mbuzi kugunda galu inu mumafuna avulazidwe ndi minyala amaponya mavendawo nawoso alindi mabanja sibwino kumakhalira kuwagenda anthuwa sizinyama nawoso ndianthu mavenawo samaziwa malamulo opangilako malonda? inu simumaziwa kokagula malonda .

 15. Amene mukunena kut apolice Ali bho matangara anu kapena abhuja wanuo, ukamat Ku phunzira ufuna unene kut chan? Ndadana nanu

 16. Apolice ali right coz anthufe tinajayira ndi zoti wa police sangaombere munthu zoona but for the sake of security alibo coz akanafa ndi miyala. So my fellow malawians dont judge before debate. Tiye tisamale ngat wapolice kukhazikisa bata

  1. That’s where police brutality comes in.Cops are taught many ways to defend themselves before they think of shooting. I can sense they used live bullets .

 17. Vuto amalawi timathawira ku xul kufuna uvenda chonsecho timkakhoza bwino pano mukulimban nd wapolice amene ali pa ntchito yake y stoning y? Police! Police shut 2 kill

  1. Iweyo nd chisiru pamodzi nd azlonda akowo muuzane monga mzika za Malawi tiri nd ufulu tikalakwisa kumatmannga not kutombera kunyadira ulondawo timalipiroso tochepa y azlonda aku Malawi zomvesa chisoni kwambiri.Mmalo mot muzrimbana nd mbava mukulimbana nd anthu ogulisa marcharger kut akasamale ana ake olo chisoni mulibe mfiti inu Mulungu amukanthe nose amene muli nd Maganizo amenewo

 18. Kumlanga bwanji Komshuta mwendo mleke mzako, ,,,,,NGati Amalawi akadagona nde Kuti dziko lathu ndimalotooo, dzuka Malawi dzuka ndikale lija unayamba kugona

 19. Tsopano chikatele muti tchani kweni kweni? Munthu akupanga geni yake kuti akadye ndi ana kunyumba inu mukumushuta mwendo kodi kweni kweni a Police chimakhala chamba? kapena umunthu mulibe. Muli nditsoka dats wy police people simumalemela shupiti

 20. Ndichomchotu zitsilu zimenezi akazipatsa mifuti zimangoombera ndi mbalame zomwe. Muwalande abwezereni ndodo zawo zija asanayambe khondo kuno.

 21. Ndichomchotu zitsilu zimenezi akazipatsa mifuti zimangoombera ndi mbalame zomwe. Muwalande abwezereni ndodo zawo zija asanayambe khondo kuno.

 22. kodi apolice mumakasayinira mfuti ma office mwanumo mmati mukukagwira ntchito yanji???? basi bola kuwombera .shame on you

 23. kodi apolice mumakasayinira mfuti ma office mwanumo mmati mukukagwira ntchito yanji???? basi bola kuwombera .shame on you

 24. Kale kale dziko likadali ndi mphonje nyama zilipo mthengo,mitengo ili katukatu tchire lobiliwira lili posepose izi kudalibe ,malawi wa lero ndiye mmmm udzifuse wekha kuphana ngati nkhuku mmmm dziko lathu liri kupita kuti.

 25. Kale kale dziko likadali ndi mphonje nyama zilipo mthengo,mitengo ili katukatu tchire lobiliwira lili posepose izi kudalibe ,malawi wa lero ndiye mmmm udzifuse wekha kuphana ngati nkhuku mmmm dziko lathu liri kupita kuti.

 26. Apolisi ndinu akuba kwambiri,ena mwalemera chifukwa cha mavendor omweo,policeman salemela osabela munthu.zikukukanikani,ngati ma gays ali ndi ufulu y not vendor? mumakhalira kupempha inu mbuzi za anthu

 27. Mapazi anu nonsenu komanso muwawuzekenso munyumbamo akazi anuwo kuti matako azikang’a awoooooo police yochititsa manyazi padzikolonse lapanse

 28. Is dat wat dey call law enforcement? I dont even no if in Malawi, one deserves a death Sentence by simply vending at a wrong place.What is becoming of dese constables? Is dat wat Dey r tought at deir trainings? Help me plz! I want 2 know.

  1. Show off indeed! tryn 2 get respect 4rom de civilians by force.Bt dis behavior of killing deir fellow citizens’ll jst fuel up de enermity dat’s already existing btwn demselves & deir sorounding comunities.

  2. Show off indeed! tryn 2 get respect 4rom de civilians by force.Bt dis behavior of killing deir fellow citizens’ll jst fuel up de enermity dat’s already existing btwn demselves & deir sorounding comunities.

 29. Koma guyz kkkkkkk mumafuna apolisi asiye mfuti zawo nkuyamba kutola miyala ndikumabwezela? Iwo mavendawo samaona kut apolisiwo ali ndi mfuti? Amalawi osamangodzudzula mokondela mbali, mudziwa kuti miyalanso imapha? Akanaphedwa wapolice ndi mwala bwez mukuti wa police oopusa.

 30. Ma comment achuluka apa nd amalova komanso anthu oti u dont knw dc place called limbe, wa malawi 24 sanafotokoze bwno on wat prompted de offcer 2 use de firearm. Wat if some of de vendors wantd 2 grab him de rifle? Enanu ndkadakonda munditumzre ma particulars anu mwna nkukuchtan consider intake ikubwerai mukuoneka mutha kugwra bwno ntchto ya police koma o in o its a challenging job. Jst hit ku inbox yanga 4 more info mupeze chochta achinyamata.

 31. Kunena mosabisa komaso mosapsyatila mau, apolice onse amene apanga nkhanza zimenezi pamtumbo panu nose panyapanu. Akanakhala akaz anu amai awombeledwao mukanamva bwanj? Anyani musandiyankhulise pambali a woman should be respected machende anu ndithu.

 32. Police officers are trained on how &when to use rifles(shoot) based on Firearms Act. If men on duty have violeted this Act,they will face a law in court.As of now i can’t fault these officers,till the matter is fully investigated. kkkkk malamulo akutinji pankhaniyi?

 33. nsonda wati muzishuta ma guy osati mavenda,,,,FAQ Malawi police,,,, muli shit,why always mmapanga parralel with public expectation in public issues

  1. Apolis Sanaphunzitsidwe Kut Azipanga Zofuna Zaanthu Ai Koma Zomwe Malamulo Akufuna.Malawi Police Si N.G.O Man.Mfut Amatenga Ndizophera Anthu Ophwanya Lamulo Tsono Sibwino Munthu Kumatamika Pagulu Lophwanya Lamulo Wapolis Wamfut Alipompo U Will Be A Victim Aise.

  2. Umeneu nde uchitsiru wa police wo, palibe lamuro loti wa police a ombele munthu ngati ampeza restricted area only if munthu akuyambisa chisokonezo a use luber bulet nt real bulet

  3. Umeneu nde uchitsiru wa police wo, palibe lamuro loti wa police a ombele munthu ngati ampeza restricted area only if munthu akuyambisa chisokonezo a use luber bulet nt real bulet

  4. Ngakhale Ruber Bullet Ukunenayo2 Imavulaza Ndipo Sapnya Ndimanja Amaika Mumfuti Ndikuombera Koma Munthu Samafa Ngati Momwe Zakhalira Kulimbeko,mavemdawo Angovulala.

 34. Some must be held accountable for this unprofesional shooting. That is dangerous how can a police officer open fire to a non threat citizen. Maybe they are other reasons apart of selling in restricted zone. That can cause crime to rise in our beautful country. Pple wil lose trust in police and who knows have ilegal firearm to fight back situation like that. Noone want to die so minister whoever in power relook in situation like this. South Africa is in crisis of police killed by civillian and the digits are scary. Who know Malawi lets avoid this tumoil b4 its to late. Police and comunity lets work together than fighting unnecesary showoff of firearm in public

 35. Mboli Zanu Mmalo mokalimbana ndi ma gay mukupha ma vendor? We are now refugees in our own country! Zitsilu inu muzingolandilabe tima salary tonyenyekato ndikumvera zopUsa kwanuko MxieE! Agalu inu ndakwiya nanu kwambili

 36. kumanena zoona apa basi apolice anagowapeza mavendawo akugulitsa malonda awo mkungowombera? Ndikumudziwa venda ine anawaputa ndie mumafuna mavendawo avuladze kapena kupha wapolice ndie muzinyodza apolice kuti ndiopepela? Awachita bwino makapewo mavenda amatenga ngati akati town ina iliyonse anamangira iwo basi kupusa mavenda muziwathira machaka mazobawo amaphweketsa

 37. If this is true it is very bad…Because A Police akumalawi ndi anthu wovutika kwambiri chifukwa they are paid little money and some of this vendors selling Mazira wophika are their own children..How could they do this..I wonder..kkkkkkkkkkk.

 38. A police sangayambe kuombera mavenda ongokhala.Ngati mumagenda ndiye asakuombereni.Sitingasekelere zopusazi.Kodi a police mumaona ngati makape eti.Police singasekelere zimenezi.Onse ogenda police ayenera kuomberedwa basi.

 39. A police sangayambe kuombera mavenda ongokhala.Ngati mumagenda ndiye asakuombereni.Sitingasekelere zopusazi.Kodi a police mumaona ngati makape eti.Police singasekelere zimenezi.Onse ogenda police ayenera kuomberedwa basi.

 40. Police, u have started it againo,i beg we dont want bloodshed! please dont start what u can’t finish,let me remind u, most of u,are living in our ranted houses, we can finishe well well,if ur government is telling u to do it this way,hey we r fully prepared,don’t try to draw a battle line,when a lion is sleeping, don’t think it is dead! we r watching!!

 41. Police, u have started it againo,i beg we dont want bloodshed! please dont start what u can’t finish,let me remind u, most of u,are living in our ranted houses, we can finishe well well,if ur government is telling u to do it this way,hey we r fully prepared,don’t try to draw a battle line,when a lion is sleeping, don’t think it is dead! we r watching!!

  1. Naweso ndwe opusa wamva ngat ndwe londa wapolice muuzani ife nd A MALAWI NDIPO TIRI NDI UFULU OKHALA NDI MOYO NGAT PENA PALAKWIKA MUNTHU KUNGUMUMANGA MALAMULO AKAGWIRE NTCHITO. Tipite mayiko azathu no mtendere kwathuso ufulu njeeee mukufuna a Malawi titani muuzane mwayambayo nd Fodya wamkulu kunyadira ulondawo

  2. Ndavomera..!Aliyese ali ndi ufulu includin wa police..if a person has a weapon in hand n he iz usin t do u think its easy 2 arrest dat person? De police ali ndi malamulo awo kulikose pa dziko lapasi..if de person doesnt cooperate den wa police anamupasa mfuti..wen a police officer dies pipo stay quite..imagine iweyo utakhala wapolisi.

 42. Zidamvetsa chisoni kuona omwe ndi a Malawi anzathu {apolisi} akumaikila anthu obwela{amwenye} ku mbuyo nanga pali chifukwa choombela anthu omwe akuyesa yesa kupanga kapena kukonza moyo wawo chifukwa cha pakhonde?APOLISI MUKUONJEZA M’MALO MOMALIMBANA NDI MBAVA MUKULIMBANA NDI ANTHU OZILIMBIKIRA OKHA CHABWINO TIONA!!

 43. Zidamvetsa chisoni kuona omwe ndi a Malawi anzathu {apolisi} akumaikila anthu obwela{amwenye} ku mbuyo nanga pali chifukwa choombela anthu omwe akuyesa yesa kupanga kapena kukonza moyo wawo chifukwa cha pakhonde?APOLISI MUKUONJEZA M’MALO MOMALIMBANA NDI MBAVA MUKULIMBANA NDI ANTHU OZILIMBIKIRA OKHA CHABWINO TIONA!!

 44. Apolisi ndi anthu and have the right to protect themselves where their lives are in danger. Where the venders are stoning the policemen what do you expect from the policemen to avoid being killed?

 45. Apolisi ndi anthu and have the right to protect themselves where their lives are in danger. Where the venders are stoning the policemen what do you expect from the policemen to avoid being killed?

 46. Apolisi ndi anthu and have the right to protect themselves where their lives are in danger. Where the venders are stoning the policemen what do you expect from the policemen to avoid being killed?

 47. Apolisi ndi anthu and have the right to protect themselves where their lives are in danger. Where the venders are stoning the policemen what do you expect from the policemen to avoid being killed?

 48. Akadakhara kuti agalu osakawo ali ku ofc awo mavendawo akanagenda myalayo anakayamba,mavendawo,chimanga kusowa anthu kumawombera,asapange besnez kuti azithandiza ma banja awo ayi,what you want pipo to do,that is bullshiit.

 49. Akadakhara kuti agalu osakawo ali ku ofc awo mavendawo akanagenda myalayo anakayamba,mavendawo,chimanga kusowa anthu kumawombera,asapange besnez kuti azithandiza ma banja awo ayi,what you want pipo to do,that is bullshiit.

 50. Pali zinthu zina a Malawi tikamachita mmutu mwathu mumangokhala ndale basi. This reporter naye too myopic does not know how to write stories. Unbalanced one, kodi ngati Lindiwe Shabaosadziwa kulemba osangosiya bwanji. People in Limbe were up in arms to deal with the officers. The police shoot in defence mwamva.

 51. Kodi mbali ya chitetedzo ikutipo bwanji,kapena ndinenepo kuti akulu akale aja ponena kuti, khoswe akakhala pa khate sapheka ndizoona.

 52. Chonde malawi police osamangafikili kupha nangamwapindula chani?

 53. Up to this day i dont understand how a sane person would believe news written by a crap and useless page like #Malawi24, nde bolanso kukamva nkhani za ku chibuku tarven bola!

 54. Nowadays No child Can say ‘I WANT TO BE A POLICE OFFICER’ Nah Pa Malawi Pano… That’s why they always ask for ya FANTA!….

 55. Apolisi inu mukuyenera kumalingalira muli inu mungatani? coz pano njala yavuta ndie mot munthu atakate bznes kut apeze yachakudya mwayamba zmenezo aaaa malawi uja

 56. Basi iwo komwe akhalako mtima ulizii akutenga nthongo yansima akudya mtima ulimalo muzao akuphuphu kuchipatala ndimabala. Asa bwanji atakhala mwana wanu?

 57. Koma mpaka ma live bullet zoona zatani akwathu utsi watsabola uja mwasiya kuti? Nkhani yokhudza ndiyoti anthu amenewo apatsidwa chilema

  1. mumapanga zinthu zovuta mudzina lakuti apolice abwela ndi utsi not live bullets, unayamba waganiza if u were a police officer ndiye kuli ziwawa as those vendors were doing ndiye akufuna kukulanda nfuti iweyo ungatani?

 58. Aaaaa Guys penapake kukhala pheee sikuputsa koma kupereka ulemu……Apolice a ku Malawi mwaonjeza zedi ndipo khalidwe umene mwayambawu omaombela anthu osalakwa ngati mavendor si ulemu ai and I don’t think kuti boma lathu la DPP under APM zimenezi akudziwa komanso kodi akuchitapo chani?????? Ife anthu wamba kupanga revenge kwa Apolice is simple ndipo tingopereka ulemu…..Dziwani kuti tiyambe kubwezera Apolice mutimva kuwawa chifukwa Mfutizo sikuti zikusowa ai ndiponso dziwani zalowa zambiri Mmalawi zedi……musatenge mwayi pomaombela anthu osalakwa mkumabisala mudzina la Malawi Police service samalani…….Tikupempha inu a President a Malawi Mr APM komanso ministry of internal affairs muyiwunikile bwino nkhaniyi ndipo apolice amene atulutsa live bullet kuombela ma Vendor osalakwa alandile chilango mogwilizana ndi Lamulo la MPS lomwe silipereka mphamvu kwa Apolice kutulutsa zipolopolo kwa anthu osalakwa…..Ndine Mmodzi wa anthu okwiya ndizomwe apanga a Policezi dziwani kuti we are not in apartherd time…….tili muboma la democracy ufulu kwa anthu…..Ndipo ife ma civilian kapena Mavendor tikazayamba kubweza kuzationa ngati anthu olakwa…..For EG dziko la RSA apolice kapena kuti Boma lilibe mphabvu zopotsa anthu omwe analisankha…..and I can tell you kuti Apolice amalemekeza anthu ndipo akaonetsa mphabvu zawo pa anthu ngati mmene achitila ku Limbe mu amapempha live ndi ma civilian ndipo sawerengedwanso…….Ndiye inu a Malawi police take care dziko likusintha ili…ena mwainu munayamba ntchito chifukwa chakusowa ntchito pamalawi,ena mwainu mukusamala abale wanu,amai wanu abambo wanu kudzera muntchito yomweyi…..dzimvereni chisoni.pangani zomwe zinapangitsa kuti muyambe ntchito kantchito kameneka….chisakhale chipsinjo kwa anthu wena……..mudzachita regret…chifukwa amene mwaomberawa akujambulani nkhope zanu….TAKE CARE OTHERWISE YOU WILL REGRET WE ARE NOT SCARED ulamuliro wa apartheld unapita ndi Kamuzu.

 59. Anthu ena amalephera kusiyanitsa pakati pa andale ndi ogwira ntchito boma ,wapolice ndi munthu ndipo angathe kukhala wa MCP,PP ,UDF ndipo ngati wagwira nthito mo lakwika si mvuto LA chipani chomwe ukuchokera kapena nthundu zimangokhala kuti za muvuta

 60. tisanamepo apa mavandor makani apolice ndiosalakwa iye amati azionese pagulu lazizake zimenezo vendor amaona ngati ndi president wa mutown akapangazionetsero kachoseniso awiri tione amene agonje :job done

  1. iwenso Davie poti mwina sunayende nkoni ukuyankhula chonchi mbale I tell you how cruel these people the do forget that they were in malawi before muyende amwene mudutse mu mozambique muzandivomeleza pano muthakunena kuti ndilibe nzeru koma mabala akupweteka

  2. iwenso Davie poti mwina sunayende nkoni ukuyankhula chonchi mbale I tell you how cruel these people the do forget that they were in malawi before muyende amwene mudutse mu mozambique muzandivomeleza pano muthakunena kuti ndilibe nzeru koma mabala akupweteka

 61. Every pain u put thru someone’s heart apolice inu ndithu God wru account u 4 dat ndi president wanuyo tchimo silichepa ogulisa jigisi walakwa chani mpaka mfuti

 62. Machende anu nonse amakupasani mifutiyoso muuze athu akunyenga amuna okhaokha muona ngt akukwezeran saraly kupusa muzigona ti zimbuz tomweto

 63. ndatopa nazo naneso ndinamenyedwa kwambiri pamapeto pake mkundilanda ma Umblella kunditengeraso ndrama zose bt akuba zamilandu anaiwala pano onse ndi a city onse ndizigawenga bas!!!

 64. The story should read, ‘Police return fire, as angry street vendors threw stones at them!’ Street Vendors in making their statement clear that they couldn’t leave the Limbe town’s pavements revolted to throwing stones at an approaching City Police vehicle. In the act of self defence the police opened fire on the angry street vendors injuring 3. However, it is not known whether the police used rubber bullets or live bullets.

  1. ‘However it is not known whether the police used rubber bullets or live bullets.[sic]. Are you informing us or you quoting the news article? The fact that you dont know whether it was live or rubber bullets it should teach you to talk less!

  2. Alex, how did they return fire as if they were shot at? You mean the vendors were armed? Dont just read but ponder upon it!

  3. You can’t return fire to unarmed person, if they were stoning, then rubber bullets should have been used hence N’quz consintiously said I don’t know whether they used live or rubber bullets! there are rules you follow after shooting a crimnal as a police officer, one of it is calling an ambulance! did they do that? Did they remain on the scene to attend to the victims? Bias reporting is problematic indeed.

  4. You can’t return fire to unarmed person, if they were stoning, then rubber bullets should have been used hence N’quz consintiously said I don’t know whether they used live or rubber bullets! there are rules you follow after shooting a crimnal as a police officer, one of it is calling an ambulance! did they do that? Did they remain on the scene to attend to the victims? Bias reporting is problematic indeed.

  5. Alex ndwe wapolisi bomboklat iwenso eti waona iweyo mmene analili unene kt rubber kapena cani nzeru iweyo? Wandibowa bwanji cimbama nkanakupatsaco! Shupit apolice ake okuphawo?

  6. Alex ndwe wapolisi bomboklat iwenso eti waona iweyo mmene analili unene kt rubber kapena cani nzeru iweyo? Wandibowa bwanji cimbama nkanakupatsaco! Shupit apolice ake okuphawo?

  7. Alex ndwe wapolisi bomboklat iwenso eti waona iweyo mmene analili unene kt rubber kapena cani nzeru iweyo? Wandibowa bwanji cimbama nkanakupatsaco! Shupit apolice ake okuphawo?

  8. #Ebrahim plz can u clarify me what the word “armed” mean?? In my on understanding it means whether aperson having apanga, aknife, agun, astone, or any object or weapon in which he/she try to use to strick someone that what we call armed not only agun. But we malawi we only call person carrying agun as that one is an armed robber plz lets understand it and react in gud manner. Remove that un’t police behaviour plz.

  9. #Ebrahim plz can u clarify me what the word “armed” mean?? In my on understanding it means whether aperson having apanga, aknife, agun, astone, or any object or weapon in which he/she try to use to strick someone that what we call armed not only agun. But we malawi we only call person carrying agun as that one is an armed robber plz lets understand it and react in gud manner. Remove that un’t police behaviour plz.

  10. #Ebrahim plz can u clarify me what the word “armed” mean?? In my on understanding it means whether aperson having apanga, aknife, agun, astone, or any object or weapon in which he/she try to use to strick someone that what we call armed not only agun. But we malawi we only call person carrying agun as that one is an armed robber plz lets understand it and react in gud manner. Remove that un’t police behaviour plz.

  11. @ J-shadre Jussa, a rubber bullet cant break a bone!! know that. To answer your question Patvual Vugaman Kapangalika Jr.: Ididnt say that they carried nothing, what you must understand is, why only gun is reffered to as fire arm not a panga? You mean you have never watched how other countries deal with unruly crowd? Malawi has one of the poorly trained police officers when it comes to crowd controling issues, be it protests or unruly behaviour like that of vendors because they want to be regarded as tough, which they are not but brutal. You remember how the young man was killed in Mangochi when they were protesting about election? Again, live ammunition was used. I asked a question you didnt answer, what did they do after shooting those three vendors? Because as police officer, you need to clear the crowd, the place be cordoned off and call an ambulance to attend to injured, did they do that? If they run away from the scene, then, they are not law enforcers but thugs who desrve no sympathy.

  12. @ J-shadre Jussa, a rubber bullet cant break a bone!! know that. To answer your question Patvual Vugaman Kapangalika Jr.: Ididnt say that they carried nothing, what you must understand is, why only gun is reffered to as fire arm not a panga? You mean you have never watched how other countries deal with unruly crowd? Malawi has one of the poorly trained police officers when it comes to crowd controling issues, be it protests or unruly behaviour like that of vendors because they want to be regarded as tough, which they are not but brutal. You remember how the young man was killed in Mangochi when they were protesting about election? Again, live ammunition was used. I asked a question you didnt answer, what did they do after shooting those three vendors? Because as police officer, you need to clear the crowd, the place be cordoned off and call an ambulance to attend to injured, did they do that? If they run away from the scene, then, they are not law enforcers but thugs who desrve no sympathy.

  13. Zamalamulo zisieni m’malalmulo,musagamule pongomva mbali imozi komanso hearsy evidence.Ngati simuziwa malamulo musazionesere kuti simuziwa dis z socio nitwiks so don’ b a ful

  14. Aise ndiwe mbuzi yamunthu suganiza. Do u kn how expensive lyf is? ma rubber bullets akuti? which constitution does allow police to use live bullets to innocent women & children?Zaugulu basi

  15. kkkkkk ukashosha police limba nazo.usalire akakubandula nacho chamoyo.ngati zakuwawa nawe joina police kuti uzikagwira ntchito mwaupolofeshono ngati m’mene ukunenera

  1. Iweso nd chisiru utakhala mamunako ungave bwanji ngat uliso londa wapolice uzwe kut a Malawi ali nd ufulu okhala nd moyo opanda chilema ife nd mzika za ku malawi kuno ndye tisamahhale mopanika chifukwa cha azilondanu muuzane

 65. Kulimbana nd a business ena akuphedwa momvetsa chisoni mwatani kodi apolice wake up my malawi and let us join hands in combatng crime.

 66. Kulimbana nd a business ena akuphedwa momvetsa chisoni mwatani kodi apolice wake up my malawi and let us join hands in combatng crime.

 67. Charity Ndozi Mlumbe, Emma Nzima, Sarah Khomba, Coreta Emperess Doxen, Getrude Fandika, Madalitso Bonongwe, Gift Kasowe, Mclean Kaliati Koma ya

 68. Charity Ndozi Mlumbe, Emma Nzima, Sarah Khomba, Coreta Emperess Doxen, Getrude Fandika, Madalitso Bonongwe, Gift Kasowe, Mclean Kaliati Koma ya

 69. Apolice !mwina chomwe munalemberedwa ntchito simukuchiziwa?kod mbava zonse zikubaz,akupha anzawowa simukuwaona?mukulimbana ndi anthu osalakwa bwanji?muziganiza mukamapanga zinthu kulinga ali abambo anu atapangidwa zimenezo mungamve bwanji?muwaganizile anthu amenewa.pa zipolowe ndiye kumathawa.mwapanga zopepera.

 70. Apolice !mwina chomwe munalemberedwa ntchito simukuchiziwa?kod mbava zonse zikubaz,akupha anzawowa simukuwaona?mukulimbana ndi anthu osalakwa bwanji?muziganiza mukamapanga zinthu kulinga ali abambo anu atapangidwa zimenezo mungamve bwanji?muwaganizile anthu amenewa.pa zipolowe ndiye kumathawa.mwapanga zopepera.

 71. U policemen do u have rispobity to kill? Why can’t u arrest or kill those pple who kill aman in machinji? Kodi amakhala mantha tatopa nazo zachambazo…..

 72. U policemen do u have rispobity to kill? Why can’t u arrest or kill those pple who kill aman in machinji? Kodi amakhala mantha tatopa nazo zachambazo…..

 73. zimandiwawa,,Apolisi anthu uchitsiru umachuluira,,komaso Malawi ,,this Prezident and its government Ufulu wathu samawutsata thats why most of our times here in Malawi timakhala tikungodandawula ,u can see nawo they shoot citizens of Malawi,,,demolish houses of real citizens in Mpingwe,,Currently Mathanyula,,mmalo moti mfuti zimene agwirisa ntchito powombelera amene akuchita zogonana ndi amuna anzawo kapena akazi okhaokha ,,kpma ayi they chose to shoot innocents.ZIKOMO IWE OTCHEDWA PITARA MUTHALIKA,,2019 Uzipenya Vote yanga wasephana nayo basi.

 74. zimandiwawa,,Apolisi anthu uchitsiru umachuluira,,komaso Malawi ,,this Prezident and its government Ufulu wathu samawutsata thats why most of our times here in Malawi timakhala tikungodandawula ,u can see nawo they shoot citizens of Malawi,,,demolish houses of real citizens in Mpingwe,,Currently Mathanyula,,mmalo moti mfuti zimene agwirisa ntchito powombelera amene akuchita zogonana ndi amuna anzawo kapena akazi okhaokha ,,kpma ayi they chose to shoot innocents.ZIKOMO IWE OTCHEDWA PITARA MUTHALIKA,,2019 Uzipenya Vote yanga wasephana nayo basi.

 75. Muthalika adminstration is o abt,shoot to kill ,malawi is America nw hahahahha kutengela zopusa zokha zokha osatengelako zabwino kwa americako mbuzi

 76. Muthalika adminstration is o abt,shoot to kill ,malawi is America nw hahahahha kutengela zopusa zokha zokha osatengelako zabwino kwa americako mbuzi

 77. Usually the vendors throw stones on the police and they are ruthless, I have seen how they injure police men and even break other people’s cars. And you can’t say that the only vendors in Limbe were at Block Buster. Sanaombere enawo bwanji? Am sure there was something that the vendors did. Awachita kanthu amenewo!

 78. Ulonda womayenda ndi mfuti yochinyilidwa dzipolopolo ndilovuta kobasi.Mukanati mudziwatengera ku chipatala musadawatenge ulondawo kuti madotolo akatsimikizedi zoti mgwanyayu alibe ziwala mmaso;sanathamangitsepo mphepo;sanalondolepo dzuwa.Kuopa phada womathilana machaka kwa anthu osalakwa ngati wachitika leroyu.Akulephera kugwira dzigawenga+mbava zoopsa zomwe zikupha mkusenda anthu ngati nyama ya mbuzi;koma akulimbana ndi woti akupanga zake alipheee.#AGALU INUUUUU

 79. Ulonda womayenda ndi mfuti yochinyilidwa dzipolopolo ndilovuta kobasi.Mukanati mudziwatengera ku chipatala musadawatenge ulondawo kuti madotolo akatsimikizedi zoti mgwanyayu alibe ziwala mmaso;sanathamangitsepo mphepo;sanalondolepo dzuwa.Kuopa phada womathilana machaka kwa anthu osalakwa ngati wachitika leroyu.Akulephera kugwira dzigawenga+mbava zoopsa zomwe zikupha mkusenda anthu ngati nyama ya mbuzi;koma akulimbana ndi woti akupanga zake alipheee.#AGALU INUUUUU

 80. zimandiwawa,,Apolisi anthu uchitsiru umachuluira,,komaso Malawi ,,this Prezident and its government Ufulu wathu samawutsata thats why most of our times here in Malawi timakhala tikungodandawula ,u can see nawo they shoot citizens of Malawi,,,demolish houses of real citizens in Mpingwe,,Currently Mathanyula,,mmalo moti mfuti zimene agwirisa ntchito powombelera amene akuchita zogonana ndi amuna anzawo kapena akazi okhaokha ,,kpma ayi they chose to shoot innocents.ZIKOMO IWE OTCHEDWA PITARA MUTHALIKA,,2019 Uzipenya Vote yanga wasephana nayo basi.

 81. zimandiwawa,,Apolisi anthu uchitsiru umachuluira,,komaso Malawi ,,this Prezident and its government Ufulu wathu samawutsata thats why most of our times here in Malawi timakhala tikungodandawula ,u can see nawo they shoot citizens of Malawi,,,demolish houses of real citizens in Mpingwe,,Currently Mathanyula,,mmalo moti mfuti zimene agwirisa ntchito powombelera amene akuchita zogonana ndi amuna anzawo kapena akazi okhaokha ,,kpma ayi they chose to shoot innocents.ZIKOMO IWE OTCHEDWA PITARA MUTHALIKA,,2019 Uzipenya Vote yanga wasephana nayo basi.

 82. Protecting foreigners,eni nthaka suffering too bad.Kuli njala chaka chino tikuonerani ngati amwenye anuwo atakugaileni chimanga mukhaula

 83. Protecting foreigners,eni nthaka suffering too bad.Kuli njala chaka chino tikuonerani ngati amwenye anuwo atakugaileni chimanga mukhaula

 84. Kusowa chochita kapena chani?limbanani ndizigawenga osati anthu woti akuzifunira thandizo lawo kuti asamale anthu wowadalira,pano inu apolisi mukudya manyofunyofu anuwo anzanu akubuula ndi ululu,muzikhala ndi manyazi,SHAME ON U

 85. Kusowa chochita kapena chani?limbanani ndizigawenga osati anthu woti akuzifunira thandizo lawo kuti asamale anthu wowadalira,pano inu apolisi mukudya manyofunyofu anuwo anzanu akubuula ndi ululu,muzikhala ndi manyazi,SHAME ON U

 86. zimandiwawa,,Apolisi anthu uchitsiru umachuluira,,komaso Malawi ,,this Prezident and its government Ufulu wathu samawutsata thats why most of our times here in Malawi timakhala tikungodandawula

 87. zimandiwawa,,Apolisi anthu uchitsiru umachuluira,,komaso Malawi ,,this Prezident and its government Ufulu wathu samawutsata thats why most of our times here in Malawi timakhala tikungodandawula

 88. Here at malawi we have got stupid leadership because they lying to us for democracy, while we don’t have democracy people they afraid to do their thoughts because of stupid leadership is it this democracy?

 89. Here at malawi we have got stupid leadership because they lying to us for democracy, while we don’t have democracy people they afraid to do their thoughts because of stupid leadership is it this democracy?

 90. zikuoneka amene mukukomenta inu simunakhuzidwe. Anzathuwa ndiumphawi omwe ukuchitisa just imagin ogulitsa zitete ngat waomberedwa banja lake litani? kod a city akatenga katundu wamavenda uja amapita. nazo kut? tiyeni tilingalire Dnt b like ur a crevas while u dnt knw evn wat u a comenting aboout Xoory ndangodusamo

 91. zikuoneka amene mukukomenta inu simunakhuzidwe. Anzathuwa ndiumphawi omwe ukuchitisa just imagin ogulitsa zitete ngat waomberedwa banja lake litani? kod a city akatenga katundu wamavenda uja amapita. nazo kut? tiyeni tilingalire Dnt b like ur a crevas while u dnt knw evn wat u a comenting aboout Xoory ndangodusamo

 92. Chokhumudwitsa ndi choti timanva nkhani kwa anthu omwe panalibepo.Sichophweka kuombera munthu.Pamene waomberedwa munthu ambirife kuti tikhale tikuwona titha kunena kuti aayi anthu anawonje.Vuto Mmalo mopanga za nkhani yao anthu amayamba kuwononga,kuba ndi kuphwanya galimoto za eni.Ambirife kuti taone anthu atakwiya akuba,kuononga katundu sitingawakonde.

 93. Chokhumudwitsa ndi choti timanva nkhani kwa anthu omwe panalibepo.Sichophweka kuombera munthu.Pamene waomberedwa munthu ambirife kuti tikhale tikuwona titha kunena kuti aayi anthu anawonje.Vuto Mmalo mopanga za nkhani yao anthu amayamba kuwononga,kuba ndi kuphwanya galimoto za eni.Ambirife kuti taone anthu atakwiya akuba,kuononga katundu sitingawakonde.

 94. The ppo were not shot at blockbuster bt at Peoles n Shoprite U save car park,i was in a minibus passing when the policeman fired straight to ppo while running to board a speeding Police Land Cruiser

 95. Not good to incite security people.It is only here in Malawi where you play around with Police even thieves be Policemen yourself and come up with your layman’s jobdescription

  1. It’s only in Malawi where police intimidate. We have seen well trained cops in other countries who doesnt shoot stone throwers they use shields to block the stones the only problem here at home is that a shield is more expensive that a land cruiser

 96. Thats MP…………..anthuwo amapanga business ya mifuti, maybe they were carrying guns? Sizochta kufuna kupitira ku xul, ngati munthu alibe chida CHOMWE chitha kukupweteka, you dont shoot

 97. MINBUS DRIVAR WAMENYEDWA MODETSA NKHAWA LERO CHAMA 6 POMPA PA ROUNDBOUT PA KAMEZAPA…CHIMBAWULA CHIMACHOKA KU CHILEKA CHIKUDUTSA PA STAGE YOPITA NTOWN AKUTI ANAWA TCHINGILA NJILA NDE WAMENYEDWA NDI A POLICE 5 MPAKA ANTENGA MOTI KOMWE ALIKO KAYA MOYO WAKE ULI PATI.

 98. Am very upset why police doing this to fellow citizens? We have been suffering with colonial rein now we have Freedom,Independent and self government then why should we suffer like this?Dziko lathu tizikhala khumakhuma ndizowona? Pliz lets look critically to this matter am very cross!

 99. No smoke without fire,apa angolemba za a police okha…why not telling us wat happened mpaka a police kuombera vendor? Ppo dnt 4gt hw vendors behave like dogs. So dnt hurry to judge the officers,they were on duty

  1. Wekha ukunena ku vendors ,tht simply means thy were doing bixnes n they were unarmed ,being civilians,or u dnt even knw armed n unarmed or,akamati civiliaz ,

  2. Wekha ukunena ku vendors ,tht simply means thy were doing bixnes n they were unarmed ,being civilians,or u dnt even knw armed n unarmed or,akamati civiliaz ,

  3. I think u dont know our laws. No one is allowed to kill no matter what condition. Now if these vendor u call dogs can have firearm and fight back. Come here in Suid Afrika then u wil never wish to join police.

  4. Wa police sangangofikira kuombera if u follw the link akuti amadelera kut sangachoke no mattr wat. Ena koma anathawa. Meaning they aware of their wrong doing. Akut amanena zonyoza too mch,imagine. So if peace fail,use force. Iwe ukukukamba za ku SA leave za ku SA alone. Am alrdy here for 6yrs nw. Nkhani ili apa ndi ya ma stupid vendors aku malawi. #mphatso ndiwenso mbuzi ya munthu…u think they shot them bcz of being a vendor? Bwanji sanaombere ma vendor onse a mu limbe? The police r there to make sure everyone follows the laws,enanu simunafikemo mu limbe to c hw these goats u call vendors hw they behave! Well done police! Gun were made to notorious creatures,use them accordingly where posble

  5. I can’t believe this guys.A vendor throwing a stone at a trained cop then a cop uses his gun against that poor vendor? Yes in Malawi it’s understable

  6. So mumafuna apolisi abwerere kuti alephera timavenda?kapena mumafuna aphulitse teargas nkupweteka anthu ena osalakwa? Tiuzeni mumafuna atani?ukudziwa kamtima kokhako kutukwana nkugenga apolisiko nkauchigawenga?anthu amenewawa ndimbava zotheratu and they were ringleaders among their frendz..

 100. Sitingadabwe. Galu amabala galu. Zinali chonchonso mu ulamuliro wa achimwene ake. Amamva bwino akapha anthu. Ichi ndi chizindikiro choti atsala ndi masiku owerengeka.

  1. If ngati pali umboni okuba, why not prove them in a court of law? And if they were selling in prohibited areas, then what does the law say about it? shoot them? arrest them? or what?

  2. If ngati pali umboni okuba, why not prove them in a court of law? And if they were selling in prohibited areas, then what does the law say about it? shoot them? arrest them? or what?

  3. Mpasuka usazitenge ngati dolo ndatukwanapo apa kuti uzinditukwana? dont be stupid to me oky and i dont like exchanging words with people av got low to play, pana me ayaso hea this magesty hea me gwan,putsy and fuck you

 101. What the f*ck is wrong with our officers? Is about promotions? I can’t believe this is happening. What???????

 102. Ths is too much, u guys are turnishing the image of the ruling party. January wavuta uyu, ngati Mzimayi akugulitsa zitete wakwitsa? Bwanji osakapha mahule kwa Kachere?

 103. A police aku malawi kupepela.

  Anthu akuphedwa mochita kusendedwa mitu ngati nyama …koma mukulephela kuonetsa luso .
  Mukulimbana ndi munthu wamalonda kusiya zigawenga ndi mbava zikusangalala.

  1. Ma Vendor wo tu ndi olakwa chifukwa amachita malonda pa malo oletsedwa but the reason of shooting them is not enough.
   Ndi amalawi okha okha that means kuti amamvana chilankhulo , why that police man never use other ways like teargas …… to chase them away than to shoot them ?

   Ntchito imene ija sibwino kuisakaniza ndi mavuto akunyumba kwako upulula mtundu wa anthu popanda zifukwa zomveka bwino.

  2. Ma Vendor wo tu ndi olakwa chifukwa amachita malonda pa malo oletsedwa but the reason of shooting them is not enough.
   Ndi amalawi okha okha that means kuti amamvana chilankhulo , why that police man never use other ways like teargas …… to chase them away than to shoot them ?

   Ntchito imene ija sibwino kuisakaniza ndi mavuto akunyumba kwako upulula mtundu wa anthu popanda zifukwa zomveka bwino.

  3. Ofoira ndiweyo cos u dont know anyone about security and wat it takes to totally eradicate such an act.up to the extent of calling them opepera?mukufuna akhale mbwee ntaunmo azikuberani mukamatuluka mmashop ngati nthawi ya chair?

 104. Masiku omaliza amenewa osazidabwa bas chofunikamkungolimbikila kupephela.dat masku omaliza amuna azidzakwatilana okhaokha c zi peter akuchindana ndimamuna mzakeu subuhanallah

 105. Mmmhhhh Malawi wa lero, masana tikuthyoledwa miyendo, usiku zigawenga ndie zingotisenda zikopa za mmutu. Koma ukalamba tiuona ife?

 106. Foolish police. Y did they kill pp???? And u jst publish the stories without tlng us the reason y the police did that. Mukufuna tizichita kulota????

 107. Is this a proper way to do it or anangowada maguy wo?? this is disgusting amapholisa kushoota mavenda chifukwa chogulisa malo oletsedwa aah come on guys where do u take this penate code achule inu??

 108. shupiti zanu ndamene wakutumaniyo, chilembwe mesa ankadana ndazungu nkhani zake zomwezi?, then wy doing this nosense tsiku ngat lero, musandiyankhulitse pambali, shupitiiiiii!!!!!!!!

 109. mmmmmmm angotimaliza basi kuzuzika dziko lathulomwe Y not using rubber bullets???? koma ayi always kufuna kutchuka pot ndi apolice ,ndizomwe amawaphuzitsa zimenezo ku ma xool apolice akawatenga et????

Comments are closed.