Malawian kills his fellow countryman in South Africa

Advertisement
knife-blood

A Malawian in South Africa on New Year’s Day stabbed to death a fellow countryman by stabbing him with a knife after a quarrel that had started on Christmas day, Malawi24 has learnt.

Both men are yet to be named but Malawi24 understands that the two Malawian men were staying in Honeydew, a suburb of Johannesburg, and are from the northern part of Malawi.

knife-bloodIt is said that the two had a quarrel on Christmas day but they did not fight.

However, on New Year’s Day, Eyewitnesses told Malawi24, the deceased who is said to be a son to a headmaster at Euthini primary school left his house in the wee hours with an intention to fight his countryman.

When he arrived there a big fight started and unfortunately he was stabbed and died on the spot.

Both the deceased and the attacker have wives who are expecting babies.

Meanwhile, South African Police in Honeydew have intensified a manhunt for the attacker.

Last week, Zion Christian Church (ZCC) in South Africa conducted prayers to pray for Malawians who are killing each other in the rainbow nation.

According to a ZCC pastor, Malawians have dramatically changed their behaviour from good to bad.

“You can agree with me Malawi nationals were regarded as God fearing people but if you can see now, most people killing each other in Zandspruit (Honeydew) and other areas are Malawians, lets pray for them,” the pastor said Malawi24 understands that almost every week 2 Malawians are killed by their countrymen in Honeydew.

This is due to excessive drinking and love triangles.

Advertisement

296 Comments

 1. anthu mukuti atumbuka inu you should be ashamed of yourselves. If killing your fellow tribesman was a trait ya chitumbuka would any of us still exist? penapake muziyankhula as if you’re a reasonable human beings with brains, because the only thing you’ve succeeded in doing apapa is making yourselves look like fools.

 2. Tawamalawi Taluwa dango ilo tilikukulila nalo la Kamuzu Banda. Its true to say that Munthu wankulu ndimudambo mozimila moto. If Kamuzu would be still alive till now, mwina anyamata amene amabadwa these times after his death or were jst too young during his passing away, mmmmmmm guys tawanyinu tikakuzgika na wofyi. Kukomana waaka nthe mbwe uzgokenge chakulya cha ng’ina mudambo. Sono anyamata mukukulila mumasiketi ndicho chifukwa mukulilano too much. Kukoma munthu mukuona ngati its as easily as slaughtering a chicken.mmmmm! Malawians think twice.

 3. Dzikolino limadana nduzindikira mopusa maka Jozzie mipeni ndiye imayendadi ukapusa amapha iweyo wachifundowe pakayipa utulutse wako basi!

 4. Ine Ngati President Wa Amphawi Kumalawi Kuno Ndimamva Chisoni Ndi Anthu Amene Mumapita Ku Jons Nkumakaphanaso Nde Mumati Ine Ngati President Wanu Ndizichita Bwanji Monga Mukuwonela Ma Donor Aid Anapita Kwawo. Thats Shameful Guyz. Tiyeni Tidzikonda Ngati Ochokela Dziko Limodzi.

 5. Nkhani ilipano ndiya infa ya nzathu mMalawi osati zogona muzipind zogawa ndimakatani no, iwe mdala wasowa chinena, uzifunsabwinobwino zakuno uzingochedwa ndizinthu zaziiiiii ukanaziwa lyf yomwe tikuphakakuno sham on u

 6. Uzikhala ndiulemu iwe bakha iwe umagona potani bwanji kupanda ulumu tikumvesa kaning’ina usamale wachita kupisila ngati ukamba zazelu fisi

 7. Atumbuka anadzadzana ku Honey Dew, @Yawo ku Lens, ndiku Lodium, anthu aku Nneno ku Thembisa ku ivory park, koma omwe amakonda ziwawa chifukwa cha ngani za akazh ndi Atumbuka, pliz guys nonse ndi amalawi.

 8. Ndikunena ndi iwe iwetu sumatilipilila nyumba zodula ndi makatanizo wamva next time ukazafuna kuchitkuchita comment usanyoze usadzayoze chotelo wamva!! Bcz umzamva kuwawa ndiwe opepela 4sek

 9. M’chewa no nkhalo fumu yinu yili ku zambia waNgoni& Tumbuka(mMbelwa+chikula mayembe in malawi)north original ngozi/nyifwa mphalipose even uko muli ku mw.mchewa no zeru,galu,fulu,chimbwe kwambula watumbuka ufulu uwu mkuka nawo apa nthe mulije cowards no mahala bt kuba pamanyuma pinu fokofuuuu

 10. Baibulo lima mwananga usayende njira za anthu opusa,lero ndi izi moyo wapita si uyo yekha zina zili kuno mmmm guys tiyeni tipewe zinazi kupewa skupusa ai moyo sagula ku Game ai

 11. Inu achewa mwaphana ku enjelu nokhanokha aku thyolo wina wa kumulanje awaso ndiatumbuka? Ku south africa kumeneko. Poyankhura mziganiza ndinu oputsa kwambiri zitsilu za anthu. Kopanda mpoto bwezi malawi kulibe malawi akuziwika kwambiri chifukwa cha anthu akumpoto.

 12. Moyo wauchigawenga sikut ukuchitika ndianthu akumpoto okha ayi angakhale akumwela kuno akumapanga uchigawenga ngat mungalowe mujoz ntawuni achewa enaponamizila kufuna kukuthandiza amakubela n de tingot toan gang allse ndamalawi komaso akumwela chinthu chimozi chomwe sinumumachisata bwino ndichoti aliyese ochoka kumpoto mumati ndi ntumbuka koma sichoncho

 13. Iwe mdala wasowa chonena eti olo timagona mnyumba yodula ndi katani umatilipila ndiiwe? Kumeneko anthu saphana? Wina aliyense ali ndi imfa yake anthu amaphana pachibale ndiye ongokumana moyenda?

 14. Get facts ryt before u publish,the 5W and H ar stil ensetial in Journalism.Ur article z jxt a clap and steriotype when u say Malawians it wz ok,it could be better for u to get their districts names than using Northern Region.Shortcut will never help u guys dis is nt Whatsapp

 15. Nkhani siatumbuka koma kusamvetsetsana mtundu wa amalawi ngati inuyo ndinu anthu enieni woti mulibe ugalu bwanji mumakana federalism? sikudziwa kuti nokha simungakwanitse! let us remember wht Skeffa said in hs song UMODZI, kungopepetsana basi kuzuzurana moti wina asachite manyazi mtundu waamalawi thekaniiiii

 16. News 24 ummh you are liers,most of da news i read pa newz 24 zimakhala za bodza,why..try to tel us the newz after a through investgation we are tired kumamva nkhani zabodza

 17. Fuck! Diz so called Mlw’ns in Joburg r de ones paintn bad image on our blvd country. I hate dem, take de hell out of ma way eish!

 18. Mose nakumwera napakati muli vindele vambula zeru we ddt ask u for help ok,kusuku nozeru ntchito kugulisa malonda.Pala mwiza kujoni ntchito yinu njakukugulisa kubamwenye nakuba.

 19. changamukan amalawi inu!! aliyense wochokela kumwela kaya pakat anthu akumpoto akungoti vachewa ivi, aliyense wochokela kumpoto anthu akumwela ndi pakat amangoti zatumbuka,u r all one kwathu ku zambia kulibe izi

 20. Mtumbuka sadzatheka, matama mukafika pa pub, mukakhala ku jonz mumaona ngati mwafika pamapeto a zonse, vuto ndi kochokera ndichifukwa chake kamuzu anatembelera kumpoto, AtsiBweni muchita vichi, mwana mzeleza uyuuu,

 21. I’m very concerned with fellow Malawian living here in Mzanzi , I won’t mention any tribes because views will think I’m a racist, but its true all those stuff you hear about killings, robberies and more things Malawians are involved in.

 22. Musakomete zoti atumbuka chani chani APA ayi ngati simufuna Ku yika comment siya a chewanso nanu nkuchuluka nzeru bwanji sisiiiiii

 23. Mitundu ndimitundu izaukirana, mafumuso azaikirana, anthu azakanana pauchibale, mwana ndikholo lake, njala, matenda osachizika, milili yina, ….. zangoyamba sizidati satana azaukira satana mzake khalani oreza ndikuidikira mwana wamunthu

 24. Tangokamba nkhan mmene ilili not timacomment taundele apa .tonse ndimbale ameneyo zimoment alikunja kukapata kanganyase ,wamva iwee! munthu

 25. Amalawife chavuta kuno ndi jelousy wina ngati zikuyenda tikumayamba kumulodza zikativuta kumulembera zigawenga. zopusa kwambiri sitikukondana kuno koma kufunirana zoipa basi ,amalawi adali akale atsopanowa manyabwisa.

 26. Nd chikhalidwe a malawi,ngat mumaphana mdziko mwanu momuno kulibwanj kwa ena,n it dosent min kut athuwo ndatumbuka coz 4rm south,kod atumbuka m’maderanji?so shame

 27. inu a news 24, ndinu abodza munthu yemwe adaphedwayu sadayambane ngati momwe mwakambiramu. zikuoneka kuti simukudziwanso chomwe mukuchita pa ntchito yanu ndipo ndi bwino kuti mwina muleke. anthuwa samakhala malo amodzi wina (wophayu) amakhala ku pretoria, winayu (wophedwayu) amakha kuno ku angelo Boksburq. ndiye mukati adayambana pa xmass adawonana liti? mind you don’t telling us stupid news!

  1. if u no de truth just tel de ppl dont criticiz malawi24 it updat us news and we love t, amalawi aphana ndizoona. Malawi24 2016 wooooyeee, mind u its not fo u pp in jonz its fo us mw.

 28. Pali mau akuti “nkhondo ndi anansi”mwaiwala olo anthu akuno amaphana musamalotse ndale pofuna kulankhula poti simumadziwa moyo wapadziko.

 29. guys stop commenting ur rubbish! imagine da one killed is ur brother hw can u feel? plz get humanity we r all Malawians!!!!!!!

 30. My concern is umbuli umene uli ndi aMalawi from south and central, wina aliyense ochokera kumpoto amangoti mtumbuka

 31. Inu a malawi ku joniko ndinu omvesa chisoni,mukunyozana a malawi nokhanokha,ife a BT, ife a mangochi etc, mukudelako anzanu ngati inu ndi kwanu kumeneko,nkwa a zulu,mabunu etc kumeneko,mumagona mma boyz quarters kapena mnyumba yazipinda zogawa ndima katani, osamadana nonse nda kapolo ofanana jst luv each other ur all malawians.

  1. Man mwanama, si onse amene amakhala nyumba zotero, mwina komwe inu mumakhala,Ine sindikhala nyumba zomwe mukunenazo, ine ndimakhala nyumba yaikulu and ndimakhala ndekha.ngatu mudakulephela ku joni kuno zanu zimenezo koma musaipise mbiri yabodza kwa wanthu.

  2. Man ndinu kape,,,ukat amadula zipinda nd cartan what u mean?,,anthu amayambana nkuphana malingana nd zifukwa zao,,,u need to mean kut mazula kuno kuna saphana?,,,izo usapezele njila zonyozela anzako ….shame on u ife tikuu3latu kuno bed yomwe ndimagonela ku MW ndukaika ngat iwe ungagule?,,,,as u know chinachilichonse pajonz ndi more

  3. Guys guys guys guys come on lets be real.fans ikuvutika there ioz a student at the university of pretoria.ioz there 4 2yez nnazionela ndekha mmene guyz mukuzunzikira kumeneko a malawi bora anzathu ma nigerianz somalis zimbabweans aliko beta,mumangoyenda cheucheu kuopa a home affairs,u wek from monday to malawi ngati mumabwera kuno ngati simubwera tizangova, zovuta,simungandinamize zakumeneko zonse mukuthoka apa zoti mumakhala ma den akulu doz are blue lies.

  4. Iwe usanyoze kuno wanva … Ine ndili kuno ku cape town za cheucheu zakozo kulibe kuno…. Kod chimakhala chani kumanyoza anthu omwe timakhala kuno?? Nzanjeeee bwanj?? Kupusa et

  5. Akunena zoona munthuyo,ngati simunakumane nazo just say thank you Lord,ngati mukufuna kumva zambiri funsani anzanu

  6. iwe uti unali ku university of pretoria ? kutereko ndiwe graduate? ma graduate akumalawi? bolanso ma garden boy a ku joni kuno tikumagulako magalimoto.kumanga nyumba za bho inu madolonu nkumapanga rent nyumba za anthu ovutikawo ndie pali nzeru kufera degree hehehe basic k60000pa mwezi ife imeneyo ndi ya 1wk.so dont be proud 4 nothing

  7. kkk…Apa mungonamizanapo, chomwe muchite aliyense amuyendere nzake pamene akukhala akachitile umboni…. Iwenso ukut graduate amalandila MWK60 000 per months ndiwe waboza kwambili.

  8. Kkkkk koma umbuli ndi matendadi guys ndakhulupiliradi they are boasting kuti amalandira dola more koma lyf amakhalayo amangokhalira kuba,kutchetcha,achizi mai wa,uhule kuchapa zovala,kusamala ana ndizomwe akunyadira,amphwanga chokani kumeneko ur wasting yo time there osafera zakudya zotchipa ife kuno ku malawi konkuno tikudya money kuli dola kuno chofunika ndikupeza nzeru zopezera dolazo which is lacking in u guyz a chewa amati kwaeni sayanga ndere ife 2 yez inatikwanira basi ma boers anayesera kundikakamira koma nnawauza kumalawi kuliso rand yotchedwa kwacha poyamba zimashupa koma pano zikuenda sindikuzipopa koma kungothandizana nzeru,ndikugwira ntchito,ndikupangaso biznes kuoda ma potatoz kutcheu ndikumakagulitsaso kwa azungu kuma hotel,ndimaoda chambo kumakagulitsanso kuma hote,dola zikupezeka,inunso dola zambiri zanuzo u can come and invest in malawi yo home

  9. Ife kun kumalawi no cheucheu,kudyaso mkosayamba ikakhala dollar bola plan dollar ndiyosayamba bwelani mudzaone anzanu agula njinga zamoto,anatelo john malunga.

  10. I liv in a medium size house ges wat ? i built it using my hard earn money from malawi madala bwerani chitukuko sapangira kwa eni am tokn ds not kuku bifani guyz koma kuunikirani tiyeni titukule our country ndi dola zopanga kwa eni ngati amwenye mmene amachitira

  11. Man aliyense komwe wasangalasidwa nako akhale komko ine ndasankha kuno ku soweto am citizen here koma kwathu mku malawi and i alwaz go visit there bt i dd choose to stay here and married here, so chomwe wakonda mzako iwe sungachikonde,,,ndangodusa sindinatchole mkhwani

  12. wu knwz my destination i gues nobody knwz so wether am livin pakatani kaya massion i dont care az far az am gettin wat i want n i wil kip on workin hard kwamene anaphedwayo tikut zimuwanu ukautse muntendere

 32. i can believe this..mm.special in Johannesburg a malawi amatha kutumizilana dzigawenga kukamuchita upandu mlw mzao chifukwa choti winao amagwila tchito yabwino……….shame

 33. Ku HONEYDEW Mkwa TUMBUKA Ndiko Kumene Adapeza Maziko Awo Nawonso, Kukamba Zomenyana Bweka Bwaka Samaibva Amalolera Kunyika Chinguduli Mpaka M’mwamodzi Atasiyana Nalo Dziko. Mwangobva Imeneyo Yokha Komanso Pali Ina Imene Yachitika Pa 31th December Last Year Imeneyo Ndiye Khawawa Man. Womwe Akutumizira Imeneyi Yobayanayi Akaibvanso Mwina Akupatsilaninso.

 34. That is the power of stupidness,you are tarnishing your images there ndiye amaiko enawo akulowererani kumeneko azikupangani zipongwe ndiye kunotu ma bus ozakutengani kumeneko kulibe kuno

 35. nkhani ndiyot adamubaya ndi botolo loskeka la black label pakhosi osat mpeni pena pake mmalemba nkhan zabodza bwanj??

 36. Fools , it”s not about a Tumbuka. Mind u in North they aren’t only tumbukas so mind yo comments, . Mindless chewaz.

 37. atsibweni amalimbikila sxul ndicholinga akaone blantyre. nde amati akagulitsa ng.ombe zawo ndikubwela kuno, akumatumbwa kwambiri. koma tithana nawo adzayelekeze kumputa wa bt azaleka

  1. Kkkkki….satha kuwelenga ndi kulemba chizungu a MR witness wanuwo akuyankha zawo. Kuzolowelatu kukumba mbewa kuwaonanso kumvetsa chisoni alibiiii ?.

  2. if u knew whr i am, u wd’t sy lyk dat miss taonga chomene. cn i tell u whr i am? dey s no chitumbuka or cicewa here so if i dont knw hw 2 wryt/spk english, hw do i cmct wth dem? mhhhhhh? tell m tumbuka beach.

  3. if u dscrb pipo, things/bhviour as racist, u mean dat dey r influenced by de belief dat som pipo r inferior coz dey belong 2 a particular race………………………she hs a hard core ov support among white racists. mwina pamene ndakumasulira bwinox2 wati?

 38. Nkhumanya makola cha kutı ka malawı sono wakuyankhu.Nkhalo zıthu yose tılıtaya kale lelo nase ndıse vıgewenga waka nthe.Tıyenı tısınthe wanganya tıwe wanthu wakutemwana

  1. Agula Ndi Amako ndi Abambo Ako,,, Useless Person,, I’ll Castrate Your Testicles

 39. Zoona zake ndikusaenda, ndine mngoni amayi anga, ndia chitumbuka, koma am not deffending them, tlibedi mkhalidwe akumpotofe. Mutidzudzuledi tikuchitsa manyazi kwambiri.

  1. Ukunena Zowona Tawona Akutukwana Apa Zao Ndizomwezo And NdiwaMbulu Kwambiri Sadziwa Ndizizizomwe Sangawerenge C0.5TS.5ou #2coo 2so

  2. Ngati munthu akutukwana zikuonesa kuti wakulira kobusa ng’ombe, angakhale ndi nzeru, not! At all coz as as northern we r selfish, we dont even welcome astranger as Loti do, we r fuckin stupid, thats y tikutukwanana tokhatokha. Ngati tikutukwanana tingalemphere kumpha, enanu chibadwileni pa umoyo wanu simunagwirepo K50 pin. Nde mukafika kuno mumaona ngati muli ku paradise. Thats fuckin, mukuchititsa manyazi kwambiri.

  3. Ndilankhule cha kwathu, munalodza abambo anga, munalodza amayi anga, munalodza mkulu wanga, ndingakhale mbali yanu? Wanu ndi ufiti basi. Mumachitisa manyazi kwambiri.

  4. I was in honeydew in 2014 April some1 from Mzimba, ngomiyawo took his gun and try 2 shoot me. I told him that am fuckin mafia. He stop the same time.

  1. A jomba sazakhalapo dolo aliyense imfa yake inalembedwa kale wakupha samalakwa,ndie coz zinalembedwa,kale kuti azafa imfa imeneyo

 40. Ndi asibweni amenewo ambwenu-bwenu kukonda kulongolola. sinanga samayenda-yenda bwino-bwino ndiye momwe angoyenda kuzafika kuno akungoona ngati afika kumwamba kwa mulungu muzifa chisawawa choncho kkkkkkkkkkkkkk

  1. Chikwapulo Wa Manoma dnt be clever coz this is Internet many tumbukas can see that u insulting us. My warning to is that we know where u live so any time anything can happen. Kodi kukhala wakumwela kapena pakati ndi kuchenjera??? Watch out!!!

  1. its tru my brother was stabd to death aftr un argument over acigalets on 25 October lase yr by guess wat? Atumbuka guy I hope he will rot in boksburg ngati atatuluka ndidxathana naye

Comments are closed.