Atcheya in love?

Advertisement
Bakili Muluzi engages again?

…photo of Muluzi ‘engagement’ send tongues wagging

A photo on Facebook that shows former president Bakili Muluzi with a beautiful young lady admiring a ring on her finger has sent tongues wagging.

Bakili Muluzi engages again?
Such a beautiful ring – Muluzi appears to be saying

The photo which Malawi24 has seen creates an impression that Muluzi, a two time divorcee, was the one who put the ring on the finger of the young lady.

However Malawi24 has established that the former head of state is not the man that put the ring on the finger of the lady.

“Muluzi was just admiring the ring when the lady with her fiance paid a call on the former president, ”  a source said.

Malawi24 has established that the couple, based overseas, decided to announce to Muluzi of their engagement and the photo was taken in the heat of Muluzi’s admiration.

Advertisement

311 Comments

 1. Amuluzi ndimuthu wankulu ndimapeleka ulemu,sangakhale bigfool,ine ndinayamba kumuona kalekale ali kunaperi,pano tikuti newnaperi,olo ine sandipangilepo ciliconse,koma mtima waumunthu alinao,nkha yanthuzi musalowense kundale,khama ndilunso lake ndilomwe linampanginsa kukhala pa no 3 prezedent olemela,anachita zambili kuntundu wamalawi,pena ulemu ndi ofunika,cikondi cizikhala osamangonyoza,Muluzi ndikufunila moyo waphamvu chaka chansopano.Mulungu adalinse tonse. mulungu a cikondi n n

 2. My understanding of the story is that the lady was sent 2 deliver a message of good will 2 a Tcheya.So why the fuss?

 3. Ndizoona mkuluyu ndimunthu olandila ulemu monga inu A nazombe komasondikuvomerezana nao AChafunya kuti ngati dziko lamalw. likuzuzika ndi akuluwa adayambabwino. koma adakachita njomba kugolo adakapatsila mpila DPP mmalo moti UDF idzilamulilabe ngati Mandela ndi chipani chake ANC mpaka pano chikulamulabe.Acheya adapereka Boma kwa ena ndi Manja ao lero Cash gate ndindan wabweeretsa?wabweretsa ndindani. ndichifukwa anthu atudana nayetu

 4. Kkk Mulimi wa mzeru Akakolola amasunga nso mbeu mosamala .koma ngati mbeu yaonongekamo safikira kutaya ngati mbeuyo imamusangalasa , amamasula ndikuyamba kusankha yomwe akuganiza kuti ingamere , ndikukaizala .ndipo ngati yatuluka ndikuisamalanso bwino imabereka momukomeranso mulimi unja. Tamvani mwina imunyo dzuro mwanyonza ndanu koma Yehova sanakuchoseni moyo koma wapanga njira kuti mulape ndi kukhala mbali yake EMEN

 5. Pali mbuzi zina apa zikupanga comment nkhani zisanave,, amalawi24 akutsutsa zoti pali chibwezi or mngwirizano uliose okhudza za banja pakati pa cheya ndi mayiyu koma tcheya ankasilila ring ya mayiyu that’s it

 6. Mwanyanya Nazo Bakili Ankati Amanga Brige From Nkhata-bay To Likoma Pakati Panyanja Ifekudikira Mpaka Pano Zazi Chaboza Ngati Inu Anakugulirani Panti Mukondeni Basi.Sinnayankhe Kapena Comment Nkhaniyo Kungoti Zimandi Gwesa Ulesi.

 7. Amene Muku2kwana Dr. Bakili Muluzi Mapwala Anu!! Dr Muluzi Nd Hero Sakuenera Kunyozedw Chonch. Ndmawakonda Atcheya Kuposa Agalu Amatanyulawa Mxiew! Gay Rights Ndy Kut Chan Muziyankh Afisi Inu Kuthako Kotambalalako Ngt Lichelo! Asatana Ogonana Amuna Okhaokha Inu Mavuz Anu Mxiiew

 8. “Muluzi was just admiring the ring when the lady with her fiance paid a call on the former president, ” a source said.

  Malawi24 has established that the couple, based overseas, decided to announce to Muluzi of their engagement and the photo was taken in the heat of Muluzi’s admiration.

  1. Abale anga tamamvani zomwe zanenedwa!! Amakuuzani zipitani kusukulu koma inu mumangokhalila kopha Mbewa lero ndi izi kumapereka ma comment osemphana ndi nkhani! Shame! APA akuti Muluzi akukhumbira ring ya msungwanayu iwowa atakachezera bwana Muluzi. Ndikutanthauza Mnyamata ndi msungwana anakacheza ndi a Muluzi. Nthawi yomwe chithunzichi chimajambulidwa chibwenzi cha mkaziyu chili pompo. A Malawi kuchititsa manyazi

 9. Guyz welengani nkhaniyo ndipo muimvetse b4 u comment coz mukupanga comment pona chinthunzi koma osawelenga nkhaniyo ngati mukulephela uzani ena akutanthauzileni

 10. Guyz welengani nkhaniyo ndipo muimvetse b4 u comment coz mukupanga comment pona chinthunzi koma osawelenga nkhaniyo ngati mukulephela uzani ena akutanthauzileni

 11. koma munthu ameneu kwa amene mumamukondanu anakupamgilani chan kwen kwen? zoti dziko la mlw li kusauka chifukwa cha munthu ameneu simukuziwa? for me i hate this guy too much coz ma President akuba ndalamawa amawatuma ndiyeyu komanso palibe president amen amalamulila malawi posamudutsa bakili kumaso which means his a responsible of all mlws problem (number 3 kulemela mu africa koma ziko lake number 1 kusauka padziko lonse lapansi big fool)

 12. koma munthu ameneu kwa amene mumamukondanu anakupamgilani chan kwen kwen? zoti dziko la mlw li kusauka chifukwa cha munthu ameneu simukuziwa? for me i hate this guy too much coz ma President akuba ndalamawa amawatuma ndiyeyu komanso palibe president amen amalamulila malawi posamudutsa bakili kumaso which means his a responsible of all mlws problem (number 3 kulemela mu africa koma ziko lake number 1 kusauka padziko lonse lapansi big fool)

  1. noel bwanali……no matter what you said i don’t care just bcz ndinu achiyao bakilinso ndiwa chiyao that’s why u always like him(ngakhakhare adzipha anthu ngat matafare ndiena otero koma kumukondabe shame) which is rong…… three things u hv t knw chipembedzo chilakhulo mntundu ndi ndale ndi zosiyana timafuna kuti ngat uli mulomwe president akhala mlomwe ngakhale akupanga zompusa koma kumukondabe that is stupid minded plz zuka malawi

  2. ndskomenta malingana ndi m’mene ana commentera athu ena…….naonso amakomenta zochemelela bakili zomwe zili zosemphana ndikhan ndiye ine ngat mbuz palibe kathu bola wawelenga comment yanga ndikudziwa chilungamo

 13. whether it is true or force thus non of our business, tiyeni tipange zathu Bakili zake zinayera kale!!

 14. kkkkkk anthu sakunva chizungu ndawatulukira kkkkk zomwe akupanga comment ndi nkhani zikusiana welenganinso nkhaniyo mpaka pa mapeto munva kulephera kwanu kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk shame!

 15. Vuto limene ndaliwona apa pa fb pachuluka anthu amene akuphunzila kuwelenga ndikulemba pompa kagulu kameneko ndikamene kamalemba makomenti opusa chifukwa sukulu yawo ndi fb yomweyi, akadakhala kuti adalowapo nkalasi sibwenzi ntikumakhalila kumva makomenti osagwilizana ndinkhani ayi, ndiye mukaona komenti yopusa yosagwilizana ndikhani ziwani kuti ophunzila pa fb aja ndi amenewo, oyimba adayimbakale kuti zoziwonela kuukulu n’zovuta zongobwela mosaziwika bwino nzolawula, ndiye ndiizi

 16. Vuto limene ndaliwona apa pa fb pachuluka anthu amene akuphunzila kuwelenga ndikulemba pompa kagulu kameneko ndikamene kamalemba makomenti opusa chifukwa sukulu yawo ndi fb yomweyi, akadakhala kuti adalowapo nkalasi sibwenzi ntikumakhalila kumva makomenti osagwilizana ndinkhani ayi, ndiye mukaona komenti yopusa yosagwilizana ndikhani ziwani kuti ophunzila pa fb aja ndi amenewo, oyimba adayimbakale kuti zoziwonela kuukulu n’zovuta zongobwela mosaziwika bwino nzolawula, ndiye ndiizi

 17. Ndindan safuna zabwino? Even the Bible says wapeza mkazi wapeza chinthu chabwino, keep it up achair. Amayi ake atupele amenewo,lulululululululululu!!!

 18. Ndindan safuna zabwino? Even the Bible says wapeza mkazi wapeza chinthu chabwino, keep it up achair. Amayi ake atupele amenewo,lulululululululululu!!!

 19. kodi mmafuna akwate mwamuna wafuna kukuuzani kuti mwamuna ndi mwamuna mzake ndi ugalu ngati zikuchita nkhumba za mdziko munozi muluzi wel done show them and lead them cz they are blind readers

 20. Aaaa! Malawi 24, Your headline and the story following is not the same. You have no experience in your job. Go back to study journerism.

 21. Amalawi 24 mwayambano kuchulusa maboza mu nkhani zanu mumatiponyela pa line,,it smz lk mukumasowa nkhani shaaaaa ,shuuuu.

 22. رأنا حصلت على 1000 طلب صداقة في يوم واحد
  احصل انت ايضا على آلاف طلبات الصداقة من بنات
  و اولاد ومن جميع الدول العربية والاجنبية
  الشرح من هنا ==> http://www.tokaproxy.info

 23. Dzinthu zina zimaonetseratu umbili nkhani siyi mwaika apay ano simasiku omanamidzana (go to opera write there today malawi news tell us again wht u read

 24. Olo atapeza nkaz ndi mulandu ngat iyaaaa muxiyen munthu wankuku aifile lyf!! ameneyo nde tcheya ndikunziwa ine zathobwa ayii

 25. Read the article before comment guys.Atcheya amadziwa kucheza ndi anthu olo ma joke ake mpakana lero ndimawafila osati Mbalame zikungodya bwembazi zofanana ndi Mr Ibu

 26. Read the article before comment guys.Atcheya amadziwa kucheza ndi anthu olo ma joke ake mpakana lero ndimawafila osati Mbalame zikungodya bwembazi zofanana ndi Mr Ibu

 27. Onse akuyankhula mokhuta apawa alibe data yokwanira sakutha kutsegula link yi, mwinanso ena ali pa free data nchithunzi chomwe sakuchiona angowelenga ma comment nkumayankhula mopepela chonchi….umbuli ndi matenda kwabasi

 28. Onse akuyankhula mokhuta apawa alibe data yokwanira sakutha kutsegula link yi, mwinanso ena ali pa free data nchithunzi chomwe sakuchiona angowelenga ma comment nkumayankhula mopepela chonchi….umbuli ndi matenda kwabasi

 29. kwaamene angoona chithunzichi ndikungokumalemba nkhani zawo zonyoza fest ifufuzeni ku link mowona zasiyana kwambiri amala check this out

 30. kwaamene angoona chithunzichi ndikungokumalemba nkhani zawo zonyoza fest ifufuzeni ku link mowona zasiyana kwambiri amala check this out

 31. our laws only talks of marrying a girl who is not above 16 as to a man the laws are silent which means even at 90 a man can marry so long u don’t the under aged” kkkkkk bigma” munthu wankulu”

 32. our laws only talks of marrying a girl who is not above 16 as to a man the laws are silent which means even at 90 a man can marry so long u don’t the under aged” kkkkkk bigma” munthu wankulu”

 33. our former head of state tiapatse ulemu.muzilemba zanzeru

 34. Koma Love ndiyovutadi, ngati alibe okondedwa osewo let them be in Love nanga tinagatanipo.

 35. Kodi ena mukumati umbuli eeee kusaphunzila pamenepo mukutanthauza chani? inu akati mbuli ndindani? kuphunzilako moti m’manena munthu omakwatila-kwatila kapenanso kukwatiwa-kwatiwa ndiye kuti simbuli? kwa ine ndimaganiza kuti pofuna kusutsa pa comment musamaikepo mawu oti umbuli (ambuli inu )

 36. Kodi ena mukumati umbuli eeee kusaphunzila pamenepo mukutanthauza chani? inu akati mbuli ndindani? kuphunzilako moti m’manena munthu omakwatila-kwatila kapenanso kukwatiwa-kwatiwa ndiye kuti simbuli? kwa ine ndimaganiza kuti pofuna kusutsa pa comment musamaikepo mawu oti umbuli (ambuli inu )

 37. To me, that pic really looks that atcheya was admiring the Ring coz when a woman is engaged we lift the hand up visibly for erybody to see. Koma walakwisa ndiojambula. #1. That pic was suppoze to remain indoors, ATcheya ndi munthu wamkulu. #2. Why leave the Lady’s hubby out of the pic. Nduonapo BadMind pamenepo. ###But still if atcheya got enagaged today there is no problem, Mamuna aliyense amafunika mkazi oti azimuchosa nkhawa. #Long Live Atcheya!!!

 38. Mnyamata wapa tauni wapeza nthiti yake basi. Wapeza mkazi wapeza chinthu chamtengo wapatali. Zabwino zonse Mnyamata wapa Tauni.

 39. this is a lie and please the editor correct this story….. Check on nyasa times for the truth….. I will never believe your page again

 40. That lady lives in Ireland . She is awell respectable lady and chairperson of MalawiAssociation in Ireland. She went to see Our DrBakili Muluzi on a business meeting.Happie Chi was there representing FatherO’Malley the retired honorary consul of Malawiin Ireland. As the chair person of Association ofMalawians in Ireland. As u know that Atcheyais full of jokes, he was joking he was looking ather dress rings and nothing more.She posted on her wall, and then people havestolen the photos and started spreadingrumours kuti engagement.

  1. I don’t think this is an attack on Moslems, bro. This is just the work of some ill-minded people who want to smurge other people’s reputations to gain ill-gotten popularity. People should begin to view elders as their own parents.

  2. Amalawinso penapake…mavuto ake nde ngosayambatu…judging tatiyeni tizimtsiyira mweniwake namalenga who r we to judge.

 41. Muzikhala ndi ulemu inu muluzi ndi muthu wolemekezeka pa zikolose lapasi ndi foma president Wa Malawi bwanji simukulemba khani za makolo anu basi kungokhalila kuipisa mbali ya ena basi ngati muluzi anakuchitilani za chabe Pali ena anachitila zabwino mukudikila amwalile muzizamuyamikila mukudana ndi yemwe watenga nkazi enawa akutengana amuna okha okha Wa ai kuma inu mukhale ozindikila pa maso pamuluzi tipaseniso zibwezi zabambo anu tioneso mukufuna muchuka ndi khani zomunyozesa muluzi basi mulibe zina khani ai ndi originaltu foma presidentetu amei si obenatu ai mpaseni ulemu wache

 42. Hahaha that’s the he’s is, i’m a big fan of him. He wanted just to make the headlines nothing serious

  1. Guys Please read English again before posting shit comment. Alendo anabwera kunyumba kwa atcheya ngati mzawo wa bakili kuchokera kunja.ndiye mkaziyo amanena kuti akukwatiwa and umboni ndi Ring ndiye atcheya amaona Ringyo

 43. Iiiiiiii heeeee heeeee umbuli,kumangoika ma coment zinthu zimene simunamve,ngati nkhani sunayimve osacomenta pliz,werengetsani kwa anthu amene amamva chuzungu

 44. Make money without side effect !!! .are you a business man or woman, are you a musician or an artist, or a footballer,do you want to be famous or you want to become rich or powerful, is better you become a member of the Illuminate and make your dream come through, this is the chance for you now to become a member of the temple and get what you seek from us, if you are ready to become a member and realize your dream then email us now [email protected] you call us through this number: +2347065758576

 45. just f*ck off ur mouth if udont have the shit to say coz some of u, ucomment shit it only shows that uhave no respect even to ur parents

 46. kukwatila kulibe malile azaka ayi kapena chikondi chimakalamba ayiso ena anachita kukakamizidwa kuti akwati dziko litawonakuti mpando umene alinawou sikoyenela kukhala pa uswazi anakwata muluzi kumuveka mphete mnkazi waka ndipokwanila

 47. Iiiiiih, amalawi sitizatheka mkazi ameneyu ndi waulemu wake ndipo ali ndi banja lake lokhadzikika……Kungogundika basi, shame on uuuuuuu ndithu! fufuzane mumve zoona zenizeni….. umbuli

 48. Nkhani sili choncho,ndi a Malawi aku Ireland ndi father wachikatolika amene anathamangitsidwa ndi Kamuzu,mmene akumenyelela multiparty, check full story on Nyasa times. Nzimaiyu anabweletsa mphatso kuimilila a Malawi ali ku Ireland siza engagement zo

 49. Zomvetsa chisoni zomwe enanu mukulemba mzopanda ulemu a Muluzi enanu ndi size ya agogo anu, Facebook idatipeza mochedwa,

 50. Kodi mungonyoza koma mwawelenga nkhaniyo kapena mungoona chithunzi cho nkumanyoza? Tatsegulani link yo pilizi chonde mumve

  1. atipusitsa olemba komapaja mmadziwa tcheya yake ija mpake anthu amakomenta choncho paja ankalawako kale zakudya zimenezi mwayi ndi nsana uja akudwalawu. pepa tcheya takulakwira

 51. Kuchithekete! life starts @ 75 remember with the muntharika`s? he is not yet there so he can still marry. after all it is during old age a man needs company most because not even money or relatives can solve that

 52. Kkkkkkkkkk ukazamuona mwana akufuna Khamisolo wakwana ameneyo ntchito igwirike.kumachangamuka pa town hehehehe!!! Atcheya kufuna kuyika chitukuko kumeneko

 53. Musiyeni awupeze naye chair..chacha ndi dolla ..ndichifukwa chake namwali wagonekela nkhosi.kkkkkkkkkk loi

 54. Koma ndiye nkhani zakutheranitu, mmalo moti mulembe zoti Agogo anu pa Khirisimasi anadya chani mukutangwanika ndi zazii mukutitenga ngati ife ana? Umphawi ndi Umburi ndiumene wativuta ife amalawi.

 55. kkkkkkkk koma naye ndye eeeetu mpaka pano akumathabe kusilila

 56. Click on that link abale the story continues to say that pic was taken in the middle of Atcheyas admiration of the ring when ths couple broke the news to Atcheya,,,sikuti anamveka Atcheya ai

 57. Xo wa@? Anayika malire oti munthu azikwatira malire zaka izi? Remember sikuti ntchito ya mkazi z all about sex basi koma pali zina zofunikabe munthu wa Mayi congrats a chair

  1. ur the one nt me,am just asking can upls come and check if iam angry,udnt knw hw to ask or angry?is it necessary to become angry with this post in ur thiking?

 58. Ameneyo ndi Tcheya, nchifukwa chake adavulala msana, alibe nazo ntchito kuti namwaliyu wachepa, amakuntha basi. Musamukaikile

Comments are closed.