Dont punish me for Joyce Banda’s sins – Mutharika


Peter Mutharika BBC Hard Talk

…says Malawi cannot survive without aid

…‘we need assistance to address this crisis’

President Peter Mutharika has contradicted his earlier proclamation that the age of donor aid was over for Malawi by issuing a strong plea to donors that they should not to punish him for the sins that were committed by the Joyce Banda administration.

“You are punishing the wrong people. Cashgate was done by the previous government. Are you going to punish the subsequent government that was not involved in the scandal? In the end, it is the people who suffer when donors withhold support. What is currently happening in Malawi is very serious. We have no medicine in the hospitals because the donors left” said Mutharika in an interview with BBC Hard Talk.

Peter Mutharika BBC Hard Talk
Mutharika: Donors me for Joyce Banda’s sins

He pleaded with donors to resume the aid to reverse the current economic crisis. He stated that his administration was committed to efforts intended to uproot corruption in order to gain donor confidence. He however said the malpractice was deep-rooted that it would take about 5 years to be successfully eradicated.

“Of course it was the donors’ decision. But I think it was unreasonable to leave when over $60 million had been depleted at treasury… Malawi needs about 5 years to be self-sufficient, to gradually change from an importing to an exporting nation. But in the mean time, we do need assistance during this crisis period” he added.

Donors withdrew aid in 2013 following the cashgate scandal as it emerged that over K24 billion of public funds had been stolen by government and People’s Party officials including cabinet ministers. A recent audit analysis also established that over K553 billion was uncounted for during the 2 years that Joyce Banda was president.

Mrs. Banda who had been implicated in the scandal by two top government and Peoples Party officials maintains her innocence. She left Malawi soon after the outcome of the presidential elections and she has never set her foot in the country ever since, leading commentators to allege that she was on a self-imposed exile, on the run from cashgate-linked prosecution.

339 thoughts on “Dont punish me for Joyce Banda’s sins – Mutharika

 1. mr bwampini i hope it’s hve been long tym now telling malawians abt jb, we ar tired of ur lies we ar not kids that u cn tell ur useless storys.jb ws there bt we did c all dis problem and jb she solved the problems dat ur brother left without nt talking too much abt ur brother regime.nw u ar jst failing to run dis country then u ar saying jb iz da cause of all dis problem, i dnt think it’s making sense to us by evrytime wen u ar on tv repeating samething……..samething…..

 2. Dzulo tinauzidwa kuti ma donors alibe ntchito. Lero tikumva kuti a presdent amachonderera ma donors kuti atithandize. Koma mitu yathu ikugwila? Atsogoleri athuwa akuziwa komwe akupita? Sakatitaya mmazi awa?

 3. Dzulo tinauzidwa kuti ma donors alibe ntchito. Lero tikumva kuti a presdent amachonderera ma donors kuti atithandize. Koma mitu yathu ikugwila? Atsogoleri athuwa akuziwa komwe akupita? Sakatitaya mmazi awa?

 4. Dzulo tinauzidwa kuti ma donors alibe ntchito. Lero tikumva kuti a presdent amachonderera ma donors kuti atithandize. Koma mitu yathu ikugwila? Atsogoleri athuwa akuziwa komwe akupita? Sakatitaya mmazi awa?

 5. Kkkkk ai zili kwathukuno
  mavuto anayamba 2099 pano ndi wors sinthuzi sizamasewera lero chomwe sagulisa kumalawi kuno kaya nde ndichani ngat afika pofuna kugulisa zipatala zaboma nde anthu amavoteranji?

 6. amalawi ambili amaganiza mopelewera nchifukwa chake tikuona mavuto omwe tikuwaonawa ndipo tiyembekeze kut mavutowa akhalapo mpaka 2019 chofunika nkuzavotera munthu yemwe sanakhalepo kunja kwa nthawi yaitali amenei ndi yemwe amaziwa mavuto akuno ku malawi.

 7. malawi, is about to collapse,,nt so long ,the only best solution to our country is to privatise the whole country bt to #lord_jesuschrist_of_nazareth,,bac

 8. Yes this is true. Today we’re suffering because of what this thing known as cashgate. Vuto timaona pafupi komanso osaonesesa. Analyse and you will find the cause. Today others have left their home becoming destitute roaming around the world because of this so called cashgate. Tiyeni nazo ensnso athawa pompano.

 9. Iwe ndiwe chitsilu kwambili matumbo oonekelawo Galu Gulukunyinda! Ndizomwe ukufunila Kugulitsa chipatala! cholinga udziipitako wekha nanga ife osaukafe ukutiganizila bwa? nzelu ulibe Galu iwe !

 10. M’Malawi muno anthu opusa ndi oyankhulo musazindikika,tilipo ambili eti,sindikuwonapo chanzelu chomwe mwalembapo apa,

 11. keep commenting buh Malawi wll Neva b de same. we proud kut prezd uyu wachoka n office yakhalilidwa ndi wina buh we nah care abot the change. ma policy athu ndionunkha contrary to our economy. hw do we buy a car(Wth our tax) coastin 84 million kwacha 4 a useless politician ov wch galimotoyo siizakhalanso ya Boma after he/she retires, & thn Malawi alibe source of income yodalilika rather thn misonkho n fodya? allowance ya minister /month bein more thn 2.5 million (our tax) tell me the logik of Malawi bein a successive country, whlst anthu ena ake akudya ndlama zathu mopusa?? stop blaming ma Presdent try to 2 blame our stupid policies, am tellin u. tizasimba zina.

 12. JB MUKUMUNENAYO ANAPEZA INU MUTABISA MADOLLAR KOMA ANAYESETSA KUBWERETSA MADONAS,VUTO LOMWE MUDABWERETSA LA KUZIMA MAGETS IYE ANATHETSA PA ZAKA ZIWIRIKUSOWA KWAMAFUTA AJA MUNASOWETSA IYE .MWANA WAMKAZI KUTHANA NAZO.IIIII MAPROMOTION WOSANENA .INU MUKANIKA MKULEMBA APHUNZITSI KOMWE .MFITI YODYA CHILONDA.MUSIYENI JB APUMULE.MUZINGOTI JB KOMA MUKDZILEMELETSA.CHOKANI ZAKANIKA MADALA .YAKULA NTCHITO.

 13. JB JB mpaka liti ? Wonesani uprofesa wanu.Mkuzipeperesa kwambiri aPulezidet.Cabinet yanuso eeish mbola zidude zokhazokha,zinkhala kale pa ndale.Zimene zikukana Information Bill chifukwa zakhala zikuba.Come march if u dont table and pass Information Bill,we shall meet there in parliament,the voters r going to pass the Information Bill.August House belongs to voters hence noone can stop us going to parliament to do business there.Watch out thieves.Mahopu ankhala kale pandale ndamene akuononga malawi,Stupid !!!!!

 14. Ndiye kut misonkho yathu imene tikukhoma panopayi joyce banda adadya kale? Koma ngati inunso mukupanga cashgate yanu musanamizile joyce banda ayi;ndikaletu lija munalowa boma koma palibe chanzeru chikuoneka ndiye sikuti chilichose mukulemphera muzingoti joyce banda ayi nthawi ikupita.

 15. Koma aPresident Peter angakulakwise kulakhula ndithu.Apa utsogoleri nde palibe.Kodi ndalama zaku Escom,Waterboard zimalowera kuti ? Nanga zaku Admarc mmatani nazo ? Mwagulitsa MSB ndalama zake zagwira ntchito yanji ? Nanga amene anatenga ngongole ku MSB abweza liti ngongolezo ? Tsono mukulimbanabe ndi JB ,nanga za 577bn ziri pati ? JB sananyamule office,mwalowamo inu A Pitala,JB sananyamule Jet pamutu kukagulitsa.anagulitsa ndi office of the president mmene inu mwalowa.Sort out the mess that z ua primary duty.

 16. asanamzle PP if hz failn to rule Malawi, let hm nt spoil pp’s c.v dus he shd solve alon & ppo wil judg 2 say he tried hz best coz Malawi woz falln bt as i cn c, hz try hz worst….. munthu mekn public hospitals private??? no medicine?? no power tym fo blakwt in hospitals??? wil poor Malawians b helpd wth dis??

 17. blame game syndrome,aproffessor ntchito yawalaka,this old pa really don’t know why he is there @ the highest office,only God knows what to do with this old man

 18. before the begining to began their was beganation factors that makes some malawian to put you in that position exclude me. some of the factors are your promices mukamwa tea wa 4 oclock on dat time ndikumawanamiza amalawi! you were saing that jb stole the money and you will install all the operating systeams to make sure your people can full fill their livelihood so wheir is the softwaire you put in your mafestor to endvour such problem! dont think that we are all full as some full malawian help you to stole money by put you in that position! we khnow all watch all what you are doing bwana and God is always protect as in any other means! but what you should khnow bwana is that we are tired with nosence!!!!!!!!and it is mypic and vargue to think that you can develop our developing country

 19. Apa pakusonyeza kt amzeru ndiocepa.mukulimbana ndi munthu mmalo mwa route course ya zonse.olo pa den ngati palibe ndalama mdala amakhala ngati ndi opusa osaziwa kusamala family.uyu anapeza dolla zitabedwa guyz lets accept tisakhale ngati andalewa omwe akunena pofuna udindo.zikanakhala ndalama zilipo sanabe sibwezi zitafika apa naye bwez ali dolo.ngati ndalama palibe palibe angazalamulile mwanzeru olo omwr mukuwafunawo iwonso azafuna ndalama.so lets accept ndalama zinabedwa mcifukwa lero ena ali mcitokosi.

 20. Kubela ma zisankho mathero ake ndi awa, u r not blessed on readership yet mukulimbana ndi zoti simukwanitsa, umbava basi, u r just killing innocents Malawians

 21. I swear this country really has funds , but we rily dont have eficient front people to manage these funds.

  Its this country’s biggest problem

 22. Kufinyidwa ndi mafunso mpaka kungovomereza kuti corruption is normal after kuiona kuti he can not detach himself from it… kikkkkk

 23. my dear president nothing to worry about remember earth and heaven belongs to God and everything in them is his. so call upon the name of God most high for salvation of our country. ipromise you malawi will never be the same. the heart that need to help does not include questions.

 24. Peter Muthalika, before you blame PP, blame DPP first regime for K579 billion missing, don’t mess up PP reputation as if your party is clean. Before JB steal such money you store first, ndalama zomwe zinkayenda m’ma carton from state House to Ndata, from there to nyambadwe zili kuti? Baba Muthalika watch out.

 25. Saw the whole interview. He was not convincing at all. Seriously up to his neck in his brothers shabby government. Malawi deserves better

 26. i had the opportunity to watch the intervews on BBC news Munthalika flooped in responding the questions!Ine manyazi kundigwira kuona a president athu akukanika kupeleka mfundo zenizeni zokhuza dziko lake!

 27. this guy is like acanoe out on the deep seas,just going with the wind_i said it i was surprised he said those “age of donor aid is gone words”werent his own!!! ….didnt we know about cashgate when he was sworn in,surely that must have meant he new what he was inheriting & now whats this…? Why doesnt he step down…”stay out of the kitchen if u cannot handle the heat” is what av heard.

 28. Zikafika apa amuna angawa kumakhala kovuta kuwachita control, mapeto ake akutukwanani za kumbuyo kkkkk. Kaya ine budget yanga ndimapanga ndekha no donors.

 29. Cashgate inayamba nthawi ya abale anu baba. Kodi ma nyumba a Malawi housing mumagulisana pa K5.00 aja mukuona ngati si cashgate??? Iyaaaaaa!

 30. Mmene ankapanga kampen muja cashgat inal ilipo kale monse amat malata sment otsika ntengo anali akziwa kale za cashgat asalmbane nd joice banda 65bilion yanchmwene wake ija bwanj kuli ziiiiii mbuz

 31. Mr. President,what all these people are saying is that you are supposed to be educated and should act like one. You have lost track, if you ever had one. You were not here when we toiled to develop the country, and you took advantage of our warmhearted-ness to PLUNDER our economy. God is still in control, lest you have forgotten.He can’t leave them in despare in infinity, hope is there. In somebody else, not you ruthless “professor”.

 32. “We need assistance to address this crisis” – what crisis? The one Muluzi caused by his corrupt ways? The one Bingu caused by his mass theft? The one JB caused by her mass theft? The one APT is perpetuating by his ludicrous lifestyle?????? It is time this man (for whom many of us, including me, had high hopes) starting behaving in a more humble manner and used the little money Malawi has got, more wisely. Why does he need to travel in convoys with 21 vehicles – holding up the traffic (and thus commerce) for what amounts to many many hours during a year? Why does he need the army, government ministers etc etc to ‘see him off’ at airports and the same to ‘welcome him back’? I watched David Cameron (whom I don’t usually admire) on tv last night – wearing wellingtons and wading through the flooded areas in the UK – not sitting on a red carpet, wasting time and resources which could be better used rescuing people and possessions from floods here in Malawi. What about the ridiculous amount of money spent by the various ministries taking adverts in the newspapers at Christmas and other times – sending Greetings and Congratulations? People in Europe and the US would fall about laughing if they saw any of that expensive nonsense in their newspapers ……….Come on, ATP, you have lived in the West long enough to know that this ‘Big Man’ style of governing is both ridiculous, expensive and damaging (but it might be very good for pampering the ego) and that Malawi will NEVER develop if tis kind of behaviour by elected leaders carries on. You DO know better, you CAN behave better – and you would go down in history as an amazing leader if you just got off your gilded throne and started working for the benefit of ALL your people instead of a chosen few in the ivory tower that is Malawian politics. My heart bleeds for my beloved Malawi whilst people like this hang on tp power …..

 33. Mbendera Wangwiritsa Bibi Munthu Wankulu! Malonda Amphaka.Inu Boma Amaba?Lelo Ndiizi.Tisanagule Malonda Timaona Kaye Qaulity! Mwagwilitsana Totenthatu Apa!

 34. Kkkkk koma bwana uyu lero aneneichi mawa icho kukalamba chani.Ndikhoza kulera ndekha anawa oloopanda inu mwezi umodzi wayamba koma bambo opanda inu sindikhathe zeru za chizimayi zimenezo

 35. JB was manage 2 change things in 3 month and everything was normal but now look wat is happening shame on u Peter 4 making us suffering coz of ur poor management

 36. Kodi a President wa akubwebweta chani apa?kodi mesa apasidwa ma conditions ofumika kupanga fulfil kenako ma donors apange resume aid omwe mwa ena ndikupanga pass access to information bill(ATI)?chilipo apa ndikungopanga fulfil basi coz its for the greater goodness of we poor Malawians,instead of kukana kutero for the sake of politics kuti abe tindalama tochepa tilipoti.Anthu andale odzikonda inu Chauta akulangilani pansi pompano!

  1. Mmmmmm akulu condition ya ATI yaperekidwa liti kuti tiziti sakutipatsa thandizo coz of this ATI bill? during JB regime this bill was there, y ddnt they pass it? sindikumubakira koma we have to be reasonable. However, this gvnt is spendng alot nde sikufuna kuti atola nkhani shld have access to this infor…lets pray hard, otherwise they can twist this ATI issue kuti ziiiiii…

 37. zathu izo tsopano coz amalawi timaiwala mwachangu tikanakhala tiķanakhala kuti tili ndi chikondi ndi miyoyo yathu sibwezi titavotelanso banja la amunthalika nde let’s just keep quiet and watch what will be happen

 38. Godwell Gondwe apepese kumtundu wa amalawi for what he say kti ma donor alibe ntchito,pamene iwo akunyambita misokho yathu akadwala they use our revenue kupita kuzipatala zakunja hw stupit they are ?

 39. panga zako aise usalimbane ndi amayi kwawo kumatha kufa safelana mamuna wanji ongokhalira kumunena mayi tsiku ndi tsiku chisilu iweti

 40. KkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkKkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkKkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkKkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkKkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkKkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkKkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
  I cant stop laughing vuto lothamangira zithu ndilimeneli

  KkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkKkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

 41. Kod cashgate inachtika pa 2yrs ya amayi yokha kapena zaka zingapo zammbuyomu?

 42. kubedwa kwa ndalama boma sikunaya pa jb iyayi zinayamba kale, ndipoti zizikukunani mwati ur being punished coz of jb sins, wat silly point for being a president, ngati zakukanikani js leave the post BaBa hamba b4 its to late otherwise people will turn back on you

 43. Mkesa amati ndi pulofesa ameneyu?Awonetsetu kuti ndi dolo.Paja amkati dzikoli likufunika kumayendetsedwa ndi mapulofesa wokhawokha.Munachita matama kuti simukudaliranso thandizo la maiko akuwulaya kuyendetsa dziko poti mumkati muli ndi kuthekera konse kodziyimira panokha.Kodi mumadalira tindalama tomwe mumapeza mukagulitsa chingambwe ndi mbatata?Lero suyu apa mukulira.Lakupotani dziko la Malawi.Dziko limatentha ili.

 44. deal with problem stop speculeting your problems and pin on madam JB,chimodzimodzi ndi moyo chifukwa anayamaba akuchimwa ndi adam doenst mean every wrong move imene utapange u shd pin on him coz he started it, just fix the problem MR presdent after all you told people of malawi that if they vote for malawi wathu will never be the same

 45. boss musanamizire jb cz iyeyo anakonzako zina bt from cashgate of muilti billions in ur brother regime munangobwera ndi matama ngati ndinu a professor omba mdziko muno,ma x presidents naonso anali ndi nzeru.ochepesa mavuto ndi nzika za momuno oti mavuto amawadziwa from foot

 46. Thts nonsese jst dil ur self hw can solve ths problm amalawi azakuvoteleniso osangopanga kafukufuku opanga zeru act like presdent of country.

 47. Nthawi ya Binguso kunali zero budget inali cashgate ya JB?Mene munkalowa munkati mukukakhoza tiyeni khonzani olo titalimbana ndi JB sitipezeka ndi ndalama

 48. Nthawi ya Binguso kunali zero budget inali cashgate ya JB?Mene munkalowa munkati mukukakhoza tiyeni khonzani olo titalimbana ndi JB sitipezeka ndi ndalama

 49. Kkk dppso ikukhuzidwa mu cashgate 92 billion anaba ndani? Ndipo 28 billion ndi 92 billion yambiri ndi iti?musaone ngati ma donors ndiopusa even 92 b peter ikumukhuza si pp yokha ikutipweteketsa komaso dpp komaso nduna zina za dpp zikukhuzidwaso mu cashgate ya pp koma sakufufuzidwa akungolimbana ndi otsutsa nanga amene ali ku cipande sakuwafufuza sazaba? Inu simungawaputsitse azungu

 50. NGATI J.B ANABA NDALAMA M’BOMA IWOWA AMACHITILANJI MATAMA AJA POLOWA M’BOMA MKUMATI TINGAYENDETSE BOMA OPANDA MA DONAR?? AKANAMUSIILA MMAI YEMWE UJA KUTI ZIMUVUTE YEKHA, ANAKAKAMILA MPANDO MPAKA KUBELA MA VOTE CHOLINGA ALAMULE LELO NDI IZI AKUVUTITSA ANTHU OSALAKWA. DPP YAKUBA MMAI UJA ANAKUGWILANIDI. AKUKANA KUTHANDIZA MALAWIWO MAUMBONI AKUBA KWANU ALINAWO MUKUBISALA PACHIPANDE.

 51. Worst leadership I have ever seen…good at blaming others instead of scoring..2019 we will vite based on what you have done not how many times you have wasted time blaming others

 52. Malawi sangayende popanda ma donors aliyense wawana mmene malawi wanzuzira mzika. Zake chofukani ndikugoja ndikuvomeleza kwakuwake ndalama basi kuti dziko ndi anthu ake azisangalala

 53. The Only presdent in africa anapanga resign was Thabo Mbeki zitamuthina koma athuwa nde nkhakamira yet akulephera

 54. You share the sins Mr. President. It all started with Bingu and you were part of that admin >K577b vanished and you’ve been silent on this.

 55. MALAWI IS STILL BREAST FED AFTER 50 YEARS OF INDEPENDANCE. WHY IS MALAWI IS NOT GOING FORWARD? WAKE UP LEADERS YOU ARE THE ONES WHO S USING TAX PAYERS MONEY TO MEET YOUR NEEDS.THE DONORS HAVE BEEN THERE SINCE KAMUZU BUT NO PURE DEVELOPMENT

 56. What Mr Mutharika say!!! is for de nation unity,togather to find solution, lets all togather having positive attitude towards response..

 57. Munthu azigonja kumene osati ndine millionaire ine what for? Tikhaule kumene chifukwa cha makani anu baba, Chala changa ine kungoda cz of u.

 58. Dnt tlk about someone do ur jb as przdnt mwalaphela tulan pasi udindo bas mpira umapweka ukamaonena ulikuja koma ukalowamo ndiye ndizi

 59. Ife kumwera Mukatibwezere kwathu kumozambique aaaaa mukutizuza kwambiri Boma longodalira ma Donors basi.Vuto ndikuliona ine ndilakuti anthu ife timakana Mfundo za donors monga,kukwatirana amuna Okha okha,satanic kulowa Mziko,Zinthu ngati zimenezo ndichifukwa chake madonors Sakufuna kutithandiza bwino uyo mukuti ndi president yo akuziwa zosenzi.

 60. Peter usatitenge ngati kuti nafeso mclass sitinalowemo mbuzi ya presdent iwe.wayiwala kuti ndinu aDPP mnayamba kuba ndalamazo pano mkunamizira adzanu.vomelezani kuti kuyendetsa dziko kwatikanika basi osati kunamidzira azanu mwandikwiyitsa kwambiri.

 61. Koma anthu inu mukanakhala kuti dzulo munaonera BBC mkuluyi akumpanikiza ndi mafunso hahahahahaha mukanamva chisoni ine mpaka ndinafika pa point chokaikira if Peter is indeed a professor

 62. The mntharika,s also crying for Donners help ? No, didn’t ur late brother Dr bingu wamntharika teach u, how zero deficient budget works ? U don’t need Donners help remember.

 63. Angotula walephela bwino kwabasi chitsiluchi chilinso ndizitsilu zina zomwe zikusapola kulephela kwa pitala kusaukitsa Malawi aliense iuzidwe zoona nkhalambayi zikundinyasatu

 64. mphoto yauchimo ndi infa alondola nkulu wake naye akuzuza anthu wt his stupid adminstration ndalama anaba nd app okha akeee …..olo atasiya kupepha just the same ndlama sizuoneka ntchito zomwe ikugwila zazii mutu suwe waka nga nadi

 65. i thnk tizangopanga hire munthu wakunja Bill Clinto, or Bill Gates, zikhoza kuzayenda osati atsogo athuwa… iwowa ayiwala zomwe DPP yakhala ikusakaza? tikumangomva za 517b yomwe akulephela kuifufuza!

 66. Am fed up with dis clueless leader. During campaign he was telin us dat @ 50 we cant continue relyin on donors., and today he has a different version. Kodi mesa u used to despise JB akamanena za ma donors munkati opanda nzeru

  1. Bolanso amayi amangoneneratu kuti azungu akuti………. Mopiya yu nde zamuvuta amayesa kugawa njinga ndikulamulira dziko kukagula bonya ngati akadya asovenge kkkkkkkk

 67. I have seen that our leaders say the truth when they talk in English and they are among the intelligent people outside Malawi.” Malawi is the poorest country in the world.” “yes” president responds. kkkkkk

 68. He is as clueless as Bingu himself. How can he miserably fail to convince donors to come back and start supporting Malawi? All he can do is to shift the blame to JB? He must account for the 577 billion the DPP regime squandered. Its as simple as all that and thats what donors are waiting for, not just making unnecessary utterances.

 69. Research revealz dat our GDP z around a trillion, ds year’s biggest budget in history 901bn MK is less than our annual GDP. We can survive without aid koma kuba

 70. Sakudziwa chomwe akuchita emweyu amati azungu alive ntchito tizuumila patokha pano wakalila konko amanyoza kuja atithandiza matchonawa

 71. APM ophuzira bwino profersor dziko si mudzi pamafunika zeru za kupya bwino osangoti poti mkulu wanga analamulira ineso ndilamulira ma talent amakhala osiyana zikafika apa ovutika ndi amphawi aja akumizi

 72. NGAT ND JB ANABWERETSA MAVUTOWA BWANJ SAKUZENGEDWA MULANDU?TAONA MUKUMANGA ALUTEPO ND ENA KOD MAIYU MUKUMUOPA KAPENA MUKUFUNA NANU MUSAZAMANGIDWE MUZAKATULA PANS UDINDO?PAENERA PAKHALE NDONDOMEKO INA YOENDETSERA CHUMA CHABOMA TISAMANGOKHALIRA KUMVA ZOT WABAMO NDALAMA KOD BOMA LIMANGOMUSIRA KUT AZTAPA NAZILIPIRA EKHA PREZIDENT YO?MULUNGU AKUONA KUZUNZIKA ND KUFUULA KWA ANA AKE.CHNANSO NDCHAKUT ONSE AMENE AMAWINA UPREZDENT AMAIWALANSO KUT IYENSO ND MWANA WAMULUNGU.ZIBANI BASI NDNTHAWI YANU.

 73. Mr president do you think donors are stupid. You was told and given a task by donars but you are failing. Dnt lie about Jb even you you’re enjoying 92billion which your brother anaba. Unauzidwa uufufuze katangale koma iwe sukufuna ndipo choti udziwa Chabwera atenga boma iwe ukubera amalawi mumatumba

 74. Nthawi zinanso a president mukupanga zinthu ngati munthu osazindikira this is 2015 en we are going another year but you still looking for the past rather than finding a solution to those problem but your still pushing Cash Gate, tayambani kuonetsa chomwe munakhalira a president…. osamango khalira Cash Gate tiziti inu olo 1 tambala simuzachoka nayo yathu pamenepo… mukuchedwa kwambiri mukamapanga za anzanu…. gwirani ntchito a Malawi azakuyamikileni osati ma news daily Cash Gate, Cash Gate.. ndiye ndizichani zimenezo

 75. The same peter who said Malawi doesnt need aid to survive, lero akuti dnt punish me bcoz of sm1 else blah, blah, blah!?

 76. Don’t punish me for DPPs fans sins I didn’t vote for Peter koma bwanji vuto ra kuthimathima kwa magetsi likusokoneza ma program anga makupuni ndimkalandira mbuyo monsemu pano muzi wathu wa anthu 30000 plus ndithu mwabwera makupuni 25only mhhh pls don’t punish us for Peter Muthalika’s fans sins. Inu mamillion omwe anaononga potenga khwimbi ra anthu ku UN aja sakanathandiza pa mtera mzipataramu mmesa anati iye ndi millionaire mkare sakutuliranji pansi udindo mmalo mwake kupitiliza kuyamwa Malawi owondawonda kareyu? The worst ever Malawi president Peter…… No job no food no security Yesss aMalawi phunzirani kuganiza musanapange chinthu why you voted for a person yemwe campaign yake inali kukwera njinga zakabanza,kugura bonya ? Ahahahaha mxieeeeeeeeeeee Malawi is ready for change couz #CHAKWERA is here…

  1. Chakwera r heavenly sent? Dont waste de tym cuz he doesnt know noting in political arena, peter is not ordinary like Yona.muzakhumudwa tikutengaso boma pa 2019.

  2. Musaganize kuti MEC izalorera kuti paberedwenso mavotes ngati chisankho chapita chija ng’oooo Mbendera amkaziwa chilungamo samkafuna Malawi atayike ngati mmene watayikiramu have you ever seen President akulumbilitsidwa no Bible or Qur’aan? Ma judge amkafufuza ngati ndi msogoreli weniweni but anaona kuti ndi Mr Ibu wopanda mzeru Love your country pls think twice mmene katundu akukwerera mitengo daily mu winawe uli still kupanga support zorakwika? Mhhh koma Malawi why?

  3. @Clement Chakwera ndi rider of opposition ku nyumba ya malamulo yemwe posachedwa pompa anachilimika pamodzi ndi chipani chake cha MCP kudzudzura ufiti womwe aMillionaire anaganiza kuti school fees ikwere mma govt schools. I think ndayankha wamuziwano Chakwera . “izi nde nyasi zen zen” ndikukhulupilira kuti makina anu opangira post comment yo amavuta nde unakwiya…..

  4. campaign ya pa facebook mupusa nayo achimwene ndipo muchedwa nayo, Dpp inabera mavoti ili yotsutsa nde ikalephere ili m’boma kale? 1 president at a time, chakwera sazalamula malawi, mark my words braa

  5. Ahahahaha JB zinamuraka kubera ali m’boma bwanji? Nde do you think kuti uyu wogulitsa bank yu muzamuvoteranso pano nde akugulitsa chipatara Cha Queens kuononga zomwe MCP inapanga karekare muzamuvoteranso? Mhhh anthu enanu ine osakumvetsani ndithu aaa Malawians why do you regard a butcher as a doctor? Njara iyiyi enanu sikukukhumzan couz muli pabwino m’ma taunimo koma ine ndi abare anga m’mizimu tikuzigwira ;-( ;-( …

  6. Iwe seleman your really stupid minded how can the country managed proper wen all the funds were ruouted. dont dare talking of chakwera here coz chakwera akuyenera kupezeka ku church since he z a pastor komanso ngat mukuona kut peter mutharika anabela mchotseni pa mpando ngat mungathe koma ndinu anthu opasadi ku MCP eti ndizomwe mukumanyengezana zimenezi kkkkkkkkkkkkkkkkkk mwauponda Peter and soulosi chilima alibo heavy

  7. Uchitsiru wa mmalawi omasapotera munthu mngakhale akuchita zopusa ….wake up guys..sindingamuikila petr kumbuyo pamene zinthu zisakuenda

  8. tell dem bro@selemaan…osagulitsa zinthu zimene linapanga boma la dpp bwanji aagwape inu???god pliz why r keeping such pipo alive..god must drag dpp to hell..

  9. Guyz Malawi azivutika chifukwa choti munavotera UDF 2gether ndi mfana wa dazi uja(Atupele)? Yemwe ali stuck pambuyo pa DPP kuipatsa mphamvu zoti izichita zinthu zorezera:::Kugulitsa bank Kumangothoka za JB kufuna kugulitsa ma hospitals mxieeeeeee kuba dollars za NAC kuvaitsa ku mlakho wa Alomwe that’s good??? Aaa too bad, Komabe it’s not too late inu ndi ine kupanga decision yokungana heavy kuti UDF izatengerepo phunzilo dat tinawatumiza ku parliament ndifeyo not there money as they think abt basi tizangovotera Chakwera. Ineyo ndikuboweka heavy ndikomwe MDUBZ(MALAWI)akuvaya soon timva Lake MW wagulitsa nde sakumamva maganizo a fans akungozipangira…..apa ndatha ine wanu,Ghetto Wiser VuJJah… Zinazo tipitiliza ku TC Basheer Bakali Twaha Mussa Nasri Kumbes Nabil Bakalie Mada Kay Kim Man Giya Uta Kukoka Jali Kaotcha Nicdinho Ashraf Likanga Raphael Paxy Rahim Frogy Funan J Hassan Jumah Kaotcha Khadijah Abdul Kandu Saidi Chisowa Msusah Culturez Ander C Mussa Seleman Big-bunzo Nak Oyimba Uja

 77. Kodi zomwe mukuba zamisonkhozi zikuchepa?nanga bwanji mukulilirabe madonors,mufuna mutuluke ndi zambiri eti? Mwatikwana bwanji????

 78. Matama atha apa pemphani man maona ngati ndalama zathu zikhoza kukwana aaaa koma ndinu azeru paja tapangan toine ku ndinu adolo inuyo

 79. we leaders lead pple with wisdom from God.Try to be patriotic with ur country,pple of God are suffering because of leaders but mind u the worth u accumulate for poor pple is not urs and not long lasting it will vanish and we put to say u won’t go to heaven with it,it will be ur good works or bad which will prevail on Gods eyes.

 80. Malawians You Are Very Funny People, You Think APM Is Not Delivering? If You Are Blank Upstairs Just Stay Mute Than Commenting On Something You Dont Uderstand. Cashgate Took Place During The Caretaker Government When Great Leader Of The Soil Passed On. So Lets Comment With Our Sober Mind Not With Jelousy. Even If We Can Give The Chance To The Leaders Of The Parties You Are Supporting To Rule Malawi Right Now, Do You Think They Can Turn Malawi Into A Heaven. Tiyeni Tisiye Sanje Ndi Kaduka Kuti Malawi Atukuke. Mupindulapo Chani Ndi Sanje Zanuza. Wakwiya Ndi Mfiti!

 81. As our president,we expect u to lead us,be a man n dnt cry over spilt milk.. u took an oath to lead the country in any situation wt ur myt.Why always put the blame on someone

 82. Chomwe ndimaona sipadzapezeka President wabwino 100% komaso Malawi sadzapita chitsogolo olo ma iko atatikhuthulila ndalama zodzadza ma truck 10 Vito tinazolowela kuba pali zinthu zina Mulungu anatidalitsa nazo koma timalilabe monga nyanja ,kodi boma silingatenge ma billions angapo kuti malo ammbali mwanyanja muzilimidwa ?tikhoza kukhala odzidalila pa chakudya ngati mkupempha tizipempha zinazo NDE inu a president to think. Deeper about Malawi

 83. Mr President i believe you have taken a right direction by accepting the fact that you can not run this country without donors aid,putting the blame on others wont take this Nation anywhere,remember whats done can not be undone.

 84. He failed to convince me that corruption was over a decade whilst he only concentrated on the 2 years of JB. If it was Stephen Sackur (sp) presenting he coukd have cried with questions

 85. malawi z not ready to depend itself,look 40%is small when comes from others bt collecting from ur pockets its much money,zimavuta 2009 zinthu zikuenda ndiye panopa sizikuyenda then u say tiime patokha.mw z poorest & standing ourself only when our resources hv started working.mwadziwa big panopa kuti nzovutadika? ma x president aja naonso anali ndi nzeru zikadzaenda tidzazidalira bola kutsogoloko(administration) musiye kuba

 86. Anthu ena mumayankhula mopusa kwambli olo zitavuta maka muthalika sangagone ndi njala ndipo sizizatheka komaso ana ake sangazaphunzile ku communinity day xool komanso nyumba mwake magesi sangadzime olo zitavuta maka nde enanu mukuyankhula mopusa mumvu ululu ndiinu ndipo mukhauladi

  1. tinamva kale ululu kape iwe a galu ongoimbira mmanja zilizonse aja ndi inu amene mukumusocheretsa chi president chanucho..kumangoikira kumbuyo ndi mabi omwe basi nde tapitatu akakugaire chimanga si ndambuyako peter yo??nyani wamtundu wanji ?hiking xool fees ngat ndalama ife timachitq kukumba moreover nothin to think about salary increment..fuck him

  2. Kkkkkkkk kape ndiiwe ndipo ulibe nzelu mavuto ngati awa akachitika amavutika ndi amphawi eni akeo siziwakhuza mabanja awo ana ao amasangalala nde ukati peter asovenge umunama umve ululu ndiwe iye sazagona ndi njala iweso uli ngulu limodzi la mbuzi zoganiza mopusa

  3. koma iyeyo peter yo sagona bp imakwera diary bola ife kumbukila mkulu wake ,olo tinkhala mumdima kaya kumphunzira ku community koma ntendele tilinawo nsakubisile zikafika apa president sagona ase Tiyeni tizingopenpherapo apa mulungu alowelere

  4. Eeeee ma zoba musandizazile peter si bambo wanga sindidyaso kwao ndimapanga zanga ngati mukuona kuti dziko lanulo lavuta osalithawa bwa???4tseck

  5. kungoti a chewa inu mwangomuda peter ndipo mukhaula mpaka 24.zi a chewa zimakape inu ngati zakuvutani bwerani kuno ku mpoto tikufuna ma tenant chifukwa makoswe anatha ..ni

  6. Hey phuma kimi!!!!!!!!!?zanu izo ngat ndinu anzelu osapita nkayankhule naye bwaaaa?more over mungozivuta kumalimbana ndiine am nt there mukhaule ndinu ine zanga kuno zyahamba

  7. Sindine mchewa koma mmalawi okhuzidwa chomwe uziwe ndi choti ine sindikhaula coz ndili ndi president wanga yesu komaso olo akhale ndi chuma chambiri koma azachisia azayakha pamaso pa mulungu peteryo komaso choti uziwe anthu akamakudandaula umasowa mtendere bwanji bingu anali ndi chilichonse k6a anafa imfa yosakhala bwino ngati si president ndiye uziyakhula bwino even thyolo,chilazulu .mulanje alomwe enieni akumudandaula si achewa oka ai uzikhala ndi chisoni ndi athu osauka ngati president wa ku tanzania chuma ndi mtendere zosiana utha kukhala wa chuma ulibe mtendere kukhala osauka uli ndi mtendere watch out.

  8. Nkhani yabwino sis komano ena asanditukwane ngat ndimadya za peter ndimapanga zanga ndipo munamuvotela ndiinu ine sindinavote zipaseni ulemu ineso ndikupasani ulemu

  9. Koma anthu ena munabadwa ngati mbuzi komaso mukuntha kuoneka kuti ndinu ma educated fulls. Sydney ndi Jastine are u sure kuti dziko la Mw likuyenda bwino kuti muzilikila boma ku mbuyo? U so stupid man n am sure about it!! Mwini wake ngati wanena kuti sizikuyenda bwino who are u kuti mukamubakile? Kumatako kwanu agalu inu ndinthu!

  10. hahahaha makoswe mukuchedwa ndikunyoza munthu yemwe zake zinayera kale palibe chomwe mungaphule olo amene uja kusiya upulesident adzakhala olemera mpaka imfa yake inu muli chonchobe kunyodza ngati mukuona kuti zinthu zakuvutani pangani plan kupita komwe mukuona kuti zikuyendako mwangokhala pansi machende phwi kudikilira mtsogoleri akupezereni chilichonse? Olo atalowapo wina muzakhalabe mukutero mpaka kufa kwanu zilimbikireni pa inu nokha

  11. Auze pasadi ulesi komaso kudalila zopasidwa (kupempha)ndevu ziliphwiii mmalo azilimbikile they r bzy complaining boma apindula chan?muzakhala ovutika mpaka kale ngat simuzitenga bwino

  12. Kodi inu a Pasadi muli sure kuti munthu amene ali ndi ndalama amakhala pa ntendere? Iwe ndi ndiopusa zedi kuposela chi nzete. Bwanji muleme nkulu wakewa bwampini anafa ngati nkhuku pomwe ndalama anali nazo kape iwe!? @ sydney anthuwo anayamba abwela pankhomo pako kapena pa a president kuzapepha? We wot gud leadership not like dis shit guy!

  13. Vuto ndikusamdziwa Mulungu.Ndipo osazindikira #1 ndiiweyo,coz ukanakhala ozindikira sukamanyoza azako amene akulira kuperepeseka ndi ululu wa mano azinkhanira zimenezi…Ukadaziwa kuti aliposo azako olimbikira ophuzira koma akusaukabe sukadakamba zimenezi.Aphwanga Mulungu simunthu,chilichose ulinachocho mwiniwake ndi Mulungu.kaya ukudzitenga ophuzira odzidalira suli ku Malawi & u think u r safe…Ok!ndimumtengo ulimo ambwana.

  14. Mayazi iweso ndiwe mbuzi kxhosha ndipo opanda nzelu #1 ndiwe ukundi2kwana y?pita ukamuyankhule ngat uli shash aunamvako kuti presdent watsekula shop?unamva kut presdent akugulisa mankhwala?vuto si presdent mesa kuli pariament ntchito ya pariament nchani?Frank manyaka akowo asandikhuze usandijaile ndimapanga zanga

  15. Amzelunu,mbulife,kaya Apresdent Tonse tikudikira tsiku lomaliza lomwe aliyense adzayankha mlandu monga mwantchito zake.Mukanakhala mukuona momwe anthu akuzuzikira,simukanamala nkhula zimenezo.

 87. Bwana Ndinu Okumva Zanu Zokha Mwamva Eti.Kodi 577 Billion Mudakaisiya Kuti?Dzikotu Inu Lakukanikani Koma Simufuna Kuvomereza Mukuopa Kuti Mukavomereza Anthu Akusekani.Ndipo 2019 Mudzawinira Kubera Basi Koma Mukadzawina Kudzera Mumphamvu Ya Satana Mulungu Adzakukang’athani Pompopo.Ntchito Lero Mukulembana Poziwana.Kodi Mumaziwa Kuti Dziko Lino Tilimo Anthu Ovutika Koma Tili Ophunzira Bwino?Koma Kuba Basi Kutibera Ife Aphawi.Nthawi Yatsala Pang’ono Kuti Mulungu Udindo Wanu Auyike Pa Sikelo Ndipo Mulephera Kufikira Mulingo Omwe Chauta Akufunira.

 88. he was sayin we dont need donor money panopa nde ati chani eeeeee dis presdent atiphetsa ndithu demos to come achoke amenei

 89. Kungoti athu’fe timaika ndale pali ponse koma bwezi tumadzifunsa pakati pa ife athu ovota ndi ovoteredwa akusangalala ndani????? Then bwezi titasiya ma coment okhala ngati inu zanu zili bwinowo APM sangadandaule ndalama coz ali nazo kale koma athu wambafe nde tikana kwapulidwabe osati maswera

 90. Tsono mr.president mmene mumkat malawi akuyenera kuyamba kuzymira payekha inu mumaganiza ngat ndalama muzitenga kut?nde anthu akamanena kut atsogoleri apa malawi pano amangotha kukamba zabwino koma amalephera kuzkwanirisa zkhala zaboza?.

  1. Cashgate started wayback during bingus term and jb inherited and worsened it.vuto lili apa ndi MBENDERA wamugwiritsa bibi munthu wankulu.anagulitsana malonda amphaka.chimphulikire basi!

  2. comment yanu ndi nkhani parallel, kodi chimakhala chamba kapena kukula mopusa? mxiiIiiii ndakwiya nawe iwe innocent wandimva????

  3. Inu mkuth comment imeneyi zikusiyana ndi nkhani ndinu mbuli za anthu. Ndan ankat akhoza kuyendesa dzikoli kopanda ma donor? Bola munthawi ya jb zinthu zinkayenda.

 91. Iyetu wanena kale kuti amene avutike ndi anthu iyeyo sangavutike mpang’ono pomwe’Ndiye mukutaya nthawi nkumati sunati iyai avutike ndi anthu nabola ine ndikudya Rand ndizigwira ntchito kuno ku South Africa’Sindingayerekeze kugwira kumuziko tinapeza yokhazikika ife kuno

  1. kkkk bola inu mukudya ma Rand koma ife iii ka xalary kochepa koma nxokho okhawo iiiiiiiiiiiiiiiiiiii

 92. Amalawi tiyeni tiganize ngati Kabowa nthawi zonse nkhani izikhala ya ma donors basi. Azungu agogo awo anagwila ntchito yolimbika mpaka anapeza zochuluka zina mkumatithandiza . Ife kumalawi kuno timangfuna kudya za eni mpaka liti.

 93. Cashgate inayamba ndi Bingu that tym he was Minister so it means zikuwakhuza don’t blame JB coz ndalama zinasowa not only in those two years she was president

  1. mu nthaw ya mbigu JB anal vise prezdent kmanxo nduna ya boma, atalowa m’boma jb kunasowanso ndalama za n’nanu, bwanj jb ankalepthera kuwamanga omwe ankaba ndalama nthaw ya bingu, pamene anal prezdent? cashgate ikumukhudza kwambli jb,

  2. Musamajoke pazinthu zaserious plz.Mmene zinaliri nthawi imene ija JB ndi Bingu,JB akanaba ndalama?KuMalawi kuno kuli anthu ambiri zitsiru.No wonder these fucking coments &poor choic.Mwina mukumadya nawo zachipani.

  3. Mukudziwa ndichifukwa ninji JB anamuchotsera kuchipani? Za cashgate kodi zinaziwika mu uramulilo wandani? Si wa JB kodi? Iwe #Jaquelline chipani cha PP chinapangidwa form JB ali m’boma or asanalowe vuto ra aMalawi mumangomvera zilizonse tamaganizani……….

 94. chomwe ndimamva ndichoti aphungu chaka ndichaka amavomereza ndalama zoti zigwire ntchito mdziko lino. Kodi ndalamazi zimagwira ntchito yanji poti ife sitimaona phindu lake? Kodi munthu wosauka angatukuke bwanji ngati inu mukukweza ma allowance omwe mumalandira mukayenda? Phunzirani kukonda dziko lanu osati matumba anu wodzadza kalewo!

  1. mukunama guyz coz chomwe ndimamva amati undina wa zaulimi walandila ndalama zakuti and unduna wakuti walandiranso zake kodi amalandira ndalama palibe? Nanga bwanji amati ma allowance amaononga misonkho yathu? you guyz muzikhala ndi mfundo!

 95. Iyayi bwana musalile inutu simunati & pankhan ya magetsi iyayi muli bwino ndipo xitizapezaso prexdent oziwa kuzimitsa magetsi ngat inu tikunena pano magetsi mwatenga kale kuzolowela zamu n`dima na pozimitsa magetsi ndiinudi proffesor

 96. Even we call him names,but we are malawians whom he z servng,everythng has got time,to achiev somthn t needs humblenes somtyms.amene tikunyofe timafuna atani tsono?bigup mr presdent,good direction!

 97. Kkkkkkkk.Nanga pamenepo woputsa ndi ndani wobera mavoti ndi 577bln ndimayesa kuti ndi wochenjera vuto ndilakuti mkumawopseza amayi poti ndi munthu wamkazi pomwe baza zili kumbuyo kwanu a APM yambani kaye mwachotsa chisoso mdiso lanumi m wona azungu ayamba kukupasani ndalama kkkkkkkk

 98. kodi ma donors amawathandiza ndi ndani ? i think it’s high time We Malawians should move on our own. asiyen amenewo dzawo zinawayendela chifukwa cha hardwork yawo.Tilimbikire nafe zidzayenda.Tiyeni tisiye dzogonalila ndi kupepha ena….

  1. Sangalire man,he is doing this for us poor pple,iwo tu zawo zinayera kale,mankhwala akusowa nzipatalawa amathandiza ife,iwo amapita zakunja ali ndi ndalama

  2. mesa amanyoza ma donors wadziwa lero? Fokof always contradictin himself why shaaaaa koma munthu amenei ndi nyapapi et

 99. let me remind you peter, the donors are not punishing you for joice banda’s sins, but for the K577b which missed from 2009 when the dpp was ruling. Pse learn not to contradict yourself. Now you are saying you need donors.Scrape fisp and malata subsdies and you will fund hospitals. Where are your eyes and brains? Remember you ran away and only came back to plunder. What a shame!You have no feelings the rural masses, for you have never been one nor lived among them.

Comments are closed.