‘Join DPP and help me solve this mess’ – Mutharika pleads with Chakwera


Lazarus Chakwera

Malawi President Mutharika has asked Leader of Opposition Lazarus Chakwera to join the ruling party to help find solutions to the current economic crisis.

Chakwera had asked Mutharika to resign, saying the President was visionless and a “problem to Malawi”. He accused Mutharika of delivering a “zero-plan speech” when the president presided over opening of the 46th Session of the National Assembly.

Peter Mutharika and Lazarus Chakwera
Mutharika wants Chakwera

“If you are admitting that our problems are too complicated for you to solve, then why are you clinging to the office you hold? We simply cannot afford to let the ship we are sailing on to sink in these troubled economic waters simply because the captain does not know the way to our destiny or how to navigate troubled waters!” Chakwera had said last week in his speech as Leader of Opposition in Parliament.

Chakwera had also warned Mutharika that opposition parliamentarians will take things in their own hands by making laws that will not pass through the executive should the Mutharika administration continue dallying in taking bills to Parliament for deliberation.

In response, a visibly agitated Mutharika asked Chakwera to join the ruling party. During a rally held in Mangoch over the weekend, the President also banished calls for his resignation.

 

331 thoughts on “‘Join DPP and help me solve this mess’ – Mutharika pleads with Chakwera

 1. Not to join DPP but to join hand in hand to develop this country as you can see the opposition side are just opposing things that can make the betterment of Malawians but they are just opposing everything and Malawi 24 be serious on sourcing information because you may end up dividing pple.

 2. Iwe mcp becareful wamva ngati muchipani mwako zinthu sizikuyenda bwino izo ndizako iwenso pp iwe zomangolondola zopusa ngati chipani chako chili ndi president usamale mavuto onsewa ndichifukwa cha iwe umbava leave Professor alone Professor salamulira chipani ngati ena inu akulamulira dziko lomwe munalivundisali pamene timavota tonse tinali ndichiembekezo kuti zinthu zikhalano bwino osaziwa kuti mwavuulamo ndalama zonse kuti obwerayo akhale oipa anthu oyipa mitima inu ndimaulamuliro angati adusa be 4 Professor leave him to rule antil 2019 basi the days r not waiting 4 us w wil talk and talk until 2019 without getting the real solutions bcoz our country now has got a bad record outside the country no country beyond malawi have interest of helping us stop pointing finger a president point finger the pipo who destroyed our resouses and money with the aim killing al malawians 4m msanje to chitipa we malawian ngati misampha yobera ndalama mboma ikutikanika tiyeni tivomereze kuti we r in a another season the s

 3. Dpp Inalowa Mboma Thru A Back Door.Kuba Galimoto Mulibe Mafuta Okwanira Lelo Ndiizi Yaathera Mafuta Pachikwera Nkumati Achakwera Tikankheni.Muisova.Apapa Zinthu Ziwiri Zikuenera Kuchitika.Kusiya Boma Or Bomalo Likusiye.So Its Dpp’s Choice.Maibaiba Awa.Munabera Zosaenera Kuba Mudziwaso.Mizimu Yakwiya.

 4. hey guys, what r we going to say,, problem is our country or the president that we hv becouse every term, we always be in trouble with economic crisis

 5. Hahahahahahahaha Soldier lucius banda tiyimbire nyimbo yazomwe zikuchitikazi.

 6. Guys dziko lanthu la malawi zinthu zizayamba kuyenda bwino pokhapokha DPP ikazachoka m’boma…Azungu otithandiza zangapereke ndalama kwa atsogoleri oti ali involvef mu cashgate, the whole of DPP top blast is involved in a way or the otha… DPP must go zinthu zisintha ku malawi..chithandizo chiyamba kubweranso…olo atalamulira Kamlepo malawi will sing and dance again..ndampaza!!!

 7. to ask opposition to help run the government isnt weakness, its only in africa where opposition and government are enemies

 8. COME 2019, DR CHAKWERA WILL EMERGE AS A VICTOR, I CAN SEE. NKHANI ILI MKAMWAMKAMWA KULIKONSE NDINGAPITE NDIYOTI CHAKWERA NDI DEAL!!!!!!!!!!

 9. 100%am not happy with idiot chakwera upon telling doners not to resume aid to mW what kind of selfishiness x that u chakwera r crazy or r u demon possesed zangovuta kuti still am far from BT udakakhala nane pafupi mbama ndidakakuswadi try to think b4 u come up with ur foolish idea

 10. hahahahahaha a malawi ndikumbuseni chonde unduna omwe bwampini aka ibu anawukwanisa nthawi imene bingu ali moyo?? ndiye mukuyembekezera kuti dziko ali kwanisa kuliyendesa?? thats a joke

 11. The tactic our president has used is if you talk too much you are shown the ground to pray and show your tactic don’t just be good on paper if only your house is fallen you think you can solve another’s man’s house kkkkkk because the word resignation is free to mention then you can be using anyhow kkkkkk what does resign after all mean a president was chosen by me after people’s views were reject through ballot box you think in parliament you can call someone to live office my my don’t waist tym with wishes that can cause you BP better think of other thing for making money

 12. Tell me who is the best President who ruled Malawi best? No president has ruled Malawi without people worrying,crying,ETC. Its not presidents who change situations in a country,its the people,U and Me .People choose leaders not them choosing the People.We can either build or destroy a country.We r the power. Its us that r moving this country,not presidents.Look,who r working day and night in factories,Banks, Bussiness, etc .

 13. Donors cut K2,9 Billion funding for Fisp; Who would rule such a country which depends on agriculture but no donors? Even if Chakwera was to become the President today, nothing will change becoz things had already been messed up by PP & DPP; The only solution is to kneel down to the donor or completely close down the country as a failed state: Or we sell the country to Mozambique & South Africa where the economy of these countries is doing fine despite some hicups;

 14. Koma Guyz pena osamalankhula coz muli ndipakamwa, mukamati Mcp izitha kusianisa Boma ndichipani mukutanthauza chani? Ine mutandiankha ndithu ndimve nawo, chomwe chimavuta kwathu kuno timatenga ndale ngati chidani pamene maiko anzathu aboma otsutsa onse amagwilila ntchito limodzi, kukhala mtsogoleli sizikutanthauza kuti umaziwa zonse & kukhala otsutsa sikutinso ndiwe olephela apo mukuenelanso kuziwanso, peter pomuuza chakwela kuti athandizane kukonza mavuto omwe ali mdziko muno sadalakwise coz nayenso akuona mmene dziko likuendela, mwina pamene tinganene kuti panalakwika ndipakuti apite ku Dpp apo mwina malankhulidwe anavutilapo, amati ich i nchani nkulinga muli awiri, nde onse akakhala ku Boma amene angauze nzake kuti pakulakwika ndani mwachitsanzo Udf isanapite ku Dpp inali chipani chimodzi chomwe chimalankhulila anthu akumamizi pazosowa zawo pano mutha kukhala mboni yanga kuti palibe zomwe ikukamba nkhani yake ose atsamila kuboma nde chonde amalawi tatieni tisanakambe tizionesesa kaye ndipo kulankhula mau onyozana sibwino coz tikanyoza palibe chomwe tingapindule ine ndimakhulupilila kuti dzikoli ndilimozi tingasiyane madela ochokela tonse ndamalawi ndipo kathuka kadziko ndikakang’ono guyz. Nkhani yapa ndiakuti Achakwela ndi Apeter angothandithandizana kukonza mavuto omwe ali mdziko muno coz onse ndamalawi ndipo onsewo akudya misonkho yathu. Pepani ndukhulupilila kuti sindinyoze munthu ndipo kunyozako kumandivuta sinditha. Tieni tigwilane manja pokweza malawi wathu posatengela Mbali.

  1. Zazeru bambo zimenezo.dziko lathu laling’ono komaso losauka koma tikupitiza kuononga chifukwa chomakokana mmalo momakoza.chipani chinabwera pambuyo pa dziko.ngati titagwiriza tithaso kukhala ndichipani chimodzi ndikumatukula dziko osati chipanicho.mavuto akabwera amakhuza dziko osati chipani.ndibwinodi kuganiza polankhula.

 15. Ndiunduna uti akuluwa anaukwanitsa?Ndiye akakwanitse upresident.kkkkk amalawi ndiathobwa mmaso.I’m not surprised,he is a failure from de beginning.

 16. Padzko lapansi palibe pulezident angatukule dzko lache payekha koma tonse ngati dziko timapeza njila zotukula dzko lathu ndiye ngti watelo ndiganizo labwino inu ndi ine kuphatikza atsogoleli athu ngati chakwela , kamlepo pezani njila ndiziti tingachit kuti malawi akule pachuma. Musatye nthawi kukambilana za ana a Msiska pali zambil za national importance. Dzko ngati situkuka malawi ngati dziko talephela.Muthalika ma mp athu inu ndi ine talephela. Chitukuko si munthu modzi

 17. Amalawi! Our population is growing dangerously unless we introduce population policy we can develop otherwise palibe ndikuona kutsogoloku ntchito ikhaleyobeleka kenako mkumapempha mathewera kuma donors?akakana pulezident walephera?Umfitituumenewu tiyenitisinthe amalawi.

 18. Among the blind, a one eyed jack is a king. APM went to polls with blind bats and we chose him because he is cream. On national level, govt is doing its best. The rest is for you, as an individual to do your part to eradicate poverty and hunger in your house holds. APM is bringing a new dawn to our country. Bravo Mr president! 2019, Ntcheu is ready to give you all the votes. To hell with Chakwera, a blind bat

 19. I dnt tink pali nzeru kumaanena a Malawi24 kti alibe nzeru o ndimbuzi kma ukumawerenga nkhani zao tym 2 tym.Zimenezo nde zamanyi mmutu

 20. u can’t go behind and conspire with donors to not resume aid then u come in front and tell us that president mutharika has failed, that’s the spirit of witchcraft, uthakati weniweni and yet u claim to be man of God, shame on u, imfa yako idzakhala yowawa.

 21. Mukhoza kuyakhula mene mungayakhulire koma choti mudziwe umfumu sasakha pa chichimwene coz ma result ake amakhala omwewa,ine pano ndkudikira mwana wa Bingu kuti alamuleso mwina angadzatichotse misozi ngati mene anatichotsera bambo ake kkkkkkkkkkk olo munene kuti profesor safuxa maganizo kwamu2 oti sipulofesa bwanj akumafusa Bakili??

 22. Mukhoza kuyakhula mene mungayakhulire koma choti mudziwe umfumu sasakha pa chichimwene coz ma result ake amakhala omwewa,ine pano ndkudikira mwana wa Bingu kuti alamuleso mwina angadzatichotse misozi ngati mene anatichotsera bambo ake kkkkkkkkkkk olo munene kuti profesor safuxa maganizo kwamu2 oti sipulofesa bwanj akumafusa Bakili??

 23. If thats the case then let them handle the develpment together what we need is malawi to another level zinazi tiyeni tokha amalawi tiziganiza osamangonyozana think of the crissis at present when some ask for a hand sikuti ndiopusa ayi

 24. the president is just being patriotic,malawi 24 can’t you see that blame game is not helping at all,open your eyes & get civilised. civilised

 25. Pepani Abale Ndi Alongo! Kodi Mwayiwala Zizindikiro Za Masiku Otsiriza? Werengani (Mateyu24v4-8) Kaya Mufune Musafune Izi Zikuyenera Kukwaniritsidwa.Palibe Chifukwa Chonyozana Apa . Chomwe Mungachite Ndikulandila Yesu Kristu Basi Chuma Mukakhala Nacho Kumwamba! Ndikumva Chisoni Mene Mukunyozela Pulezidenti Koma Ngati Simusitha Muzachita Manyazi! YESU AKUFUNA MUTULUKE MDZIKO LAPANSILI! AMEN! MULUNGU ATATE AKUKHUZENI!

 26. THis is y we re poor Here in MALAWI, we criticise much instead of working hard 24hrs. bas bizy pointing finger@our Leaders;Go 2china you slugged malawians yu r so gush!!

 27. Who is Prophet Muhammad, may peace and blessings be upon him?
  من هو محمّد، صل الله عليه وسلّم؟

  He is the one who defended the rights of all humanity 1400 years ago.
  هو الذي دافع عن حقوق كل البشر منذ 1400 عام.

  He defended men’s, women’s and children rights
  حفظ حقوق الرجال وحقوق النساء وحقوق الصغار

  He commanded and fostered the love between relatives and neighbors
  أمر بالحب والود بين الأقارب والجيران

  He established a coexistence relationship between Muslims and Non-Muslims
  وأسس علاقة تعايش بين المسلمين وغير المسلمين

  He organized the relationship between the members of the family putting duties on sons and daughters towards the parents
  ونظم العلاقات الأسرية التي تضمن للأب وللأم حقوق كبيرة وعظيمة على أبنائهم

  He fought injustice, called for justice, love, unity and cooperation for the good.
  منع الظلم ودعا للعدل و المحبة والتكاتف والتعاون للخير

  He called for helping the needy, visiting the patients, love and exchanging advises between people.
  دعا لمساعدة المحتاج وزيارة المريض والمحبة والتناصح بين الناس

  He prohibited (by orders from God) bad manners such as stealing, lying, torturing and murdering.
  منع على المسلمين المعاملات السيئة مثل السرقة والغش والقتل والظلم

  He is the one who changed our lives and manners to be better.
  إنه من غير حياتنا وطباعنا السيئة إلى حسنة

  A Muslim doesn’t steal
  المسلم .. لا يسرق

  A Muslim doesn’t lie
  المسلم لا يكذب

  A Muslim doesn’t drink alcohol.
  المسلم لا يشرب الخمر

  A Muslim doesn’t commit adultery
  المسلم لا يزنى

  A Muslim doesn’t cheat
  المسلم لا يغش

  A Muslim doesn’t kill innocent people
  المسلم لا يقتل الأبرياء

  A Muslim doesn’t harm his neighbors
  المسلم لا يؤذي جارة

  A Muslim obeys his parents and helps them
  المسلم يبر بوالديه و يخدمهما

  A Muslim is kind to young and elderly people, to women and to weak people.
  المسلم يعطف على الصغار وعلى النساء وعلى الضعفاء وكبار السن

  A Muslim doesn’t torture humans or even animals, and does not harm trees
  المسلم لا يعذب البشر ولا الحيوانات ولا يؤذي الأشجار

  A Muslim loves his wife and takes care of his children and show mercy towards them until the last day of his life.
  المسلم يرحم ويحب زوجته ويهتم و يعطف عل أبناءه حتى آخر يوم من عمره

  A Muslim’s relationship towards his children never stops even when they become adults
  المسلم لا تنتهي علاقته بأولاده بعد سن الرشد أبدا

  He is Muhammad (PBUH)
  إنه محمد رسول الله صل الله عليه وسلم

  Did you know why all Muslims love Muhammad (PBUH)?
  هل عرفتم لماذا يحب كل المسلمون محمد صل الله عليه وسلم؟

  Did you know what does Muhammad mean for Muslims?
  هل عرفتم ماذا يعنى محمد صل الله عليه وسلم للمسلمين؟

  Every Muslim loves Muhammad (peace be upon him) more than himself and more than everything in his life.
  كل مسلم يحب محمد صل الله عليه وسلم أكثر من كل شئ

  Before judging a Muslim be fair and:
  قبل أن تحكم علي أي مسلم كن محايد:

  1-Listen to this person, and watch his doings.
  1- أسمع منه هو شخصياً ، أستمع الي أفكاره ومعتقداته ولاحظ أفعله.

  2-Compare his ideas and teachings with what is Islam and Prophet Mohammad PBUH ordered.
  2-قم بمقارنة أفكاره ومعتقداته بما دعا له الإسلام.

  3-If you think that his thoughts are typical to that of Islam and Prophet Mohammad PBUH, and then compare them with his doings; is he applying these teachings?
  3- إذا تطابقت أفكاره ومعتقداته مع ما دعا له الإسلام فأنظر إلي أفعاله، هل هي متطابقة مع أفكاره ومعتقداته؟

  4-If he is applying these teachings and sayings, so for sure represents Islam, if not then he calls himself a Muslim but doesn’t represent Islam.
  4- إذا كانت أفعاله تطابق أفكاره ومعتقداته فهو يمثل الإسلام، إذا كانت تتناقض فهو يدعي أنه مسلم ولكن لا يمثل الإسلام

  Hint: Prophet Mohammad is the best Muslim, no Muslim can be as perfect as he was, Muslims try their best to be the typical Muslim like Prophet Mohammad PBUH but sometimes they disobey God and Prophet Mohammad PBUH as they are normal humans who are subject to do wrong but the repent and get back to the right path.

  ملحوظة: محمّد صل الله عليه وسلم هو أفضل مسلم، لا يمكن لأي مسلم أن يكون في كماله ولكن المسلمون يبذلون قصاري جهدهم ليكونوا المسلم المثالي الذي رأوه في محمد صل الله عليه وسلم، أحياناً يعصون الله ورسول الله محمد لأنهم بشر معرضون للخطأ ولكنهم يتوبون ويعودون للطريق الصحيح.

  “Whosoever kills an innocent person, it shall be as if he has killed all of humanity, and whosoever saves the life of one, it shall be as if he had saved the life of all humanity”. QURAN 5:32
  “مَنْ قَتَلَ نَفْسًا بِغَيْرِ نَفْسٍ أَوْ فَسَادٍ فِي الأَرْضِ فَكَأَنَّمَا قَتَلَ النَّاسَ جَمِيْعًا وَمَنْ أَحْيَاهَا فَكَأَنَّمَا أَحْيَا النَّاسَ جَمِيْعًا ” سورة المائدة – الآية ٣٢

  M#MuslimsAreNotTerrorist
  احبك ربى
  i love allah

 28. ,A.C.P if u want 2 make Alliance go 2 join with another party not pp, paja musayiwale kuti malawi ili pa presure ya cashgate scandle bcoz of pp, ndiye ngati ndalamazo munaba nao gwirizanani tikufufuzirani limodzi, ngati mwini wake joy wachithawa, ndikukumbukira M.C.P inazapanga mgwirizano ndi UDF DPP inawakutumula ndiye lero akufuna agwirizane ndi chipani cha cashgate asiyeni 2018 ali Mmazi

  1. kkkk koma ndiye wakwiya ukuoneka kuti ndiwe supoter wamkulu otsutsa, kaya muzalalira liti? madona anapita aja akubweleranso nanga si mayi uja tinampasa Red card, pano tili muofesi tikumwa wamkaka kkkk wina azinjata pakhosi, osusa akuti sizikuyenda kwa inu koma ife ndiye zikuyenda heavy

 29. IS Their anything too hard for GOD? he who chooses YOU can not fail, he is with you,you are Doing great! by healing this Nation MALAWI from POVERTY! NO! 1 shuld criticise HIM! IF YOU Continue GOD will bring a terrible Sickness on YU! ! you foolish citizens! !

 30. sava zazake adakha ntudzi pa bwalo a president akudziwa kuti zofunika kuthandizana izi ,tikamayankhula tisamaikile malire munthu chifukwa sitikudziwa chomwe adakoza mulungu .Sindikuona chomulalatila Chakwela .Nthawi zina munthu ukamazuzika sumadziwa kuti ukuzuzika umazazindikila ukapenya . Ena mpaka pano zoti muno muli mavuto sakudziwa chifukwa chozolowela moto .

 31. kodi pakati pa wolemba nkhani ndi inu mukutukwana wopanda zeru ndindani? Amalawi phunzira ukhala anthu zodzisungira ulemu. Ena apa ana amati ndinu makolo awo koma pa FB mukuchitika uchitsiru potulutsa zichewa zoipa. Dziko langa lokondedwa ulemu wako wavulira ndani?

 32. The best way is 2 kuvomela kt zandikanika matengedwe a boma anu opanda chilungamo ngat simuvoleza bwana zinthu zivuta mulungu wakwiya nanu vomelezani bas musanapeze milandu yambir

 33. Koma Chakwera uchenjere naye Ibuyo chifukwa mukhoza kuzamangidwa nonse kutsogolo kuno. Mzako Ibu wakalamba kale kwake kwatha koma iwe Chakwera ukanali mwana ndiye usamale.

 34. If i was in syria i would have abducted the the repoters reratives until he cames and beheaded hiyes its true this media is full of madeya go ahead tell lies don’t fight with mg you half backed idiot ,are you going to win ?

 35. Aliense Ali Ololedwa Kupeleka Maganizo Ake Mmene Dzikoli Liyenela Kuyendela Chomcho Tonse Pamodzi Tkhoza Kutukula Dziko Lathu Koma Enanu Mul Ndi Vuto Apm Monga Mtsogoleli Ckut Walephela Ayi Koma Tithandizane Kutukula Malawi

 36. Mr President is running out of words from his mouth.A true $ transparecy leader can not give such rediculous respond to the leader of opposition in the house.What a joke to the nation.Ha ha ha ha ha ha.Kraal.

 37. hahaha Dpp simayenda ndi mwana imayenda yokha muzisankho zonse fufuzani zambiri yake simuzaipeza ndi mbiri yangwirizano ndi chipani china ngati mmene imachitira mcp

 38. Iwe patrick ndiwe chitsiru ngati muthalika wakoyo mtundu wa amalawi upwetekeke chifukwa cha upolofesa wakewo,,,we are really tired of selfish leadership.

 39. where iz kucius mbanda sikono pakamwa kuyambira 2012 ambwiyewa mmmm! ndi ziii koma thawi imene ija kunali, achoke!!achoke!!

 40. Whether u lyk it or not dpp iz rulling u and peter z ur przdnt… So am very sory mulamulidwa ndi munthu amene simukumufuna till 2019

 41. Bullets=TNM , Noma= Carsberg , Civo=Standard bank. Chimozi chimozi basi palibe vuto. Mukukula ku kamwa ngati zikho zonse mwatenga nokha bwanji?

 42. President ndi amene akupempha Chakwera to join him dealing with malawia crisis osati inu akampopa ngolo omwe simudziwa chilichose kwanu mkutukwana Chakwera pa chabwino or choipa, muyende mmidzimu muone anthu mmene akuvutikila and those Malawians are the one who voted whilst enanu mumakhala mtown and coming to elections you dont vote what you kno is noise on comments. This is not campaign period this is time to develope our country….

 43. Namondwe akavuta pa nyanja captain salephela ukuwawuza anthu amene ali mu ship kuti apa zinthu zavuta tiyeni tipange chimvano cha mavu musandisiye ndekha(UNITY)

 44. Lembani zoti zikuthandizen,peter alibe nthawi yomakaitanira chipan ngat min bus yachirimba,chomwe mungaziwe ndichoti munthu wolephela sungamupemphe kut akuthandize home work.chakwera ndimunthu watsatchuka pa ndale,sanakhalepo even mp,sono ife timukhulupirila bwanji? Munthu saziwa kanthu uyu yona,Dpp simatenga ma reject sory.

 45. Bwampini nyaphaphi must resign. Otherwise atisaukitsa.
  Empty headed shupit APM

 46. Bwampini wanuo atisaukitsa anyaphaphi inu!!!!!!!!!!
  Shupit -empty headed APM.

  1. Iwe ndiye ndimbatata zikuwavuta makolo ako kukusamalani kuti mukule ndinkhalidwe labwino lero ukayime apa kuti president ndi mbutuma. Mbutuma ingakhale prof. wa law ndiwe zoba. 14tin

  2. Mbuzi ndiwe #Nazo. Umafuna uzidyetsedwa ndi president? Unya uona.Ingolimbikila ntchito. Mzako ukulimbana nayeyo zake zinayenda kale ndipo simbuli ngati iwe.

  3. ataye kulimbana ndi atumbuka mkutaya nthawi yako uzingoona mainawo mkandawire,msisya.mkazi ndi anthu opanda tsogolo koma ulesi anadzolowera ma handouts kugwira ntchito safuna koma kutembenuza ma9 kukhala ma 6 mmaoffice mu

  4. Thom whch xul did you go to? Dont you know that am feeding your mbuzi president, mbutuma ya ma president through my tax? What kind of people are you guyz? Tatsegukani maso anthu opusa inu?

  5. Pasadi musawanyoze atumbuka man ndi anzathu amenewo wamva. Behave as gents please. Umbuli wanuwo keep it in your house and let your wife and kids enjoy it. Wayenela kufanana ndi president wakoyi anthu opusa kwambiri!

 47. WHY MUTHALIKA WANTS EVERY OPPOSITION MEMBER TO JOIN HIS PARTY? IF HE KNOWS THAT HE CAN NOT ABLE TO RULE THE COUNTRY .INDEED IT IS BETTER TO GIVE OTHER PEOPLE’s CHACE TO RULE THE COUNTRY.
  FURTHER MORE,IF HE WANTS CHAKWELA TO JOIN HIS PARTY ,
  MEANING TO SAY NO NEED TO HAVE PARLIAMENT IN MW.NEITHER THE LESS ,LEADERSHIP IS PUBLIC TRANSACTION WITH HISTORY.

  W

 48. Guyz Vuto2 Ndi Amalawi24wa Titha Kumangotukwana Kaya Amacra Akuwasiya Pat Osawalanda Chiphaso Kaya? Ife Mabodza Ai Even Zbs Idaleka Mabodza Pano

 49. Amalawi24 Musakhale Ngat News Sitiwelenga Apatu Ndipomwe Mutharika Amafika Kudzasekulila August House Osat Amapempha Chakwera Ai! Chakwera Amalandila Apm Ngat Leader Of Oposition Osat Bodza Mukunama Pali Mwasowa Cholemba Et ?Mutaona Ma Coment Omwe Aperekedwa Anthu Akungokutukwanani Coz Of Lack Of Profesionalism? Musamapange Kut Amalaw Akumven Ai Technology2 Idapita Patali Mukamanena Amakhala Kut Anthu Amva Kale

 50. Kkkk banthu wotukwana imwe ma frnd tisamakangane apa kuti zonse zithe zotukwanizana bambo pitala atule pansi u president coz palibe chimene akupanga amalawi nkhayowoyanga ine kt uyu simunthu ndi mbuzi ya alomwe muzaona palast bola Jb

  1. pipo from south will never have peace..last year floods dis year floods…u r cursed.mbuli ndichonch,chanzelu kwaiwo nkutukwana..anthu ophwanya ndichonch kkkk

  2. Iwe unamva zoti ati afa ndi njala mmexa ndinuyo achewa kuzolowela kulima utenant ndikugwili kmanso kuba ife tiliphee muvutinge ndinu kubelekana ngati mbewa ma rubish wat

  3. Kkkk bwampini mulinaye pafupi kma mavuto alithoo! Chifukwa chake mazi angosefukila muwona ife tili phee kumpoto kuno njala eee tinaiwala zoti kulinjala musuzgikenge nkhule zinu

  4. ndinkona atumbuka mulungu anakupangani okuda kwambiri anadziwa kuti mwada ndi ubongo omwe inu Kkkkkkkkkkkkkk Kkkkkkkkkkkkkk Kkkkkkkkkkkkkk

  5. Chakwera is a malawian and mavuto wa ndi a tonse..ndi udindo wake naye kuthandiza boma osat coz he is leader of opzsion then he should stand against evr dcsion of the curnt regime…and u malawi 24 plz learn to write thngs of uniting malawians osat anthu azitukwanizana apa coz of ur NOSENSE posts…we are all malawians lets stand as 1

  6. Chakwera is a malawian and mavuto wa ndi a tonse..ndi udindo wake naye kuthandiza boma osat coz he is leader of opzsion then he should stand against evr dcsion of the curnt regime…and u malawi 24 plz learn to write thngs of uniting malawians osat anthu azitukwanizana apa coz of ur NOSENSE posts…we are all malawians lets stand as 1

 51. Who would unite with a theft? Munalowa cho vencha nde pamene zaku vutani you then want unity. If you feel you cant do the job resign. Period

 52. the problem is every politician dreams abt ruling this country rather than developing this country…no wonder pano chakwera all he is looking foward to is next elections and Mutharika too…why Malawi..!

 53. ngt utolankhani wake ukhale umenewu muzalandira pension pa fb pompa basi, tsogolo mulibe ndithu,. msonkhano wake uti omwe APM ananena zimezi??? mkalasi munkakhoza ndithu?? olo munali a “may try”.

 54. ngt utolankhani wake ukhale umenewu muzalandira pension pa fb pompa basi, tsogolo mulibe ndithu,. msonkhano wake uti omwe APM ananena zimezi??? mkalasi munkakhoza ndithu?? olo munali a “may try”.

 55. Prof..inviting mbusa?…u must be joking …..even in exchange for death sentence idont think Prof.mutharika can opt for this short sighted chakwera ….

 56. l don’t think the president ment what mlw24 is saying,othherwise the president wud v kod chakwera4a miting not on apolitical rally

 57. Sakutanthauza kuti dziko lamukanika ayi 2 develop our country means tonse ndife amalawi prezdent ndi mmodzi wa dziko si nthawi yokokana ino ayi, kodi wa opposition anthu sanamuvotere? Iyeyo ali ndi udindo othandiza anthu omwe anamuvotera, paja pali mwambi omwe amati: zize pano ndizatonse, wa opposition akuyeneranso kukhala stearing ya boma, amalawi tikuyenera kusiyanisa pakati pa boma ndi chipani, boma limayimira anthu onse pamene chipani chimakhala ndi anthu ake, kaya muzadziwa liti a mcp kusiyana kwa boma ndi chipani?

 58. Kkkkk being a profesor doesnt min ur so briliant..chakwerao sikut cant decide 4 beta amalawi stmafuna kupanga unite bsiz kukhala pa position yapa high mmadznva hevy dats y stmatukuka…lets unite 4 beta malawi

 59. What we can do to make malawi abetter place. (1) stop wasting fingers and come with better solutions. Forget all the debate in the national assembly coz the past 50 years Malawians did not benefit from their dabates and we are experiencing poor deliverance from our Mps. Malawians are tired seeing them sleeping in the house no visionfor better malawi. Malawi ans don’t want speaches for 2 hours but brings nothing. We need aperson who can change and develop the country. Media’s try to bring articles which people will contribute their views for the better Malawi

 60. DPP inaoloka yokha ndiye ingafune a Chakwera? Kodi a Chakwera anakhalapo president wadziko kuti APM akawafunse nzeru? Malawi24 mwazungulira mutu

  1. Odala vetsetsani nkhaniyo kenako ikani coment osakhala mgulu losavetsa nkhani then kuika coment yosemphana ndi nkhani ayi…i love peter and hate no one coz this world is round we dont kno wat tomoror will bring us….and mudziweso kuti andale ali ngati abusiness satayana

  2. To be a leader its no what u have in ur account or knowladge but humanity(umunthu)!!! That why God choose David to be a leader.So please take a note!!!!!

  3. Oscar! wat u hv said its true and i agree with u,bt knw that its easy to turn diginity person to join fools than turning fool to personality,this theory is true in all senses,Now #ODALA is a master deceiver.he does’nt knw that, for a man/woman to led country it needs #devine-intervetion,this is wat #CHAKWERA is all about.

 61. I can’t see that happening in malawi. Chakwera has no brain to give advise to the Professor. His brains may seemingly be validated towards the likes of other opposition parties not the ruling. There is a door opened already for the sitting president to deal with the current situations once for all. I trust that will be the end after a long toiling, talking, bad mouthing against the president. No more loosing hope for him at all!

 62. i don’t sense any defeat vibe from this news. hbu???……i hadn’t realised those two were competing… elections are in 2019 for God’s sake!!!!

 63. That is why i like this page full of jokes. thumb up admin with your practice of writing, you will be good reporter.

 64. Peter Has Invited Anybody Who Think Has A Solution To Contribute Not This Man.Has He Changed Name To Anybody.Foolish Gwape Who Cannot Support A …….Fools.By The Way Does He Has Any Apart From Opposing???

 65. kodi mumangoti chakwera this chakwera that, ,anapangapo chani chomwe chimakupasani chikhulupiliro kut iyeyo ndi 100% atati watenga boma? iyeyo ndindani? Yesu christu? inu musamandinyase mwamva iyaaa ndakutoperani tsopano shupitii!

 66. Kodi atsogoleri osaphunzira bwino anakwanitsa bwanji kuyendetsa dziko lathu mosavuta mzaka za kumbuyoku?koma panopa kuli proffesor ophunzira bwino,nanga zikuvuta pati…

  1. Utsogoleri ndi mpaso yochokela kwa mulungu. Uphuzila akusauka osaphuzila mkumalemela. Nzeru ndi chuma osamaganiza mofoira

  2. kkk usandiseketse dyomba unamva kut kuti osaphunzira anayendetsapo malawi bwino kkkkkk shame…lero tili mmavuto chifukwa cha osaphunzirawo mcxxxxx

  1. Koditu sikuti chifukwa choti akuluwa anaphunzila ndiye kuti angakhale pabwalo nkuweluza milandu ayi,komanso chifukwa chaSchool ndiye nkukhala ndi nzelu zoyendetsela dziko ayi.chimene tingadziwe akuluwa adatchona ndiye mavuto amudzimu sakuwadziwa ndiye tiyeni aMalawi tilimbe mtima

  2. a good leader amapanga consult and delegate…atleast simunthu wa nzeru zuyenkha he knows dziko ndilatonse…mukapitiliza kufina kumuonetsa president kuti ndi osadziwa mudzapeza kuti each president will try solve issues on his own and fail-one man alone cany build malawi-pena zimangofuna kumvetsetsa!its not him who has failed-but ordinary malawians who goin to suffer more….tiyeni tiikonde dziko

  3. Amalawi chomwe ife timadziwa ndi kutukwana instead of getting lead of de problem we are facing.malawi will develop coz of these.hahahahahahaha amalawi when will u crever?very shame indeed.

  4. MUFUNE MUSAFUNE NA INE OLO MUTANDINAMIZA MOTANI KOMA NGATI NDILI MMALAWI MOMMUNO NDIZAKHALA NDIKUZIWA CHOONA SINDIZADIKIRA KT MUCITE KUNDIUZA, AND VOTE YANGA NDI YA YEMWE MUKUTI MUTHALIKAYI, ZIKOMO NDINE WANU MWANA WA A MELEKA.

 67. After finishing typing this comment I’m unliking this page. It’s just some piece of shit. Tizikhalira kuwerenga za zii. Why don’t you come up with sensible news other than demonstrating your political affiliations!

  1. Palibe chomwe ungave coz sudziwa chilichose umadziwa kuseka basi….akananena kuti Chakwera amafusa nzeru kwa Pitala ndiye ukanasangalara….asiye atolankhani ndi ufulu wawo olemba iwe just be cool 2019 udzamuvotere Pitala basi

  2. Palibe chomwe ungave coz sudziwa chilichose umadziwa kuseka basi….akananena kuti Chakwera amafusa nzeru kwa Pitala ndiye ukanasangalara….asiye atolankhani ndi ufulu wawo olemba iwe just be cool 2019 udzamuvotere Pitala basi

 68. This is the Malawi i would prefer to live in, let us all hold hands to build our nation. If we choose to be divided then we shall never be united, let us stop pointing fingers at one another.

  1. hahaha wat does chakwera know anyway…….u think he can run this country alone? no man is an island …..n APM has shown great maturity in asking for all to work together… shows he’s not q self centred leader like,probably chakwera

  2. where is that Malawi that respect elders? Where is that God fearing country that always preach about harmony, peace & stability,? bwampini? You must be ashamed for yourself,respect is needed, though your given tht opportunity even to be a councillor, you can’t do anything all you knw is insulting president. To hell with negative thoughts & learn to respect & if there’s a prblm raise a point that can help.

  3. Patrick#i knw you are 4 dpp you cnt feel pain when our fellow malawians die in the hospitals everyday not that we dont have doctors or nurses but there is no medicine. Am nt 4 mcp but its wise to praise someone who can rescue malawians from hunger and finacial criss.i knw it wil pain you coz you love your so called #bwampini why called bwampin he is not considering that some one who is vry poor living in the village cant afford to go for a private hospital.i wish if i could’ve syd alot kma wanzeru ava apa.

  4. I dnt have any political party to support, I do support any president who is currently on that position bcoz he is there as a the 1st citizen of the country, I’m not even there (Malawi) but I do respect him as a president, there’s no one who is 100% fine, Obama is facing huge prblm, here Zuma, is criticised by many, but still they respecting him as their president, he dnt wnt people to suffer while he is ruling, but it will take time to build Malawi, as we all knw that, is not him, who made things to be in tht situation,

  5. Patrick ,correct you are not in malawi dats y u dnt even knw wat huge problems pipo are facing here.,ask ur relatives if they are happy with his ruling had it been he has @list do some priolities lyk food and medicine, maybe you my friend evryone in ur family is rich that he/she wil nt die coz of no medicine in government hospitals you wl be jxt flying wa ku U.k.

  1. Iwe peter kupusa kwake kwantunduwanji kokuona ndi anaonwe iwe chisilu wamva udzikula, ukufuna chakwela azikuthandiza kupanga zopusazo alomwe tawona atsogoleri mubukhu lamboni osati mbuzi zakubanja kwa amuthalika,zopusa.

Comments are closed.