Exclusive: MCP fires back at Mutharika


Jessie Kabwila

…who will apologize to who?

Opposition Malawi Congress Party (MCP) has categorically stated it will not apologize to Malawi President Peter Mutharika as he requested on Thursday during a press briefing held at a Kamuzu Palace in Lilongwe for being criticized on his trip to the United Nations General Assembly (UNGA) in New York .

Peter Mutharika
Mutharika: Demanded an apology.

Addressing the media, Mutharika said the criticism by MCP and some media houses hurt him.

He cited the criticism were aimed at inciting people against him and the Democratic Progressive party (DPP) and demanded an apology.

But in an exclusive interview with Malawi24, MCP Publicity Secretary Jessie Kabwila fired back at Mutharika citing that the party is not going to apologize for the criticism it made.

She added taking over 100 people to New York is not just only unquestionable but also undemocratic.

Kabwila said the criticisms were aimed at providing checks and balance at a poor Malawians are crying out.

Explained Kabwila, “This is very irresponsible, the list they could have done was to apologize to Malawians and say it could not pen again but not actually to come and spit fire at hungry people. MCP wants to make it categorically clear that it will not apologize for standing with Malawians and criticizing what is wrong. It shows he is insensitive president. How can he come back with nerves and guts to people who are dying with hunger and tell them he is rich with billions in his accounts. In fact Malawians are congratulating MCP for standing out for them. This is very irresponsible; the list they could have done was to apologize to Malawians.”

MCP Spokesperson further sided with Civil Society Organization (CSO’s) who have been calling with Mutharika step down.

She reminded the Malawi leader that he was put into power by Malawians who also have the power to bring him down. Kabwila expressed shock that the DPP government continues to parade executive arrogance at a time when Malawians are leaving in pains.

“He must always remember that he is on the sit on trust of Malawians and if Malawians have lost that trust they will remind him. He seems to have forgotten what his brother went through. It was the same DPP during Bingu wa Mutharika that was shouting at the Media and messed up the economy. He should remember that Malawians reduced the twenty points CSOs wrote his brother into one.”

Jessie Kabwila
Kabwila: MCP will not apologize.

“Malawians are not looking for someone who is not frugal when he talks but frugal at development. How can he compare himself with other African countries when Malawi is ranked as the poorest country in the world?” questioned Kabwila.

Speaking with this publication Lilongwe based Political Analyst Loudon Malingamoyo Phiri concurred with Kabwila.

Phiri said Mutharika’s remark is a clear indication that what he did is wrong.

According to Phiri, criticizing the opposition and the media is a sign of fear and intimidation which aims at paving out some of the issues.

“It’s wrong to criticize the opposition and media because it shows that what he did is wrong. It’s something that even someone barely from the village would actually not agree with looking the situation we are passing through in this country. Criticizing the opposition and the media is a sign of fear or intimidation. He is trying pave out some of the issues. It’s wrong to criticize people when they are being constructive. It’s not just criticizing the president but making sure he is leaving up to date. Media are there to inform the public and they are supposed to do that to the president,” he uttered.

Meanwhile the political analyst has justified the by opposition MCP and the media saying that were constructive and is allowed in a democratic country.

He added, MCP has demonstrated its democratic right and is not supposed to apologize.

367 thoughts on “Exclusive: MCP fires back at Mutharika

 1. KAMPHODZA NGOZO was among those who went to NEW YORK on UNGA ticket. This is very true.

 2. Iwe jezelo nthawi ya kamuzu ,@bakili amayi ndi bingu sumadziwa kuti amalawi amalipira misonkho? Muuzane ndi chakwera wakoyo kuti ndinu oskonda dziko lanu y alwasy siting at the ag of the cup only to tell pple lies u r no gud for malawi , insulting the leader is insiting God who put him on the sit. Be careful wth ur tete-a-tetes within ur stomaches

 3. When comment Malawian you should see the angle which a particular person has taken ndi chifukwa chake zimati vuta Malawi muno chifukwa pokasakha atsogoleri we go with proximity not ability of a candidate. There many things the government is not doing them in a rightfully manner and there the opposition side should protect the citizens .may b it can sound ok in your mind today but wait you will see with your naked eyes uphawi wadzaoneni mu dziko muno .whenever the speaks first let’s analysis using all five lens we have as humans then make a meaningful judgement not just a hatred in our mind be civilised Malawian by express our freedom oyakhula by comment momanga zithu osati chifukwa akudzudzulidwawo ndi akwathu naa

 4. kodi chifukwa chani azimai mukumavutitsa kumalawi.mcp sidzalowaso mboma ndinu anthu asanje.mukufuna tiziona za ku nigeria ife toto.mademoalstration kapangani nokha.kdi kabwila ukulandila ndalam zingati.bwanji sumanena kuti umalandila zochuluka.pamene anthu ena akuvutika.uwauze achakwela ayamba ntchito yasatana yosupa gule wakulu kkkkkk.ngati mwasowa zochita mungotsegula mafamu muzilima.kdi mukufuna kutenga Bingu ngati mulungu ndimunthu ngati inu ali ndizofooka zake.kungokhala nyau zochita zanu.mcp sidzabwelaso mboma mukuonetselathu kuti mudzayambaso kusokhetsa anthu khuku.

 5. kodi chifukwa chani azimai mukumavutitsa kumalawi.mcp sidzalowaso mboma ndinu anthu asanje.mukufuna tiziona za ku nigeria ife toto.mademoalstration kapangani nokha.kdi kabwila ukulandila ndalam zingati.bwanji sumanena kuti umalandila zochuluka.pamene anthu ena akuvutika.uwauze achakwela ayamba ntchito yasatana yosupa gule wakulu kkkkkk.ngati mwasowa zochita mungotsegula mafamu muzilima.kdi mukufuna kutenga Bingu ngati mulungu ndimunthu ngati inu ali ndizofooka zake.kungokhala nyau zochita zanu.mcp sidzabwelaso mboma mukuonetselathu kuti mudzayambaso kusokhetsa anthu khuku.

 6. Mayiwa sindigwilizana nawo pazina,koma izi zokha zanyanya mmalo moti ntundu wa a malawi upepesedwe pazimene mwapanga poononga ndalama za nthu.Ndiye mukutembenuza zinthu kuti mupepesedwe,pazifukwa ziti.Penapake president anthu muziona kumene tikuchoka ndikumene tikupita.Anakakhala kamuzu sakanapita kumeneko nkusiya khani yanjala mbuyo ayi.Mwaononga ndalama pofuna kusangalasa anasi ndi alongo.God is waltching you and me,We can not hide upon the eyes of God.

 7. My prsidnt a p m osafuna achoke mmalawi muno inu a mcp mukuiwala kt nanu kulowa m boma zodiak izakutembenukilani exmple bingu vs jb it oz jb side bingu gone jb cme it oz a p m side nw it z u take up zodiak mungoziwakt mulingo womwe umamuyezela mzanko wakoso ndiwomwewo

 8. POLITICAL CORRECTNESS: Those who love to talk will experience the consequences, for the tongue can kill or nourish life. PROVERBS 18: 21

 9. Kabwira kwa iyeyo akati opposition nde kuti azingotsutsa ndidzabwino zomwe which d government is doing…amalawi timanvera zinena za ma opposition parties nt wht the government says that’s why sitikutukuka we never support our government….ngati iwe uli wa mcp nomatter wht good DPP does yu will still oppose

 10. Kabwira kwa iyeyo akati opposition nde kuti azingotsutsa ndidzabwino zomwe which d government is doing…amalawi timanvera zinena za ma opposition parties nt wht the government says that’s why sitikutukuka we never support our government….ngati iwe uli wa mcp nomatter wht good DPP does yu will still oppose

 11. NOSE NDI AMODZI, NGAKHALE KUKUIKAPOSO IWEYO UZAPANGAPOSO ZAKO ZOLAKWIKA. NAYESO AKULAMULAYI AMKATELO ALIKUNJA NTHAWI YA JOICE BANDA. BOLA ALOYESE AZIKWANITSA MISSION YAKE YOMWE ANAKHALILA PA MPANDO. ZABWINO ZOSE ANDALE NOSE.

 12. Dpp iz a virus and its suppoters r carriers, blind in triblism,politic glaceses till their doom comes.Mcp recieve ur blessings transform Malawi for our gudnes…

 13. Kunakakhalakuti kupepesa nkofunika tinakawonela kaliyati nthawi ija anantukwana john tembo munyumba yamalamulo muja amvekele tachokaniapa mukutinunkhitsa chimbuzi apa

 14. kodi kabwira amadzimva chani? amaona ngati angagwetse boma amayankhura ngati angachotse president bwanji? ngati mkwiyo ukanari wa masankho aja nde uphurika coz munthu urimbana nayeyo si size yako akhoza kukuthothora mosavuta chakwera amakumvera chisonj koma safuna kukuuza chirungamo kuti mai izi ndi ndare sizipanganika tikhoza kukhara pansi mochititsa manyazi

 15. # Owen wakamba chilungamo , sindikuona kuthekela koti MCP kulamulila Malawi, komaso inu atolakhani musabwelese zipolowe dziko muno ndikhani zanu zopanda umboni ngati uli uphawi mufa nawo

 16. Kabwila muthu mukulimbana nayeyu simumukwanisa olo pang’ ono pomwe, choyamba ziwa ichi, sadasiye pingo, kuyamba ndale kuti alemele, ndindalama zingati zomwe mulinazo potengela chopeleka chomwe athu Ku church munawabele? Tsono mutawona kuti ndalama zayamba kuchepa munati Mulungu uko koma ndale hahahaha muzafela Ku opposition koko chifukwa pomwe kuluyo akhale akukapupa after 2019 victory apo pomwe Chilima, Atupele akuzatenga boma inu mukhala chocho paka Yesu kubwera

 17. Pya Nooo Alomwe Nthawi Zonse Mumbafuna Anthu Azikupepesani Inupo Mungagodame Ndikupepesa Tayi Baba Alikujulu Alikuona Pypntchenene Munachita Inupi 2019 Dpp Ikuyenda Mmuji Ikalime Kabwila Longa Pyako Pyontchenene Pili Mumtima Mwako Mapakawa Asakuopseze Tayi Ngamala Zipani Zonsezi Zabaliwa Na MCP MUKALONGA ZAKUPHANA PANO ANTHU AKUPHIWA TAYI mapanga ndinu adpp misolo nonga ana abanja liboji mofire kabwila aleke agalu aseluke pyao hehede DPP unankenkedeka ne lowaso boma biiiii

 18. MCP Jessie z the political fighting machine & Jessie z one of the African Real Feminist On the Black Continent. MCP Z THE ONLY AFRICAN BIGGEST POLITICAL FORCE ON THIS BLACK CONTINENT. MCP WAZ,WERE & SHALL ALWAYZ BE MCP. GEM CHILL!.

 19. KKkkkk i didnt knw that Stevie Kaliati is so stupid,why talking about the people who are voting are coming frm the south hey who the hell are you?Dont take things for granted ask UDF where are they now bongololo sazola pa gulu,time wl come when your party wl say goodbye like what UDF did,what about in Zambia where is MMD?You must knw that this is the world it changes like the colour of the Chamelion so day your so called DPP wl be like UDF en leave MCP en Kabwila alone en Kabwila is agenius if you remember about the academic issues with the late Bingu then u wl come to your senses about who she is.

 20. Tanenani zina zimene Peter wachita zaka zimenezi abale. Malawi ndi dziko la fodya ndiye amalawi za fodya zomwe mukupanga mupitirize. Tolani nkhani zotukula mtundu wa a Malawi please komanso chonde kkkkkkkk

 21. olo munyoze iye nde akumwa wamkaka dairy inu muzingozikanda uku namutukwana..muzafelamo olo Jet inenedwayo osayilawa..ma savage apamalawi kunyela nokha mkumamvanso kunukha nokha..mumkamusankha kuti azathetse umphawi wammatumba mwanu inu muli phwiii iye azikakusakilani moti muthandizane naye…

 22. Mcp chomwe mungadziwe anayambitsa kunyamula anthu kupita nawo kunja ndi chipani cha Mcp. Muyezo mukumuyezera mzanuyo inunso adzakuyezani ndi omwewo.

 23. To The Malawi President: mr president forget it, Mayi Kabwira will not apologise and she will continue to do her work. A president with nothing in his head like you is a good president. Stop that hit right now. Swallow your pride and apologies to US Malawians. Ungamati unangobwela kudzatithandi? Tinakuyitana ife. Galu wachabechabe.

 24. Aaaaaaaaaha!!! Koma inuyo amene Mukulimbikila zoti Mcp ipepesenu mwaona cholakwika chani chanji? Kodi2 paja ndalama ikamalankhula chilungamo chilunga mo chimakhala chete. Komanso kuchita zinthu moloweza ndikomwe kukutivula lisa amalawi, apa simwati mcp ipepese mukuiona kuti sikulamula ka ndichifukwa chake mukulankhula zimenezo, koma zomwezo ikanapanga Dpp yanuyo mukanaamikila coz ndimene ikulamula, koma nkuona kwanga ineyo Mcp ndichipani chimene pochita zinthu sichimanyenge lela coz chimadziwa zoenela kulankhula. Nde tikumbutsanepo apa kuti kabwila asanyozeke coz amalankhulila chipani chapani Cha Mcp komanso pachilungamo umunthu tizikhala nawo, ngati muli ndikwanu tukamba zakumudzi osati mma town munabisalamo ayi mutamapita muzikaona kuti ena amene mudawasiya aja akukumana ndimavuto otani, nanga uyuyu uyu ndalama zomwe anakaononga ku UN chifukwa chotenga chigulu chaanthu akwawocho zikanakhala kuti anapita ndianthu ochepa zina nkugulila mankhwala kapena chimanga anthu ena sakanathandizika? Mcp sipepesa sindikuona chopepesela, komanso apapa nde timati chipani chamaso mphenya. Jassie Kabwilanso paekha ngati munthu siani kumunyoza ali ndizinthu zoti enanuso ngakhale kubanja kwanu kulibe amene anafikapo tukamba zamaphunzilo nde akamalankhula sikuti samadziwa chomwe akunena, ndipo ndimunthu yekhayo amene amafuna kuti anthu azimva zoona zake. Ndineneso Komaliza kuti Mcp kulibe kupepesa!!!!

 25. APM tizimuvetsa akati wakalipa ndiye kuti wasangalala kwambiri.

 26. Ali ndi dollar??? Iyeyo ndi Messi kapena Ronaldo Ali ndi dollar ndindani???

 27. a J kabwila(MCP mouthpiece), pepani ndifunseko, kodi muli pa banja? Coz munakhala pa banja munakadziwa kuti sibwino kubweletsa nkhani zakale pa nkangano wa new one, ndikuona ngati munakangokamba za lerozi mopanda kutchulapo Prof Bingu wa Mutharika(pajatu munthuyu anamwalira), Akabwira usiyeni mzimu wa malemu Bingu uwuse mu ntendere..! What do u mean by sayin Prof APM wayiwala zimene zinanchitikira brother wake Late Prof Bingu? Akabwila mayankhulidwe oterewa ku MCP kwanuko mukuti ndi kutsutsa Boma kapena kumuopseza President wa dziko lino? Mwina ku MCP kwanuko thats what u call balance & check? In Democracy(Malawi Democracy) MCP ndi Atola Nkhani ndi okhawo amene amanena zoona/salakwitsa? Coz mukuti President za UN walakwitsa, mayankhidwe mukutinso walakwitsa, ndikanena kuti chakula apa ndi “Nsanje, Nthenda”(in our Nation Anthem) yosatha kunena zabwino za ena.. nanenso ndilakwitsa? enafe kukhululuka timakhululuka koma kuyiwala kumativuta.. enafe nthawi ya MCP tayimitsidwapo attention Nation Anthem ya Malawi ikamayimbidwa pa MBC Radio 1 & ndiri ndi scar mai anga anandigwela atakankhidwa pa khomo la msika chifukwa chosandidulira khadi la umembala, ndinu nomwe munkati Bingu si wa bwino(man behind new look Lilongwe ) koma Joyce Banda, zaka ziwiri zinakwana asanakuipireni?(lero kaya alipotani kaya?) Lero mwabwelanso ndiyanu ija yongowona zitsotso mmaso mwa ena 24/7, 365, a J Kabwila Malawiyu palibenso wina, lets love it,tinakagwirana manja developin it, kuyamikira boma pamene lachita bwino, kutsutsa (koma momanga osati mwa Nsanje, Nthenda..)pomwe sirinachite bwino. Malawi tiri ndi madzi, nthaka ndi anthu koma chaka ndi chaka njala, blackouts,dry taps.. politics too much, aJessie Kabwila & MCP, maganizidwewa.. mwina ndi bleme(blame) dzuwa liri pa flag yathu ya Malawi, a good 51yrs silinamalizikebe kutuluka..!

 28. mc donald mhango now ur god of pipo chifukwa chani ukuwagamula mr chakwera ngat iwo anasiya za ubusa iweyo sizikukukhaza ndichisakho chawo man oky mind on ur business

  1. Man open ur eyes n see n lm nt highlighting somebodies mind about Mr chakwera so achakwera anuwo ndinawakonda heavy ali pa upresident wa S D A nt zandalezi man ndimbola chisankho anachitacho kaya

   1. Vist your google again, he has never been a president for SDA. Which means you don’t know what you’re saying. Pray that this veil of ignorance should be taken off.

 29. mc donald mhango now ur god of pipo chifukwa chani ukuwagamula mr chakwera ngat iwo anasiya za ubusa iweyo sizikukukhaza ndichisakho chawo man oky mind on ur business

 30. mc donald mhango now ur god of pipo chifukwa chani ukuwagamula mr chakwera ngat iwo anasiya za ubusa iweyo sizikukukhaza ndichisakho chawo man oky mind on ur business

 31. mayi kabwila amalakhula mopusa and she must apologise adziwe MCP olo zitavuta singalamulile dziko la malawi adziyelekedwa bwino mawa angazakhale pa dzuwa ndi u lecture wawoo

 32. Kabwila galu ndiwe osaonekanso bwino hule Dpp 4ever twinanso 2019 until 2056 ufune usafune kabwila wamva ife nde ovota

  1. Iwe ndi Mbuzi Yayikulu eti pamodzi Nkhandwe yako yomwe ilibe manu mkamwa ija. Ndiwe ndaninso ndi kachipani ka china ko kuti udzilimbana ndi fighting political Jessie. MCP Z THE ONLY BIGGEST POLITICAL FORCE IN THE WHOLE AFRICA.

 33. Kodi amadikira kupepesedwa?azichita zosakhala bwino ndicholinga choti akazuzulidwa azikalip kuti ena apepese.Kukalipa kumasonyeza kusafuna kuonesa kugonja.Palibe choti munthu angapepese apa,akanakhala olemera kare sakanabwera ku mw kuno,koma anabwera ndichoringa chozatibera.

 34. Tell him he wounded us during election and he want to continue wounding us impossible this is Malawi may be he don’t know

 35. Amalawi….chonde ndife amodzi…..sizonenana kut mtumbuka….mnchewa….muyawo….mnsena….sizititengela kulikonse….kungoyankhapo zomwe zili mmaganizo…mwanu…osat zosakhana…mitundu…kapena…kunyoza Kamuzu yemwe sizikumukhuza…or Tembo….sizabwino.

 36. Ehee titawelengesa ma comment okwana 193: Zili motere 3 akuti kabwira apepese 176 akuti asapepese kabwira more fire more fire more firee.14 enawo achita kunenelatu kuti ka APM mkachani kuti kapepesedwe,ena achita kuonjeza kuti APM pachakuti pake,pachakuti pake.Ena achita kulozapo
  ZIKOMO,Ine markson Mbendera .

 37. Kodi anthu nose mkumuyika kumbuyonu mukudyanaye galu ameneyi nanga chabwino ngati mukudyanaye, nanga osawukafe mwatikozela chiyani? Nanga pa chimene mwakonzacho nchifukwa chiyani mpakana lero sichikuwoneka? Muzindikile kuti Nyaniyi walephela avomeleze kulephela kwake .tisadzasoweso Mafuta chifukwa cha u professer opanda chithandizo waliuma losathandiza dziko lawo

 38. Mzingokhalira kulalata koma apa ca nzeru palibe,peter pano ali pampando.kabwira uziwe cipani unalowacho chonunkha magazi anthu sangacivotere,ukafuse ambuyako aja aku Dedza nde anaciononga cipanicho,pano nde izi mkungolalata nzomwe mkapanga ndi akamuzu zilipobe zoyamwira,mkafuna ndale dikirani 2019

  1. Inu Adpp Paja mudapha Robert Chasowa,mwaphaso Issa Njauju Komanso Mukupha Ma Albino,Mulungu sakusiyani choncho, tionanso cardiac arrest ina.u

 39. Palibe opepesa apa ! Ku malawikuno palibe msongoleli anachita chazelu amalawi ndikuyamikila , amadikila alakwise. Chisanzo: malamulo amat min bus anthu azikhala 3, koma kaoneni ku lilongwe , za city central muzava chisoni

 40. Kaberekanan ngati mbewa, kaya panopa malo mukadzigulira kuti? Poti DPP + APM agulitsanso kwa azungu malo anuo.kkkkkk MCP oyeeeeeeeee

 41. ADPP onse asova kuzomba sinjala yalowa. APM adakwatira kuti awapatse ufa tione siwati ndi billionaire ku USA. Awathandize anthu akewo tione. MCP More Fire, ngati anakaniza mukhito ndie akufuna anzao apepese kkkkkk kupanda mano mkamwa thyolo pipo.kkkkk

 42. Ameneyo ndie kabwira ndimadzia ine. Ask BINGU Kundata, He knows better, 2yrs Chanco closed, ndie kabwira mukuti atann???? Sangaimve imeneyo. Peter iz challenging as Bingu did aziona.

 43. Nthawi ya Bingu adasowa mtendere ndi aphunzitsi atatu ku Malawi University mpaka miyezi 8 ataitseka, Peter mutharika anali nduna ya maphunziro. Kabwira ndimmodzi wa aphunzitsi amenewo, adakhaulitsa Bingu, wa mng’onoyu ndiye pa mpunga weniweni.

 44. DPP no more recruitment of Nurses, panopa ku hospa ayamba kulandira kamodzi food @3pm.kkkkk kuprison with dpp and peter clue.

 45. Amalawi tikulowera kuti campaign sanatsegulile a MEC hold ur petience guyz jst God may help malawi koma koma ukakhala pansana wanjovu usamati kulibe mame chili kwanzako usamati chigwile nyanga yanga mpasa ndayalula pamenepo

 46. Zoona Amai Tilankhulireniko Musaope Palibe Amene Angachite Chilichose Muli M`manja Mwa M U L U N G U Akusamalani Osaopa Lankhulani Mulungu Awalanga Amewo Mtundu Wa Amalawi Ukulira Koopsa

 47. DPP ppo u r very stupid….. mwaiwala zot kuli ma poor malawianz suffering inu kumatengana Ku new York over 100 ppo…mukuyesa boma ndi La azukulu any eti????.. no nid of apologizing it will b compromisation of tym…talk of HW u will help the poor Malawian s n not telling us of ur fury…..r u serious with your job…..go 2 hell n die with the devil if u have failed 2 manage our beautiful Malawi…..

 48. zouna zakendizakuti MCP ekufuna etalamulila mwachangu 2019 esanafike,tiyenazoni mudzaziuna kulemela kwake mudzakawina.ndipamene mudzazindikele kuti chili kwazako usamati …………

 49. Instead Of Apologising To Taxpayers For Being Exravagant, Now He Wants The Taxpayers To Worship Him. What Evidence Do We Need When Commentors Say Dpp Do Things In Upside Down Fashon? How Can A Leader Ask International Support While On The Other Hand He Is Spending The Scarce Resources In A Willy Nilly Fashon? Is Not A Shame For Us Malawians To Hear What The German Ambassador Said In Dedza That They Are Not Father Xrismas? Let Us Wakeup And Show Him That We Are Not Fools. Has He Forgotten How His Brother Was Trimmed To Size. We Are Not Stupid To Apologise To Trickstars Like The Dpp.

 50. Fidesi Misiri ndikugwirizanawe kwantunthu Mulungu ndiye Msogoleri wabwino palibenso paziko pano ati Akabwira ndiyenso ndani liwakanika ndi Banja lomwe ndiye akhale atsogoleri abwino never

 51. makani ake amenewa mkupatsidwa utsogoleri wadziko amalawi adzakhala chani we never kubwenzeretsa mcp as a rulling party in this nation ngati akupanga makani ali ku opposition atalowa mboma angamumvere ndani palibe kupanga brander pa kuvota mcp sidzasintha magazi ake ndiamodzi palibe kuvotera mcp, dpp idzalamulira mpakampaka

 52. makani ake amenewa mkupatsidwa utsogoleri wadziko amalawi adzakhala chani we never kubwenzeretsa mcp as a rulling party in this nation ngati akupanga makani ali ku opposition atalowa mboma angamumvere ndani palibe kupanga brander pa kuvota mcp sidzasintha magazi ake ndiamodzi palibe kuvotera mcp, dpp idzalamulira mpakampaka

 53. If the party will not apologize then no problem. Kabwila and others, they think that what they are doing is democracy but no thisis insane and everyone knows , the statement by the president was clear koma Kabwila,Kabwila ndekuti chani she educated zochitika ndiye ndimbuli mbuli

 54. Pliz my beloved President don’t organise the meetings with fools again look they were asking the questions with all boldness the questions that has already clearly justified open & blank very !very s SHAME!

 55. makani ake amenewa mkupatsidwa utsogoleri wadziko amalawi adzakhala chani we never kubwenzeretsa mcp as a rulling party in this nation ngati akupanga makani ali ku opposition atalowa mboma angamumvere ndani palibe kupanga brander pa kuvota mcp sidzasintha magazi ake ndiamodzi palibe kuvotera mcp, dpp idzalamulira mpakampaka

 56. Kabwila z still frustrated ndi May 2014 polls results n sh wil owez be even atakhala kut Peter/ DPP sikulamuliranso…dats a fact..sh z js a DPP hater bas..aish..

 57. Kodi akati KABWIRA apepese apepesa chani ngati adalakwisa.kungoti anthuwa safuna kuuzidwa chilungamo kwakula apa ndi kuzikonda koma m’mawa azatifuna.stupid people.

 58. what do u mean who is kabwila? ine ndimadana ndi ndale zonyozana ndibwino anthu azidziwa zoona & Andale okha okha sangatiuze zinthu zomwe zingasithe malawi ino cz wonsewo amakhala akupanga business yofuna mpando womwewo kulibe wabwino kundale

 59. Kabwira iwowo asazione ngati ndi dolo,kuli anzao ulendo wa nga ntafu alikt,nthawi nzina ng,oma yolilitsa siichedwa kung,ambika,choti muziwe ndi choti kuyendetsa sichinthu chophweka,ngati mkuufuna udindo dikirani 2019 koma mkakhalira kunyoza boma mmalo molithandiza mzafera kotsusa komweko

  1. kkk 2019 tidzavotera mcp kukhala chipani chotsutsa bomabe ndani angavotere mcp kukhala chipani cholamula boma asa munapanga bwanji a mcp

  2. Anthu opusa inu, mukuona ngati anthu azavoteranso dpp ndi mtsogoleri wanu wopanda masomphanyayu. Paja munazolowera mavuto eti, muzakhumudwa.

 60. Dziko la Malawi lilipamavuto azachuma kuyambira kale ndipo ngakhale timati economy ofunika mtsogoleri ophunzira bwino ophunzira omwewo akuliononga kwambiri dziko palibe chabwino chomwe chikuoneka limachuluka ndi dyera basi koma mwayi okhala pa udindowo ukapezeka ndimalephera kukwaniritsa zofuna komanso zofunika mu dziko lathu shame.

 61. Kubvomeredza kulakwa sikupusa ayi, aPitala bvomeredzani kulakwa maka ndi mavuto a chuma mudziko mwathu. Kuphunzira kuli yapo or kuti ndinu aphunzitsi a Obama sizingathandidze koma kugonja basi. Wakusina nkhuku ndi m’nasi.

 62. i can’t take views of someone who doesn’t even recognise th existence of God like you Jersey Kabwila. and a Chakwela mumatikaikitsanso nanu, You are known to be a man of God but work hand in hand with someone who doesn’t even agree with th existence of your master.

 63. Dont even try to apologise to this stupid govt better they apologise to poor tax payers.These bastards they cant think 4 poor malawians

 64. MONGOKUMBUTSANA
  SOME OF THE FUNNY THINGS
  THAT PRESIDENT PETER
  MUTHARIKA HAS SAID

  1. Ku Malawi kuno tilimbikitsa ulimi otaya madzi (irrigation)

  2. Boma langa lilimbikitsa
  program yogawa zilombo
  (livestock pass on program)

  3. Tiyeni tilimbikire kulima
  tchipisi (potato) chifukwa
  muli ndalama kwambiri

  4. Dzulo ndidapita ku boma la Ngabu ndi Chikhwawa
  kukacheza ndi anthu
  okokoloka ndi madzi

  5. Malawi ndi dziko la fodya
  ndiye amalawi za fodya zomwe mukupanga
  mupitirize.

  1. Keith-Rio Namalepeta Travis Phiri ambuli ndinuyo baba coz palibe chanzeru chilichonse pazomwe inuyo ndiumbuli wanuwo mukuziona ngati zanzeru….. osamanyoza anzanu pomwe inunso ndiopelewera m’mutu,ngati mwasowa choyakhula ndibwino kungokhala chete basi NO HARM!

  2. Munthu onyoza makolo ake,amakhala munthu odabwisa.Mwatani kumanyoza msogoleli wanu chonchi.Mwambo wa chikhalidwe chanu mwausiya kuti?mwatani kodi?koma ndinu amalawidi?

 65. Ndale zachikalekale akabwila inuso munali gulu la athu opita nawo.tiuze zimene inu mwabwelanazo,ngati munapita.osati zoteteza chipani,tiyeni tisithe kachitidwe kazithu.

 66. Kodi Anthu Enanu Adakupepetulani Eti.Zoti Dzikoli Silikuyenda Bwino Simukuona?More Fire Kabwila!!Athire Mphepo Amenewo

  1. U need to think very critical before when u comment..do you know what cashgate is? It seems u dont know wat it is…zidayambika ndi Muluzi kenaka Bingu mudazidziwa nthawi JB ndinu mavubwa u dont know politics khala chete …selfish president like peter sakufunikaso aii

 67. ZOONA PALIBE KUPEPESA APA! CHOTI ADZIWE CHILUNGAMO CHIMAWAWA, KABWIRA NDIONSEWA AKUNENA ZOONA. PRESIDENT NDIYEMWE AKUYENERA KUPEPESA KWA A#MALAWIFE PAZOMWE WACHITA. PAMENE AMALAWI TIKUVUTIKA MUNJIRA ZAMBIRI WINA NDIKUMATINJOYA CHONCHO NDIZOWAWA! THUMB UP KABWIRA, MO FIRE #MCP!

 68. NGATI KULI MUNTHU AMENE ADZALEPHERETSE CHAKWERA PA VOTE YA PATSOGOLOPA NDI KABWIRAYU . SHE IS A VERY BAD ADVISER TO THE TOP MCP MAN .

 69. Kabwila, Tangopepesani Mukupangitsa Kuti Tisadzakuvoteren 2019 Coz Mukuchulukitsa Zolankhula, Basi Ndasintha Maganizo D P P 2019 Boma!!! Palibe Wazelu Wazelu Ndiyemweyu A P M.

 70. Dpp my party peter my president till 2024 ovota ndife anthu akummwera or mcp ingapange makani maka ife akummwera will make sure mcp will never rule malawi we had had enough of them eg killing of innocent opposition individuals. harrassing pple of malawi. mcp youth league men raping women so mabala amenewa ali fresh than kukwera ndege kwa peter zopusa basi

  1. MCP will never bounce back.Malawian had suffered many atrocities,totures,killings and many more.Say NO to MCP.keep the fire burning.Viva DPP!

  2. sakudziwa kuti southern ndi eastern region ndi imene imaika mtsogoleri pampando achewa ndi atumbuka amasankha atsogoleri otsutsa mdziko muno

  3. Mukumaberekana mwachisawawa nchifukwa munachulukana. Umphawiso wakula kumwera konko, mutha ndi njala anthu opusa inu. Mukumaberekana ngati ziweto zoti kuli kulera anthu akumwera mumanzimvera kwa anthu aku central ndiku north.

  4. inu obweranu mumafunako chani kummwerako? obwera anapanga chitukuko kummwera ndi ndani? tili ndi ma billionaire kummwera umphawi kulibe timakhala nazo zokolola zosiyanasiyana. timaberekani coz ndife amphamvu enanu mumapita kwa asing’anga kuti mubereke ife ayi. producing presidents is our culture.

  5. people its not about who is ruling its about how he is doing it…china is richer than malawi but it only took 6 individuals to the UN and yet malawi a country with a lot of problems takes 118 people to the UN. If u dont see anything wrong with that then we have a problem and we cant move forward

  6. Kod Mukut Mcp Imapha Anthu Osalakwa Nanga Dpp Sikupha Anthu Osalakwa? Kod Robert Nd Brother Wake Chasowa Anaphedwa Ndndan? Popeza Nd Inuyo Adpp… Mukut Chitukuko, Chilungamo, Chiteteze, Koma Kunena Zoona Zonsez Palibe Chomwe Chachtikako Kuphana Ndye Nd Dairy.. Kod Pitalay Ali Nd Mano Angat Mkamwa Mwake? Think About It Ndangoyambapo…

  7. Iwe ndiye chisilu chachabechabe wakuthandiza chani president wakoyo ukumamutchula kuti peter wanga poti wanena kale kuti ndiwe wakumwera mbuzi yachabechabe Ngati iwe anthu mukuvutika iwe ukuti wabwino ndi uyu, poti ndiweso mbuli kagwere uko kape iwe.

  8. mac Reen mgommezulu here we are talking a bout parties not insulting each other. 4 ur own information am not ur type even ur father cant match me.yes ndine wakummwera then whats wrong ? uchitsilu wako umaona ngati aliyense ndi mbuli? kummwera anthu mmati timavutika do u have any idea whats we do in south? ghow do we produce presidents while ndife ovutka? where do u gets billionaire bussiness men like the mulis and the like.why white pple managed to love south by making zomba capital then? stupid

  9. mgomezulu wheather u like it or not peter is our president not ur idiotic, uneducated father so called mgommezulu who may happen to know how to make babies only. so dont hate peter hate ur father for not getting proper education. viva peter viva Dpp till 2024 ngati zakubowa samuka mmalawi no one will miss u bastard

 71. Even if MCp z firin back bt it doesn’t make sense cz DPP z ruling so osasewera ndi boma cz osusa azakhalebe osusa basi J U P TEMBO tried bt failed nde inu achakwela mulungu wakwiya nanu cz munasiya kutumikira pano ndinu achikunja ndemungawine choncho?? kdi mesa wanu ndi ubusa nde chaza ndiyani kujoina kanyama koipaka kotchedwa ndale EISh apa nde mwabexa ka kkkkkkkk

  1. Iwenso zandale suzitsata,sudziwa kuti president waku Korea ndimkulu wampingo wa Presbyterian church ndipo CHAKWERA 2019 ndi boma osati SATANIST wanuyu.

  2. Pulezident wanuyu nde wanyanya bolaniko enawa anayesesako,,koma uyu first ya ulamuliro wake kungoyamba ndi kuononga zaka zitatu sidzinathe nanga zikatha nde zikhalla bwanji?nonse amene munavotera uyu nonse ndinu mbuli,munadzolowera kudya kalingonda osatenthesa,

  3. # Emmily chitanda ineyo sindinavote nawo koma comment yanga muivesese cz sindikusiyanisa pakati pitala ndi chakwera ayi so ndikudabwa zomwe mukunenazo kti president wathu wake uti mmmmm ???

 72. KODI IFE A MALAWI TIMAZIGANIZIRA BWANJI, NANGATIMAFUNACHANI CHOKUTI BOMA LIZIPANGIRA NTHAWI ZONSE PAMOYO WATHU WASIKU NDI SIKU. NANGA DZIKO LIZITIPANGILACHANI.

 73. Kabwila Lankhula Zoyenela Kulankhulidwa, Asakuopsezedwa. Kodi Akukana Zoti Analakwa Kutenga Nantindi? Koma Bwanawaaa! Aa!

  1. Palibe zoopsezana aseeee MCP idatha kale kale kuchokela 1994 up to now ndichaka chiti chomwe idapangako zosangalatsa boma lomwe likulamula. ntchito ya MCP ndikupha ndi kunyoza chilichonse chomwe likupanga boma limene likulamula mukamufunse tembo man adzakuuzani bho bho za MCP

  2. Alice, after seeing your fake profile picture I’m not surprised with your comment. So just because Kabwila is also politician then she doesn’t have to speak out when something goes wrong? Really? Remember she is a Malawian before she’s a politician and she is entitled to speak for the voiceless citizens in times like these.

  3. what do u mean who is kabwila? ine ndimadana ndi ndale zonyozana ndibwino anthu azidziwa zoona & Andale okha okha sangatiuze zinthu zomwe zingasithe malawi ino cz wonsewo amakhala akupanga business yofuna mpando womwewo kulibe wabwino kundale

  4. Do you really want me to tell you who is Kabwila? If you meant to be sarcastic then it’s sickening. Looks like everything I stated went over your head or your #loyalty with DPP & it’s president is making you more dumb. Good night Alice.

  5. Alice ithink u dnt love your pple n country iwe anth akulir miyanda miyand,ndip Mulung akukhulukir ndi anthut awa ndip owalengay akumva kulira kwaw

  6. Iweyo Gi nawe sukufotokoza kanthu.mot zot anthu ena wnt there thru NGO’s potential sikukhulupilira? Ok nanga mukudandaula za Ndege yoDula? Ha ha!! Kutagulixidwa chitukuko chathu cha Jet ija mkugula ma Cruiser/ROLLIPrado? Mudali kut? Mudalankhulapo? Tizit zot kuli Democracy simumkadziwa? Kunabedwa2 ma change ku Jet imene ija

  7. Uwu nde uchitsilu weniweni,Ndege ndichitukuko chonyadira?mukanakwerako kapena?njala ndikukwera jet zingafanane?isanabwere jet yanuyo si amakwera ndege zomwezi mawulendo nkumatheka,tiyeni tikonde dziko lathu,akuti ali ndi ndarama pitarayo bwanji osagula yake ya personal azikwera

  8. Amos chitsilu ndiwe, kuli anthu ma individuals ali ndi ndege nde what about us as a nation tilibiletu,development is seen in assets .

  9. Alice i think mutu wako ndi ofoira umadya kanundu…fotseki iwe ndindaninso….stop taking nonsence…inunso ndiandale?????

  10. I think Frank W Betha you are so stupid you don’t know kuti mcp was burnt with nyale pa refrendum iwe ndiwandale bvumve wachabe chabe mcp ndikumanda

  11. Arnold ine sindimabwezela kuwauza anthu zoyipa but am tel u truth kuti MCP ndiyolephera nthawi zonse & anthu ake ambili alibe umunthu ngati iweyo amakinda zakupha ndi zonyoza anzawo.

  1. Its mcp,they ruled malawi 4ova 30trs but no tangible development.zambirizi kamuzu adachita kuzipeza,koma adafuna kuonetsa udolo pozitcha dzina lake eg kamuzu stadium,kamuzu bridge,kamuzu barrage etc.nchani chimene adapanga mzunguyu????mwinanso sukudziwa kamuzu sadali munthu wakuda.

 74. This tym around no one should point finger at one another. let’s come togather and solve the problems that has masked our beloved country. no need to politicise our problems but find words of eradicating them

  1. Awa nde umbuli weniweni,,,mnzanuyo she is proud of herself that she went to xool inu nanga,,tis is very sad comment indeed,

  2. u hav to sit dwn & realise u’r comment, ths shows hw bombcrat u r.she iz educted she haz to proud haself no need to praise 4 dat.shame on u

 75. #KABWIRA ,ur right tikufuna Azimayi olimba Mtima ngati inu,Osangoti Phee!zinthu zikuonengeka”Ithink that apology shld go2 his wife nt our #NATION,bcz he knwz when he maket that trip 2#UN he left his pipo hungry &calculation ws almst 3Million pipo face hunger’wy he cld be happy yt our Children r ‘suffering 4rm MALNUTRITION,due 2lack of food..?#NO MERCY.we hv alot of prblms 2b solved {#corcened citizen}

 76. Kulibe apologising pitala asowe basi ngati nyanga zikuchepa tisonkhelane tipange imodzi afe ndithu

 77. Mmmm Komabe Uyuyu Pitalayi Waonjeza Kwambiri Bolaso MCP Ikadapanga Zakupya….Apresident Aziyankhula Nkhat Mwana Wachaka Chimodz.. Kabwira More Fire Osamufookera Ameney Waonjeza Kwambiri

  1. Petera wanuyo chilipo chimene chikumusata anthu akamalira chonchi,,kafunseni a bingu lero ali kuti,,,,,, peter ndi mbulinso zedi,

 78. EE! APA NDI NGOTI MPIRA ULIPATI? JUSTICE VERSUS LEADERSHIP? VENUE AT DEMOCRATIC MALAWI: CUP TITLE: CHECKS AND BALANCES: REFEREES:ACTVISTS; SUPPORTERS TAX PAYERS AND ORDINARY CITIZENS: BEST PLAYER; TRANSPARENCY AND ACCOUNTABILITY. THAT IS GVT OF THE PEOPLE FOR THE PEOPLE AND BY THE PEOPLE. THANKS

 79. SITICHEDWA KUYIWALA – By Melifa yao

  Padzana Mabanja anali kutha ati chifukwa wina anachezera panzere wogula mafuta a galimoto,
  Makono Mabanja akutha ati chifukwa wina akumachezera kotunga Madzi a pakhomo,
  Kafufuku naululula kuti Chipala chinatulutsa Amalume ankatiyang’anira nthawi yovuta mafuta,
  Mchipala chomwecho chinatulutsanso Amalume akutiyang’anira panthawi yovuta Madzi inoyi
  Tilimbe Amalawi, Mabvuto akadali, ntheradi anthuwa ndamodzi, angosiyana Silang’i (Slang).
  Onena nkumanena, Amalawi sachedwa kuyiwala!

  Tsano yatentha nkhani ya UNGA, mosasiyana ndi kutentha kwaku Jahena,
  Koma yayi, Mapulezidenti athu, ku UNGA ndiye kokaziziritsira kummero,
  Enawa kuwadzudzula kuti ku UNGA mwatenga khola la Mbuzi latunthu
  Iwo akubweza mokumbutsa, amvekere enanu padzana mmatengera makola a Nkhuku ku UNGA komweko,
  Nkhuku zake nazonso, Misoti yokhayokha, a Tambala makamaka akuda ali phee kulera wana pa Nyasaland,
  Nkumapitiriza amvekere, Amalawi sachedwa kuyiwala!

  Tichilimike posunga bwino nkhani zochitika Masiku ano,
  Zidzukulu zathu zisazawaphonye za a katswiri a amasiku ano,
  Palitu akatswiri oyenda mmalere,
  Palinsotu madolo ena akafuna kutsuka nkamwa ndiye kuti aopanga Pinyolo,
  Pakuti iwo wawo, ndi ukadaulo wopanga ‘Chanji Golo’ ndalama za boma nkukhala zawo
  Nkhawa ili bii kuti anagakhale manja awo ayamba kuvala maloko,
  Akuwerengera kuti posakhalitsa sikisi julaye izawatulutsa,
  Pakuti Amalawi sachedwa kuyiwala!

  Wati Zii Mpira wa Ntchemberembaye, pamene wina akunyadira kuti waja ankati ndichoke aja pano andiyiwala.
  Zisankho zayandikira za woyang’anira mpira wa miyendo, inde matchona akumati mpira wamapazi,
  Achulukirenji wofuna kuyang’anira, a Samvamgugu nkati okakamira mopanda Manyazi
  Tawafunsani za ndondomeko za makobidi mmene akhala akuyendera, amayankha thima lili zii,
  Ali ngati wafunsayo ndimmalawi, osandaula, sachedwakuyawala.

 80. INSTEAD OF APOLOGISING HIS INSULTING MALAWIANS PEOPLE WHO VOTE FOR HIM THATS BAD EH!

 81. You need emotional intelligence to govern this nation

Comments are closed.