‘Arrest Robert Chasowa killers or face rejection’ Mutharika told


Robert Chasowa

Malawi President Peter Mutharika has been asked to bring to book all people connected to the mysterious death of a fourth-year engineering Polytechnic student Robert Chasowa, or risk facing a rebellion from the youths across the country.

The remarks were made recently by President of Youth Freedom and Democracy (YFD) Black Moses.

Moses who was Chasowa’s closest ally, according to an initial report a special set Commission told MIJ FM in the programme known as Zili pati over the weekend that Mutharika was supposed to show love for the youth by fighting for justice on the matter.

Robert Chasowa
Chasowa, died mysteriously.

YFD, is a student political pressure group on campus. They publish the “Weekly Political Update” that is circulated to students on campus. They have been critical of Malawi’s governance, and of the Paladin Energy mining company.

In mid September, Malawian police arrested several members of the group. They also arrested 21-year-old Black Moses, president of the YFD and interrogated him.

A week later, 25-year-old Chasowa was found dead. Police ruled this a suicide but critics believe that he was murdered.

Moses while branding himself ‘Julius Malema’ said that five years down the line after Chasowa’s death arguing that it was not true that Chasowa had jumped from a higher building to kill himself.

Moses says that Chasowa was not a coward and findings by police that he killed himself are not true.

“No. He (Chasowa) did not kill himself but he was killed. It is time the President starts findings now. We are tired, but we will never relent to fight for the youth” said Moses.

“ If he loves us and want us to support him, he must probe the death of our friend”.

A team of investigators had said that Chasowa died having thrown himself from a tower at one of the building at the University of Malawi constituent college five years ago.

Black Moses
Moses: Youths want justice.

Late President Bingu wa Mutharika was highly connected to the death because Chasowa had been behind a force of rejection at the university.

Chasowa’s death came as the Unima was fighting for independence, an unrest it branded ‘Academic Freedom’.

When Bingu died in 2012, and when Joyce Banda, a vice President who had gone separate ways with the Democratic Progressive Party (DPP) she ignited probe into the death and a commission of enquiry told Malawians that the death remained mysterious naming some people who were interrogated to now when the case has stalled.

Assertions from critics have been made that the current leader, Peter Mutharika has been very silent about the issue because it painted a bad image about the DPP, which won a disputed poll last year.

Critics argue that Chasowa’s death remains something the DPP does not want to be brought into the limelight even now that five solid years have gone after the death.

 

381 thoughts on “‘Arrest Robert Chasowa killers or face rejection’ Mutharika told

 1. Musandikumbutse kale ndaliraaaaaaa!!!!!!!! (singing)

 2. man has failed to rule over manhood and has just increased the situation to worsen. Let JEHOVA GOD take over rulership other than mankind

 3. palibe chilungamo apa nkhan imeneyi sidzatha,joice banda anayesetsa kuikoka kom palib chomwe chimapindula,kom ofunika kugwilana manja achinyamata tose

 4. Forsake!!!!!!!! Nzako akapunthwa iwe podutsa umalumphapo. So is better to kip queit than kuika ma comment outsa mkwiyo kwa ena. Chala mmwamba, DPP woyeeeee!!!! Peter woyeeeeeee!!!!!!

 5. Mzathu chasowa adapita kuli chete, ngakhale mukambe motani sitizamuonaso pansi pano , musawanamizire achinyamata ingonamani ku anthu kuti mwaipeka nkhaniyi pofuna kuononga mbiri ya achinyamata dpp booomaaa ndipo kukakhala kwa moyo tizavoteraso yomweyo dpp yo

 6. Chifukwa chake kwa2ko Ku Malawi ine nidachokako ,ndikugwilizana ndi zimene wanena Marrah Alfred Shadreck ,umphawi suzathatu ka dziko ka Malawi ,zinthu zoonongera ndrama za zizzz, aaaa haha,

 7. I think Amalawi enanu umakhala umbuli cuz only God knowz chilungamo n his in a good position to judge too…nde mukamati achinyamata muzionetsetsa kuti siachinyamata onse amene ali opepera ngati inu nomwe….ndale ndi department imodzi ya mphavu yomwe satana amagwiritsa ntchito,nde enanu mukumazinva odziwa posting stupid staff kumaphatikiza tonse mudzasiya mutakakumana ndi chasowa wanuyo Agalu inu mukuona ngati timadya ndale ife???mukafa amunu azitinyasa apa…chasowayo ndioyamba kufa mu mbiri ya malawi???mukati achinyamata muziyamba mwafufuza kaye osati kumapanga post maumboni abodza apa mmalo mokasaka msima uko mukulimbana ndi boma kuti muli ndi chani???inuyo pamodzi ndi pitala yemweyo dzakuti dzaamanuu…shupitiii

 8. Nde kuti mulibe nkhani zotukula dziko kupatula za president peter muthalika?tsekani basi osati zomwe mumapangazi,bungwe lanji loona zolakwika basi osaona zabwino za munthu.?pakatipa Bushiri lero zina aaaaaaa musamatisokoneze pliz…..

 9. MAGANIZO ANGA NDI AKUTI NKHANI ZOPUSA NGATI IZI MUZISIYE, MUZAZIYAMBE NTHAWI YOKOLORA, MWAIWARA CHASOWA AMAGWILISIDWA NTCHITO NDI ANDALE, NKUMAONA NGATI IYE NDI DOLO OSAZIWA KT KULI MADOLOLO ANZAKE.

 10. kamalawi ndka usiwa kale ndi kale nsono kafukufuku ameneyo angowonongapo makobili moti dollar zimenezo mungowabweleka achinyamatao athamange pa Town or zipite ku reach out and touch

 11. The coin has too faces.. though many on earth there just too types/ kinds of the verious things on ds platform called earth… though you may try to paint t your emforts will not mean anything else than how? & what t was created for…. these are wise words profitable to those with good understanding..

 12. Bwanji boma la PP linakanika kufufuza .?Mukafuna kupanga attack boma musamatinamizire ife achinyamata?Mpaka kampeni ya 2019 mwayiyamba ?kkkkkkkk .Ngat ankapanga za ndalekufuna kutchuka ndiye zinamusata .Ndikulimbana nditsogolo langa kuti pofika 2019 ndizakhale ndili ndi plot yanga not zozavotazo,u want or u don’t palibe wandale wachilungamo .And zomabweretsa ma topic opusazi ife ayi ,bwanji osakamba za maphunziro abwino ,zamalimidwe ndi zaumoyo wabwino kuti pofika mu 2019′ achinyamata tione kusintha

 13. Inuyo amene mwalemba nkhaniyi mukupanga kampeni ya 2019 kapena kufa kwa munthu? Ngati muli anzelu simukanalemba izi.mukufuna kusokoneza anthu mitu . ndi angati omwe afa moganizilidwa kuti aphedwa ndi boma kuchokela 1994- 2015? Ndiyetu mungokhala inuyo atsogoleli amalawi mwina muzachita bwino. Amalawi tisanyoze atsogoleli athu tilemekeze dziko potsata malamulo ake. Mulandu umaweluzidwa Ku khoti osati pakhonde pa President.

 14. iyaaaa haha tidzlimbkla kufufuza zaokufa tizngotaya ndalama zaziii,,,anafa anafa bax,,,kamufuxen yekha kumandako ine ndekha my trust is in him n I wil cast my vote for him

 15. Iweyo olo utafa atsluxe ndani ? Tiyeni titukule dziko psamangogwera za Eni emanu midzakhala a president ndu na za boma nthawi ya nu ikafika tiyeni tilemekezane a Malawi

 16. ine ndili mu gulu la achinyamata.. izi sindinaikepo maganizo anga,nde mukuyendela ziti??? musamale inu aa malawi24 musakhale mukumapeka nkhani zomwe mumacheza kwanu ndikumapangira an2 maganizo

 17. achimwenewa adafa chifukwa chamwano sanganyoze mtsogoleli ndikumuyalutsa chonchija kuli ku ilac inali shaliyakale imene ija koma kuno aaa basi adangotelo kukoza kwake

 18. The fact is Robert was killed, but the Question is how the Killers new dat Chasowa anyamuka kusanache Ku Room ya gelfrnd wake wautali Ku L.City, kd adauzidwa zakusintha foni # yake kmnso zofuna kupita Ku Lilongwe ndi ndani ???? Ameneonso mkati, thank ye for yo tym.

 19. Mkasa anaimba kale za izi kuti ana asukulu musalowelere ndale, ndale ndikanyama koipa mwasoka ndikukumana nako samala kangakuchite #Tintin

 20. admin pena kumalemba nkhani zoona, awa simalo wopangira kampeni kapena decampeni munthu. shame on u. if tizavoyabe, APM yemweyenso

 21. Dem ! Tiye Nazon Uko Za Chasowa Zanuzo , , , , Ine Ndi Madana Ndi Munthu Omaztenga Ngat Dolo Ali Kape Chasowa Anali Munthu Opusa

 22. Mukunama inu mwangodana nalo boma uyu sioyamba kodi iyeyo adapanga chiyani? Tiuzeni remember what lusifer did he wanted to overthrow the Kingdom of God what happened? Zinazi osamangoyankhula popeza mukufuna kunyoza gd day

 23. Kunena za Peter ine ayi,,,,, koma mboni aliyese payekha payekha, ali ndimaso awona, ali ndimakutu wanva za bwana wathuyo,,,,,, zophana ine noooooooo comment

 24. Kunena za Peter ine ayi,,,,, koma mboni aliyese payekha payekha, ali ndimaso awona, ali ndimakutu wanva za bwana wathuyo,,,,,, zophana ine noooooooo comment

 25. George ndakunyadira chifukwa chakumasuka kwanu. Uthenga wanga oyamba upite kwa a bale a Chasowa sindikuziwa kuti mumanva bwanji akamakhamba nkhani ya bale wanu m’mitima mwanu kuchokera panthawi imene mudaluza munthu wanu kufikira lelo. Peteryu asaputsitse anthu iyeyo akuziwa bwinolomwe chimene chadapha robert chasowa ndeno akufna kuti azipedza njira yobela ndalama za boma ngati pali gulu limene limafufudza za imfa ya chasowa zotsatira adazipeza kapena sadazipeze akupitilirabe kufufudza akufuna apeze chani? Ndi ndani amene sakuziwa za munthu amene adapha chasowa kodi munthuyo alikuti pano naye mulungu simunthu asiye gululo lisakhalepoyi akuluwa ndikuta kuona kuti nzeru alibe chifukwa gulu limenelo lidzifuna ndalama kodi ndalama za gulu limeneli zizichoka kuti ngati ali ndi ndalama angotenga ndalamazo akapereke ku banja kwa a chasowo ndikukhalimbitsa mitima yawo kuti boma lalepera kupedza chimene chidamutengera chasowa kuli chete. Munthu wina aliyese akagweredwa amakhala olila pakapezeka ena omafufuza anthu amalimba mtima kuti tidziwa chomwe chidachitika koma mpaka zaka mkumatha palibe chochitika ine zimaphweteka mumtima kwambiri anthuwa ndi amisala. Pempho kwa amene muli pa fb ndipo boma mulinalo mkhonde mauthenga amene tikumalembawa muziwaonetsa akumipandowo kuti aziona dziko la malawi lili ndi mavuto ambiri bwanji osamalimbana ndimavuto kuti chepe uphava basi nde poti chilungamo chimawawa koma kwaizi zokha zikuwaweni mmuthitha tonse amalawi mutsale ndinuyo mzimu wa robert chasowa uutse munthendere mulungu azikudalitsani anthu akupha inu.

 26. Maganizo Athu Ndiopanda Tnchito Pa Nkhaniyi Ndipo Sangathandize Kuti Chilungamo Chiziwike!! Abale Ake Muli kuti????
  Anyamata Atelo Ndi Angati Kuti Mpaka Peter Adzaluze 2019??.

 27. zopusa basi achinyamata ake ati? ndizachiziwikire kuti ndi anthu andale omwewa akufuna kugwilitsa ntchito achinyamata ndipo mukuziwa kuti 2019 ndiliti? inu mukuzitcha achinyamata, do u min nkhaniyi ndiimene yakuwawani kuposa abolishment of loan ya HIGHER EDUCATION and many more issues in our country? by de way wht r u going 2 benefit? mwaonetsa kuzindikira koperewela.Nevertheless justice must prevail.

 28. Ndilibe chonena poti amati chiri kwanzaka chifukwa munthu akalakwa samayenela kuphedwa bwanji munthu okupha zake samaphedwe ndiye munthu wangonyoza chomuphera ndichan? Mudziwe izi palibe kanthu kuti ndiwe president kaya siww president kma chilango cha Mulungu sichidzayang’ana udindo wako

 29. Tio, Msogoleri wina aliense amanyozedwa.
  Nde ngati chilango cha onyozayo izikhala imfa nde mupha anthu angati?
  Ngati amanyozedwa olenga moyo nde iyeyo ndi ndani kuti aziyamikidwa ndi win a aliyense?

 30. achinyamata omwe amagwiritsidwa Ntchito ndi Andale potukwana ndi kunyoza anzawo zotsatirazake ndizimenezo tidzidziwa kulemekeza akulu mzathuyu anapusitsidwa ndi mayi banda kaya amafuna kupeza mwachangu tidzikumbukiranso malemba amatiphunzitsa kulemekeza akulu. guyz osamangompatsa phuma mtsogoleri wathu ndi nkhani zankutu. yemwe sadzamuvoterayo ndi ufuluwake kutero

 31. Kodi Chasowa anali ndani pamaso pa a Malawi? Kodi iyeyo amatani kuti afe? Aliyense amakolola zomwe wadzala! Ndiye musatinyanse. Zimenezo ndi ntchito za manja ake!

 32. Achinyamata? Ineso ndinyamata koma sumunandifuse and iwonder with this story Malawi has lost high profile pple the likes of Matafale,Gadama,Chiwanga,Matenje but nothing happens what special is with Chasowa get a lesson political its a dirty game

 33. Eny how,lwili Be The Seme,how Iam, Bora Ndimadya,zaine Ndimazipezande Kha! Ndi Vote,ndi Savote No Change, Ndithaku Ngotayanthawi Kumaringariza Mapresitent, Ariyese Warowa Akungofuna Achoke Ataphula, Inezindikhudze? Tangoganizani Ati Kumapitaku Misonkhano Yongokawononga Ndalamakunja Ndikutenga Anthu Ambirimbiri, Enaoti Sakapangako Karikose, Kungowononga Ndalama! Akufunakusanga Ratsa Chipani Iyaa!! Zachasowa, Aaaa Mungochedwa Dzikasosani, Ino Ndinthawiyorimatu Mongochedwa Akugwiritsa Ntchito Dora Anthuwa, Ingopangani Pran Yotukuriratsogor Ranu Basi, Ndingangothaso Battery Ranga Apa, Ndipiteku Bussines.

 34. Chasowa anachita kuphedwa ndi amene amkakonda DPP ndi Bingu. Mkuluyi analankhula moyesezela Bingu koma zamwano zoti Bingu sanalankhule. E.g ankati Calister Chapola ndizamukwera plen plen, John Tembo ali ndi dazi pamutu pake ngati airport, Bakili Muluzi ali ndizitsuro pamsana. Zinali zambiri zomwe analankhula Chasowa zachipongwe ine ndimangomvanawo anthu atagawana zili muma fon. Mwano wopangira akulu ndiomwe unamuphetsa. Ofufuza inu fufuzani za Njauju ndi Evison Matafale basi.

 35. Imfa sithawika musiyeni president wanu alamulire osamuwuza zochita as if a DVD player over remote control Mlungu ndi yemwe akuziwa bwino.

 36. Kuma nkhani za muthalika peter zakambidwa kuchoka asanakhale pa u president , bwanji amalawi tizisiye zonsezo tigwirane manja zinthu zayambeso kuyenda bwino i remember a chair anat ndale saadyaaaa!!!

 37. Chasowa anamwalilira ndale kuziona udolo kwambiri koma achinyamata what you shud kno is ndale ndi za azibambo,mukafuna kutchuka kundale sikochitira matama.

 38. Achinyamata ake ati akunenedwawo munthu samangidwa popanda mboni milandu yachasowa ena anayiyamba kuyilephera bwanji sanawine masankho? Agwidwe asagwidwe DPP IZAWINABE

 39. kodi chasowayu azazukaso kumanda mumatilirisa mukamakamba zachasowa ngati munamupha wosangozisiya chauta azaweruza ekha wosamangolimbana ndimadzi wopanda ntunda chasowa was my best friend i dont want to hear more about him

 40. Mukungotaya Nthaw Nd Nkhaniy. Kut Anal A Cashgate Bwenz Atamangdwa Kale Womwe Anamupha. Ndan Angapange Follow Pamunthu Wot Anaphedwa Kale, Palbe Ndalama Yinayake Angogwla Ntchto Ya Chifundo. Chenjeran Pamenepa Anthuwa Amathamangra Pa Ndalama Osat Pa Malro, Kumbukran Zomwe ZinaChtika Pa Player Wa Bullets.

 41. Ine sanandifuse bwanji achinyata ake ati omwe afutsidwa osaiwala kuti Nkasa adaimba kale kuti ndale nkanyama koipa ife achinyamata koaso Billy adati okonda zandale. ndindale zomwe zizamupha ndiye tizisamale ife achinyamata ngatitapita ku school tiyeni tipange za school don’t be used ndi achina Kamlepo and the likes tifa iwo. tiwasiya our politics is full of dirty

  1. ine I don’t follow any party but I always stand for the truth be honesty Kwenda have you been asked or concerted of this even if they can bring to book those killers are you going to benefit anything to my side I think it could be wise if the youth are demanding the president to address the pressure of job scarcity among est the youth not that stupid thing

 42. Tchulani mayina aachinyamatawo ife tisanatsilirepo ndemanga. Kuopa kupusitsidwa monga nkhani ya bakili ndi james phiri

 43. Achinyamatawo tinakumana kutiko????? Amene wanena izi zimenezo wanena maganizo ake osati aphatikizemo achinyamata tonse ayi, makonda makonda, komanso nthawi ino siyokamba za mavoti iya, 2019 ndi pano???? Get out!!!!!!!!!!

 44. ine ngati nyamata wa mudzikomu sanandifuse maganizo anga so stop kundipangila zochita ine ndidzavotela APM yemweyu olo inu mutapanda kudzavota anawina bwanji inu pamene simunamuvotele?

 45. Ngati achinyamatawo ali ndiumboni onse zakuphedwa kwanyamatayu bwanji sakupita kukasuma ku court coz zikuoneka ndimmene mwalembera nkhaniyi kuti iwowo akumuziwa

 46. AMalawi24 ndi amayi anuwo musova.Tiyang’ane mavuto achuma amene mzimayi wa TB JOSHUA, wakuba uja adabweretsa.Enanu kaya Chasowa ndi m’bale wanu,let me tell you the way the world has reached now,DON’T PLAY WITH IT.Ine odzamuvotera sadadziwike koma Chakwera ndi 0/10,JB ndiye ayi pothera ,and APM tione zaka zakhalazi ‘cos ndinamuikapo ndekha.

 47. ine ndi anyamata onse tikukondwa ndi ulamuliro wa mbwiye che mutharika ndipo tizawavoteranso,zikomo

 48. Tiyeni zonse tingozisiya in hands of god,siwoyamba kuphedwa iyeyo,like #matafale anafa ngati zomwezi,ndiye ngakhale tingalimbane ndi boma, boma sililuza tizangotaya nayo nthawi.

 49. Mmmmmmmm Malawi akupita kuti Abale?? Sizoona kuti nzathuyu anadzipha yekha apo ndikukana kochokela pansi pamtima, vuto lake linali chani kuti mpaka adziphe? Mukamalankhula inuyo amene mumadzitenga ngati amuyayanu musamalankhule ngati mukuuza anu akwanu kuti mukuwanamiza zowagulila galimoto pamene iweyo ngakhale ntengo wanjinga yakapalasa suudziwa. Zoti chasowa munachita kumupha andalenu samadziwa ndani? Vuto ndilakuti ndalama ikamalankhula Chilungamo chimafatsa, koma oweluza ndi Mulungu inuyo andalenu tinamizeni koma ndakuuzani ife siana anu kuti muzitinamiza, mukanena kuti adziponya pansi yekha anakwela nyumba yanu?? ndikupempheni inunso andale maka Boma la dpp lomweso linapha mwana uja ngati mumafatsa nkumawelengako timalembazi sindikuchita nanu mantha ndipo ngakhale pang’ono inu anthu oipa kwambiri, Mulungu akukuonani, vuto ndilakuti anthu amene mumasankhawo kuti afufuze zankhaniyo amakhala anu akale nde mumati adziti chani osatenga ena kunja bwanji? Ndakwiya nanu kwambiri, analakwa chani mwana amene amene uja kudana ndichilungamo, inuyo nde mukadziang’ana mukuona kuti ndinu ambeu? Ndikuamikeni inu amalawi 24 kuti mumatolela nkhani ndikumatifunsa maganizo, koma na nkhani yachosowa yokha ineyo inandipita powawa ndipo zoti bingu adafa ndimaona ngati bodza, mzimu wa ROBERT CHASOWA UUSE MUMTENDERE!! Ine zodzavotazo ndinatemesa kale nkhwangwa pamwala ndipo chikhalileni changa ndisaambe ndavotelako amfiti amenewa, ngati kuli kuwina adzawinila kubela amapangako komanso zinthu zikusintha nawo amalawi akuzindikilanso. Muzinamiza ana obeleka nokha kwanuko ndazibale anu enafe ayi.

 50. TIZALEPHELE KUVOTA CHIFUKWA CHA POLY? WH’S RC & DO U THINK ONLY YOUTH R FOUND ONLY AT POLY IN THIS COUTRY? TAKE CARE MY BELOVED FRND.

 51. Achinyamata ake ati?? Chamba eti. Anazipha yekha nde muzitinyasa ife apa. Moya samaufuna ameneyo zauchisiru eti osamakamba zanzeru bwanji. Nde mukawagwira chasowa wanuyo azuka kumanda??? Stupit.

  1. Ndiposo achinyamatafe tmazpha tokha chfkwa cha matama kfuna kutchuka ndindalama osamatnamzr apa ai mwatmdwa inu et? Azpanga ndiomweo osowa zchtawo musandiyakhulise morkwika mwanza

  2. naweso iwe choona ukuchzawatu kma,zopusa eti,pamene paja kuzgwetsa angafe chomchja? ulimbali iti?usatengele mbali kma kuisata mmene inaendela. ndan amend sazwa zankhan imeneyi,ngakhale kobadwa kumene(kamwana)kakuzwa.

  3. Chasowa anaphedwa chifukwa chamwano wake. Amkayesezela mmene amalankhulira bingu koma amalankhula zopusa zomwe Bingu sanalankhulepo. E.g kumati John Tembo ali ndi dazi ngati airport, Bakili Muluzi ali ndi zitsuro pamsana, Patricia Kaliati anayiwala pant ku Sanjika. Analankhula zamwano zambiri amaoneka ngati dolo koma zotsatira zake anakumana ndi madolo enieni pano ali kumanda.

  4. Guys imfa imapepuka ikakhala kwanzako n umaiziwa kupweteka kwake ikakulowera munyumba!dont talk like that tizakuonerani mayi anubambo anu kapena mwana wanu akapangidwa chimodzomodzi watch out

 52. Ifè yathu ndi bussiness, “tatengani ma belo ashuga, mkatawo, migolo itatu ya Kukoma muike mu lorry iyo”. Kufa kwa Chasowa mwadikire mai Jumbo ya Bonya akadzabwera.

 53. mphulupulu zake ndizomwe zinamuphesa amalimbana ndi anthu osakhala a msikhu wache.Anthu a mphulupulu sakhalitsa pa dziko. Ine zanuzo ayi ngakhale ndili waChinyamata.

 54. Tikufuna agwire amene adapha Njauju ife. Nenani za Matafale apa osati ana amwano anuwo. Chasowa udamuphetsa ndimwano wake womwe. Iyeyo anganene kuti Kaliati adayiwala pant ku Sanjika.

 55. mukungotaya nthawi za Matafare ziripati nanga za anthu anaphedwa ku Mzuzu aja palibe chimachika mukungotaya nthawi guys tiyeni tiyeng’ane komwe kuri chipulumuso coz tikudusa munyengo yovuta masiku oseriza amkanenedwa mu Bible ndi amenewa okumva amve osamva asamva bible limati tizasowa chowilingula

 56. aaaaaaaaaaaaa ine anyamata anzanga Zimenedzikukambikaapa ine ! zomwe mwatidzamavotinzo aa ine njeee! chifukwa kwanthuko kulibe cabwino aliyetse presedent amangothandanzawaka banja lake! sakufunakuthandidza anthufe tomwetinamvotera ayi! akumangotengeladzake basi ; so ine zomvotanzo kulibilethu? dont to put me in with N

 57. Inu A Malawi 24 Mwayamba Kutibowa Penapake Why Waisting Time With Such Nonsense Pamene Anthu Akuvutika Ndinjala Mmidzimu

 58. Sitingasiye kuvotera APM chifukwa cha Robert Chasowa. APM sanali president munthawi ya imfa yachasowa. Oyenela kufufuza za chasowa anayenela kukhala JB chifukwa iyeyo anatenga udindo wa Bingu.Kodi Apm kukhala mng’ono wa Bingu ndiye chikhale chifukwa?Musiyeni munthu aone za term yake. Robert chasowa samamenyera ufulu wa ife achinyamata. Anali ndi zifukwa zake ndi boma la mmbuyomo. Ife zisatikhudze zimenezo. Mukusiya kulondoloza za matafale oyamba kuphedwa uja bwa?Chilungamo chikazaoneka pa imfa ya matafale then muzabwele ndiza Robert chasowa. Choncho musamati achinyamata tonse tili kumbuyo kwa chasowa. Ine mundipatulemo. Maganizo anga.

 59. by the way, who is chasowa?kodi nkamenyela ufulu wadziko lino?vuto ankafuna kutchuka,adafela zake and nkasa adaimba kale kuti “ ndale nkanyama koipa samala kangakuchite tintini!

 60. Anafera zace ameneyo ngakhale anthu atamangidwa iye ndiye abweleranso? mfundo less kkkkkkkkkkk muziona ine ndi Zuma kakaka kumkakamila basi ngakhalebe aziti Xeno kaya zawo ine sindiimva ndili kuno

  1. Ada ndinu ofoila kupanda umunthu kotani. Akamati awamanga they dnt mean abwerela bt kut chilungamo chidziwake. Thnk of Chasowa ali brother wako wina nkumayankha manyi ngat akowa, hw cn u feel. Chouluka chingauluke aise chimaterabe. Udzatipeza kumudzi kuno.

 61. you did not raise him to the seat and you cannot bring him down.nations and men of powers have failed.you are just a brit of a sick dying goat.only god can do that if he so wills

 62. Mukadangoti mbava zati not achnyamata amene mukutchulawo inu simukudzwa kt munthuyi amafuna kutchuka? Ndye waziona kikikikiki! Zake zmenezo coz mukufuniranji akufa paamoyo.

 63. This topic iz so #raw….choyamba:kumalawi mavoti savota ndi anthu koma computer ndi owerenetserawo,chachiwiri monga mmene mwanenera kuti a#chinyamata ndatsangalala kwambiri,ife ngati achinyamata ,#Mthalika z nothng but ka#chikhadabo chabe, all wee nid z a hot topic whch wil sensitize and provoke achinyamatawo

  1. Me Wonder Kuti Zukhala How? Kapena Kunali Meeting Simunandiuze Hahahahaha Akuona Ngati Achinyamata Ake Ndi Akalekale Agona Aja Omatumidwa Kukapanga Zipolowe Ndikupatsidwa Phone Ya Huawei Aja Eti Kkkkkk

  2. Achinyamata ake ati KO’d????????? Mudatituma kut tikamuvotere kapena chiganizo tidapanga tokha hahahaha tidzamuvoteraso chimox MOX posauzidwa chochita ndi Malawi kaya mukut 34 kaya 24 ZANU izo ife ndi APM yemweyo bas

 64. olo achinyamata atati asadzamuvotere olo achinyamata atataya chikhulupiliro mwa Peter Mutharika,koma nothing can change from him being the president of the republic,there are a lot of problems that the youth are encountering in this nation e.g.HIV AIDS,lack of employment,robery,etc,ndiye kumachedwanso ndi za Chasowa,zinthu zoti sizingatithandize konse kaya amapanga zionetsero,Kamuzu amadana ndikugalukira,ndiye wina chifukwa cha Democracy basi kuzitengera pa mgong`o

 65. zitaeni zimenezo,ndiwo moyowo.kupha ndi normal.

 66. anapha chasowa ndi bingu, kodi lelo binguyo alikuti?kutelokotu bingu akumatuma chasowa kuti akatungile madzi okumwa koma chasowa akumakana akumamuuza kuti mesa unandipha nanga ukupezeka bwanji kuno?ndiye zoona zake za athu ose amene anaphedwa aja tizaziziwa bwinobwino siku lobwela yesu athu azikoli sitingauzane chilungamo ndiathu ambili amene anapha azawo zovesa chisoni kwambili

 67. kodi mkulu anapha linda gassa alikuti. za chasowa tizakambe after dpp ikazachaka odiiiiii ukuuuuu pp yanyamuka amai akubweaanxio. achakwara ndi akabwira akulira @ akanawatenga ku UN akadye nao soseji. naye Kapita @ kusowa ntchito akufuna akachingamire Peter the fantastic elpresidedento

 68. Stupid post!! Ife tinatopa nd nkhan ya chasowa. Kodi nd yekha? Nanga si imfa za achina gadama, matenje, kalonga stambuli, matafale, bingu, chatsika ndi………..? Bwanji osakambakonso za amenewo? Bribery, corruption, defilement….at malawi24.

 69. stone mwamadi, Isaac jomo Osman ntopwa 1 enuwakewa amazitama kuti nyonoz ndi amene anapha chasowa. koma Bullets team ya anthu akupha , amagazi

 70. stone mwamadi, Isaac jomo Osman ntopwa 1 enuwakewa amazitama kuti nyonoz ndi amene anapha chasowa. koma Bullets team ya anthu akupha , amagazi

 71. Who is Chasowa after all? Kuli anthu eni eni amene adafa koma pano kuli ziiiiii. The likes of Gadama, Matenje, Chawanga, Matafale, Njaunju eeiishhh too numerous to metion. akatero Black Moses akufuna la mchere lamusowa, ukachenjeletsetsa umafa mopusa. Palibe wachinyamata angave fundo zakozo ngati ukapeza ndalama ukuzifunazo udzatigawila.

 72. chasowA anadya ndalama za Dpp Bingu zokwana 10 million ,kuti asiye zioneselo,komaso anapasidwa list yamaina oti aphedwe athu,koma chasowa anakhala kwa week osapanga kathu,boma la Dpp linatutumuka kuti mwanayu aiphedula ndipo apolice anakangwira chasowa kumupha kulemba kalata ngati wazipha yekha kuiika ku pyrotechnic ku room kwake ,chasowa ndiamene amasongolera grup ya freedom fight ,imene athu inu makonda kunvala za red mukakwia ameneyu anali youth president,kwamene musanaziwe khani ndimeneyo anaphedwa ndi bingu muthalika Gorvement

 73. Robert Chasowa is rensponsible for his own death,blame no one on this matter.How can you start politics whilest at xool?.This might draw as a leson to other stupid poly students.

 74. Say marching because the president has failed to rule the nation
  Not because DPP killed Chasowa
  They killed many
  At one time they killed 21 people dzuwa liri phwe

 75. inu musatinyase ndipo musati bowe mwanva!kumene amadyera ndalamazo ife tinaliko?zoziputa dalazo?and you say the youth wil take to street which youths?zapokhalila zanuzo mudziuza mbuzi zosanka nkalasi mwanva?fotseki!

 76. BLACK MOSES be careful its the same DPP who kllled Chasowa: There is a Mafia like gang which can silence you: They are still free & alive, Pliz stop this madness you may loose your life; When a true Malawian President wins in 2019 you can come up with this issue & it will see the light of the day; Bwinotu Bwino muzayamba kusowa; You know why Joice Banda left this murder case die? Its very senstive, it involves akulu akulu adale zisiyeni:

 77. ife iz nzatitopesa kumangova khan ya chasowa palbe chazeru chlchoso chomwe chimatigwera moyo ndie mungozisia ndalemba chchewa coz muvetsetse asatana inu

 78. They r themseves culprits they cant tak themseves t court:Khoswe wakhala pa mkhate.But u wont CONCEAL th truth for keeps.

 79. Zachamba basi, Chasowa Chasowa Chasowa nde kuti chani? iyeyo akhale ndani? Mudauzako Presdent uti kuti afufuze imfa ya Evison Matafale? kapena mukufuna munene kuti imfa zimasiyana? Imfa ya Chasowa nde yeniyeni pamene ya Matafale nde si imfa?…mxiiiiew!!!

 80. Nde who is going to suffer? Hw long hv we been talking about Chasowa? Don’t u think we need to move forward… Nde rejection will bring donors back… Penapake put Malawi 1st over individuals… We need to move forward osati zomangothamangila ku UN ndi zithu zoti we are just punishing ourself… Apa tikulirira ma donors si ife tomwenso tinawathamangitsa, ndi zonga izi. Let’s for once stop promoting donors interest in Malawi…

  1. Inu mufufuze bwino mbiri ya United Nations?? Dziko lina lilose limayenera kupanga participate ngati lili mu UN unless patakhala zovuta zina dzikomo you can send a representative Guyz !!!! Ndichifukwa chake a Ministry Of Education akulimbikitsa kuti tizitenga History coz people you dont understand about UNGA of cos pankhani yotenga anthu ambiri ikhale apo !!

 81. All am thinking about is the abnormal hiking of prices of goods,the unemployment level by qualified teachers & some nurses,faluire of the teachers to receive their monthly salaries on time,the eradication of Primary School Leaving Certificate Exams(PSLCE) & Junior Certificate Of Exams(JCE),shortage of medicine in hospitals.Let the president tackle very important issues first so as to save the live citizens from death.It is imperative that he(president) deals with this murder case later.Why do you want to waste our money…i mean taxes on taking the suspects to court instead of paying the civil servants?Why not buy medicine to save the patients who are about to lose their lives in that hospital due to lack of proper medication?Why not allocate the qualified teachers & nurses to their working places for them to feed their families?What shall we(citizens) yield if we are to handle this matter first?Deal with issues of national importance first & personal ones should be last#Concerned patriotic citizen.

 82. Ngati amai anakanika kuulura za chasowa ndiye inu mukufuna APM aulure,funso lanuro is like busy doing nthng. He wantd to be popular and ithnk he got the popularity he deserved,who was he kulimbana ndi mikhatheya. He was uncivilised graduate.

 83. Which youths u idiot? Who chose u to be da mouthpiece of malawi youths? I dont even knw who da hell chasowa was and i dont give a damn kuti anafa….how special is chasowa anyway? Or maybe becoz he was a useless tumbuka?

  1. Mmalo mocommenta bwino bwino ukunyozaso mtundu waanthu(atumbuka) bwanji?ubwele kuno uzawone wekha mtundu wakwanu kuchuluka kwake mmaminda kulima utenati-samalazoyankhula zako-ukufuna tiyambe kumakupangani nkhanza eti?

  2. Mmalo mocommenta bwino bwino ukunyozaso mtundu waanthu(atumbuka) bwanji?ubwele kuno uzawone wekha mtundu wakwanu kuchuluka kwake mmaminda kulima utenati-samalazoyankhula zako-ukufuna tiyambe kumakupangani nkhanza eti?

 84. kodi mungotu chasowa mpaka pano mukudandaula munthu mmodzi yekha basi? maiko anzathu anthu akuluza miyoyo pali chani apa,amamenyera ufulu wandani?kaya moti muzikamba zanjala mukulimbana ndizaziiiiiii

 85. Not all the youth can do that,why do we have to follow things blindly, who is Robert chasowa? is he not the one who joined politics while at school and hoping to fight with government something contrary to his faculty ,therefore as a concerned youth I feel this is total trash and it’s better to concentrate on other things that to ride this natty ride

 86. Apha ambiri agalu amenewa munthu akadandaula amamupha lero tikadandaulanso zamagesi mutipha tizingokuyang’anani poti dziko ndi lanu ndimulandu wanji nyumba mpaka k3,00000 nyumba yogona,yes endeed we look forward na voti yaine mukunama mwandikwana kwabasi mphawi tili mmavuto

 87. Apha ambiri agalu amenewa munthu akadandaula amamupha lero tikadandaulanso zamagesi mutipha tizingokuyang’anani poti dziko ndi lanu ndimulandu wanji nyumba mpaka k3,00000 nyumba yogona,yes endeed we look forward na voti yaine mukunama mwandikwana kwabasi mphawi tili mmavuto

 88. Apha ambiri agalu amenewa munthu akadandaula amamupha lero tikadandaulanso zamagesi mutipha tizingokuyang’anani poti dziko ndi lanu ndimulandu wanji nyumba mpaka k3,00000 nyumba yogona,yes endeed we look forward na voti yaine mukunama mwandikwana kwabasi mphawi tili mmavuto

 89. Apha ambiri agalu amenewa munthu akadandaula amamupha lero tikadandaulanso zamagesi mutipha tizingokuyang’anani poti dziko ndi lanu ndimulandu wanji nyumba mpaka k3,00000 nyumba yogona,yes endeed we look forward na voti yaine mukunama mwandikwana kwabasi mphawi tili mmavuto

 90. DPP will never arrest those responsible for the death of Chasowa coz its late founder(Bingu) was connected with that painful death.Our hopes were on Joyce Banda but nothing materialised and no one was arrested when she was in power.This world is full of injustices and only God is the supreme judge in this case

 91. When the president won the 2014 presidential election chasowa s issue was already there and that was the time to reject the president not now.How do you reject someone who has already emerged the winner?Those presidential candidates who lost the general elections are the ones who were rejected.

 92. As i can see now malawi wabalalika ndi democracy,cuz pipo r doing wat dey want posaganizira de consequences.anthu amwalira ambiri who was freedom fiters instead of remembering dem ur now talking about chasowa,but remember dat de opotunity u hav tody next tym u wil cry 4it.

 93. Inu nkhani ya ameneyu ndinaletsa kale, simumva bwanji? iye ankafuna akhale shasha anthu amutame nde zinamuonekera. nkhani imeneyi lero komaliza ndisadzaimveso fokoku!!

 94. shut to kill,,,,,loading some deserve bcoz they wanted to b known,,,,,,and anaziwikadi,,,,,,dn’t provoke any dangerous animal coz it will kill u or wound u,,,,,coz if u provoke u deserve these 2

 95. shut to kill,,,,,loading some deserve bcoz they wanted to b known,,,,,,and anaziwikadi,,,,,,dn’t provoke any dangerous animal coz it will kill u or wound u,,,,,coz if u provoke u deserve these 2

 96. who can reject the country president bringing to book those killers won’t help our country stop that noses this is not time for campaigning let’s change our mind set please that’s why we are still the poorest country in the earth because of this thinking

 97. A GIRL WITH FISTULA (17 yrs old) SAID “Fistula is a very bad thing. Feces would come out from my urinary tract. I smelled badly, leaked urine and my friends isolated me. My boyfriend quit school to start work as a bus conductor to support me. But all this happened because I accidentally got pregnant while young, cos I didnt know about emergency contraception”. Fistula is just one of the complications that happen to ladies. 529, 000 women develop complications like these every year in Africa. Millions more die from pregnancy-related causes. But all this is because of lack of information. For this reason, “Ubereki Health Network” is providing reproductive health information to all men, women and youths regarding issues like contraceptives, fistulas, circumcision, menstrual problems, fibroids, cervical cancer, pregnancy issues etc!!! Please like our page by visiting this link m.facebook.com/profile.php?id=954957171233367

 98. Zauchitsilu zimangopweteketsa anthu opanda kanthu izi! Amafa ndamphawi anthu ovutika opanda kalikonse inu muliphee kumangodyelela ofulu wa anthu ovutika basi! Zausilu muthane komweko,we r crying for another wich is affecting the whole Malawi then u r bringing some thing wich can not help pipo of Malawi but helping a family,by the mata of fact ”who was chasowa to the history of freedom fighters of our nation?” plz guyz lets resolve this crisis that we r facing right now than fighting fo questions without answers! Lets look forward fo da nxt level!

 99. koma gyz mukuona ngat zimenezo ndizotheka? boma la dpp linapha Chasowa boma la dpp lomwelo mwati lifufuze? mukunatu

 100. “…..or risk facing a rebellion from the youths across the country!” Wowww, what a time to be alive! I, being one of the youths of this country, dont remember to have ever delegated anybody to make such a fallacious announcement on my behalf! What kind of weed are you ppo smoking???

  1. kodi mukamati chasowa, chasowa! nde utiuti ameneyo? anali ndani ku mbiri yadziko lathu? mesa ankafuna kukhala shasha iyeyo? nde ndizimenezotu

  2. If w think w hv seen enough wet w r jst deceiving urselves cause they r so much prblms to come wht is needed right nw z to seek the face of the Almight for a help on our on we cnt achiev anything. If w cn figure out wat z happening nw z wt the Bible said abt the last days

 101. Who have that power to tell the whole president to do that? What is so special about the so called chasowa? Malawi lost very important&innocent people like matafale. Why not asking the presdent to bring to book those who killed matafale first instead of those who killed the attention seeker

  1. Iwe wht wz so special mwa wachamba ngat ameneuja tel me anakapindulitsa chan dziko lathu lino munth opanda xul ngat ameneuja iwe u cnt see pali kusiana mbuzi

  2. ndipo ine nkhani imeneyi imandinyasa bwanji. kanali kandani kwenikweni kachasowako iyaaa! mesa amafuna akhale shasha, malipilo ake ndi amenewowo ka

 102. it is said, a life for a life. a tooth for a tooth. If man does not avenge, God does avenge. If Bingu Mutharika’s government was responsible, do you consider his death has not paid for it?

  1. Never the less, there was an enquiry set up for the matter. Did this enquiry finalise its work? Then steps expected to follow must do so.

 103. Being aMalawian that statement iz childish &its betr jst 2stay quite than putn salt on adry wound! it iz vry sem Dpp who killed Chasowa so wat r thy sen nw??r we blind dat u cn kill us&then do investgations?do u thnk malawians av 4gotn wat haz bin happening 2our mothrs,c*’s&brothrs evn intym ov kamuzu?? these pple r really satans coz at the sem tym they r eatn our taxes then kutpheraso our brothr Chasowa! Icn beg 2 Jehovah dat de blood ov Chasowa shud add de dayz ov thz Satans,,am Furious

  1. Sindikuikila kumbuyo amene anapha chasowa.Komabe penapake chasowa analuza target. Politics is a dirty game.Iye uja anali mwana wa xool,tsono chomalimbilana ndi boma ndichiyani? After all sankapanganso maphunziro apolitics. Tisamangoona mbali imodzi.Chasowanso naye anaonjeza kutha mantha.

  2. Inu muli ndi umboni wanji woti Robert Chasowa anaphedwa ndi regime ya DPP???? Pena pake muzikhala ndima reason.You need to go deeper with your investigation if you are political activist concerning death of Chasowa chifukwa nkhani yophana pena pake ndiyovuta just imagine ifa ya Issah Njauju ikuvuta kufufuza bwinobwino kuti anaphedwa ndindani!

  3. @Bright , r u abroad or ur in Malawi?? Ithnk szochta kukamba kt Chasowa killd undr Dpp regime coz u cn c hw dis cases iz handled,till nw no bg dhilu at o,iz dat fair Mr Bright

  4. @Shadreck,it doesnt rily matr eithr ndiwe mwana wa xul or nt coz nzeru tmasana evn alito kid cn guid u there4 Chasowa sanalakwse coz h woz demonstratn wrong doings dat Dpp regm dd

 104. Who will reject the president? Chasowa’s frnds? Was he a freedom fighter or a politician or an opportunist? What the guy did to the Malawi nation? Plz remind me!

  1. stupid plus your family,what dd u want him to do ? then u ll kill all malawians.If u r a good killer,then kill all thieves who stole 577bn frm 2009 to 2013.We are crying fr Chasowa bcz he was a citizen and had right to live.

  2. stupid plus your family,what dd u want him to do ? then u ll kill all malawians.If u r a good killer,then kill all thieves who stole 577bn frm 2009 to 2013.We are crying fr Chasowa bcz he was a citizen and had right to live.

 105. You Black Moses, Robert Chasowa (RIP) And Mukhito, Were Against The Demostrations That Claim The Life Of 22 Inoccent People. You Were Paid For Taking Court Injuction As Concerned Citizen. It Was Like Your Job. So Dont Take Us To Fight Your Gains. Memories Are Still Fresh, We Lost 22 Inoccents People Becoz Of Your Childish Character. Unless You Address Us The Youth.

Comments are closed.