![hiv-ribbon](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2016/01/hiv-ribbon-235x176.jpg)
Mauthenga ena abodza akuika pa chiopsezo miyoyo ya anthu omwe ali ndi HIV — yatero NAC
Bungwe la National Aids Commission (NAC) ladandaula ndi kukhudzidwa ndi mauthenga ochuluka komanso malonda okhudzana ndi machiritso a HIV ndi Edzi omwe akumafalitsidwa kwambiri. Chikalata chomwe bungweli lalemba mosogozedwa ndi mkulu wake Betreace Lydia Matanje… ...