Tulani pansi – alangizi a Mutharika auzidwa kamba kobisa matenda a Tate wa dziko lino
Alangizi a mtsogoleri wa dziko lino alamulidwa kuti atule pansi udindo wawo ati chifukwa akhala akubisa matenda a mtsogoleri wa dziko linoyu.
Izi zanenedwa ndi mtsogoleri wa chipani cha Umodzi a John Chisi.
A Chisi ati alangizi a mtsogoleriyu akumulangiza kuti azipanga zinthu zolakwika zomwe zina mwa izo ndi kubisa matenda amene akuoneka kuti avuta mtsogoleriyu.

“Ngakhale ali mtsogoleri wa DPP, iyeyu ndi mtsogoleri wa dziko linonso,” anatero a Chisi. “A Malawi ayenela kudziwa za umoyo wa mtsogoleri wawo, osati kunamizidwa iyayi.”
A Chisi analankhulaponso pa ndemanga zimene wathila mtsogoleri wa zipani zotsutsa mu nyumba ya malamulo amene alinso mtsogoleri wa Kongelesi a Lazarus Chakwera amene pamodzi ndi a Uladi Mussa, mtsogoleri wa chipani cha Peoples’, amati a Mutharika atule pansi udindo.
“Tiyeni titsogoze mapemphero kwa mtsogoleri wathu, tisakhale ndi dyera pa udindo,” anatero a Chisi.
A Mutharika anafika mu dziko muno lamulungu akuoneka odwala. Iwo amakanika kugwiritsa ntchito dzanja lawo la kumanja zimene zinatsimikizila anthu ambiri kuti mkuluyi ali mdziko la Amereka anadzela kuchipatala.
260 thoughts on “Tulani pansi – alangizi a Mutharika auzidwa kamba kobisa matenda a Tate wa dziko lino”
Comments are closed.

UP fire!!!!!
Koma panopa ali kuti? Nanga akupezako bwanji? Kodi papeza athuwa akukamba zambili wena akuti wa mwalila wena akuti amalawi kukonda akazi tikachoka kwathu kupita kwawena sitifuna kupotoloka kodi akulowa chinawavuta ndichiyani?
Kkk Masiku ano , zaphweka! Zokwera, zachuluka “ndi mchaka achule akumaziwa . Chifukwa chilinchonse chikutenga mphavu , komwe kuli achule
Atule udindo Pasi. ife ndamene tiyeneleka kumadziwa chilungamo monga tinasankha tokha ngat mutibitse ife nde itiyo imeneyo
Up 2019
sosendizachabe zimenezi ngachitike tizirandire koma akakhara kuti wamwarira tivomerezesikuyamba kuti president afe paribe voto bora atiuze chirungamo chammene ariribasi osatikubisako atakharakutiadafatiyamikirapakutisitikumufuna chifukwadziko ramukanika afe basi tiribenayentchito afe ndithu ife tikondwa basi
àmene ánapangà nyimbo yafuko lathu anqlingalira,dalisani mw “izi njára,nthenda kmanso nsanje apa pansanje mulungu ayikepo dzànja chonde Amen
osatangwanika anthuni chija ndi robot
Àmipingo nthawi ya vote mumapempera kti mavote ayende bwno,vula ikapanda kugwa mumapanga chimozimozi nankuĺu akadwala simutero bwanji ollo titasi ntha kngati siziyande basi mulungu adalinse malawi
t
Kwatsalaku tingoonda nazo izi.ngati ndizoona timvera kwa mwiniwakeyo alengeza.
WHY CAN’T U TELL D NATION YOURSELF IF U KNOW ALL ABOUT DE PREDIDENT’S HEALTH RATHER THAN FORCING SOMEONE TO RESIGN IF U HAVE D GUTS
Ine ndakwiya heavy
Had it been kuti anatiuza that my no1. Worker is sick i could have left him in the states kuti alandire treatment yokwanira. Panopa tingoyang,ana patsogolo, not zotula pansi udindozo, president wathu wokonzamiseu uyu.
Inu mufuna kuziwa mutani? muli ndichani? kt mungamutengere ku hospa?
POOR REASONING DEMONSTRATED. IN A POLITICAL WORLD, LET’S LEARN TO BE CRITICAL WHAT SOME TINGS LIKE WHAT HAPPENED WITH US ARISE. THERE WAS NOTHING WRONG….
Kkkkkkkkkkkkkkk Achisi inu mukadwala amadziwa ndani?Sibwino kukhala ngati anzeru pa vuto la nzanu moto umamka komwe kwasala thengo.
Kkkkkk koma kumalawi umbawi siuzanta
Palibe akubisa matenda aliyese akuziwa kuti munthu akudwala mufuna muonere chani ?osamakadwazika ambuyanu kumudzi kwanu apa muli buzy ndi matenda ayinyake
UTULE PANSI NDIWE WA NYANSITIMES,NTHUTUMBA YA CHABE CHABE IWE
Ndicgikhalidwe
Si njanji ndimunthu ameneo or mubise taziwabe