CHRR yauza a Chakwera kuti achepetse kuyendayenda

Bungwe lomenyera ufulu la Center for Human Rights and Rehabilitation (CHRR) lalangiza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti achite kaye tchuthi cha maulendo awo ponena kuti ndalama zaboma zankhankhani zikusakazidwa. Izi ndimalingana ndi mkulu wa bungweli a Michael Kaiyatsa omwe amayankhula ndi imodzi mwa mawailesi mdziko muno ndipo anati potengera ndim’mene chuma chadziko … Continue reading CHRR yauza a Chakwera kuti achepetse kuyendayenda