
Mu Meyi tikuchotsa a Chilima osati kusintha boma – Uladi Musa
Yemwe ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cholamula cha Democratic Progressive Party (DPP) mchigawo chapakati a Uladi Mussa ati chisankho chikubwera mwezi wa mawachi sichoti anthu asinthe mtsogoleri wadziko koma ndichoti dziko lino lichotse pa… ...