Nduna yakale ya za masewero mu ulamuliro wachipani cha UDF yamwalira
Nduna yakale ya za masewero mu ulamuliro wachipani cha United Democratic Front (UDF) a Moses Dossi yamwalira. Mwana wamalemuwa Susan wati a Dossi amwalira kuchipatala cha Blantyre Adventist kucha kwa Lachinayi ali ndi zaka 70… ...