
A Ngalande adasiya kutilabadira – adandaula anthu a kwa Kachenga
Anthu okhala m'dera la mfumu yaikulu Kachenga m'boma la Balaka ati ndi okhumudwa ndi phungu wa nyumba ya malamulo wa m'dera la kumpoto m'boma la Balaka a Tony Ngalande ati kaamba kakuti adasiya kuwalabadira mu… ...