Tay Grin-Chipapa

Tay Grin abweza moto

Mfumu ya zinyau Limbani Kalilani imene imatchuka ndi dzina lodyera loti Tay Grin yakwera pa chulu ndikunena mokweza kuti anthu abalankhula chifukwa za iyo zinayera kale. Tay Grin ndiotchuka pa mayimbidwe mu zamba zosiyanasiyana, choncho… ...