A Suleman mubwere mudzafokoze chifukwa chomwe munadziwitsira dziko kuti ku SFFRFM kulibe feteleza – Hara
Sipikala wa Nyumba ya Malamulo a Catherine Gotani Hara wapereka masiku asanu ndi awiri kwa Phungu wa Blantyre City South East a Sameer Suleman, kuti afotokoze chifukwa chomwe anapitila ku nkhokwe za feteleza za SFFRFM… ...