
Osamadikula mu tchalichi mukamavina — Bishopu wachenjeza a Katolika
A Katolika awachenjeza kuti asamadikule mu tchalichi chifukwa kavinidwe kotero kangathe kupangitsa kuti akhristu anzawo achimwe. Bishopu wa ku Ndola a Benjamin Phiri ati ndi okhudzidwa ndi m'mene anthu amavinila mu tchalichi pa nthawi ya… ...