Inu, ati musiye kutukwana pa Facebook
Saliokha a Peter. Patangidutsa tsiku mtsogoleri wa dziko lino ataopseza kuti boma lake linjata anthu onse osamalika pa Facebook, naye sipikala wa nyumba ya malamulo walangiza a Malawi kuti pa Facebook sipotukwanila. Malingana ndi a… ...