
“Ndinyasi”: Sindikudzapikisana nawo pa chisankho cha 2025 — watero Bushiri
…ati iwo si asataniki …ati iwo sanayambane ndi Mlaka Mtsogoleri wa mpingo wa ECG Jesus Nation mneneri Shepherd Bushiri wanenetsa kuti iye siwandale ndipo wati sakudzapikisana nawo pa mpando wa utsogoleri wadziko pa chisankho cha… ...