Papa wa mathanyula

Papa Francis yemwe ndi mkulu wa mpingo wa Katolika pa dziko lapansi wati anthu ogonana amuna kapena akazi okhaokha ali ndi ufulu omanga banja  ndipo mpingo wa Katolika ukuyenera kuvomereza ma ukwati otere. A Papa… ...